A MCP BWANJI MWAPANGA MSONKHANO MASIKU OLIRA ASANATHE ? IVANI YANKHO LA MCP I

  Рет қаралды 21,463

DZIWE TV

DZIWE TV

3 күн бұрын

Пікірлер: 80
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk 2 күн бұрын
Koma tili kumalilo or ku chisangalalo koma Amalawi tinalozedwa chani malilo aja apanga expare basi china chiziti pa 10ma demo ayi
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s 2 күн бұрын
Ngati mukufuna chithandizo mupangeni Chithyolayo ali ndindama akupatsani anthu oputsa kwambiri
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 күн бұрын
Mcp ndichipani choti ambiri zeru ndizochepa amapanga zinthu mosaganiza okha ananena tilile kaye maliro lero akupangisa musonkhano masiku asanakwane 21 days.pali zeru pamenepo anthu akamawazuzura muva amangidwe
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 2 күн бұрын
Kulila mwasiya mmmm munapadi chilima kathawi komweka
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb Күн бұрын
Some of the people who were together with SKC ku Dpp, adachoka nawo ku Dpp following SKC... That means,, ma vote ose omwe onabwela ndi SKC ku tonse alliance, will definitely go back to Dpp... I think there is a great chance yoti Dpp itha kudzalowaso mm'boma Dpp, afford and UTM atadzapanga alliance, MCP can not withstand that. Olo atatani atatani (My ideology)
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 2 күн бұрын
Enanu mukamati mudzawina akukunamizani ndani ganizanu kawili njira zowinira zake ziti ndipo campaign mukapangira kuti nokha simukuona kapena mudzikavota ka 10 times aliyaense Kaya tidikire amalawi ayankhure ndivote yawo basi zinazo pambuyo
@user-yk9ib1bg2b
@user-yk9ib1bg2b 2 күн бұрын
Ukapha munthu olo unene zabwino koma ngati unapha, zonse zimene umachita ndi zomwe zimaonetsa kuti ndiwe wakupha Ndi momwe zililionso ndi chakwera, Zimene akupangazi zikuulura kuti ndithu mwazi wa anthu aja akiwavuta Musavukatu mungoti phee
@MisheckAselo
@MisheckAselo 2 күн бұрын
Panyapanu nonse MCP mudapha chilima, mukuona ngati malawi wa 1960 mitumbo yanu
@pempheronawani4627
@pempheronawani4627 Күн бұрын
😂😂😂😂 koma adha
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 күн бұрын
MCP NDI CHIPANI CHONYASA NDIYE ENA NKUMAIKIRA KUMBUYO MCP, AWA ZA MAKILO A CHILIMA ALIBENAZO CHIFUKWA CHOMWE ANKAFUNA CHINATHEKA , NDIYE IWE UKUDANA NDI MADEMO BWANJI SUKUDANA NDI NSOKGANO APANGITSA A MCP? AKUGULA ETI
@user-xe5lb4uf3n
@user-xe5lb4uf3n 2 күн бұрын
Achite msonkhano panopa ziri bwino akwanirisa zofuna zawo Chipani chakupha ichi.
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 күн бұрын
MCP ndi tizipani tanu tamapanjati ndizosiyana ndiye dzinamizanani kwanuko MCP ndi pagalaundi
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 күн бұрын
Agalu anzelure okupha mwasiyano kulira afiti inu maso anu ali pandalama afisi
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Күн бұрын
Achule adpp kod inu kuntchito simapita vichule ivi ainu mwina mwayiwala kuti mnapha njaunju robert chasowa atambala ndi banja lawo bwanji adpp simyankhulapo mmene afela bingu tikanena kuti anzathu mmaziwa kupha anthu abingu mnapha nopha nokha ndiye chifukwa chake simkunenapo eti zisillu inu
@GoodsonLindani-gf8pn
@GoodsonLindani-gf8pn Күн бұрын
Iweyo uzimuyankha ndani ,ndiwe opanda nzeru eti,ooh paja MCP imapha magazi akukuendani mmutu.koma mkazi wa chilima sakukunvesani chisoni.
@JamesIngeni-ku3qj
@JamesIngeni-ku3qj 2 күн бұрын
Ndachewa awa school nje koma kuvala nyau forgive them kupanga zithu ngat ana
@ClementMutala
@ClementMutala Күн бұрын
This is a party with great thinkers. I love this party
@SameKaposa
@SameKaposa Күн бұрын
😂😂Akutuma
@AndrewSimakweli
@AndrewSimakweli 2 күн бұрын
Makape awa, chifukwa olira sananthe
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Күн бұрын
Ngwilidzano wa bambo ako mesa chilima munapha 😢😢😢 mavuzi anu ifa ya chilima inandikwana
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y Күн бұрын
Palibe cha mzeruuu apaa. Ndipo mukuoneka kuti za malirozi sizikukukhudzani ayi. Apezeka bwanji late Chilima still alibe ndi nsapato komaso otemedwaaa. Aaaaaaa ubwino wake Mulungu anali komweko adaonaaa. Pa Limpompo ija akuti adatemema ngochoka ku Mchesi ati who is who.
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 2 күн бұрын
Members and leaders of Malawian political parties must undergo an intensive training focused on Philanthropy and Patriotism the only portal to genuine democracy and solidarity in Malawi or invective will be the order of the 2025 National Elections.
@godrickmapepu2754
@godrickmapepu2754 2 күн бұрын
MCP chipani chowononga
@mussamapira801
@mussamapira801 Күн бұрын
MCP chipani chakupha anthu opanda chisoni Inu mulungu akulangani 😢😢😢😢😢
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 Күн бұрын
The murder party woyeeeee wakupha wakupha, akupha woooo mukala mulira azibale wanu nyini za Manu,sindinu amene mwalirisa A Malawi wonse aja inuyo Kuno kuma Ngoni musa za tiwerengerenso dzi achewa ambuli nonse nyero za Manu
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 2 күн бұрын
Mudamputa nchakazulu kumangoni
@ClementMutala
@ClementMutala Күн бұрын
Ndi zoonadi tili mu 21 days of mourning koma pamaliro pamakhalapo zolengeza sikuti anthu amangolira osapanga zina ndi zina pa Siwa ayi kumeneko nkusazindikira kapena kuti anthu mukuliwetsa ndale pamaliro
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e Күн бұрын
Inu kukuyenelan nd ku opposition kokuja nzeru zikuchepa zoyendesela dziko
@user-ev4or2kg4z
@user-ev4or2kg4z Күн бұрын
Osaiwala a Malawi paja adapha chilima kuti alamilletso mpaka 2030
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda 21 сағат бұрын
Kuvera za MCP ndi manyi okhaokha onyera chakwela
@frankiejackzy9862
@frankiejackzy9862 Күн бұрын
Chipani Chakupha ichi moti pano aliyense kuchipani kwaoko akuopa kukhala vice President wa Chakwera kuopa kuti Aphedwa mmene adaphedwera Sidik Mia komanso Saulos Chilima....mizimu ya anthu amenewa ikukanthani simudati Mpaka kuphanso Ralph Kasambara
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Күн бұрын
Mcp sizatheka ai ndinanena ine osavotela mcp ai onani lero tikulira😢
@andrewmazunda3846
@andrewmazunda3846 2 күн бұрын
2025 tili limodzi. Rest well SKC
@ClementMutala
@ClementMutala Күн бұрын
Munthu ukafika potukwana zimadonyeza kuti ulibe mfundo komanso ndiwe ofooka mkaganizodwe. Chipani Cha mcp sichili Cha gawo limodzi ayi ngati tizipani tinati. Mulira chaka chamawa mbuzi inu
@hendresonsande5156
@hendresonsande5156 Күн бұрын
Ife ndiye titangoika malilo basi tinabwelelaso ku DPP chifukwa yemwe anatibwelesa ku tonse alliance anatisiya ndiye muona Kuti mupanga bwanji
@GibsonBakha
@GibsonBakha 19 сағат бұрын
Mukamati acewandizitsilu mukavotanokha alomwenu khalambayanuyo kkkk
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Күн бұрын
Apatu ndiumboni oti chilima anamupha ndi MCP ndi chakwela nsono kulila mumanena kuja ndikuti apa otsasintha bwanji nsonkhonowo kkkkk KOMATU MWADZI WAMUNTHU SUPITA PACHABE APA KULI MASEWELO KUMWALULA KWA CHILIMA N MAFUMU KUKAPETPESA MALILO KWA CHAKWELA POBWELA APASIDWA NDALAMA ADZIBUTSA KUPITASO KOPEPETSA POBWELAKO ATENGA MA MILION KKKK kodi inuyo ndiane mukupepetsa pena chakwela akukupepetsani inu iiii chenjelani Mafumu ndi adzibutsa NDALAMA ZA MCP NDI CHAKWELA ZAMAGADZI IDZI MUKUFA NADZO
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Күн бұрын
Mmene mnaphela arodweel mnyenyembe agoodwell gondwe robert chasowa njaunju albiino ndi ena basi mkuganina kuti wina ali yese ali ngati inu adpp satanic inu
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Күн бұрын
Kodi mwalira kale maliro kapena bwanji ndi yankheni ndi sanakuwudzeni kuti nose machende anu
@RajMass-nr3uy
@RajMass-nr3uy 2 күн бұрын
Ndipo machende apite kwa anyamata opanda dzelu amene akusatila chipani chimenechi machende awo pamodzi ndi machende abambo awo fukwa anakoza umuna ofoila mxm
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 күн бұрын
Only fools will joun you...experts in killing...point of collection:MCP is not mighty😅
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 2 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 inu apanga musokhano wachani samalani kunyanja kuribe magazi akufuna magazi chakwera uyo nikachivwati kake
@DaudJulius-hz8uy
@DaudJulius-hz8uy Күн бұрын
Leya chimalayacho chitsilu cheni cheni azingokunyenga ku mcp ko mbuzi
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 Күн бұрын
Lea Malekano ku MCP kulowa cha mutu
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 күн бұрын
To west date for this monster 👻 👽
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Күн бұрын
MCP Mwatikwana Chakwela u mast go Galu
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI Күн бұрын
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 Күн бұрын
Kodi 21 days yakwana kale eti koma MCP ndi yakuphadi
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda 21 сағат бұрын
Chakwela kukamwa ngati nyini ya hule
@WANANGWAMoyo-mh5cq
@WANANGWAMoyo-mh5cq 2 күн бұрын
Inu moti simudziwa kut MCP ndi Ng'ona?
@StewartGoma
@StewartGoma Күн бұрын
Amsukwa ndiwe opusa
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda 21 сағат бұрын
Mudaphatso sidiki mia afiti inu chilima nayo mwaphaso
@MichaelJannah-hn9qv
@MichaelJannah-hn9qv 2 күн бұрын
Tikumana 2025 Anyani inu
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Күн бұрын
Nsonkhano wama criminal's
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 күн бұрын
Ubwino wake nonse mmapanga phokoso apa sindinu a MCP ndipo simunabvotelopo MCP mwatelo or mutukwane bwanj MCP 2025 ndi boma kale mukhaula
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 2 күн бұрын
Tiye uko nyani lwe chitsiru nose ndi MCp Yako fiti lnu
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 2 күн бұрын
Mbava Za oyipa inu
@RabeccaMkandawire-i9j
@RabeccaMkandawire-i9j Күн бұрын
Mcp mmmm amene adzavotere nde wamisalatu
@FrankAbraham-e9o
@FrankAbraham-e9o Күн бұрын
MCP is my vote
@user-hk2ow8ey2g
@user-hk2ow8ey2g 2 күн бұрын
Kkkkkkk zisilu m😂😅😅😅
@PreciousKARINGANIZA
@PreciousKARINGANIZA Күн бұрын
Bava zokumpha chilima
@VishonVishon-sj4cx
@VishonVishon-sj4cx 2 күн бұрын
Koma sondayo akudyanao ndalamazo wawonda bwanji amenei angafunile amalawi onenepa zabwino amenei
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g Күн бұрын
❤❤❤❤
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i 2 күн бұрын
Nkhandwe😅😅😅😅
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq Күн бұрын
Mbolo dzanu nose a mcp
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 2 күн бұрын
A kupha inu
@HastingsShaba
@HastingsShaba Күн бұрын
<a href="#" class="seekto" data-time="947">15:47</a> <a href="#" class="seekto" data-time="947">15:47</a> 😅😅 <a href="#" class="seekto" data-time="947">15:47</a> <a href="#" class="seekto" data-time="947">15:47</a> <a href="#" class="seekto" data-time="947">15:47</a> <a href="#" class="seekto" data-time="947">15:47</a>
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s 2 күн бұрын
AGWAPE INU
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi Күн бұрын
Afiti a mcp
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 күн бұрын
Afiti awa the don't care about VP wanthu😢😢
@user-ys4lt4ev8z
@user-ys4lt4ev8z 2 күн бұрын
Satana inu mcp
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 күн бұрын
Chipani cha fuko osati chakubanja ai MCP 2025 boma kale cadet amwalila ndithu
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Күн бұрын
Tizikuyankhani sopano chifukwa ndinu achule mwaiwala ku dpp ndi chipani chazikwanje komaso maliro achilima tikaganiza kwambirili achilima mnapha ndinuyo chifukwa chot chilima asasunge mnayamba kutulusa maodiyo kuti ndimwayi wanu adpp kumwalira kwachima ndiye kuti simagona naye tulo zisilu inu adpp mkukhala ngati ndinu wamyaya foseki
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 2 күн бұрын
Iam a floating voter.My fellow Malawians if you don't know nothing about the political game of life,MCP once again will be a winner only if you avoid regionalism when selecting leaders.Donot overtake Dr.Chakwera's position or you will fail with distinction in 2025 National Elections
@EmmanuelNkosi-ts8bn
@EmmanuelNkosi-ts8bn Күн бұрын
Ku Malawi timangopanga ndale from January to December, za ziiiii
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 2 күн бұрын
Pafikapa timati misala yafika pachiweniweni. Eeeeeeeeeee anthu amenewa Ali ndi umunthu .
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Күн бұрын
Kodi mwalira kale maliro kapena bwanji ndi yankheni ndi sanakuwudzeni kuti nose machende anu
Kenya on the Brink | A roundtable interview with President William Ruto {Full}
1:53:10
ОСКАР ИСПОРТИЛ ДЖОНИ ЖИЗНЬ 😢 @lenta_com
01:01
THEY WANTED TO TAKE ALL HIS GOODIES 🍫🥤🍟😂
00:17
OKUNJATA
Рет қаралды 9 МЛН
DO YOU HAVE FRIENDS LIKE THIS?
00:17
dednahype
Рет қаралды 33 МЛН
Nawakwi Speaks On National Issues Live on Radio
1:45:20
J Cool
Рет қаралды 214
HOT CURRENT  LERO ACHAKWERA MUGANIZE BWINO MCP |
53:40
DZIWE TV
Рет қаралды 12 М.
NKHANI YOMWE YATIPEZA KUMENE |
4:02
DZIWE TV
Рет қаралды 9 М.
BON KALINDO LERO NDE WANG'ALURA KWAMBIRI |
15:00
DZIWE TV
Рет қаралды 23 М.
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Jimmy
Рет қаралды 85 М.
LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA
41:25
Club Junta
Рет қаралды 29 М.
ОСКАР ИСПОРТИЛ ДЖОНИ ЖИЗНЬ 😢 @lenta_com
01:01