wankulu ndani? mu video iyi tikufotokodza za chinkulilano chomwe chilipo pazokhuza u legend wa lulu
Пікірлер: 172
@wrights1732 Жыл бұрын
Doc anavaya!!! lets give credit were its due at the same time Lulu is also a good artist
@marthachapepa2692 Жыл бұрын
According to my decision, I SALUTE Lulu he is the best humble intertainer in music industry, he is a man who accepts the defeat without talking too much, but he also receives FAVOURS from God depending on his behavior. You are really a legend.
@chrismatekenya6084 Жыл бұрын
CORRECT
@beformw Жыл бұрын
To be honest Namadingo ndi moto wamalasha olo mutatani sizikutigwedeza Namadingo umakwana Zodekha zawozo kwawo konko
@Esther-jg9iv Жыл бұрын
Namadingo has the best smooth/silk voice, no doubt about it. The guy has the confidence too
@jenojames3813 Жыл бұрын
pankhani yozichepetsa Lulu ndi number one, koma tikanena za nyimbo Namadingo ndi international artist 💪💪🎶
@collinsassenga3711 Жыл бұрын
Anzathu maiko ena oyimba amakondana ndicholinga chopititsa patsogolo luso loimba , amalawi tigwire manja, lulu ndi namadingo onse ndi superstar, ndi ofunika kumapanga colalation ndi anthu amaiko akunja otshuka osati kumalimba.
@preciouschifundo9390 Жыл бұрын
Lulu is the best.... He is humble in everything just like Sam smacks....... Keep it up Lulu
@jonathanchimugwabu8162 Жыл бұрын
Lulu is the best artist namadingo he is still young in music industry
@ThoccoMkhwayi11 ай бұрын
My favorite musician Lulu very humble man
@Malani41 Жыл бұрын
They are both legends but not historical or generational legends yet. I agree with Namadingo on this. These are two very talented musicians but you have to be real when you come to the definition of legend. Legend transcends and encompasses decades of preeminent work and name recognition in music industry! It’s stupid for them to even argue over this. They don’t even begin to be considered “living or generational legends” at this moment!
@jimmyalisen5772 Жыл бұрын
Mmmm NAMADINGO
@tingamasi106 Жыл бұрын
Mukudziwa kuti lulu adayamba kuimba liti? If u say skeffa ndi legend why not lulu? Lulu anayamba kuimba kalekale ngati achina skeffa
@richardchimatiro56078 ай бұрын
iweyo ukukamba zoona, this was wat doc meant not what the fanz were insinuating
@lastonkandiyado4526 Жыл бұрын
Lulu he's legend ever we can't compare him and namadingo
@kingbutao2023 Жыл бұрын
How can you copare Subaru and BMW.... Team Lulu, as far as I understand panopa I like Namadingo, koma Lulu it's a greatest of all time. Lulu ndi bwana pamene Namadingo ndi mwana
@gracioussinoya2850 Жыл бұрын
Mau amzeru
@richardchimatiro56078 ай бұрын
aaaaaaaaaaa Namadingo amanama ngati. infact amanena zoona , Lulu si legend is in making, kukhala legend sichifukwa choti amaziwika nde ndi legend
@chisomomasakatira5080 Жыл бұрын
Lulu is the legend ✨
@user-gb8hf2gu1j3 ай бұрын
Doc anavayaa!!!
@williambotha5283 Жыл бұрын
Doc tsimngayerekedze ndi Lulu Doc anavaya
@dezideriojere7823 Жыл бұрын
I love both of them, Doc anavaya
@SamuelChiotchaАй бұрын
Lulu is the best❤❤❤
@emmanuelkhamula9886 Жыл бұрын
Team Doc Namadingo even in my computer/phone you can't find music ya Lulu
@bobkenneth2947 Жыл бұрын
My Brother Namadingo be Humble please,I'm one of your fans so please don't disappoint us
@trizahkafuwa3541 Жыл бұрын
Team Lulu since day munthu ozichepetsa team Capetown 🎉
@rajabtambula3769 Жыл бұрын
Your presentation is partial, you're leading us to judge that Lulu is best
@user-di2pq5cy8q10 ай бұрын
Lulu he's the best regards singer namadingo his nothing in industry
@antonychika15 Жыл бұрын
pa Lulu timacedwapo ife MACHINE
@taylorbanda51545 ай бұрын
Lulu ndi number one pa zonse pa ine amakwana
@manuelmakonda2324 Жыл бұрын
Lulu number 1 than namadingo
@MikeMbewe-mb9it4 ай бұрын
Lulu ndi dolo mbali zose mwachidure ndiodekha Lulu thanks for that
@swadickbasheer3665 Жыл бұрын
Lulu anakhoza ndi machine omanga ndi mawaya
@emmanuelnamukhoyo4790 Жыл бұрын
Lulu is the legend
@BornMandala-rz1dk10 ай бұрын
Lulu it's my artistic
@giversonkaselo6139 Жыл бұрын
Lulu Nde Dolo man,enawo angochulutsa zo lubwa lubwa
@lithembajujwana5577 Жыл бұрын
Lulu on point,💪🏽💪🏽🔥🔥
@janenkhoma6447 Жыл бұрын
Kwaine lulu namuziwa ndili mfana nyimbo zake ndiye doc eeee basi zaziko izi
@daudmasikam Жыл бұрын
We love lulu
@goodsonchimberenga5737 Жыл бұрын
Lulu ndi akatundu pamaimbidwe sitingafanizire ndi mthumbidwa multi Namadingoyo💪💪💪💪
@vanessachimbayo1247 Жыл бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@user-zu8jq5co1k Жыл бұрын
Onse ndi madolo, Patience amatha Lulu nso amatha, ndipo palibepo udani, koma anthu mumakokomeza nkhani.
@mervinmorris7754 Жыл бұрын
Lulu number one
@clementchimela11 ай бұрын
Namadingo he's legend ever we can't comparer him and lulu🎉🎉😂
@dytonwonderful83826 ай бұрын
Lulu❤
@azunguauskay4903 Жыл бұрын
Udolo amakuwona ndi anthu osati wekha kunena monveka bwino dolo ndi Lulu
@chifundonkhoma3642 Жыл бұрын
Legend suzimveka wekha, amaona okha mmene udayigwirira ntchito anthu, ndiye lulu ndi legend musamumvere Dr Namadingo, kumene akupangako ndikupereka ulemu kwa lulu chifukwa akudziwa kuti ndi dolo koma Ali pa denial chabe 😃😃😃😃
@zaqueuadelinomoiseskanjaut5284 Жыл бұрын
Ku mbali ya mayimbidwe Dr Namadingo ali kutali kwambiri kwakuti tingadzayambe kumuyerekeze ndi Lulu chifukwa Lulu ndi machine
@tingoalex6370 Жыл бұрын
Lulu ndi best all time
@noel1886 Жыл бұрын
Mayimbidwe lulu hi Is the legend
@richardchimatiro56078 ай бұрын
Doc Anavaya,
@chawanangwamkandawire5850 Жыл бұрын
Kunena kuti wina satha kuyimba pakati pa Lulu ndi petience nkuzi namiza, ose amath kwambiri. Inde ndi zowona kuti petience ali ndi advantage yotha marketing kuposa mzake koma limenelo so vuto lomwe anthu kuno ku Malawi alinalo. Chikusiyana kwambir pa awiriwa ndi personality, Namadingo ali ndi kuzimva, anthu amudziwa lero pamene watchuka ndi secular koma ndi mene aliri sikuti anasintha, pamene Lulu naye ndi wo dekha kuyambira ndi kale. Kuzipopa kwa Namadingo Kuma tulutsa nsanje mwa anthu ndipo olo atapereka professional advice kwa artists wina imawoneka ngati mwano maso mwa ma fans.
@KissDaud-zw3jy3 ай бұрын
Lulu ndi star mapeto adolo
@lameckkanga4090 Жыл бұрын
Lulu ndi fire 🔥🔥🔥
@fannylaudoni973 Жыл бұрын
Lulu ndi wa one Malawi music 🎵
@martinkapito9418 Жыл бұрын
Namadingo ukaoneka Ngati Muthu wabwino Koma ndiwe chisiru ndipo ulibe nzeru iwe ungamupose lulu maimbidwe Mutu wako suyenda bwino eti ungamuphunzitse lulu umadziwa chani ulemu ndiofunika wamva umakhala ukunyoza anthu ena iwe ndindani mbuzi yamunthu iwe eti auncle lulu timakukondani mumatha kuimba musakhumudwe ndi namadingo alibe nzeru kucokera Kuno kuthyolo thekerani fifity miles lulu ndi otchuka zedi tsogolo jdiliona ndilowala ND lotheka
@damzyjohn6188 Жыл бұрын
Lulu ❤️
@sir-kalekaboy6126 Жыл бұрын
Doc & Lulu they are not enemies but we try to create it. Doc & Lulu onsewa ndi ma dolo basi
@lameckkanga4090 Жыл бұрын
Bodza Lulu ndi fire 🔥🔥🔥 🚒
@sir-kalekaboy6126 Жыл бұрын
@@lameckkanga4090 that’s your opinion boss. Unfortunately I don’t listen to their music 🎶 at all.
@abdullahgeorgemdoka Жыл бұрын
Lulu ndi legend, Anamadingo olo mau ochita kubera kwa Lulu nchifukwa amanena kuti aphunzira zambiri kwa Lulu
@hucklyrajabu7137 Жыл бұрын
Lulu ndi machine
@frankkennedy8088 Жыл бұрын
Paziko lapasi parib dolo
@frackidi2566 Жыл бұрын
Lulu 🤴
@user-bv3px8ie5n Жыл бұрын
Ndi munthu oipa amazitgenga ngati ndi ozindikira koma palibe ,lulu ndi munthu wofasa, end mulungu azmudalitsa Lulu
@ChipiriloMchimphangwe6 ай бұрын
Namadingo akuyenera kulemba mawu woti leka Kwa Lulu chifukwa chifukwa ndipame alipo iye
@gwendolenegeraldine2215 Жыл бұрын
dolo ndi lulu palibe anagayime kunena za lulu ndiozichepesa odekha sindinamumvelepo akukangana ndi ndi anzake .thats a legend
@chrismatekenya6084 Жыл бұрын
LULU , He is LEGEND!!!!
@macdonard3896 Жыл бұрын
Doc international artist 🔥🔥
@wilsonsamson8715 Жыл бұрын
Lulu amatha doco azichepetse basi
@medsonkesale7962 Жыл бұрын
Of course Lulu ndi legend koma Namadingo ndi International Artist.
@ganizaniyonam5041 Жыл бұрын
International ya Zambia?
@fishanngwira3438 Жыл бұрын
International wakuti inu u think ku south africa amavela nyimbo za namadingo?
@AlfredMbungo12 күн бұрын
❤
@offiemsiska7622 Жыл бұрын
lulu ndi legends
@justinedamson8862 Жыл бұрын
Lulu ndi machine ❤❤
@hamdanmasuku4800 Жыл бұрын
Lulu ndioyimba wa luso namadingo kutali tali nd Lulu
@mimhossan8886 Жыл бұрын
Munthu kuimba nyimbo za anthu ena ndiye kuti kuziwa kapena kumakhala kusowa mfundo zopekera nyimbo?. Lulu ndi legend
@LusunguMsiskamwase-qh1jk Жыл бұрын
Aaaaaah inu ndiolephera inu basi mngokharira against aaaaaah zaziii Namandingo si level yanu,,, Lulu nayeso nd doro
@Malambia Жыл бұрын
Lulu he is legend
@enochkapaswiche-vm5bq Жыл бұрын
Thanks
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 Жыл бұрын
Komatu ndayiwona mochedwa iyi kodi mukankhilanji galimoto yosayenda Namadingo kusiya ya 1 kick Lulu?
@HAWAHANDRWE Жыл бұрын
Ine sindikonda nyimbo za namadingo ai km lulu munthu wamkulu komaso ndimafuna nditawonera interview yake zikomo kwambili sam mavintha ndimakunyadila potiziwutsa Khan za malawi
@sammalvitha Жыл бұрын
Thank you so much Hawah Tomorrow morning ndiponya another video imene mukhale ma interview a anthu awiri onsewa .. and i will give a shout out to you .... . 🤗🤗💕
@HAWAHANDRWE Жыл бұрын
@@sammalvitha Thacks so much Sam malvitha TV ndikhala ndikudikila zikomo
@blessingsmaulid8776 Жыл бұрын
Legend ndi Lulu
@ChiccoJelly-wp5wj8 ай бұрын
Lulu is the best than namadingo
@angelogerman8122 Жыл бұрын
Lulu is the best.
@Ndakonderedwa Жыл бұрын
Akulu akulu zomapanga compair zi muzipereka maudani kwa anthu aliense Ali ndi okonda wake. bwezi simunafuse fuso lakuti opambana ndindani maudani kunalibe
@ZungeniBanet11 күн бұрын
Ndi Lulu dolo
@frankchigana2467 Жыл бұрын
Namadingo sioyimba or ND driemo sangamache
@user-sq9ys1jq6o9 ай бұрын
Lulu amatha
@adijamajawa7744 Жыл бұрын
Dolo ndi lulu osati amenewo amangotithera data za ziii pano ndipo mnaleka ndiku danloder kumene 😂😂
@kell_dreamer293 Жыл бұрын
Onsewo ndima legend palibe zot winayo alibe khalidwe
@ZungeniBanet11 күн бұрын
Namandiko zakuziwa kuyimba
@hanafi4766 Жыл бұрын
Mu nkhani yoseyi kuyambila pa chiyambi mpakana pamathero olakwa ndi namadingoyu komaso mukafunsa za dolo PA awiliwa dolo ndi Lulu kusiyana kwa udolo wawo tsopano Lulu anadziwika chifukwa chopeka nyimbo zake pomwe namadingoyu wadziwika chifukwa choyimba nyimbo za anthu ena ine ndiye olo nyimbo imodzi yomwe ya namadingoyu sindimayidziwa nsaname koma pomunyoza Lulu sitingadabwe naye Tiana ta satanic ti ndichoncho timakhala tokula ntima ndiye usataniciwo
@christopherkagona7797 Жыл бұрын
Doc
@iqrajames2030 Жыл бұрын
Lulu ndi legend 🔥🐐🐐🙏
@muchasangambe Жыл бұрын
Lulu ndi one
@ismatandika Жыл бұрын
Clearly eni channel awa ndi a Lulu.
@user-qi6ku8js9p7 ай бұрын
Lulu ndidolo
@chancyjiwawo6574 Жыл бұрын
Lulu ndi Dolo!
@GodfreyChizenga-ou8dg Жыл бұрын
Iwenso ukulakhulawe ndie wamabodza
@AsemahleFutshane-id9wh10 ай бұрын
Lulu
@stevenevance7319 Жыл бұрын
Lulu ndi legend
@amzaayami2267 Жыл бұрын
Doro ndi Lulu
@frackidi2566 Жыл бұрын
Doro ndi lulu
@sammalvitha Жыл бұрын
Dzikomo poonera video iyi 👏👏❤️❤️ Chonde pangani subscribe 💕💕💕 Chitani like vide iyi💖💖💞
@shaibuali1435 Жыл бұрын
Ok
@samuelmwale1385 Жыл бұрын
U legend suudziveka wekha koma anthu , APA wina akudziveka u legend
@hajiwillard7623 Жыл бұрын
Lulu Alaways Is Humble Guy And I Never seen Guy Ĺike Lulu Iwe Namadingo Stop Insulting Lulu For Nothing Utaya Thawi Yako Pachabe
@christofagolden1595 Жыл бұрын
Lulu ndi dolo, Tsogolo, kumalembe eeee
@kennethsuliwa9712 Жыл бұрын
NDI LULU
@abdullahgeorgemdoka Жыл бұрын
Lulu ndiye oimba osati Namadingo .iyi si mbali yanu Anamadingo pangani zamalonda
@estherkamwendo7971 Жыл бұрын
Stop comparing them.
@caphyasibu501 Жыл бұрын
Kunena zoona Lulu ndi dolo
@theresazuze311 Жыл бұрын
Lulu ndi shasha
@wonganikaunda7704 Жыл бұрын
What I know is Doc anapita ma levels atali atali...koma kuzoyimba onse amatha