Guys tikufunika kulangizidwa mwapaderadera we Malawians😅
@mercymanda259811 ай бұрын
Just leave young boy alone I don't want to hear death for young musicians it break my heart may God bless Pop young
@EstherDebwe3 ай бұрын
Iwe ndy wangong'aluratu😂
@ezekielzaicokaira3567Ай бұрын
Exactly even to me
@user-yl7vn7qh6p11 ай бұрын
Achita bwino kukana komaso kubweretsa mitengo pa mbalambanda oyimba onse akumalawi atengerepo phunziro big up pop young
@user-ge5su6ex8k11 ай бұрын
❤❤❤❤
@AlfredMbungo12 күн бұрын
😅
@dj_simba-de_dancer_official11 ай бұрын
Well done pop young management enawa ndikakhalidwe kawo kokhomerera anzawo pa ndalama
@johnmakawa429511 ай бұрын
We need to pray hard for Pop young 🙏🙏
@Malambia11 ай бұрын
That's true oyimba akunja amapita ndi ma million kom ma local artists amakhomeleledwa kwambili anakakhala kuti ma local artists amapatsidwa ma million bwezi oyimba ambiri ali olemeta kom kupondelezana
@joemlelemba657211 ай бұрын
Amapita ndi ndalama coz ndi ma international artist, inuyo mutumize pop young yo ku zambia anthu akavinako? Tisamanamizidwe guys winau ndi udani wao basi , olo inuyo mukupanga wedding mungamuitane pop young? Si bolanso giboh Pearson,
@edokazika779811 ай бұрын
Alucius Banda osatimphelaso mwana uyu Chonde paja simuchedwa mwana akatchuka
@maxwellChitsulo11 ай бұрын
Well done pop ......... chilungamo wayankhula baai
@83kwak11 ай бұрын
You have open eyes for alot of Musians
@tomthompson442911 ай бұрын
Sam Malvitha, nkhan unayiyamba bwino, koma kumapetokonayi, usamakwere munthu, uzitisiya tizijaja tokha nkhan ,
@user-ut9ye7fk2s6 ай бұрын
Fire pop young keeping the price no worry big
@jameswajumpha679011 ай бұрын
Athu omwe timawaona ngat ndi athu olemekezeka ndi athu omwe amaononga zithu soder ndiwakhaza nkhaza yakabisila silungwe he is right
@Ngamanyachipapa305511 ай бұрын
Thanks alot Pop young
@83kwak11 ай бұрын
Freedom fighters its high time management take a stand well Pop Young team
People are going far 😢 please pop Young we are not ready to lose you stay away from him 😢
@jimmyalumando378511 ай бұрын
Mwanayu ashoshaaa zidaaaaaa zachabe uyuuu
@thomasgamah76411 ай бұрын
Ngati ku Malawi oimba akuvutika it's just because of Banda misomali kwambili.
@patrickchapitapita144611 ай бұрын
Mmmmm do you have evidence?
@thomasgamah76411 ай бұрын
Yes the evidence is arleady there just follow what is it on Calvin's page
@promisebanda878511 ай бұрын
Kalikose tikaona😮😊
@user-cq6tc1lh5v11 ай бұрын
Ndukuuzani
@JamesZiba11 ай бұрын
Popo Young osadzayimba ndi akulu akuluwa
@mmalecmz406211 ай бұрын
Amalawi tilimudima ndichifukwa chake enafe timabwelera kumbuyo, pop young komaso a silungwe ndawayamikila tikapita pa tanzania pompapa ma artist akunjoya kunkhan ya ma bookings koma kuno ayi
@user-zu9zh7du7p11 ай бұрын
Bwana soldier asamatelo
@MphatsoLuhanga11 ай бұрын
Well done pop young
@gospelmcandawire281711 ай бұрын
Big respect Mwatimasula
@EstherDebwe3 ай бұрын
Sam Malvitha unabwera iweyo
@successngoma11 ай бұрын
Thanks pop young
@user-nj5hc6jb7l11 ай бұрын
Soldier ndi mfiti period
@DJLUCKSTARMW8 ай бұрын
Please just leave him 😢 pop young
@brightmpombeza481611 ай бұрын
Palibe udani, don't bring unnecessary beef...
@browncoffee916411 ай бұрын
Pop young need security for this. Heavenly father the world is worse🙏🏽
@ErnestChanza9 ай бұрын
Pop young 🎉🎉
@user-gn8fi6ch3o9 ай бұрын
We need to pray hard for pop young
@user-rq6wu4vn4i11 ай бұрын
Km mulungu aliko otsandaula
@blessingsngosi734711 ай бұрын
Lucius Banda amalakwitsa. Asamadyele anzake masuku pamutu. Sulungwe anapanga bwino
@albertolchiphwanya380911 ай бұрын
Apa taphuzila ndithu
@Jayloudaud-xi5jh8 ай бұрын
Fact up
@bridgetchinseu395411 ай бұрын
Unabwela kudzakhala pop young chilungamo chimawawa
Lucius amayenela akule munzelu asamalimbane nd Ana awasiye iyaaaa
@KaykMw-ql6mxКүн бұрын
Oimba ndala amazitenga kut
@clydenyasulu764211 ай бұрын
Samala mwana wakwinthu ungafwa luwiro
@MuhsinSauluka-cv7hi10 ай бұрын
Yah
@joemlelemba657211 ай бұрын
Mmmmm you can't have alot of money usanapange dzina , I know music very well, apapa nkhaniyi ndi udani musatipusitse we can't talk about music in malawi without lucious Banda , tiyeni anthuwa asatipake matope mmaso a pop young wa Ali ndi dzina Kodi?😂😂 Koma guys matama odumpha popanda dzenjetu
@jameswajumpha679011 ай бұрын
Inu ndi athu aja mukadaganizilabe za auje aja while simukuziwa akukuonongerani zithu kumavomeleza chilichose muthu wayenda unyamulaso dj komaso management yako kugona plus ukudya and transport u have to think ndilama pano inagwa mphamvu
Kkkk siunalakwe bale even Krazie G collabo it's 25000😂😂😂😂😂 Kelvin sulungwe unabwela
@GentlebreezePurifiedwate-wm9ot11 ай бұрын
Momwe analongosolera Mr Banda ,anafotokoza mwachindunji mu Last post , Komabe poti amalawi Timanva nkhani pofuna kuyankha osati kunvetsetsa ,zikhalebe chomwechi,Aliyese Ali ndi ufulu opanga izo zamusangalasa
@LytonBlessngzphiri-wu6dg10 ай бұрын
Be cul pop young ,osalimbana nd meneyo
@user-nu9dp3gm1p11 ай бұрын
Ukatero upheso mwana ameneu chitan manyazi ndithu Banda
@vusoacquaron908411 ай бұрын
Ayi mtele Ku Malawi Tu kuno mpaka 3 million ayi tazikanani tikuwonani Ka 100pin kmwe mumapasidwako azanu ena sakapeza nde tikuwonani Mene zizikhalira
@user-np6bh6hw7o10 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉
@Summer2k-bx7je2 ай бұрын
Hy
@brendawingah507111 ай бұрын
Please pray hard
@Papie5911 ай бұрын
Inuso nkamwa mwanu nde chichewa chimakuvutani.....
@sammalvitha11 ай бұрын
Tinabadwa mosiyana and ndimakondwera ndi momwe ndimalankhulila popedza Pali ma sauzande aaanthu amene amasangalasidwa ndi zolankhula zanga kuposera omwe zimawabowa ndikamavutika kulankhula...
One man's food is another man's poison, sungakhale wabwino kwa wina aliyense. No need kunyozana, aliyense ango panga zake basi, bola business ikuyenda.
@user-nu9dp3gm1p11 ай бұрын
Masiku ano siwopephedza zilizose
@christophermmakiwa782911 ай бұрын
A pop young ndi ati kwenikweni mpaka kumafuna 3mita?munthu wangoziwika kwa anthu ochepa ngakhale sindinanverepo nyimbo yake ndiye basi kumakhala buy kukamba za kape ngati ameneyi,bola giboh Pearson
@joemlelemba657211 ай бұрын
Ndipo bro Inu kkkkkkk, munthuyo nde ndi giboh Pearson kutali , ine ndimaona ngati munthuyu anangofuna kuzitukwanitsa mwamva hahaha, 3 mita munthu wa ku zolozolo olo ndi chibade kutali aise
@alinafeanderson306511 ай бұрын
Giboh amatha pa level yake kma pop young wabwera kuzakhala he brings what new generation needs
@thandienyirenda672811 ай бұрын
Ndipo pop young wabwela kuzakhala ndakatundu
@user-et1bi1lv2k10 ай бұрын
Tiyen uko agalu
@BridgetKaziputa-bo2gn10 ай бұрын
God is with u mi bro,no worries😭😭😭😭😭😭😭😭
@Ishriss199911 ай бұрын
Lucius yo nde alindivuto, why not just stay quite on other peoples business? 🚶
@mbawabuliyan970411 ай бұрын
Soja ndi dolo Ana osasamba inu
@user-nx8gy8lq4q11 ай бұрын
Km yah
@user-kk5wz3br6s11 ай бұрын
Achina Lucia's ndi athu opusa osamawamvela ngt akufuna aphuzitse mwana wake kuimba😂🎉 azipasa mtengo ofuna iyeyo
@liftedphiri273511 ай бұрын
Banda ndi galu asamapange zopusa pokhala mubalewanga koma izi ndinyasi