Dziko Lafika Pa Mwana Wakana Phala - Bon Kalindo

  Рет қаралды 13,442

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

3 ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo says he has a cheat sheet on how Malawians can still do well despite Malawi facing numerous socio-economic challenges.
Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo wati ali ndi chinyengo chofotokoza momwe Amalawi angachitire bwino ngakhale dziko la Malawi likukumana ndi mavuto ambiri pazachuma.
#malawi

Пікірлер: 43
@raytavares2256
@raytavares2256 3 ай бұрын
Mr president wherever you are we love you and may ABBA bless you for fighting for justice against the the oppressed and the voiceless.
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 3 ай бұрын
The DC Bon kalindo good Message
@dalitsonambazo
@dalitsonambazo 3 ай бұрын
Kkkkkk km Mr DC number one😂😂😅
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 3 ай бұрын
Keep the fire 🔥🔥🔥🔥 burning.
@user-lr2wx5xd9d
@user-lr2wx5xd9d 3 ай бұрын
Malawi anawola eshiiiii
@JoshuaKangombe
@JoshuaKangombe 3 ай бұрын
the DC ulemu wanu simukunama ❤
@DavieNthole
@DavieNthole 3 ай бұрын
Boss
@Pangolinimw
@Pangolinimw 3 ай бұрын
My DC
@AYATU730
@AYATU730 3 ай бұрын
Karindo ndi mwana oooowopsa kwambiri 😂😂😂😂😂
@user-fl7br3dw4h
@user-fl7br3dw4h 3 ай бұрын
Ndimakublemani Mr kalindo ndininu nomwe munapangisa mumatilimbikisa za hi 5 komaso kudya katatu koma mumaziwa kut mukuwatengela amalawi kuchionongeko. Pano sitikudziwa yemwe azatiombole mmumalawi muno
@chrisneySwanepoel-yu5vd
@chrisneySwanepoel-yu5vd 3 ай бұрын
The DC ichi mchifukwa ndinafulira phone makwanira, ati phirip chakwera 😅😅
@Amgwagwa
@Amgwagwa 3 ай бұрын
Kkkkkk
@ChristopherMapondo
@ChristopherMapondo 3 ай бұрын
Tiye nazo big
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 3 ай бұрын
Boonnnnn kalindo mwana oopsaaa kwambili
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 ай бұрын
Ulemu wanu the DC. Membala Wa assembles of God aliyense akumalandila 70 000 kwacha pamwezi ili ndi boma lakuba
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 3 ай бұрын
The DDDDDDDCCCCCCCCCCCCCC😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-fy5hc5xe4p
@user-fy5hc5xe4p 3 ай бұрын
Bwana kalindo ngati nkutheka ma audio anuwa nthawi zina muziwatulusanso muchingelezi cholinga anthu akuja owe samva chichewa azimvanawo
@marryphili5419
@marryphili5419 3 ай бұрын
Malawi wuli mumanja mwasatana tiyeni tipemphere mwakuya
@PhilipMatolino
@PhilipMatolino 3 ай бұрын
Kkkkk ...the dc timakudyadira
@LacksonGonani
@LacksonGonani 3 ай бұрын
Tiyenazo mbuyanga osabwerera mbuyo more fire
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 3 ай бұрын
Kkkk😂 mr kalindo mumatiyimilila
@user-fl7br3dw4h
@user-fl7br3dw4h 3 ай бұрын
Kulakhula ndye mwalakhula koma musasiye mpaka mupedze munthu amene azatiombole ku ukapolo umenewu
@PaulChitete
@PaulChitete 3 ай бұрын
Mwana oopsa kwambiri DC
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 3 ай бұрын
A malawi ife ndi anthu onvesa chisoni, chakwera anachita kunena kuti iye alibe experience ya u president koma ife kuchiyikabe pa mpando chi mbuzi ngati chimene chija.
@AbdullahDewas
@AbdullahDewas 3 ай бұрын
Ayi zikomo wamkulu
@alexsumani6823
@alexsumani6823 3 ай бұрын
DC ndi akatundu
@jamusnamwino-br2iz
@jamusnamwino-br2iz 3 ай бұрын
😮kkkkkkk inendine Ben longwe chakwera munuro chakwera kkkkkkkk
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 ай бұрын
Osazankhanso munthu osauka kukhala president chifukwa chimafuna kuti chibe kaye. APM ndimulela khungwa.
@graciousstanford5228
@graciousstanford5228 3 ай бұрын
Mbava zokhazokha za MCP
@johnkambala692
@johnkambala692 3 ай бұрын
Inu ndi sanje mumanama sitikukhulupililani
@gloriambale2277
@gloriambale2277 3 ай бұрын
Koma iwe ndiwe chisiludi ,,...ife tikukulukutika tokha kuno tamangodyani volosi kumeneko mutipeza
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 3 ай бұрын
Amalawi tikuramuriridwa ni sataniki chakwera iyeyu angofuna kupha anthu angopanga vula kuti izipha anthu tiyeni guys tizipephera kwambiri mlungu azitimenyera khondo ife tirichete
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 3 ай бұрын
kalindo ndigaluuuuuu kwabasi chisilu chamunthu mutu wakob
@gloriambale2277
@gloriambale2277 3 ай бұрын
Pantumbo pako wamva I think suli mmalawi muno....bwer uone zimene akuchita chakwera muno mu malawi 😢😢
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 3 ай бұрын
@@gloriambale2277ndiye chokako mwazolowela zamanja lende amalawi inu ulesi makaka kumwela uko
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 3 ай бұрын
Asilamu a fake amene anasiya mpingo wawo mkukajowina wachakwela wa asembulesi ofu GOD chifukwa cha ndalama ndi omwe amatamika ndikumuitana chakwela ku ma function a chisilamu a like function ya EID, anthu ake ndimonga ulad musa ndazimzake obisalila kuchisilamu, otherwise msilamu genuine ngat ine msingapange nawo zopusazo ayi
@danielsulani8689
@danielsulani8689 3 ай бұрын
😂😂😂
@EmmaJohn-ke2wx
@EmmaJohn-ke2wx 3 ай бұрын
Ziko tinali peleka Kwa satana
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 3 ай бұрын
Kkkkkkk ziliko 🔥🔥🔥
@samuelmpetamlenje7708
@samuelmpetamlenje7708 3 ай бұрын
Bon Kalindo ngati iyeyo ali ndi nzeru zotsutsana ndi Boma Why can’t he join or open his own party and show us what he preaching about.. It is absolutely nonsense kuwukila boma pomwe iyeyo zomwe akuchita ndikungolalata He must bring solutions to our country not just talking Talking is cheap Tell he is stupid and foolish. You can’t claim you know everything that happens in the state house. It’s like you are saying the state house is not safe for any president Two how did he know that the president made a call to Eskom to make prices high? Should the government take this easy saying he knows everything that happens in closed doors by the government? Is that possible? Kalindo must start his own party We need actions not cheap talking… Kalindo doesn’t have directions Those see that they are better than the president or the ruling party they participate in elections and become the president Not just confusing a small country that is poor like Malawi 🇲🇼 I don’t know Kalindo But whatever he talking it’s just cheap and nonsense He should make his own party and show Malawi 🇲🇼 that he is better than every president as he claims
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 3 ай бұрын
🤣🤣Ine ndine Gabriel Chakwera
@user-jc9gy9ou3v
@user-jc9gy9ou3v 3 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣ayi zikomo
@stevenfrancism3638
@stevenfrancism3638 3 ай бұрын
😂😂
Alex hid in the closet #shorts
00:14
Mihdens
Рет қаралды 11 МЛН
Пранк пошел не по плану…🥲
00:59
Саша Квашеная
Рет қаралды 4,9 МЛН
A Opposition Mwafatsa Kwambiri   Bon Kalindo
14:08
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,2 М.
Malawi politics part1 - DJChizzariana
42:53
DJ Chizzariana
Рет қаралды 10 М.
Ku UTM Zoti Kunali Saulos Chilima Ena Ayamba Kuyiwala -  Bon Kalindo
15:18
Ma Cadet Mulimba? - MCP Supporter
7:10
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 902
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20
Times 360 Malawi
Рет қаралды 240 М.