TAMVANI ZA IMFA YA CHILIMA IJA

  Рет қаралды 133,436

FRANCIS MTAWAYA TV

FRANCIS MTAWAYA TV

10 күн бұрын

Пікірлер: 214
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed 8 күн бұрын
This is true and he was warrior and may his saul rest in peace 😢😢😢😢😢😢😢. Chakwera akutinyasa. Chakwera ndiopa kwambiri ndipo akulitenga dzikori ngat ndilamake.
@sulleahmnyimbili1362
@sulleahmnyimbili1362 7 күн бұрын
Rest well SKC, thanks for the information
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 8 күн бұрын
Well spoken Mr Man,, tikufuna anthu olimba mtima ngati inuyo Mr,, Mmene mukuyankhula chonchi ma Members a MCP akusakani bwana.
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 8 күн бұрын
Mzimu wachilima mmmm ndi waukali
@Kilocssreaction
@Kilocssreaction 9 күн бұрын
Amene akudana ndi voice iyi machende ake ndichakwera manyi ake
@user-hs6sh3xz1f
@user-hs6sh3xz1f 8 күн бұрын
Upole mototu koma kkkkk
@peterjailos1879
@peterjailos1879 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@McneverMauwa
@McneverMauwa 6 күн бұрын
Ndipo live brother nkhani ya straight iyi
@christophergibson72
@christophergibson72 5 күн бұрын
Naweso akowo pali chotukwanila apa? Mutul ngati chibonga
@thomasmfune5150
@thomasmfune5150 2 күн бұрын
UTM ndi Malawi Tapya kusogolo ndi pansanapomwe. MHSRIP 😭😭😭
@CHAKAKACHAKA-MANMW
@CHAKAKACHAKA-MANMW 4 күн бұрын
MUSIYENI CHAKWERA ABALE AKUZIWA NDI MULUNGU, R.I.P BOSS MAN CHILIMA
@CambioJumanjih
@CambioJumanjih 5 күн бұрын
Incompetent leader Malawi ever hard........ Lazarus chakwera
@GracePhiri-ox8wr
@GracePhiri-ox8wr 8 күн бұрын
True bigman live and direct
@user-ek9dj9qk4v
@user-ek9dj9qk4v 9 күн бұрын
Muziika zinthuzi zizipanga slide, zimapangitsa munthu kuonjezela chidwi pomvetsera. Thanks for the information
@gomesavirgo3987
@gomesavirgo3987 6 күн бұрын
That's very true, I think uli ngat ine
@cosmasnkanda8193
@cosmasnkanda8193 8 күн бұрын
imfa yapweteka iyi eeeh!
@nancynkumbira1466
@nancynkumbira1466 6 күн бұрын
Ndipo yowawa eee sinazionepo ,,i feel for the family
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d 9 күн бұрын
Chilungamo chomveka bwino kwambiri 😢😢😢
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 9 күн бұрын
Koma eeeeeeee chîungamo kuwawa or kuli agule Pena mudzivesa chilungamu
@StevenLazaro-nm9pk
@StevenLazaro-nm9pk Күн бұрын
Nice massage
@homeremedys3748
@homeremedys3748 8 күн бұрын
Dziko tengani ili achakwela ndi anthu anu, anthu opanda chisoni, Now Mukufuna Kupha APM ndi Born Kalindo, Zonsezo tikuzidziwa
@BlessingsNjanji-dj7oq
@BlessingsNjanji-dj7oq 9 күн бұрын
Chilima rest well ,until we meet u again
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 9 күн бұрын
Chimenetu amaiwala, Technology,ili ponseponse,si nthawi imene anaphedwa nduna,4 zija kunalibe, technology.lero.kutelo,ungoonekela, poyela.si,izi.mabvutotu, awayamba,okha.
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim 9 күн бұрын
Munthu wanyau chakwera .my br chakwera akudziwa imfa yachilima
@AllieGeorge-ec2cl
@AllieGeorge-ec2cl 7 күн бұрын
Chonde chonde tibweretsereni poyera zigawengazi ziyaluke
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 9 күн бұрын
Good Messnge Chakwela you mast go
@user-gg6uh2wo4x
@user-gg6uh2wo4x 8 күн бұрын
We are to gether brother
@giftttsukuluza4264
@giftttsukuluza4264 8 күн бұрын
I salute u for good update only God knows, mmm malawi
@Willardpiches-ci4yi
@Willardpiches-ci4yi 8 күн бұрын
Ili ndi pemphero ameen
@user-ju1hw9po8u
@user-ju1hw9po8u 6 күн бұрын
Thanks my lady 😊😊
@McneverMauwa
@McneverMauwa 6 күн бұрын
MCP chawo palibe azakawinila kumwamba chakwerayo
@HaroldBonface
@HaroldBonface 8 күн бұрын
Utsi sufuka popanda moto
@Tenjklvtcy
@Tenjklvtcy 8 күн бұрын
Kumalawi kulibe fiti iyaaah 😂😂 amalakwa chani chakwera
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 8 күн бұрын
Do you have humanity?
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 9 күн бұрын
MCP yatipweteka kwambili
@user-qf7jw4ho3h
@user-qf7jw4ho3h 9 күн бұрын
Only God knows the truth
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 8 күн бұрын
@@user-qf7jw4ho3h to know about now because it's obvious chakwera killed Chilima umbuli kapena ufiti inuso nanu aaaaaa
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 8 күн бұрын
Criminal party mcp.
@JamesNgwaya-vz1ox
@JamesNgwaya-vz1ox 8 күн бұрын
Wapha ndi chakwera akutsutsawo ndani mbolo yake yosadulayo foolish
@ChaletsMukona
@ChaletsMukona 12 сағат бұрын
Ziyankhule zitsilu zozala ndimagazi kuyambila kale mpakav kale
@user-bc3tx3wp1i
@user-bc3tx3wp1i 8 күн бұрын
This is reality big man
@janemshanga5349
@janemshanga5349 3 күн бұрын
Like my dad also ananena choncho kuti kumukhulukira uku inali nyambo
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 8 күн бұрын
💯 %true brother 😢
@andrewchirwa2193
@andrewchirwa2193 6 күн бұрын
Amuphela Dala chilima sazawinaso 2025
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 8 күн бұрын
Winayo masoti ngati mphaka , mr kilimora
@CharlesBande-yr1yb
@CharlesBande-yr1yb 9 күн бұрын
Tienazoni,angotsola kunjira,ndipo njira sadatseke aí,inunso mutero basi sinu Mulungu aí.
@kalimawandale7161
@kalimawandale7161 2 күн бұрын
Komatu Chakwerayu atafuna kukubwezelani mutha kuona zosaona
@user-dn3gp6yi4y
@user-dn3gp6yi4y 3 күн бұрын
Chilungamo ndi mwano amene ikumukhuza nkhani imeneyi audio iyi sakupuma nawo bwino akuwona ngati awanyoza koma ayi wayankhula chilungamo Zimveka bs any time chilungamo chizatuluka
@user-wb5ym2qm6y
@user-wb5ym2qm6y 4 күн бұрын
Komaditu a Huwa Mkaka adalankhula kuti ndale za kuMalawi timapanga ndi usiku.
@babranzima8120
@babranzima8120 9 күн бұрын
Idalidi nyambo pama plan athuwadi😢😢
@Pangolinimw
@Pangolinimw 9 күн бұрын
😢😢😢😭😭😭 mcp ndi yakumpa
@nephitalychitedze2118
@nephitalychitedze2118 8 күн бұрын
Kusokosera pano sikuthandiza china chilichonse nkhani ndiyakuti. Ngati muli ndi umboni pitani ku Court. Sizomangosokosera zotibweretsera misozi ayi... RIP my Veep SKC
@OFG-th3st
@OFG-th3st 8 күн бұрын
Chippewa chija Ndichoopsa😢
@Hong_sing
@Hong_sing 8 күн бұрын
Excellent 😭😭😭😭😭
@kubengovender6996
@kubengovender6996 9 күн бұрын
We are together big man!!
@MillieMalakam
@MillieMalakam 6 күн бұрын
Cakwela ndiwosalakwa anavomeleza kt cilima zayimila koma nduna xakezi ndizimene zikumuzocelesa kt azipanga zoipa koma mcp must go akazizi achabecabe afiti osekelera
@KelvinPhiri750
@KelvinPhiri750 8 күн бұрын
zosakhala bwino...i do know when we will change a s a country 😭
@CharlesBanda-kv8bh
@CharlesBanda-kv8bh 8 күн бұрын
Ndiwe chitsiru amene ukutukwanawe udikire uwone cho me mulungu amanita ndizitsiru ngati iwe
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
@KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 күн бұрын
Umbuli wakudanawo osaziwa chimene akuchita
@SaidiMdoka-pn3zm
@SaidiMdoka-pn3zm 9 күн бұрын
Mfiti yayikulu ndi Chakwela m'busa wonyenga
@FortuneAndrew-nb2im
@FortuneAndrew-nb2im 8 күн бұрын
Respected may his soul rest in peace
@reymondpetermaster5697
@reymondpetermaster5697 3 күн бұрын
Skc rest in peace, only God knows about your early departure.
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 6 күн бұрын
Mawu onse amayankhura a mcp aphelezera anthuwa ngakupha basi ngakhale zi siru za anthu ena zikubakira as if they don’t see wat is happening n it’s just only few people amene akumusokoneza president.
@louismagongwa
@louismagongwa 8 күн бұрын
ndakulakwila chani fuko langa lokondeka , mtima ukuwawa bwanji😢😢😢
@paurosi123
@paurosi123 8 күн бұрын
Bwandeeeeeeeeee!!!!!!
@francis12fombe54
@francis12fombe54 8 күн бұрын
Kkkkkkkk koma ya 2025 tidzawone kuti ndolo ndani
@user-os7qt6lw2c
@user-os7qt6lw2c 4 күн бұрын
Wayakhula momveka bwino2 uyu..muciyakhulo cathu
@ModesterThomas
@ModesterThomas 9 күн бұрын
Chooona chimamasula❤❤❤❤❤
@NOKIAMalawi
@NOKIAMalawi 2 күн бұрын
Zoona
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z 8 күн бұрын
Sizingatheke kut achakwera osaidziwa opanga nde chakwerayo
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 5 күн бұрын
Chilima R I P
@homeremedys3748
@homeremedys3748 8 күн бұрын
Achewa ndinu oipa kwambili
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 8 күн бұрын
Zomvetsa chisoni dziko lapita ili💔💔
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 8 күн бұрын
Chipani choipa ichi ever in Malawi Kma thaw yawathera next year onse amangidwa after kuluza
@charlesmartin6990
@charlesmartin6990 9 күн бұрын
Komaa!eeee dzikoli
@user-sr6fb3dw2y
@user-sr6fb3dw2y 7 күн бұрын
Mukadakhala anzeru sibwenzi mukungolalata pamene Malawi ali pa moto.osatenga bomalo kuti amalawi tisiye kuvutika bwanji? Tatopa inu chilungamo mukuchidziwa koma mwabisala
@user-mm5mn9fc6e
@user-mm5mn9fc6e 9 күн бұрын
True
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 8 күн бұрын
Anthu awa amalawi zigewenga zikuluzikulu, dziko lino kulisiya mumanja mwa anthu amenewa ndiye kuti tiluza anthu ambiri ofunikira mdziko muno komaso amalawife titengelepo phunziro kuti sibwino kuvotera zigewenga kapena azibusa
@worldfamous_23
@worldfamous_23 8 күн бұрын
Akutha thobwa akuluwa
@user-un6mw5wm3x
@user-un6mw5wm3x 8 күн бұрын
True story brother
@Moses51
@Moses51 8 күн бұрын
Chakwela achoke
@jeffngwira1987
@jeffngwira1987 5 күн бұрын
This is Deus Sandram's voice
@BesterSengeledo
@BesterSengeledo 8 күн бұрын
For sure biggman
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 8 күн бұрын
Chilima dzathu wa chinyamata 80s 90s 2000
@user-nq9bg8zo4v
@user-nq9bg8zo4v 8 күн бұрын
MCP should go
@promisemenge
@promisemenge 9 күн бұрын
Or azipha nayenso kukumusidikila
@PaulKalambo
@PaulKalambo Күн бұрын
Rest in peace legend
@JamesMwangolera
@JamesMwangolera 4 күн бұрын
Chilungamo chimapweteka😢
@user-qf7jw4ho3h
@user-qf7jw4ho3h 9 күн бұрын
Only God knows the truth
@ChristinaMALENGA
@ChristinaMALENGA 4 күн бұрын
Rip acle😢😢
@PettyMadondo
@PettyMadondo 6 күн бұрын
Ndipo khaniyi ndiyoona ndinthu koma mulungu alipo
@AndrewChiponga
@AndrewChiponga 8 күн бұрын
Zomvesa chison + urem akurandira ndi mutharika
@LupakishoMwenisongole
@LupakishoMwenisongole 7 күн бұрын
Go ahead brother
@MisheckAselo
@MisheckAselo 9 күн бұрын
Gule kwao please
@user-rq2qb9ql1i
@user-rq2qb9ql1i 8 күн бұрын
Tisaweluze timusiye Mulungu akhale yekhayo aweluza pansipompano Koma tikhale manso kwawo kwantha kwasala Kwa ine ndi inu
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 8 күн бұрын
Amen
@RAFIKIZULIAN
@RAFIKIZULIAN 8 күн бұрын
Watsala ndiwe kufa ndiwe galu 😂😂😂
@user-yj5xv4cy8x
@user-yj5xv4cy8x 7 күн бұрын
Mudziwa chani chakwera khaniyi ampaka mmodzi mwa ndunazake kenako iye aziyeretse basi kuteroko muona
@MelvinVanRooyen
@MelvinVanRooyen 8 күн бұрын
Koma gayz m'dziko likuchita dzinthu yhoo
@RanitaMbalule
@RanitaMbalule 5 күн бұрын
Rest in peace skc
@AfricanKingdom-uv1qb
@AfricanKingdom-uv1qb 9 күн бұрын
Mcp ndiyakupha
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 8 күн бұрын
No way chakwera ali momwemo
@KabilaKabuka
@KabilaKabuka 4 күн бұрын
Mlahu.akibaru
@user-qb2lt6qj1p
@user-qb2lt6qj1p 8 күн бұрын
Chilichose chomwe anachita anthu amenewa chiululika nzimu wachilima ndiwoophsa
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 8 күн бұрын
Ulemu wanu Malume osaopa kunena chilungamo
@rosamwenelupembe6856
@rosamwenelupembe6856 8 күн бұрын
Mulungu achitile chifundo dziko lathu la Malawi.
@promisegregory8397
@promisegregory8397 8 күн бұрын
Vuto lanu a Malawi 🇲🇼 Kusankha kwanu kuti mumulande Boma Peter Mthalika.....wakwiya mzimu wa Bingu,Munya muzingophana shupiti....
@andrewmaluwa2713
@andrewmaluwa2713 8 күн бұрын
aaa uja adationjeza kwambili APM, nkhaza zomwe ma cadet amachita zija muona ngati tayiwala? aliyense adzafatu including APM yo, osamalakhula motumbwa, dzikoli si la amuthalika, chakwela naye 2025 akadzaluza ndekuti amalawi samufuna osati adzidzati andilanda boma
@PRECIOUSMKUTE
@PRECIOUSMKUTE 8 күн бұрын
Lero akutifuna okhatu. Ankatinyoza
@sokojane4015
@sokojane4015 8 күн бұрын
Zinthu zimayenda bwino only with Bingu. Munthu uja aaaa anathesa njala ndipo zinthu zambiri zimaoneka ndi maso. Bingu wa Mthalika miss him always​@@PRECIOUSMKUTE
@PociahMack
@PociahMack 9 күн бұрын
Dikilan wosat kumayakhula ngat wokhoza apa. Kuyakhula maganizo anu anthu ndikumakuwombelan m'manja
@user-rz9rm4cb8x
@user-rz9rm4cb8x 9 күн бұрын
Achitsilu inu
@Tenjklvtcy
@Tenjklvtcy 8 күн бұрын
Ndiponso aaaa😅
@Tenjklvtcy
@Tenjklvtcy 8 күн бұрын
​@@user-rz9rm4cb8xamakuptsani Ufa kodi
@user-tb3my4wb1k
@user-tb3my4wb1k 8 күн бұрын
Big up sir
@MarthaMartha-rw4zz
@MarthaMartha-rw4zz 8 күн бұрын
Chakwera ndi satana amachita kuoneka pakhope mbudzi imene ija atipweteka fitsi imeneyi asazafe garu amneyi
@mgarachimsybwoy9239
@mgarachimsybwoy9239 8 күн бұрын
Only God knows 🙏🙏
@grinesskuyere
@grinesskuyere 6 күн бұрын
Sad
@FrodrickAwadu
@FrodrickAwadu 3 күн бұрын
RIP skc
Ine Sindingasiye U Akitivizimu - Bon Kalindo
11:12
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,5 М.
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Jimmy
Рет қаралды 73 М.
🌊Насколько Глубокий Океан ? #shorts
00:42
Sprinting with More and More Money
00:29
MrBeast
Рет қаралды 191 МЛН
Must-have gadget for every toilet! 🤩 #gadget
00:27
GiGaZoom
Рет қаралды 11 МЛН
버블티로 체감되는 요즘 물가
00:16
진영민yeongmin
Рет қаралды 59 МЛН
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 109 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 62 М.
LIVE: Fraktionsstatements Die Grünen
12:36
ntv Nachrichten
Рет қаралды 1,5 М.
DAKELOT - ROZALINA [M/V]
3:15
DAKELOT
Рет қаралды 295 М.
ИРИНА КАЙРАТОВНА - АЙДАХАР (БЕКА) [MV]
2:51
ГОСТ ENTERTAINMENT
Рет қаралды 4 МЛН
Duman - Баяғыдай
3:24
Duman Marat
Рет қаралды 65 М.
QANAY - Шынарым (Official Mood Video)
2:11
Qanay
Рет қаралды 134 М.
Bakr & Бегиш | TYTYN
3:08
Bakr
Рет қаралды 763 М.
IL’HAN - Eski suret (official video) 2024
4:00
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 528 М.