Gotani Hara ali pa chikondi ndi Nankhumwa chifukwa chani?

  Рет қаралды 65,852

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Күн бұрын

Пікірлер: 239
@user-nn9mx5tt6d
@user-nn9mx5tt6d 6 ай бұрын
This guy from bakili muluzi TV need support bro my Allah continue bless you❤❤
@georgechikafutwa1334
@georgechikafutwa1334 6 ай бұрын
😅😅😅😅😂😂😂😂 big up Nankhumwa akufunika mademo akeake akusokoneza
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 6 ай бұрын
Navitcha woyeeeeeee❤❤❤
@StanleyWachazaBanda
@StanleyWachazaBanda 6 ай бұрын
You are forgetting that it is MP's who vote Leader of Opposition, not necessarily parties. Yes, the ones with the majority are at an advantage but could be any from the opposition parties in Parliament. What you are advocating is to cause confusion. Let the due course of rule of law take its course
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 6 ай бұрын
Thanks for the video we have been waiting for this boss continue to give us the best
@FrancisNgoma-sn9cj
@FrancisNgoma-sn9cj 6 ай бұрын
😊😊
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 6 ай бұрын
My best Chanel
@owenskabazanechiumia3543
@owenskabazanechiumia3543 6 ай бұрын
Nzovetsa chitsoni Malawi ilibe atsogileli okonda dziko lawo,koma kulemerera ndale basi
@marthansaliwa7732
@marthansaliwa7732 6 ай бұрын
May Thunder from God strike all those betrayers in Jesus Name!
@user-oc6xd4tv9l
@user-oc6xd4tv9l 6 ай бұрын
😂😂😂
@shakilasaid705
@shakilasaid705 6 ай бұрын
You bring joy to us keep on going
@Benty_Pro
@Benty_Pro 6 ай бұрын
Strong Woman Navitcha🙌🔥🙌
@MisheckAselo
@MisheckAselo 6 ай бұрын
Tisankhe mwanzeru a Malawi kupanda kutero tikanali padiwa ulemu wanu munthu wamkulu 👍
@WinzyMark
@WinzyMark 6 ай бұрын
Kkkkkk iii koma adha awanso ee mpaka kufufuma ngat namfuko? Kkk big up to you brother continue bringing us these updates we proud of you
@johnw.posomanchanel4023
@johnw.posomanchanel4023 6 ай бұрын
mcp is trying to introduce one party system. chakwera wants to diminish DPP by intimidating so that he can be a long life leader. As Malawians we'll not tolerate this nonsense.
@MwenyeCheNsoma-gb2yz
@MwenyeCheNsoma-gb2yz 6 ай бұрын
Pajatu court lomweli linalowelera kuti boma lilipoli lithe kulamulira. Ndangodutsamo
@BenissoneErnesto-eh6zs
@BenissoneErnesto-eh6zs 6 ай бұрын
Kufufuma ngati nanfuko kkkkkkkk koma nzeru alibe nkaz sakuwafuna koma iwoooo angokakamirabe kkkkk live in Mozambique
@stanleykaludzu-bm4pm
@stanleykaludzu-bm4pm 6 ай бұрын
kkkkkkkkkkkkkkk
@joshuaagabu3032
@joshuaagabu3032 6 ай бұрын
Bwanawa saona nkhope amangophothyola Hahahaha. Mpaka kufufuma ngati. namfuko 🤣🤣🤣
@user-zy1eh3pt8v
@user-zy1eh3pt8v 6 ай бұрын
Wishing you all the best, you the Big man from The Best Tv
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 6 ай бұрын
Koma ndiye mumanyonza abwana ..😂😂😂😂😂 ukadakhala ulaliki tikadati Amen go deeper the man of God...😅😅😅
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 6 ай бұрын
I was waiting for you brother true
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e 6 ай бұрын
Kanankhumwa kachakwela ndi hara otse panyopawo agalu mbudzi😊😊😊😊😊😊
@WinzyMark
@WinzyMark 6 ай бұрын
😎😎😎😎akumangatu phwanga
@user-mj3ms4jt3b
@user-mj3ms4jt3b 6 ай бұрын
Mulira a DPP simunati ichichi ndiyambi chabe. Vuto ndi utsogoleri wa thyolo basi. President from thyolo, leader of opposition thyolo regional governor thyolo. Chimenechi ndipani cha anthu adziko la Malawi kapena chipani cha anthu adziko la thyolo? Muchila koma mochedwa khulupilirani mau angawa ndi amaliseche anu akumwelawo
@user-mz4tk1pw3f
@user-mz4tk1pw3f 6 ай бұрын
Nankhumwa Ali ndi chibwana kwambiri kunali anzawo amene amapanga zimenezo lero Ali kuti samale kwambiri
@user-nu3zg6pr1l
@user-nu3zg6pr1l 6 ай бұрын
Kodi MA, soldier akuyanga zimenedzi Malawi akupita chikhalire makolo awoso ku mudzi ndi amene akumvutika ngati alibe Ana 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@MorrisMapiri
@MorrisMapiri 2 ай бұрын
"Munthu ofufuma ngati namfuko koma opanda nzeru " that's what I have quoted. But the title of movie if different from content. You named it " Nankhumwa is in love with Gotani then boom another issue
@senaherbo3714
@senaherbo3714 6 ай бұрын
More fire bakili muluzi tv
@petermasenti2084
@petermasenti2084 5 ай бұрын
I respect you comrade
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 6 ай бұрын
Very pathetic that the house of Commons, the house that was supposed to bring hope to the hopeless, has turned to be a disgrace but, God is watching.
@AndwatchMambo-gn5bs
@AndwatchMambo-gn5bs 6 ай бұрын
Ndiwe wa DPP no wonder. Tilipo ambiri amebe timadana ndi DPP si Hara yekha. DPP tayipanga divide and rule. That's politics. Democracy is all about winner take it all. DPP yatsala ndi aphungu 24 basi. Osatinamiza APA.
@user-lv4qd4pm1e
@user-lv4qd4pm1e 6 ай бұрын
Aaaaa awa ndi ambuli because akuonetsa kuti Ali mbali yonyoza MCP sali pa chilungamo
@henrynandolo4520
@henrynandolo4520 6 ай бұрын
Very sad story! We are tired of these personal issues in parliament! Favouring some people on personal issues! There's lack of justice in Malawi because politicians are running national matters as personal business. Shame! Parliament should constrate on development issues because poor Malawians are suffering!
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 6 ай бұрын
i quote,munthu ofufuma ngat nafuko nankhumwa😀😀😀😀
@aubreymayenda5441
@aubreymayenda5441 6 ай бұрын
Ine mawu amenewo sanandisangalase
@zeckbmalawi8017
@zeckbmalawi8017 6 ай бұрын
Best tv
@user-md5uv2cg6i
@user-md5uv2cg6i 6 ай бұрын
Amalawi muli ndisoka Gotani mkandawire wakhala akudula anthu dziwalo ku mzuzu😢😢😢😢
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o 6 ай бұрын
I love tv,, mwina Catherine gotan a kudwala a nankhumwa misala ya maluz yamukwana koma aiwala kuti ndizosiirana
@ashikalam8616
@ashikalam8616 6 ай бұрын
Go deeper sir. We love you ❤ sir.
@TiyaMtete
@TiyaMtete 6 ай бұрын
Best of TV, Vote for Dpp
@ishakatimbe7341
@ishakatimbe7341 6 ай бұрын
Chakwera ndi nduna zake ndagalu ose
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 6 ай бұрын
😢😢😢😢😢 Malawi wathuyu tilinaye pamavuto chifukwa cha anthu Adyera ndi odzikonda ngati Nanku ndi gulf lake 🫢🫢
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 6 ай бұрын
Thanks brother
@chifundonkhoma-uv4bw
@chifundonkhoma-uv4bw 6 ай бұрын
Your content is always inspiring but you should know that there is court injunction...DPP should go to court to have this revoked first but It's busy trying to bring politics in parliament... you should be non partisan guys
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 6 ай бұрын
The injection is between nankhumwa and chaponda
@chifundonkhoma-uv4bw
@chifundonkhoma-uv4bw 6 ай бұрын
Okay if so then MCP sikupanga bwino.... parliament si Malo opangapo zibwana... they should not defile the house of Malawians
@ashikalam8616
@ashikalam8616 6 ай бұрын
Mbuzi zonsenzi
@ashikalam8616
@ashikalam8616 6 ай бұрын
Don't let them to divide us
@harrispheleni2205
@harrispheleni2205 6 ай бұрын
Exactly this channel ndiyachigoba ndi cadet koma ana user bakili muluzi ATI kutiphimba mmaso
@user-md5uv2cg6i
@user-md5uv2cg6i 6 ай бұрын
Mai Hala akuchindana ndi kondwani dog style
@augustMag
@augustMag 6 ай бұрын
Nankhumwa ndi opanda chifundo ndi dziko lake Ndipo ameneyu akadzalamulira dziko linoli andifuse sangathandize dziko ata pang'ono
@FefieTenisha-du7ge
@FefieTenisha-du7ge 6 ай бұрын
Well articulated
@WillieMakoza
@WillieMakoza 5 ай бұрын
Mpaka mawu okuti zitsiru izi....aaaah kusowekera ulemu, do u think tose tingakonde anyalumbe inu a UDF? Bakili ewww wama blunder, a nyooo pa Malawi pano, kumavomereza kuti UDF inapita, inatha, enaso apangeko nthawi yawo, ndiyo democracy
@noordeenmsamu6652
@noordeenmsamu6652 6 ай бұрын
Bigy up fadah ✊️
@user-xx3vi1gt2i
@user-xx3vi1gt2i 6 ай бұрын
Big man wathu Inu ulemu wanu simuumila Mau pachilungamo nakhumwa sakuziwadi chimene akuchita
@user-dt6ot7vs8q
@user-dt6ot7vs8q 6 ай бұрын
Zovetsa chisoni sukulu zifikire ponse ponse kuti umbuli uthe ngati zingatheke.
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d 6 ай бұрын
My vote for APM
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 6 ай бұрын
Koma a Malawi munachita mistake Povotera MCP mukuona zomwe zikuchitikazi zimenezi kumapeto Kwame ndi nkhondo😭😭😭😭
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Wofufuma ngati nanfuko kkkkkkk bwana mumaziwa kuyankhula kwambili .....nankhumwa ndi hisilu
@user-ro1mi6yg8m
@user-ro1mi6yg8m 6 ай бұрын
Bakili tv yimayankhula mosabisa Marry navitcha woyeeeee❤❤❤❤❤
@Littlefair7
@Littlefair7 6 ай бұрын
Taperekanu mfundo zomveka abulutu inu, umbuzi wanu uzatha liti? Ma comment basi kukhala yonyoza ma comment a ena? Iwe ndi mbuli yomvetsa chisonu kwambiri.
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 6 ай бұрын
Ndipo kwambiri
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 6 ай бұрын
Dzikoli Ngati lafika APA nankhumwa munthu opanda nzelu nkhani ndiunafuko omwewo
@harrymicah6140
@harrymicah6140 6 ай бұрын
Nde mwati namfuko kakaka amenei kukakamira leder of opposition
@mlakatulimfumuchembynelson2404
@mlakatulimfumuchembynelson2404 6 ай бұрын
MCP for eva , DPP Neva again , Ukusokeretsa anthu iwe
@andymasingajunior
@andymasingajunior 6 ай бұрын
Awanso alowa ndale, i though he has was Genuine, ndi wa ndale eti?
@LukaThawe
@LukaThawe 6 ай бұрын
Inu Nanu zimene mukumakamba ndizopanda pake mungonena zogawanikana amalawi Choti muziwe palibe zabwino apa
@usumanidaudi
@usumanidaudi 6 ай бұрын
Osatiso nankhumwa akufunikira ma demo nankhumwa ndimusowesa pa ziko rapasi pano azikasokoneza kwina
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 6 ай бұрын
,😂😂😂 koma ndaseka mwati ofufuma ngati nafuko😅😅😅
@user-wb8jv9um4h
@user-wb8jv9um4h 6 ай бұрын
Mwati nankhumwa ndi ofufuma ngati namfuko kulankhula kwa bwanji uku
@LienHavenga-jy9yy
@LienHavenga-jy9yy 6 ай бұрын
Thanks bra
@user-om7ol2mp6z
@user-om7ol2mp6z 6 ай бұрын
Channel chonena chilungamo ndi Bakili muluzi TV 📺
@nyasavoicebox
@nyasavoicebox 6 ай бұрын
Bakili Muluzi TV makina okonzela makina anzake. Ntchito mukugwila amwene!
@AndwatchMambo-gn5bs
@AndwatchMambo-gn5bs 6 ай бұрын
Tiyeni nazo simumazitama kuti mumaziwa ndale. Manage that crisis now which has rocked your DPP
@usumanidaudi
@usumanidaudi 6 ай бұрын
May gotani hara akufuna amarawi awone zimene akumapanga nda nankhumwa ku ma hotero ari mariseche ndi nankhumwa
@alexbanda460
@alexbanda460 6 ай бұрын
Nde mwati kufufuma ngat nafuko nde nzeru alibenso, mkazi kuwakana koma munthu wofufuma angokakamilabe kkkkkkk
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 6 ай бұрын
Dpp ikoze mavuto ake osati kumalimbana ndi mcp ai
@JohnMilo
@JohnMilo 6 ай бұрын
Kufufuma ngati chani? 😂😂😂
@austinvincent773
@austinvincent773 6 ай бұрын
Komatu pena pake tikambe zoona pano mumaonetsa mbali pazolankhula zanu inde zinthu zulakwika komano munthu olankhulila amalawi samakhala oonetsa mbali ai mumayenela kumaunikilaso magawo ose ku opposition komaso kuboma lulamula panoli coz pena sitimakumvetsani akulu inu
@marryphili5419
@marryphili5419 6 ай бұрын
Ooo God why this president enough is enough tatopa ndi zigawenga izi zimanamizira ngati ndi abusa
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 6 ай бұрын
Inu mumakwana for ur information
@user-kj6qj1md5e
@user-kj6qj1md5e 6 ай бұрын
Km fidye uyu kd nakhumwa ndikanyama Kanji ameneyu nde tidzachitad kanyenya
@CatalinaLupiya
@CatalinaLupiya 2 ай бұрын
Big up bro
@user-uj6ik4xx5i
@user-uj6ik4xx5i 6 ай бұрын
Mmakwana brooo!!
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 6 ай бұрын
Uyu sim'busa koma mwana wanjoka ndipo zake wadyeratu pansi pompano
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 6 ай бұрын
Harayo Panyini pa mache chihule Musiyeni asowa posa chedwa ineyo ndine chigawenga choopsya koma kwathu koba dwira straight ndi ku Malawi Mulanje sapitwa koma chibwana chiku chita MCP,masiku ake si ano aí,siku lina tiza kalipa ndipo kuza Lira mfuti we don't like this stupid government like this, DPP you must GOES fight for malawians people,we are with you DPP party and you have got strong soldier here IAM
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 6 ай бұрын
Ifenso DPP yakoyo sitikuyifuna ayi, ukunya manyi Peter wakoyo salowa m'boma. Wabodza iwe, ukhawulabe.
@user-lc6up3qx4s
@user-lc6up3qx4s 5 ай бұрын
Akulu mukudya ndalama za Dpp
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 6 ай бұрын
Laws are not respected in Malawi by the court,
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 6 ай бұрын
a DPP zanu zili pabwino udari munthu kare lwe koma pano uli mu chipani aaaaha
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 6 ай бұрын
Ndalama za misonkho yamalawi kukokoloka ngati nyengo ya fredy politics has come to aworse stage zikutisowetsa mtendere mudziko lathu lomwe
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 6 ай бұрын
Ine anayamba kale kundinyasa mai amenei
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 6 ай бұрын
Ngati mutharika adzakakamire udindo mchipani kutha kwa chisankho uku kudzakhala kutha kwa dpp ( Austin Liyabunya )
@danjacksonlakalaka2039
@danjacksonlakalaka2039 6 ай бұрын
big up munthu wamkulu following mwachidwi DPP woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 6 ай бұрын
Boma ilowaso dpp osakaika
@user-dj5hd4ys3n
@user-dj5hd4ys3n 6 ай бұрын
Big up malawi
@kubengovender6996
@kubengovender6996 6 ай бұрын
Big up!!
@harrison-it6el
@harrison-it6el 6 ай бұрын
😂😂 Uku ndikulila kwa anafedwa tingoti pepani pepani, pakanakhala pamalilo bwedzi titatelo koma poti ndindale tingoti kadeti iwe eeeeeee wayiwala, kudandawula kwa alubino,kubedwa kwa ndalama,kubedwa kwa chimanja ndi kaduka ndangonena zochepa zomwe midzimu ya A MALAWI ikudandawula chipani sichingakhale pa tendele ikufunika DPP ilape pazoyipa omwe inapanga kwa A MALAWI and akulu akulu chilangodi chili pasi popanodi ndawonela pa DPP kmaso bwana mwayakhulazo ndendende zomwe mumapanga muli BOMA chonde chonde tsekani pakamwa panupo mukunenazo mutitsutsula mabala akale sanapoletu.MUNATIBELA MISONKHO YATHU KUNAKWANA BASI.
@user-ym6ky2wi3t
@user-ym6ky2wi3t 6 ай бұрын
Fundo ndiyakuti chakwela agula nafuko😅😅
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 6 ай бұрын
Iiii mpaka mkaz wake wamutuluka kkk
@ArnoldBinali
@ArnoldBinali 2 ай бұрын
Ofufuma ngt nafuko 😂😂
@HildatoweraMhango-et4mz
@HildatoweraMhango-et4mz 6 ай бұрын
Adausi nda chakwera amangopusitsa adpp
@MayesoChingoma-zq8fg
@MayesoChingoma-zq8fg Ай бұрын
❤ you guy you are very welcome❤
@user-oc6xd4tv9l
@user-oc6xd4tv9l 6 ай бұрын
Zimayamba choncho kenako kuponyelana mawu,kenako wuta ndi mipalilo
@mussamapira801
@mussamapira801 6 ай бұрын
Ndi chibwenzi cha mr chakwera a mai awa
@user-rc3ze2oi7u
@user-rc3ze2oi7u 6 ай бұрын
Maiwa gotani ndi opanda nzeru
@christopherchirwa7644
@christopherchirwa7644 6 ай бұрын
Apapa inu mwanama
@Moses51
@Moses51 6 ай бұрын
Akundya chibazi Ku MCP
@gaddiemkandawire6436
@gaddiemkandawire6436 6 ай бұрын
Koma zoti akudya ndrama za mcp mulindi umboni?
@maxwellgondwe2395
@maxwellgondwe2395 6 ай бұрын
Iwe ndi galu wachabe chabe kawiri kawiri kuyankha zausilu xx onkhazonkha
@shushahmuhammad-rx2hu
@shushahmuhammad-rx2hu 5 ай бұрын
Kkkkkk mbutuma Kankkhumwa😀
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j 6 ай бұрын
Nankhumwayo ndi galu payonkha ase mmmmm kaya
@gaddiemkandawire6436
@gaddiemkandawire6436 6 ай бұрын
Komaso zoti muziti zitsilu musamayankhule chonchi ayi amwene ingoyankhulani bwino bwino atchuleni athu maina awo osati zitsilu mukatelo nde kuti chani ?
@lusolawo73
@lusolawo73 6 ай бұрын
Uli pa top
CRUISE 5 WITH CATHERINE GOTANI HARA
1:28:13
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 23 М.
艾莎撒娇得到王子的原谅#艾莎
00:24
在逃的公主
Рет қаралды 54 МЛН
Just Give me my Money!
00:18
GL Show Russian
Рет қаралды 585 М.
Incredible Dog Rescues Kittens from Bus - Inspiring Story #shorts
00:18
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 28 МЛН
LIVE | PM Modi Addresses Indian Diaspora In Poland | Warsaw
11:55:00
Hindustan Times
Рет қаралды 10 М.
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Malawi News Update
Рет қаралды 197 М.
Mr Jokes Performing live at Mzuzu University, (Full Video)
33:43
Malemu John Tembo; Tidzamukumbukira bwanji ngati amalawi
22:38
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 62 М.
GOtv Malawi Izeki ndi Jakobo Kukhala Awiri Simantha
19:56
Baby rilyn123
Рет қаралды 1,3 МЛН
艾莎撒娇得到王子的原谅#艾莎
00:24
在逃的公主
Рет қаралды 54 МЛН