As a #1 fan, I tried typing out the lyrics below, in appreciation of your work 😁: Pofunika ndikonze ndi pati ma member? Verse 1: Ndani angaongole zomwe mwapinda Kuulula zomwe mwabisa Ndani angabwezeretse zomwe mwasintha Palibe (zainu) Simkusowa kudya Mbusa (fusa) Ndine mboni ya moto olusa Chipani cholamula nkhondo kwa otsutsa Chuma kwa nzeru Umphawi kwa opusa (pusa) Pre-chorus: Dekha uone Amapanga za ine ndili gone Ngati amasamalila zombe (Why would I worry) Chorus: Ndingaduse muzikhomo ayeah khomo ayeah Koma yesu alimomo ayeah Momo ayeah Andikuta ndi chisomo ayeah Somo ayeah Ndicho chindigwila nkono Nkono ayeah Chisomo ayeah chisomo (Amandigwila nkono) Chisomo ayeah chisomo (Samandisiya momo) Zikomo ayeah zikomo (amandigwila nkono) Chisomo ayeah chisomo (Samandisiya nkono) Verse 2: Ndine ochepekedwa iye ndi odzadza Nyonga zikachepa amakankha, kankha Ngini, yanga amatsata Yake ija ija Ana ake amajaja Ndikamakhala ndikamadzuka ndikamayenda Ndimadzimva chilichonse chilli mmanja mwa Namalenga Chilamulo chake pena ndikazemba Chisomo chake ch'dzadza dengadenga (wuh) Pre-chorus: Dekha uone Amapanga za ine ndili gone Ngati amasamalila zombe (Why would I worry) Chorus: Ndingaduse muzikhomo ayeah khomo ayeah Koma yesu alimomo ayeah Momo ayeah Andikuta ndi chisomo ayeah Somo ayeah Ndicho chindigwila nkono ayeah Nkono ayeah Chisomo ayeah chisomo (Amandigwila nkono) Chisomo ayeah chisomo (Samandisiya momo) Zikomo ayeah zikomo (amandigwila nkono) Chisomo ayeah chisomo (Samandisiya momo). (And you can follow me on Facebook @Tio Sambo, thanks)
@lhaniie084 ай бұрын
Truly appreciate it 🙏. Google translated most of it to english😅 nice to understand the entire song
@GriffinBanda-zi8mp7 ай бұрын
Nice song ......madala suffix anakaikaa verse ...unakavaa eish mwana suffiee " chisomo chake chachikulu koma sichifunikira lamba/ chisomo kwa patuma chisomo kwa grace eyah /
@user-wn9lm4sy1n6 ай бұрын
My favorite I think will only like to have mp3 Hair style nd gospel siri bho amwene
@tupomitole10837 ай бұрын
Feels good to be born again and vibe with Christ with bangers like this 🎉🎉🎉all to he's glory
@mcfieldmchisweka57687 ай бұрын
Straight 🙌🙌
@Shipmark_7 ай бұрын
Kumenya kugwetsa 🔥🇲🇼💯
@linlydumuka76687 ай бұрын
"Dekha uone" NKONO wa Yesu
@graciousmabaso11576 ай бұрын
Sings ndi dolo...tulutsaniso Ina 🎊🔥loving the tunes
@Njeru2557 ай бұрын
Again, Kelvin sings sings!!
@thompsonbng63877 ай бұрын
Your mother didn't raise a fool 🎉❤❤ you never disapoint💐💐💐