No video

KWACHEMA ZIPANI ZOMWE ZAYAMBA ZAPOMPANO🙌🙌🙌🙌🤔🤔

  Рет қаралды 7,324

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 30
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 3 ай бұрын
Ifee ndi ana a APM mpakana kale❤❤❤❤❤
@royie1956
@royie1956 3 ай бұрын
Musamukhomerere, ndi ufulu wake.
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 3 ай бұрын
Vuto kumalawi atsogoleri akufuna dyera. Muone aliyese akufuna kukhala mtsogoleri ndichimene chikusonyeza kuti mmupando wa wu president anthu akulemererapo ziko lathu ndilalingono koma zipani mbweeee
@NumbDee
@NumbDee 3 ай бұрын
Dpp my vote
@KondwaniJ.Nkhoma-wt5zo
@KondwaniJ.Nkhoma-wt5zo 3 ай бұрын
Mmaganizo anga zikusonyeza kuti anthu akuona kuti business yamphanvu ndi u presedent. Komaso zikuonetsa kukanika kutsogorera kwa chakwera. Tagoganizani padutsa ma purezidete anga ndipo mpresident amene watusita zipani zina ndi chakwera.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 3 ай бұрын
Zimene zikuchitika ku Malawi ndi masewela okha okha, bwanji asalowa mzipani zilipo kale kuti ukapeleke mfundo zakezo. Kutaya nthawi, za ziiiiiii!
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g 3 ай бұрын
okay Zitheka km 50+1😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 3 ай бұрын
Zipani zinazi ndi za MCP muzaziona ndakuuzani
@georgeabigailmaseko-ts3fq
@georgeabigailmaseko-ts3fq 3 ай бұрын
Zipani 40 😂😂😂
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 ай бұрын
Apm it's fine
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 3 ай бұрын
APM woooooyeeeer
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 3 ай бұрын
APM my vote ✅
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 ай бұрын
Dpp my vote ❤❤❤❤❤❤
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 3 ай бұрын
Misala yimeneyo zipani zambili mbili anthu ochepa kumalawi
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 3 ай бұрын
Zipani zinazi ndi zanyumba mwanu ndi apabanja panu,kadziko kake kati komapanga zipani zonsezi?dyera basi
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 3 ай бұрын
Atsogoleri Dyela ndiye yakula.Zinazidi Zilibe phindu Zingotisokoneza.Ubwino wake Aliyense adzasankha Icho achifuna basi
@Mahmoodwargison-op2gm
@Mahmoodwargison-op2gm 3 ай бұрын
AFORD my vote✌✌🙏💪
@amontchuwa6876
@amontchuwa6876 3 ай бұрын
AFORD better
@phindiswatshibo7101
@phindiswatshibo7101 3 ай бұрын
Dpp woye next year 😂😂😂😂
@user-oh5vs1gl4n
@user-oh5vs1gl4n 3 ай бұрын
Dpp ❤❤
@ChimmsRichardOrden
@ChimmsRichardOrden 3 ай бұрын
Akuluwa asatitayitse nthawi lakula ndi dyera
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 3 ай бұрын
🤣🤣🤣 Ati mutaima olo ukhansala mungapambane? 🤣🤣🤣
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 3 ай бұрын
Koma nankhumwa yekhayo yiwalani bola mbeweyo
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r 3 ай бұрын
Amalawi mwatitola kwambiri Eti?
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 3 ай бұрын
Zilibe ntchito zimezoo
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 3 ай бұрын
Ife ndi dpp bas chipani chimene chinalowa paka kutuluka otsa gwetsa kwacha
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 3 ай бұрын
Ndipo brother DPP ndiakatundu zedi oganizira amphawife, kutchipitsa zinthu, zitukuko ponseponse osakondera, kuthesa njala anthu nkumanjoya aliyense
@alexsumani6823
@alexsumani6823 3 ай бұрын
Wasting some other peoples time mxeuw
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 3 ай бұрын
Munthu amene angatukule Malawi nd Mr Simbi phiri basi enawa mbamva zokhazokha
@BostonGwazani-hl3bg
@BostonGwazani-hl3bg 3 ай бұрын
0/10
One-on-one with Jacob Zuma
55:52
Newzroom Afrika
Рет қаралды 1,3 МЛН
АЗАРТНИК 4 |СЕЗОН 1 Серия
40:47
Inter Production
Рет қаралды 524 М.
娜美这是在浪费食物 #路飞#海贼王
00:20
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 6 МЛН
MWAMBO OYATSA MA KENDULO KU NTCHEU 29 August 2024
27:58
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
ZOMWE ZIDALI KU NSOKHANO WA DPP 29 August 2024
24:21
HOT 265
Рет қаралды 7 М.
KUNONG'ONA - Episode 157
13:41
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 49 М.
CHITHANDIZO CHAKU MALIRO - Episode 151
12:23
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 61 М.
A MICHAEL USI SI AUTM ENI ENI
16:41
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
АЗАРТНИК 4 |СЕЗОН 1 Серия
40:47
Inter Production
Рет қаралды 524 М.