Tili nchisoni chanji,anagawana zovala zanga yesu anatero
@user-xx4jb9se3z6 күн бұрын
Wakupha uyu chilima adali amfanaoganiza bho .akutha Mau sakudziwa ZA mawa a usi mau awawa adzakutembenukilani soon.ife tli ku ma stand
@user-ve2ts3yr2n6 күн бұрын
Ndipo mukhalisepo atumwi inu.....aaaa ma compassion aanthu mpaka zaka peletu ati sanasayinile.....
@AlfredNazombe-me2ly6 күн бұрын
They think that this TTV it's belong to them kom kumakhala bwn ndi anzanu zatsogolo lamunth amaziwa ndi Mulungu
@corretabanda76856 күн бұрын
Ine sanandipeze speech yawo nsaname
@user-xc2zm9bu1i6 күн бұрын
We are waiting incompetent inquiry Poor leadership Not following the democratic values Remember next year is just around the corner Things are not working on the ground Guys we need a servant leader
@EsnartMartin6 күн бұрын
Ma guy inuyo simuli serious ndale zakulowani
@user-wx1jt5fd2j6 күн бұрын
Ndi andale ochepa amavomereza kuti chiweluzo chiliko ndi chifukwa chake samasamala za anthu Ena ngakhale akubvutika bora iwo zawo zikuyenda koma mulungu ndi oweluza olungama
@user-co3wr3rn4h6 күн бұрын
Manganya ndi ka yudasi kakafupi kwambili fiti kapha, zake chilima
@yusufbakali5 күн бұрын
❤ Manganya ndiyekhayo maso a malawi
@josephhchimpepa87536 күн бұрын
That's a good discussion! Those who have ears have heard something!
@chitanibenito11095 күн бұрын
Yaaa aghothiiii akhutukunve malo moti azitengera mphunziro pa zinzawo.
@clintonhodda98306 күн бұрын
Kodi malamulo adziko amachokera kuti ndipo amapangidwa ndi anthu akuti?
@ykzt5 күн бұрын
Walowa dziko litavunda kale palibe chingasithe apa😢😢
@blessingkamanga17816 күн бұрын
Very educative discussion
@blessiousphiri31096 күн бұрын
Suziwa zamawa yes. Fact to the point ❤
@MustafaAbdullah-pb5zv5 күн бұрын
Powerful message
@user-nw6ie3xx8b6 күн бұрын
Wishing you the best , help chakwera he is the man of God
@MichaelWilliamsNyirenda6 күн бұрын
😅 killing man
@AlfredNazombe-me2ly6 күн бұрын
Zomwe lankhula sizingatheke muone azangoti pasakhale owasokoneza nduna zina zidangowelamila pansi muona when it comes to action let's wait
@user-oj2jr6kf9c6 күн бұрын
Unawomaso eti!!?
@user-bl6km6kx7n5 күн бұрын
Mabwana chonde kuyamikila tiyamikile koma kod chikalidwe chathu monga amalawi chimati chani munthu akafa plz timakukulupililani
Tikuferanji amaLawi pomwe Manganya ali m'bwaLo??!!
@LovemoreTaulo-yj3pj6 күн бұрын
Times mcp tv mbuyomu inali times ya bwino km pano anawadyesa Baz awa
@wonganichakakanyirenda32996 күн бұрын
Inu inu abrayan musazafee
@RobertNyaude6 күн бұрын
Tizikhala bwino ndi anthu🤣🤣
@SamukLungu-zg7fl6 күн бұрын
Ausi kaya ndi usi wamutengo utiwo koma mumbari yopha chirima arimomo koma nawo apitabe basi
@maulanaallie61945 күн бұрын
Umbuli
@ZungeniBanet6 күн бұрын
Inu chupiti
@AlexKaunda-ny2eg6 күн бұрын
Agalu atatuwaso atinyasa machende anu
@adibwekumz30854 күн бұрын
That's illegal. Kupusa
@Yungjoe7866 күн бұрын
Pachoka nzako palidi Malo...
@PaulChaleka-lb4vx6 күн бұрын
Koma mcp tikuchotsa 2025 yatililitsa koopsa
@user-gs7wc3nx3q6 күн бұрын
Iya mapazi anu
@RABSONSIKELO6 күн бұрын
Moyodi ndi pelete
@polesanamakwenda69326 күн бұрын
Kkkkkk
@user-nf3ik3ff6y6 күн бұрын
Dziko latha
@ChrissySasenga5 күн бұрын
Chilima anali dolo simukunama
@ykzt5 күн бұрын
Kod pali chodyadira pamenepo anthu inu
@MAYGOSPELALBUMSChawawa6 күн бұрын
Don't take malawian as stupid because the president has got powers to make decisions like on this situation to change the decision because you can see when did we did the barial for Chilima and today you're busy enjoying with the post of vice president shamm on you mr. President and your vice president
I hate nyana these guys bcoz even they isolate Jona Pankuku every program they put Jona at last sit why and they use to cat him word on the mouth when ever he is speaking just wash 5 kwagwanji and hot current u will agree with me
@IssaJohn-cb8vn6 күн бұрын
This stupid radio this days we must stop listening and trust
@FrankKambwani6 күн бұрын
MCP yamagazi yanuyo ngakhale itachita zabwino komabe mbiri yake ndiyamagazi basi
@SaidiMbawa-st6bj6 күн бұрын
Dpp so ndi yamagazi ndiye musathe mawu boma ndi Boma
@tasmania5276 күн бұрын
Ndipo DPP yinathiphela abale athu 20 ku Mzuzu mu 2011. Yinapha Chasowa, Njaunju, ndi ma membala a UTM ku Lilongwe; kodi amenewo si magazi a anthu? Kodi anthu onsewa ophedwa ndi DPP anali nkhumba? Nde musamalankhule kuti MCP yamagazi ngati muli ndi umboni- DPP umboni ulipo.
@MaryNyirenda-nq3mh6 күн бұрын
Kod anthu mulimbalibe ya MCP yomweyo uhuuuu bola zipani zina osat MCP yakupha
@tasmania5276 күн бұрын
Za zii. I would rather support MCP than family parties of killers like DPP or UDF
@kingsleyhopematchaya51846 күн бұрын
Nanga popeza yakhala mcp yokha chipani cha phavu nanga muthu wa zaka 92 angaganize zulu zinatha tiyenazoni bola mukavote katatu aliyese koma kamodzi aaa mcp ikudutsa
@AlexAlick-bx9by6 күн бұрын
Times it's mcp TV
@MOOSANOWAH1846 күн бұрын
Kuyambila liti?
@JafaliAkimu-ll1bf6 күн бұрын
boma lolamula ndi chigawenga
@IssacMateyo6 күн бұрын
Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥
@IssacMateyo6 күн бұрын
Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥