KWAPHULIKA AUDIO YACHILIMA MU NDEGE ISANAGWE. TAMVANI

  Рет қаралды 226,803

FRANCIS MTAWAYA TV

FRANCIS MTAWAYA TV

7 күн бұрын

Пікірлер: 884
@BeatriceMagwira
@BeatriceMagwira 5 күн бұрын
One thing we should know is, when a person who has posted a vedio reaches one million views, they get paid in dollars. Ndiye imfa ya a Veep anthu, may his Saul rest in power, anthu akupangilapo business. How can someone speak so calmly when his life is in danger? Makosana, let our dear Veep rest in peace. If you want to earn money through KZfaq, please be a productive content creator but not behind Chilima's death. A big shame to everyone who is making dollars through Chilima's death.
@jimmykaunda3034
@jimmykaunda3034 5 күн бұрын
Just imagine
@bennkumbira1123
@bennkumbira1123 5 күн бұрын
My thoughts too.. Only fools will believe this audio.​@@jimmykaunda3034
@wisekanyinji5377
@wisekanyinji5377 5 күн бұрын
That's very true, this voice wasn't related to Mr veep, not at all, rest in peace our hero
@user-ok6rl9yb5h
@user-ok6rl9yb5h 5 күн бұрын
Ndipo straight
@franknamaona8906
@franknamaona8906 5 күн бұрын
Powerful comment.
@SolomonShaibuh
@SolomonShaibuh 2 сағат бұрын
Ndmakonda kuletsa nkhn zopqnda umbon but this voice it's Real direct from our hope SKC ❤❤❤
@MirriamKambale
@MirriamKambale 4 күн бұрын
What makes him talk so calmly despite knowing that his life is in danger, please let him rest in peace
@WaluSungu-gn7on
@WaluSungu-gn7on 4 күн бұрын
That ain't him this page is misleading everybody where did he get the audio? I believe it's AI at work not him speaking
@isaacsongola2897
@isaacsongola2897 5 күн бұрын
I feel this audio is doctored. He sounds so calm and not in distress. The background sounds like it has been added to the recording.
@halhimahkalhim315
@halhimahkalhim315 4 күн бұрын
Remember he was unshakable man that's why it seems calm
@ChikuHappytiwale
@ChikuHappytiwale 5 күн бұрын
Mulungu atiwululire zonse kings komwe father Msusa ananenera kuti mulungu analiko ku chikangawa
@DoreemSemu-ho3lt
@DoreemSemu-ho3lt 5 күн бұрын
Litania lamagazi ambuye yesu mutichitile chifundo Amen
@RuthJafali-tk4lz
@RuthJafali-tk4lz 5 күн бұрын
Amen ​@@DoreemSemu-ho3lt
@user-ww7rx6ke4o
@user-ww7rx6ke4o 3 күн бұрын
One day is one day!! Chilungamo chiyima moyera!!
@binosjoseph142
@binosjoseph142 4 күн бұрын
Ambuye ndinu nokha amene mukudziwa I believe that in Your time tizadziwa
@BLESSINGSMAKOMBOLA
@BLESSINGSMAKOMBOLA 4 күн бұрын
The voice is Chilima's . Izi zingopherezera zomwe ena amafotokoza zammene zinachitikira Mchikangawa kuti anthuwa afike pomwalira. If you are following everything of that crash, you will be able to connect things like these. More will be coming. No secret under the sun. Ukhoza kusowetsa umboni pobisa zipangizo zamndege and alike but simunabise Yehova Mulungu yemwe amawona chilichonse chimachitika kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto. Mulungu yemwe anavumbulutsa imfa y Abel Kaini atamukwilira mnthaka ndi yemwenso aike chilichonse poyera. Ngati inali ngozi chabe zidziwika, ngatinso zinali zokonza zidziwikanso no matter what. Lastly, I pray "God, inu mwalora izi kuti zitichitikire ife ana anu ndicholinga, chaubwino osati choipa. Tipulumutseni ku chopsa chilichonse ndipo inu kumene mukutitengera mukudziwako. Titsogolereni" Amen
@MovableSoundSquad
@MovableSoundSquad Күн бұрын
Amen zooona Mubale wanga
@Anti_social_938
@Anti_social_938 5 күн бұрын
Nanuso mwasowa Nkhan et . Let Chilima rest in peace please
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 5 күн бұрын
Iweyo ndamene wasowa chochita bola ngat sukufuna kuva better no comment
@TachikoMwanamanga
@TachikoMwanamanga 5 күн бұрын
Osangosiya osavela bwanji. Mwasowa zochita ndinu mukhala busy kumvela
@Anti_social_938
@Anti_social_938 5 күн бұрын
Haha mulibe zonena ma guy . Let him rest .
@Anti_social_938
@Anti_social_938 5 күн бұрын
@@TachikoMwanamanga tikuyenera kumvera kuti tidziwe kuti akulawa alibe content ngakhale mukuti ndi a content creator... Koma this is just complete BS ..
@LukaThawe
@LukaThawe 4 күн бұрын
Matumboyino palibe zachelu apa mathyaka mundikwiyiskenge
@tasmania527
@tasmania527 5 күн бұрын
The other voice is either AI mimicking Chilima's voice or it is someone else mimicking Chilima's voice. Either way, the one behind all this wants to build a case that Chilima knew his fate before the crash and that he knew the Masterminders. But the question is: why would Chilima board a plane knowing there's a plot to crash it or knowing he would die? Did Chilima speak while in the plane? Everything doesn't add up. This is all fake. Musamapeke mabodza ndikumapakanawo anthu ena, this can create civil conflict.
@Midy265
@Midy265 5 күн бұрын
I agree with you...
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 5 күн бұрын
This is Chilima's... Mkunamizana apaa
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 5 күн бұрын
This is Chilima's voice, I can hear other people crying
@user-gm9xj1wc2m
@user-gm9xj1wc2m 5 күн бұрын
Number
@tasmania527
@tasmania527 5 күн бұрын
@@JusticeNyirenda You recorded him in the plane or outside? Who extracted the voice, and from what source? Phone possibly? Who got hold of it? This is all nonsense. A Malawi, khalani anthu amene ali productive not kukhala busy ndi social media propaganda.
@FrankKambwani
@FrankKambwani 4 күн бұрын
Ine siwandale mmm apapa pali kabodza voice siya Chilima.kuti munvetsetse azimayi akumveka pansipansiwo akumvera alimkati mwachina chake pamene akuyankhulayu akumveka alipanja mosiyana ndi mpweya wake.
@MovableSoundSquad
@MovableSoundSquad Күн бұрын
Inuyo nde ndinu abozatu Akuyankhulayo ali mkati and ndi voice ya Chilima imeneyo nde sound ikumvekayo ndi ya chani
@QassimuKatsobola
@QassimuKatsobola Күн бұрын
Kukupa zafikapa ndikumayakhula zonyera app
@QassimuKatsobola
@QassimuKatsobola Күн бұрын
Kupusa galu iwe
@FionaKhoma
@FionaKhoma 5 күн бұрын
Ndichilima azimayi akumvekawo ndiomwe anamwalira nawo athu amene mukutsutsanu ndiinu achakwera akutsogozan kuti muyakhe km mwini wake chilima watchura ekha mainawo amene mwayakha koyambanu ndiwachiwiliwe machende anu mukuikira kumbuyo chakwera ot mwiniwake chilima wamutchura dzina ndizoona izizi kukhot kukufunika
@PatriciaNabanda
@PatriciaNabanda 5 күн бұрын
I agree with you 💯
@Henry_Banda
@Henry_Banda 5 күн бұрын
Only idiot will believe this Audio, for someone who understands will clearly hear chilima's voice, sound of the plane and clies of people were not recorded same time. So many things are not adding up in the Audio
@DuniaMalinga-gw7of
@DuniaMalinga-gw7of 4 күн бұрын
I agree with you dear
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 4 күн бұрын
Agalu amcp akuyikila kumbuyo namachende chakwela
@KhefasKhembo
@KhefasKhembo 3 күн бұрын
Ayi sichilima
@StevenTembo-mb7rm
@StevenTembo-mb7rm 5 күн бұрын
Iyi siyojudula ndi ndendende SKC komanso voice ya azimayi ikumvekanso
@user-rv8pq8yg4s
@user-rv8pq8yg4s 4 күн бұрын
Real voice yachilima iyi ndipo azimayi akuveka pasi pasi kulira ndithu,
@Paenda-pt6gb
@Paenda-pt6gb 5 күн бұрын
The voice doesn't come anywhere close to that of Chilima's.
@Peterchirwa-tf1ox
@Peterchirwa-tf1ox 5 күн бұрын
Ubwino wake, he said, it's not it but it's just sound like, 50%, true or Felse 50%.. One day we will all know...
@BlessingsMafuleka
@BlessingsMafuleka 4 күн бұрын
Mmmm simau a chilima voice yot ndege ukugwa ingamaveke choncho
@QassimuKatsobola
@QassimuKatsobola Күн бұрын
Galu iwe sukuva bho bhoo mot
@happychavula4469
@happychavula4469 4 сағат бұрын
ndiposo iyeyo anadekha dwanji upakakuyankhula mopanda matha mmmmmm
@augustMag
@augustMag 5 күн бұрын
Pamaso panu Ambuye palibe Chobisika Mulungu atipase mayankho pa ifa ya munthu vice president Chilima komanso ndi anthu onse amene anali mundegemo I am sure kuti mwezi mwa anthu amenewa singapite pachabe 😭😭
@MphatsoKaliza
@MphatsoKaliza 4 күн бұрын
😭😭😭😭😭
@MercyJohnsonkanchure
@MercyJohnsonkanchure 2 күн бұрын
Ndipo zoona Mulungu akuva ndipo akuona 😭😭😭😭😭😭😭
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 2 күн бұрын
Amen 🙏🙏 mulungu si Lazaro
@DesmondOzuzu
@DesmondOzuzu 5 күн бұрын
All in the hands of God almighty n watch listening n pray
@RobertNkhomanyamuka
@RobertNkhomanyamuka 2 күн бұрын
Mmmm zoona
@AndyChisunda
@AndyChisunda 4 күн бұрын
Mwatipasa zopepuka. Mwapeleka interview yayitali mmalo mwa audio yayitali mogwilizana ndi chiyembekezo chathu malingana ndi mutu mwapeleka.
@BlessingsMikeyasi
@BlessingsMikeyasi 5 күн бұрын
God is good we are going to here everything soon
@tenfordmacboby
@tenfordmacboby 5 күн бұрын
Zovuta, mulungu ndiye mfumu yopanda chinyengo
@evans4613
@evans4613 5 күн бұрын
These are two different voices all together. The real Chilima spoke with boldness.
@ChiefJustin-cl8jl
@ChiefJustin-cl8jl 5 күн бұрын
The voice is very different. But that doesn't change anything the man is gone 😭
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 4 күн бұрын
If you say so then why people their need to investigation?
@user-jk7pd8yn3w
@user-jk7pd8yn3w 4 күн бұрын
Very deferent
@chekiamaabdul5083
@chekiamaabdul5083 4 күн бұрын
Can't change anything at all only Allah knows best
@GreshamKadzembe-tn8cq
@GreshamKadzembe-tn8cq 5 күн бұрын
Mulungu anatipatsa mutu mzeru kuti tidziganidza, munthu wafa kare alankhulanso bwanji pa audio, mawu amene akunvekawo si achilima, achilima mawu awo anali akulu sono uyuyu mawu ake ndi angono zikustsiyana kutalitali
@vitumbikochinguwo6227
@vitumbikochinguwo6227 5 күн бұрын
Their is no linked any thing nonose
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 5 күн бұрын
Anu amedia tiyeni kumachita zithu zodzetsa mtendere osati zimene mukukozazi , munthu wamwalira angakhaleso ndi mau ngati amenewa ?ife tonse tikulira olemekezeka avice president kuti sanapite ndi imfa yabwino komaso Inu atolakhani kabweletsani zithu zomveka osati mbwelera ngati zimenezi ifeyo mitima yathu ili mmalele
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 5 күн бұрын
Yes mau ndi a achilima
@leviefeston7626
@leviefeston7626 4 күн бұрын
Akulu usakane ndimau chilima awa ndipo ndi Munthu ekhayo amene anali olimba mtima mundegemp kut unve mkatimo uva mau achizimay kulila
@user-us9et2fq3k
@user-us9et2fq3k 4 күн бұрын
Ineso ndimatha kupanga izi,munthu angayakhule zimenezi munthu atafa koma kkkk poor editing, tipezeni tikupangireni ixi ndikudya kwanthu uku
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 3 күн бұрын
Remember, next will be us.... You and me... Izakhalanso history komaizakjala yopanda phindu, chofunika ndikukonza ubale wathu ndi Mulungu.... Mbiri yathu, izakhala yotani kwa Mulungu? 😭
@user-vq7rs7zj2r
@user-vq7rs7zj2r 5 күн бұрын
Ndiyemweyo anthu macadet a mcp musamangolesa zilizonse, and nkazi wachakwera uja ali ndizambiri sure
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 5 күн бұрын
That is real chilima,,chilima anali muthu olimba mtima even mwina ngozi itachitika ngati adali ndi moyo ndimulungu yemwe mwina adapangitsa kuti audio akwanitse kutero,,mulungu ndi wadongosolo,,zikhoza kutheka izizo.koma ndikulakwa kumeneku.
@IssaZiyada
@IssaZiyada 5 күн бұрын
No way that's a true voice of our loved may his soul rest in peace
@akuzikekamchacha2370
@akuzikekamchacha2370 5 күн бұрын
Then you dint know chilima
@user-be1ox7jk3i
@user-be1ox7jk3i 4 күн бұрын
That’s not Chilima’s voice it’s AI
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 5 күн бұрын
The voice seems chilimas but there is no tension
@frankdomingo1109
@frankdomingo1109 5 күн бұрын
So I think our king would have been tensed even in death...he was ready for it daily.
@johnandreya420
@johnandreya420 3 күн бұрын
To my oppinion, it shows the time this was spoken doesn't seem any danger happening
@hannakacha5245
@hannakacha5245 3 күн бұрын
I don’t see how any person could stay that calm in such a terrifying situation. Allow this great man and the souls of the other eight to rest in peace please
@FelixMcDonard
@FelixMcDonard 5 күн бұрын
Mulungu analiku chikangawa komweko😭😭💔💔
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 5 күн бұрын
Amene akusutsana ndi voice iyiyi kuti siyachilima siku lachiwerudxo ndiwakumoto kumbaura .
@Mohammed-sk1fy
@Mohammed-sk1fy 4 күн бұрын
So sad 😢😢😢😢😢
@SimeonMicah
@SimeonMicah 3 күн бұрын
Voice is so calm meaning ndiya copy. Imeneyo.
@QassimuKatsobola
@QassimuKatsobola Күн бұрын
Galu iwe wa mcp aku akudziwika mavaphaya
@NilaGondwe
@NilaGondwe 5 күн бұрын
This is voice no secret under the sun my heart so broke
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 5 күн бұрын
Wanyera apa ndani ?ayi si ine chonsecho akupeza ukukwezera trousers patchire anthu ayaluka tazimvera tokha audio ilibe propaganda.
@dalitsonkonya7241
@dalitsonkonya7241 5 күн бұрын
Iiiiii.... Real voice iyi azimayi akumvesa kulira pasipasipo
@GreshamKadzembe-tn8cq
@GreshamKadzembe-tn8cq 5 күн бұрын
Akunveka kulira which means ndi kumaliro achilima ndiye funso ndilakuti, kodi anadzuka nkumapanga record??
@rafiqsaidithepoet
@rafiqsaidithepoet 5 күн бұрын
@@ellanivytaulo9073 anthu ena ndi achamba
@McDonaldLembani
@McDonaldLembani 4 күн бұрын
He sounds something like calmness... How can he speak so calm like that while he's in obstacles 😢??
@brudgetmambwe463
@brudgetmambwe463 4 күн бұрын
Am not a Malawian but a human being, this is s great shocking loss for Malawi and his family. No need to bring more pain to the situation. Let their souls rest in peace. 😢
@dsabwe2024
@dsabwe2024 3 күн бұрын
This is a very dangerous and very naughty post. May the VP Chilima and all who died continue to rest in peace. Do not find comfort in causing confusion
@mercychakwera6498
@mercychakwera6498 Күн бұрын
Sir you think malawian are fools Moto sufuka popanda utsi
@owenskabazanechiumia3543
@owenskabazanechiumia3543 5 күн бұрын
Those two voices are similar, and they are the same for Chilima, and the women heard crying deeply in another short voice for chilima😢It heard like, that was the voice after the plain was just exactly crashed.
@MisheckAselo
@MisheckAselo 5 күн бұрын
Mzimu wa chilima uziusa mumtendere komanso utiunikire mpaka chilungamo chidziwike, iwo sadapite kumanda ndi anthu anyau anapita ndi anthu amzimu wambuye. RIP Mr president 😭😭
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss 5 күн бұрын
Amen
@user-qb2lt6qj1p
@user-qb2lt6qj1p 5 күн бұрын
Mau a chìima ndiomwewa ndithu
@chimwemwephiri7627
@chimwemwephiri7627 5 күн бұрын
He is the one😢😢😢😢
@user-bm3po9dx3x
@user-bm3po9dx3x 5 күн бұрын
Kkkkk koma anthu mumatha zinthu.... akanakhala iyeyodi voice ikanamveka mwamañtha chifukwa ndege inali ikupita kokugwa guys
@user-ky8eq5ek1p
@user-ky8eq5ek1p 5 күн бұрын
Ndizoona ndithudi Chakwela nditimuyake ndiameneanapangazinenezi.
@user-mq3mh5md5e
@user-mq3mh5md5e Күн бұрын
Zoti zinthu zinabedwa ndege itagwa ndi bodza achi lima anapezeka ndi cash mthumba,watch ndi korona chonde mukulemba izi chenjerani mukamangidwa muzazioona,,,,,,musapupulume dikirani kafuku fuku amene akupangidwa nda katwiri aku Germany
@mercychakwera6498
@mercychakwera6498 Күн бұрын
If Germany is in touch with our government this won't work unless they find an independent group to do the investigation. Otherwise the truth will never prevail
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 5 күн бұрын
Zikunvekeza bwino bwino ndikulira kwa anthu ena omwe anali m'menemo.
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 5 күн бұрын
Number 1
@FranciscoKamange
@FranciscoKamange 5 күн бұрын
That is Chilima's voice......bcz you can hear also a voices background and sound of a Plane ....
@mipeacemakermw9501
@mipeacemakermw9501 4 күн бұрын
Yes of course there is sound. But u have to listen to it very well. Chilimas voice is very clear 😅😅😅😅
@princechafutsa3352
@princechafutsa3352 4 күн бұрын
Zitsiru mulipo ambiri
@Okalekale
@Okalekale 23 сағат бұрын
Kkkkk,you can easily be fooled.Inuyo ndiye ma target a channel yi.Musandiseketse inu plz
@juniortsegula3847
@juniortsegula3847 5 күн бұрын
Ndiyemweyo😮
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 5 күн бұрын
Oh really,yes this audio must go together with the phone it came through when going to court and when evidence is there
@DecemberAstonsunset
@DecemberAstonsunset 5 күн бұрын
The background sound is repeatedly whis proves to me that its edited and the use his voice to make it sounds more likely but it's not really
@isaacsongola2897
@isaacsongola2897 5 күн бұрын
As a sound engineer myself, I totally agree with you. This has been doctored
@user-ln5xd9my8i
@user-ln5xd9my8i 4 күн бұрын
Ndyemweyooo chilima keep on updating us our VP is gone
@fosterkashoni9100
@fosterkashoni9100 4 күн бұрын
Umbulitu uwu, mundege sayankha 4n
@user-dn8pt4uz3q
@user-dn8pt4uz3q 4 күн бұрын
Tili pa diwa amalawi😢😢chakwera achoke wakupha MCP yama ngazi😢😢😢😭😭😭
@ShadreckChipojola
@ShadreckChipojola 5 күн бұрын
That's very true indeed this is a voice of chilima rest peace (RIp)
@jamesWilson-xn4qo
@jamesWilson-xn4qo 5 күн бұрын
Apanso palinso kufuna umboni wina kapena tikamusosole ku state house komweko azatiuze chilungamo. 😢
@chievocollins
@chievocollins 4 күн бұрын
Kwa inuyo umeneu ndi umboni ?
@charlesmasauko4651
@charlesmasauko4651 4 күн бұрын
People will make alot of money with this incident, but at same way we are getting ideas of what happened. Nobody is believing that Chilima's death was natural accident, so in the end will understand the truth either is a created plain crush or natural. No secrets under the sun
@Christopherpioh
@Christopherpioh 5 күн бұрын
Mboni yaikulu ndi Mulungu let God be God
@JacobSoko-es2uh
@JacobSoko-es2uh 4 күн бұрын
No doubts about this its Chilima's voice may his soul rest in peace
@RichardKaunda-lf2nl
@RichardKaunda-lf2nl 3 күн бұрын
Ili ndiye bodza la come & see,this is a well doctored voice note just to ashame someone who has nothing to do with it
@user-te1kl3ze9m
@user-te1kl3ze9m 5 күн бұрын
Amene akuti mbuli zinachuluka iwowo ndi akuti
@AnthonySiyasiya
@AnthonySiyasiya 5 күн бұрын
It's Exactly our let vice president of Dr Soulos klous Chilima
@user-ss9bj5eh6b
@user-ss9bj5eh6b 4 күн бұрын
exactly the voice of chilima and you can hear inside people crying
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 5 күн бұрын
Someone who survived a plane crash will and can never speak so calmly like that person.
@michaelcohen2372
@michaelcohen2372 4 күн бұрын
The audio was recorded before the plane crashed, tamamvesani chizungu
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 4 күн бұрын
@@michaelcohen2372 You don't have common knowledge, why did he board that doomed airplane if he did know their plan. Don't be a fool bro.
@Okalekale
@Okalekale 23 сағат бұрын
​@@michaelcohen2372iwenso ndiye ukanakhala m'mbale wanga ndikanakunyanyala.Tulukani mugombeza inu,kunacha kale kale.Simunganve kuti mauwo ndiochita kupangidwa si Chilima,kapena simunanveko za AI?.Eish,aMalawi enanu mumatitukwanitsa bwanji.
@user-ps1hv9vy4q
@user-ps1hv9vy4q 3 күн бұрын
Si mau a Chilima ndipo mau oti munthu ali muululu sangamaveke choncho .... Continue resting in peace Our favorite VP 😓😭
@AuspiciousKalambula-hp7gj
@AuspiciousKalambula-hp7gj 4 күн бұрын
Exactly! The voice is the same, rest in peace comrade chilima
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 5 күн бұрын
Iyi ndi voice yakedi late Chilima, zonse zoululika , mulungu aliko.
@user-ty4pq5ub3q
@user-ty4pq5ub3q 3 күн бұрын
100% CHILIMA'S VOICE.
@MargretSlinger
@MargretSlinger 2 күн бұрын
Aaaah ndi mau vp awo ngat ndinganame AMBUYE okhala kumwamba andikhululukire koma mullungu akuziwa zonse
@FarooqPias1625
@FarooqPias1625 14 сағат бұрын
Even olo mawuo atakhala ao sakukwanira kukhala umboni oti anachita kupedwa ndi anthu amene akuchulidwao. Ifa ikamakuyandikira zimatheka kutchula even agogo ako ndamene abweresa ifayo chifukwa choyandikana nowo, olo mwanawako kumene,mutha kumuchula, ifa guys ndiyowawa.
@pempheroraynnoxmpesi8713
@pempheroraynnoxmpesi8713 4 күн бұрын
He sounds so calm.. it doesn't add up
@user-ck3ld8nx7l
@user-ck3ld8nx7l 5 күн бұрын
This voice is belongs to late Vice president of Malawi.May His Soul Rest In Eternal Peace.
@akuzikekamchacha2370
@akuzikekamchacha2370 5 күн бұрын
It is not the grammer is off boss
@Dentera215Music
@Dentera215Music 5 күн бұрын
Ma barz a voice waphatikizawo achepa nkovuta kutolera zenzeni.
@Okalekale
@Okalekale 23 сағат бұрын
Za ma phone zonso akunama,phone ndi wrist watch zinasungidwa ndi akunanfedwa according ku eulogy ya elder brother was late VP pa Mwambo wa maliro.
@godfreyedwinmwale2477
@godfreyedwinmwale2477 4 күн бұрын
taking no sides, how is he sounding very calm in an accident of such a situation? I personally loved Chilima very much but I feel that is AI
@EmmanuelKazembe-rw1mb
@EmmanuelKazembe-rw1mb 3 күн бұрын
Yes exactly is him God please show us justice
@user-sr6fb3dw2y
@user-sr6fb3dw2y 3 күн бұрын
Azibambo àkulu akulu ngati inu mwakuliramo basi komangokhqlira bodza zoona. Musiireni mulungu plz.chobisika chidzaululikq
@HEZEKIAMajuta
@HEZEKIAMajuta 5 күн бұрын
😂😂😂😂😂the audio u say is not same size 😂😂 rest well SKC
@user-ym6xb9cy8u
@user-ym6xb9cy8u 5 күн бұрын
Real voice ya chilima 😢 chakwera ND gwenembe wachabechabe ,,, almighty God if chakwera is responsible the death of chilima punish him 🔥🔥🔥 ngati sakuziwapo kanthu mukhululuke
@olipamaseko2693
@olipamaseko2693 3 сағат бұрын
Let's wait for kafukufuku zolankhula zathu zitha kusokoneza chilungamo Mulungu akumva ma dandaulo athu
@nellanzimba8181
@nellanzimba8181 5 күн бұрын
ndiyemweyo bas
@McomexChitsumba
@McomexChitsumba 3 күн бұрын
Mmmmmm azathu zidangovuta kuti mulungu alikutali koma uyuyu si chilima ayi . Zokonza izi may the. Soul of SKC rest in peace
@user-sm6pr9cg2q
@user-sm6pr9cg2q 5 күн бұрын
As much as people around the environment said the Air plane stop formore than 10 minutes meaning the massage of people abord have and they might talk. Wait until the probe
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 5 күн бұрын
That's not true that plane can't stop in the air like a helicopter .lf you can google you will learn .sizaumbulizo Plane inayima for 10 mins . that's insane
@edonellzrmw
@edonellzrmw 5 күн бұрын
😮😮😮his voice sounds calm though. Wasn't he supposed to be panicking in that situation. Ion know man but if its real then its sad
@raytavares2256
@raytavares2256 5 күн бұрын
It is a genuine voice code of late KS Chilima however the arficial intelligence soft ware has been used to articulate the coded voice of the lateVP.
@isaacsongola2897
@isaacsongola2897 5 күн бұрын
This audio has been doctored. They have just used Chilima's voice
@Amgwagwa
@Amgwagwa 5 күн бұрын
Tsono mwati chani mutu wankhaniyi
@fannyzimba149
@fannyzimba149 4 күн бұрын
A man die when he is forgotten 😭 Gone but not forgotten 😭😭😭Keep Resting in peace Mr Saulos Chilima
@GrantMCharles
@GrantMCharles 5 күн бұрын
Aaaaa I'm still thinking about the audio
@AtupeleLikwanya
@AtupeleLikwanya 5 күн бұрын
Kkkkk mwalephera kufananiza mau 😂
@user-go4pg6qp5g
@user-go4pg6qp5g Сағат бұрын
A Ashiii, voice ndi yake but sakanalankhula modekha choncho imfa akuyiona komanso sakanakhala ndi nthawi yotchulira mayina koma kunenapo zachomwe chinavuta
@aliekay1348
@aliekay1348 5 күн бұрын
Kufuna ma subscribers bwanji...!? Zabodza zakezo hiiii
@WilliousNyirongo
@WilliousNyirongo 5 күн бұрын
Ladies & gentlemen! becareful,for w shalll be answerable on judgement day. Every word that a person utters doesnt fade but stands untlil judgement bar. Yes we have the mandate & free will to say anything but truth will prevail & make us inocent people in the presence of God.
@Yungjoe786
@Yungjoe786 4 күн бұрын
💯 % that's his voice....But the good thing is palibe wamuyaya zonsezi za Tempolale.
@chidimoksy-rg7go
@chidimoksy-rg7go 5 күн бұрын
Secrets will be exposed one way or the other and God is Watching
@AufiThera
@AufiThera 5 күн бұрын
This voice exactly chilima 100% I know him even when am sleeping I gonna tell you KT mau awa ndi achilima
@chievocollins
@chievocollins 4 күн бұрын
How can someone whose life is in danger speak so calmly? Clout chasers everywhere shame
@AbelKaludzu
@AbelKaludzu 4 күн бұрын
Then you didn't know Chilima
@Chipiemangani
@Chipiemangani 4 күн бұрын
Was the voice spoken before or after the clash??? Coz I don't understand it propa
@RomeoPrecious
@RomeoPrecious 4 күн бұрын
Inu mwadzitengakuti musakhale inuso wangopanga recording ndikumatisokoneza mutu apa izi zisiyeni ziululikq bwino bwino chilichose chikhqlqa mmalomwake ndipo mbewa ina iwonekela poyela
@halhimahkalhim315
@halhimahkalhim315 4 күн бұрын
If I search in my self I once find that I can copy the voice of someone but not it's tongue..there is something true in this voice 2 much familiar 😢😢
@dearntv6875
@dearntv6875 4 күн бұрын
Ku Malawi kuli drama😂 someone has time to record an audio after plain crash and die afterwards as if it a Nigerian movie 😂😂😂
@patricklichapa9297
@patricklichapa9297 4 күн бұрын
Koma ngozi mumayidziwa Inu?? Life kunkhara pa chiopsezo Munthu angalankure nchoncho?? Muli pa tchito yayikulu,, anena kale Usi kuti pa ntanda panali Atatu koma aliyese analankhura
@thiyahdyton
@thiyahdyton 5 күн бұрын
Angofanana mauwo, koma siawo
@davidjames679
@davidjames679 4 күн бұрын
very different!!! and underground pa voice yakugwa kwa ndege pakumveka anthu kulila what are they crying??? meaning audio ndiyopanga record after the plane crash ,SKC REST IN PEACE tichotse umbuli amawi amzanga
@joycelupiya5027
@joycelupiya5027 5 күн бұрын
Mau si a Chilima awo. Please let the man rest in peace.
@AlinafeNafe-s8p
@AlinafeNafe-s8p 5 күн бұрын
Hi
@user-jy4do9iy1j
@user-jy4do9iy1j 4 күн бұрын
Fighting for views Mbuzi iwe
Пробую самое сладкое вещество во Вселенной
00:41
孩子多的烦恼?#火影忍者 #家庭 #佐助
00:31
火影忍者一家
Рет қаралды 3 МЛН
MEGA BOXES ARE BACK!!!
08:53
Brawl Stars
Рет қаралды 33 МЛН
BON KALINDO LERO PA 28 JUNE NDETU JULI NKHANI |
17:01
DZIWE TV
Рет қаралды 28 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 121 М.
8 year anniversary of the Brexit vote
20:42
Times Radio
Рет қаралды 22 М.
Arsenal latest news: Kimmich transfer links | Gyokeres rumours | Jorginho criticism | Eze reaction
20:23
Charles Watts: Inside Arsenal - News and transfers
Рет қаралды 35 М.
ZOMWE AYANKHULA VICE PRESIDENT MICHAEL USI.21 June 2024
15:51
A Simbi Phiri Akhuza Imfa ya Dr. Saulos Klaus Chilima
22:44
Zodiak Malawi
Рет қаралды 78 М.
Ofunika Kupanga Zoti Achina Chakwera Athawe | Watelo Khad
10:01
A UTM Nthawi Yakwana Mubwelele Komwe Munachoka - Bon Kalindo
14:26
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 105 М.
KUCHIPANI CHA UTM CHADABWITSA ANTHU🤔🤔
49:16
HOT 265
Рет қаралды 68 М.
Ozoda - JAVOHIR ( Official Music Video )
6:37
Ozoda
Рет қаралды 6 МЛН
Duman - Баяғыдай
3:24
Duman Marat
Рет қаралды 79 М.
Райымбек Нысанбек - Сүйдім аруды
3:39
Райымбек Нысанбек
Рет қаралды 71 М.
Iliyas Kabdyray ft. Amre - Армандадым
2:41
Amre Official
Рет қаралды 119 М.
Kobelek
4:11
6ELLUCCI - Topic
Рет қаралды 82 М.
Алмасхан Насыров - Ауылға барасың ба? (official video) 2024
4:14
Алмасхан Насыров
Рет қаралды 122 М.
DAKELOT - ROZALINA [M/V]
3:15
DAKELOT
Рет қаралды 321 М.