MALO ABOMA AYAMBA KUTENGEDWA KUMAGWIRITSIDWA NTCHITO NDI CHIPANI

  Рет қаралды 8,573

TIDZIWE TV

9 ай бұрын

Пікірлер: 13
@omanm2919
@omanm2919 9 ай бұрын
This nkhanga is the eyes of poor Malawi continue Komuledi
@user-md5uv2cg6i
@user-md5uv2cg6i 9 ай бұрын
Kuona mwaona koma palibe chosintha tapezani futi kuti wausiluyo azingophedwa
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Nkhanga zaona
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw 9 ай бұрын
No Brian amubwezelese sikukomaso MBC please
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr 7 ай бұрын
MCP boma loipa sheet
@user-nw6ie3xx8b
@user-nw6ie3xx8b 9 ай бұрын
Aaaaaa zaboza izi
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr 9 ай бұрын
Kodi chakwera ukamalimbana ndikumapha anthu nkumawalanda chuma amakhala kuti akuyamba chiyani udzifunse wekha chakwera pachitengereni boma wapha anthu angati komanso anakuyamba chani cholepheresa kukambirana nkutha koma kokathera nkukhala kumanda upresidernt simbali yanu vomeredzani. 😂😂😂😂😂
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Koma izi nkhanga zikuona patali kkkkkkkkk
@WonderMinjale-bg6kd
@WonderMinjale-bg6kd 9 ай бұрын
Pano nýakwawa ina ku Neno ayilipiritsa kamba kothamangitsa alangizi omwe amadzatorera ma ID
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 9 ай бұрын
Thanks bg
@husseinmoffatt
@husseinmoffatt 9 ай бұрын
Bomailindi lakuba azisogoleliawa ndi manyiokhaokha
@marryphili5419
@marryphili5419 9 ай бұрын
❤❤❤
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e 9 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤