Mbiri ya Dr Bakili Muluzi PART 1

  Рет қаралды 92,090

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

3 жыл бұрын

Dr Bakili Muluzi ndi president wakale wa dziko la Malawi🇲🇼

Пікірлер: 75
@bonjechaula8542
@bonjechaula8542 3 жыл бұрын
1981 bakili muluzi anaba ndalama za makad a MCP, mbava yeni yeni.
@fanizoabrahamchimbalanga6529
@fanizoabrahamchimbalanga6529 3 жыл бұрын
God bless bakili muluzi adathandiza amalawi kuwachotsa muumbuli waukulu
@amisichiphiri8227
@amisichiphiri8227 2 жыл бұрын
Kwambiri anatisambisa kumanso
@ImeedFranck
@ImeedFranck Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 15 күн бұрын
Better anatipangisa tinkhare ndi maphone pano tikunvera pa phone good man
@davidbulla9390
@davidbulla9390 Жыл бұрын
Wonderful di
@Littlefair7
@Littlefair7 3 жыл бұрын
Kodi achair kuba anayambira patali eti? Mpaka kuba £6? Ndi kudzasololanso K1.9bn
@franciskaponda8608
@franciskaponda8608 3 жыл бұрын
Komanso kulemera pamaso pa kamuzu zizinali zocheza ayi ameneyu adzafotokoze bwino part 2 akunenayo akhatiuza kuti a Gadama ndi amzawo aja akhati mukutipheranji akuwakhoma ndi hamala iye anali kuti ????????
@lastlevel1999
@lastlevel1999 3 жыл бұрын
We will waiting for part 2
@mosesharoldngolombe
@mosesharoldngolombe 10 ай бұрын
Anyamata apa town❤
@charlesmuyaya8839
@charlesmuyaya8839 3 жыл бұрын
Thanks for the info. Keep it up
@EsnatSayiwala
@EsnatSayiwala 2 ай бұрын
Wow ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@ibrahimyusufu3927
@ibrahimyusufu3927 2 жыл бұрын
FDU... NICE
@fredrickkhebozy6683
@fredrickkhebozy6683 3 жыл бұрын
Well done sir
@maongambonde1004
@maongambonde1004 3 жыл бұрын
Kamuzu inali mbalame
@sharifsaidi6706
@sharifsaidi6706 3 жыл бұрын
Please upload it, we are waiting
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 Жыл бұрын
I like this man chair
@richardnkosi1934
@richardnkosi1934 3 жыл бұрын
Anagwetsa dziko la Malawi koposa Mafia wakuba
@mouricesaidi5348
@mouricesaidi5348 3 жыл бұрын
oky?????? zako zimenezo
@m00n_pInK
@m00n_pInK 3 жыл бұрын
kuti malawi ilowe pansi ndi bakili akuluwa amakondela zoika apa.
@bashirbanda6519
@bashirbanda6519 3 жыл бұрын
Timakunyadilani tiphuzila zambili kuchokela kwainu
@chimwemwechimwaza7512
@chimwemwechimwaza7512 3 жыл бұрын
Bakili ndi mbuz imoz ya president mu africa opanda vision aaah tisabise apa
@m00n_pInK
@m00n_pInK 3 жыл бұрын
zoonadi abraz.
@BashiruIshumael
@BashiruIshumael 5 күн бұрын
​@@m00n_pInKndi dolo wachiyao tinakuonesani kuona patali panya panu
@hardworkkayuza6353
@hardworkkayuza6353 18 күн бұрын
Anyamata othamanga pa town
@BashiruIshumael
@BashiruIshumael 5 күн бұрын
Wachiyao kwao kutulutsa wangalutsa
@umaliisah6920
@umaliisah6920 3 жыл бұрын
Fast part 2
@user-we4ue5dc4e
@user-we4ue5dc4e 2 ай бұрын
Anatiombola ,palibe analimba mtima nthawi imeneija.
@olipamaseko2693
@olipamaseko2693 Жыл бұрын
Narrator sangayankhule zonse zoipa za Bakili ndi abwana ake amenewa agwira ntchito ku Bakili muluzi tv
@taongahshaba
@taongahshaba Ай бұрын
❤❤❤❤❤❤
@humairamalombe295
@humairamalombe295 8 ай бұрын
Nawoni osawasiya abwele poyela masatanawa
@olipamaseko2693
@olipamaseko2693 Жыл бұрын
Bakili anali wamabodza kwambiri ndi amene anapangitsa kuti dzikoli lisauke kwambiri atagulitsa ma company onse a boma ndalama ndi kunyambita
@yamikanimkanthama4354
@yamikanimkanthama4354 4 ай бұрын
APA NDe mwakwanilisaatu
@shabbanmatewere439
@shabbanmatewere439 3 жыл бұрын
Dr Muluzi /kuchitekete
@lovemapwina6661
@lovemapwina6661 3 жыл бұрын
Following
@nkhwaziaeros1845
@nkhwaziaeros1845 2 жыл бұрын
nkhani ya mcp or bakili muluzi? adha inu penapake simumakhala objective with your narration
@hurdgejanatu1812
@hurdgejanatu1812 Ай бұрын
Wachi Yao uwejo
@warlubie
@warlubie 2 жыл бұрын
I do owe his car from 1998
@PeaceIslsm
@PeaceIslsm 11 күн бұрын
DPP❤❤❤❤❤
@PeaceIslsm
@PeaceIslsm 11 күн бұрын
Bhobho 😊
@PeaceIslsm
@PeaceIslsm 11 күн бұрын
mt😂😂😂😂😂
@KametaMasina
@KametaMasina 9 ай бұрын
❤❤❤❤
@alexanderkaunda9554
@alexanderkaunda9554 3 жыл бұрын
Kudzindikira kodula dziwalo
@allanmakwiti5145
@allanmakwiti5145 3 жыл бұрын
Ali ndi ana angati?
@m00n_pInK
@m00n_pInK 3 жыл бұрын
zokuti anapha matafale simunanenetu amwene anakakhala wa mcp bwezi ndizoipa zomwe mutanena.
@charlesmuyaya8839
@charlesmuyaya8839 3 жыл бұрын
Nkhani ya Matafale anthu ambiri munayimva mukuthamanga. Amene anakasuma Ku polisi kuti Matafale wamubera katundu wake anali O.G ISSA. Matafale anapita Ku shop kwake ndi marasta anzake nkukaphwanya katundu yense. Sizikugwirizana ndi Bakili Muluzi izi.
@charleskafodya7019
@charleskafodya7019 10 ай бұрын
Bodza tu ili adapita ku Malosa uti???
@luciuschigoga2607
@luciuschigoga2607 3 жыл бұрын
Nkhani ili apa nnja Bakili or MCP? Koma akulu awa😂😂😂😂😂😘
@charlesmuyaya8839
@charlesmuyaya8839 3 жыл бұрын
Monga wekha sukuona kuti zikugwirizana? The narrator akufotokoza zomwe zinachitika kuti Muluzi apange resign.
@olipamaseko2693
@olipamaseko2693 Жыл бұрын
Bakili anali nduna ya Kamuzu zonse zoipa amapangira limodzi ndi Bakili sikuti Kamuzu amapha yekha anthuwa ayi
@uthmanalex
@uthmanalex 3 ай бұрын
@@charlesmuyaya8839 chisiyeni amwene ndichitsiru they miss understanding amavera alipanjinga 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@hopesonnsongolo1049
@hopesonnsongolo1049 Жыл бұрын
Bakili ndi dolo
@chikondimwale7517
@chikondimwale7517 3 жыл бұрын
Ati "mfana upange resign"
@goldencitytowerent9554
@goldencitytowerent9554 3 жыл бұрын
Hahaha eyetu
@Ibrahimson-su5ks
@Ibrahimson-su5ks Жыл бұрын
Skype Skills
@olipamaseko2693
@olipamaseko2693 Жыл бұрын
Or pano ma school achisilamu Ali kuti? Awa akungoyankhula za mmutu mwao pano ndi ndani anaphunzirapo sukulu ya chisilamu ndipo zili kuti?
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d 4 ай бұрын
Masukulu achisilamu kumalawi sukuwaziwa😂😂😂
@goldencitytowerent9554
@goldencitytowerent9554 3 жыл бұрын
Mbiri ya Bakili ija mwalowaso za khaza za MCP kkk
@LouisjrSaka
@LouisjrSaka 3 жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂koma adha
@goldencitytowerent9554
@goldencitytowerent9554 3 жыл бұрын
@@LouisjrSaka kkk koma kamuzu anamulakwira chachiku mukulu ameneyu, ofcourse a MCP anali akhaza koma kumapolako
@LouisjrSaka
@LouisjrSaka 3 жыл бұрын
@@goldencitytowerent9554 chomwe adalakwa kamuzu kwa mkulu ameneyo nchachikulu heve 🤣🤣🤣🤣
@alankasiya7329
@alankasiya7329 3 жыл бұрын
Zabodza izi Bakili sanaphuzile ankagulitsa matumbi ku zomba. School anaphuzila atasankhidwa kale u president
@charlesmuyaya8839
@charlesmuyaya8839 3 жыл бұрын
So You mean Bakili Muluzi anapeza scholarship yokaphunzira ma college akunja mzaka za mma 1960 ali osaphunzira? I think mbuli ndi iweyo palibe chomwe ukudziwa chokhudza Bakili Muluzi.
@danielmaluwa7896
@danielmaluwa7896 3 жыл бұрын
Bakili muluzi ankagwira ntchito ngati clerk wa Ku court poyambilira penipeni. Ndie ukati anali osaphunzira ukutanthauza chani. Moreover bakili muluzi anali principal wa Nansawa technical college, kamuzu banda anamusankha kukhala MP komanso nduna ya boma pa nthawi yomwe anali mphunzitsi wamkulu wa pa Nansawa technical. Ndie ukati anali mbuli ukutanthauza chani. He was even minister of education mnthawi ya kamuzu. Mwina unangomvera ma propaganda a anthu kuti bakili muluzi anali osaphunzira iwe
@alankasiya7329
@alankasiya7329 3 жыл бұрын
U have been mis informed Bakili ankamphuzitsidwa school ndi Dr Ken lipenganga Ali kale president. Jce and msce anazipeza Ali kale president.
@charlesmuyaya8839
@charlesmuyaya8839 3 жыл бұрын
@@alankasiya7329 kutanthauza kuti ukutsutsa kuti Bakili Muluzi sanagwire ntchito Ku khothi ngati clerk? Sanagwire ntchito ngati principal pa nansawa college? Sanapite kunja mzaka za mma 1960 kukaphunzira ma college a ku Denmark ndi ku Britain? Sanakhalepo minister of education mnthawi ya Kamuzu? Ukamati we were mis informed what do you mean? Ife tikunena zoona zenizeni zooneka ndi maso pomwe iwe ukunena zongomvera anthu za mabodza. Bakili Muluzi was even minister of portfolio mnthawi ya Kamuzu, and you think munthu angakhale minister of portfolio ali mbuli?
@alankasiya7329
@alankasiya7329 3 жыл бұрын
@@charlesmuyaya8839 maphunzilo amene anenedwa kuti anaphuzilawo that's what I'm against kale anthu ankamphuzila up to STD 5 nkumapeza ntchito ngakhale Aleke Banda anali minister nthawi ya kamuzu koma anali ndi jc . Ngakhale ma minister ambiri muthawi ya amuluzi anali osaphunzira. Kukhala minister sikuphunzira
@kool2493
@kool2493 3 жыл бұрын
He was more worse than useless
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 3 жыл бұрын
Following
Mbiri ya Dr Bakili Muluzi PART 2
26:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 87 М.
Happy 4th of July 😂
00:12
Alyssa's Ways
Рет қаралды 67 МЛН
39kgのガリガリが踊る絵文字ダンス/39kg boney emoji dance#dance #ダンス #にんげんっていいな
00:16
💀Skeleton Ninja🥷【にんげんっていいなチャンネル】
Рет қаралды 8 МЛН
Slow motion boy #shorts by Tsuriki Show
00:14
Tsuriki Show
Рет қаралды 8 МЛН
Женская драка в Кызылорде
00:53
AIRAN
Рет қаралды 385 М.
Times Exclusive featuring Bakili Muluzi - 11 May 2024
58:41
Times 360 Malawi
Рет қаралды 211 М.
Assista na íntegra o Fala Moçambique 25/07/2024
Portal FM | Fala Moçambique
Рет қаралды 1,2 М.
CRUISE 5 WITH JETU
34:03
Zodiak Malawi
Рет қаралды 328 М.
Happy 4th of July 😂
00:12
Alyssa's Ways
Рет қаралды 67 МЛН