😂😂😂😂😂for the first time Mercy wayankhulako za mzeru
@user-xy2xs8ct2o4 ай бұрын
Sandra abakathena okazinga😂😂koma mlelemba iih😅
@isaackadayera-xd3ly4 ай бұрын
Mlelemba dzina latsopano ndi Sandra makathenda😂😂 meaning akuyidziwa yekha, kaya sandrayo anamulakwira chani kaya🤣🤣 watching from Capetown, timakunyadirani guys more fire,
@user-wq6wd9oe8j4 ай бұрын
Paja amamukwatira Sandra.
@user-rz4ks4ie5h4 ай бұрын
Mulelemba 😂 ndidolo
@user-dq9dg4rk7c4 ай бұрын
Mayi mdyangu ati akuoneka mwa chitengo tengo olo nkhope yake ikuoneka 😂😂😂😂😂
@LucyShaibu4 ай бұрын
M,busa uyu amwene 😂😂 amumpa zindi
@IshmaelNgalauka3 ай бұрын
Kkkkkkkkkkk koma yaaa mulelemba
@lukazulu-bt1kc4 ай бұрын
Mmmmmm amulelemba vomerani kuti akugwirani mpakana fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 koma nimapemphero yaboza mmmmmm mulelemba utumiki wamulungu waboza!!!!
@user-tk6qh9zs7h4 ай бұрын
More fire Guys Mercy Malangizo abwino kwa Mkazi Mulelemba
@user-rc8jn1uu8l4 ай бұрын
Kkkkk ati mwana wachithengothengo
@LuzelleHendricks2 ай бұрын
Km mureremba katumbu ichi ndichiakita ❤ mbambande
@kayondowsilumbu98284 ай бұрын
Mulelemba nice one. Ndimakunjoya
@KenedyJolamu-rs9xx4 ай бұрын
Akango atulukirano pa home 😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣 ndimuone mwana ngati akufana ndi inetu
@felixphiri24654 ай бұрын
Nepman wapata womwetamweta 😂😂😂😂😂
@user-zb6ch1zc9g4 ай бұрын
Nep man wabwela ndi ulusi dzaka dzino😂😂 big up guys
@user-lo7gq7xd6d4 ай бұрын
Iyayi sopano usatengele kutamika😂😂😂
@johnlufai26654 ай бұрын
Mwana wa queen wachithengothengo
@user-gf7yo6qj7d3 ай бұрын
Sandra bakhathena mlelemba😂😂😂😂
@PatriciaMitengo4 ай бұрын
😂😂😂😂 khwini watha nzeru eeeeeee koma kuli zinthu mpaka Mercy malangizo😂😂😂😂
@kelvinkhudze62414 ай бұрын
Mwanawankango kuzangotulukila😂😂😂😂😂😂😂😂
@lingstonenagoli77294 ай бұрын
Mai Dyangu is right mwana wa Queen ndi wa ashokoshoko 😂😂😂
@jenniferchigona30034 ай бұрын
Mimba can humble you. A queen kungobereka maulemu akewo
@patrickmkhalipa-my4en4 ай бұрын
Mulelemba sazatheka 😂😂
@samuelmpahuwa38454 ай бұрын
Wa Chithengothengo komatuuu😅😅😅
@JayMilazi-fv6px4 ай бұрын
Mwana wa mkango wabwera moilakwisatu 😂😂😂😂😂
@AbdullahBullah-jj6bm4 ай бұрын
Chokochoko ❤❤❤ 😂😂 talent
@RamseyMbendera4 ай бұрын
Mwana wa chithengo thengo sakufunika Kwa Mayi mdyangu😂😂😂😂😂😂 anyamata amzanga tisamagolora zilizonsenpena makolo amakhala akuziwa kanthu....
@user-uc2ov6kz7u4 ай бұрын
Kkkkkk km shokoshoko nde mwati onana
@EdythGloryNamponya4 ай бұрын
Mayi mdyangu kkkkk queen wakumana nazo eeee
@thulanimpphiri68734 ай бұрын
Kkkkkkk muleremba mubusa wonama
@user-cs5ss4rj7g4 ай бұрын
Kkkkkk mulelemba abutsa
@BernardoDonocianoHonorio4 ай бұрын
Mwana wankago watulukira ndi milandu kkkk koma ndie tiva zinthu
@user-um2es1yp5y4 ай бұрын
Ashoko shoko awopa madam awo 😂😂😂
@stalickkafera34544 ай бұрын
Mwana wa Queen akuoneka kuti ndi pa nthengo 😂😂😂😂😂
@llewellynkhungwa47124 ай бұрын
Osamakwiya.... Palibe zothera banja apa
@jessienkhoma24924 ай бұрын
Mdyangu half part yonse yikuthela mlelemba mudzimudulako
@BernardoDonocianoHonorio4 ай бұрын
A Messe afikaso polanguiza anzawo kkkkkkk
@MathewsBanda-nu1ec4 ай бұрын
Ambiri akudyela dzina la mbuye km mulungu mwini awalange kt ukuluwake awudziwe❤❤❤❤ to Jesus
@user-rh1jw8hg7d4 ай бұрын
Km akaz amdyangu achiwiriwa mmmmmm nawoso amapanga makan bwanj hiyaaaa
@user-hs8px9mp8g4 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 mr pasta mleremba polani moto kkkkkkkk koma mmakwana guys watching you from SA Cape Town
@SamukLungu-zg7fl4 ай бұрын
Mese hule kabwino limangorangiza asari mahule kkkkkkkk🤔
@fanuelwakumangoni4 ай бұрын
Welcome back mwana wa Mkango
@patrickdzombe4614 ай бұрын
Faya faya guys mumayitha, apa munabwela Kudzakhala
@tholo864 ай бұрын
Mlelemba wapusa kkkkkkk
@DavieChimera4 ай бұрын
Shokoshoko wayamba kugura mpunga 😂😂
@user-rh1jw8hg7d4 ай бұрын
Mulelemba kutopetsa mmmmmm ai zanyanya km
@ChisisiSaynett-nm7uq4 ай бұрын
Koma mulelemba ayi anakoza 😂😂😂😂
@patriciaphiri20594 ай бұрын
😂😂😂😂 mulelemba aaaah ubusa wake sindimaumvetsa
@user-kt5ev4pn7h4 ай бұрын
Mercy unayakhako bwino Kwa sindi
@chiletsobisweck50074 ай бұрын
Budget mmayidziwa bwana chokochoko🤪😜
@danielkabango16334 ай бұрын
Ati onana wake amene uja😂😂😂😂😂
@LolenUziel4 ай бұрын
Mulelemba ya lakwa 😂😂😂😂😅😅😅
@ambrosepemba29454 ай бұрын
muli bho heavy mdyangu
@llewellynkhungwa47124 ай бұрын
Khisimasi kumayiyandikilitsa😂
@user-tn2qg1vs9j4 ай бұрын
Chokochoko more fire 🔥🔥 with your in law ❤❤ without chipwanya and sasoka chokochoko is one no boundaries ❤❤❤
@grayjames9044 ай бұрын
Shokoshoko 😂
@grayjames9044 ай бұрын
Eunice Wayamba kutwanima wabeleka iyetu😂😂
@cassimyusuf66834 ай бұрын
Ashokoshoko akuwopa onana 😂😂😂😂 arsenal pakwawo
@blessingsmimu52364 ай бұрын
Senior superintendent pastor MULELEMBA
@marymuhahara7914 ай бұрын
😂😂😂 koma mayi mndyangu uko munali tsikana kunali ntchito. Mwana wanzanu kumtero zoona mpaka wapatchire🏃♀️🏃♀️🏃♀️🏃♀️🏃♀️
@user-hj8wr7zb2m4 ай бұрын
Ilove you guys mumatha ❤❤❤
@azunguauskay49034 ай бұрын
😂😂😂Mulelemba ndi galu
@OmarWK7904 ай бұрын
😂😂😂 akuti wapachitengotengoo😂😂😂
@user-bq9ch3mb4s4 ай бұрын
😂😂😂😂 koma mulelemba
@FaithNgwalidi-hn8di4 ай бұрын
Mlelemba ndiwe otopesa aaaaaaaa
@JameelahJaffar-hy9ov4 ай бұрын
Mulelemba ndamene akusokoneza Mdyangu
@anniewhite34974 ай бұрын
Unice ndi Queen zadana tsopano😂
@LucasBetiasseJairosse4 ай бұрын
mulelemba upasta kapena misala kkkk
@user-fn1go1bt7j4 ай бұрын
Ndimakunyadiran ma guys ❤❤❤
@user-kl5fo1rb5z4 ай бұрын
Shokoshoko nfundo akuzitenga kuti 😂😂😂
@Martha14364 ай бұрын
Koma nyimbo ya Unice?? hmmm
@AfickDaud2 ай бұрын
Queen chitenje chimakukhala
@SydneyPhiri-hr7lu4 ай бұрын
M,busa nayenso ndi munthu kkkkk
@stalickkafera34544 ай бұрын
Mulelemba ukumachulutsa zolakhura ukumatikwana
@felistarmgemezulu58234 ай бұрын
Ati kuphika kuposa onana 😂😂😂
@edgarmax-pi1bx4 ай бұрын
Moto moto moto kuti buuuuuuu❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-uh6jg2ni4d4 ай бұрын
Ine nde mlelembayo sakundiwaza bolaso sindie
@user-hn6ye1yc7x4 ай бұрын
Kungokhala ndi a Mlelemba atatu pa line ndi mavuto
Sometimes if we do not like the TV program or something of that sort, we chose to prevent ourselves from that,and not showing personal hatred on actors. I do not think this is a stage for movie or comedy analysis. The Dyangu's keep the fire burnig❤❤❤❤