Nice one but u could repeat that one with late atoht manje
@simonandrewkambwera44759 ай бұрын
😂😂😂You're deserve award
@user-lv4pd5nh1i9 ай бұрын
Ine ndimadabwatuu kuti uyu alipiraaa😂😂😂😂
@franktembo20079 ай бұрын
Munthu woba ndalama ngati che mandota ukhara ine ndishi nsima azamupasira pa waya phone nitenga komanso ayenda apanda silipa.😜😜😭😭
@Maria-nv8ev9 ай бұрын
Kkk taphunzira mobile money ya zibwana
@user-cx5oi5uf9q9 ай бұрын
Ameneyo ndimbava,ndiye mbava timalanga
@user-zz4bw2mq9u7 ай бұрын
Kkkkkkk kma mandota ndiwan 🙏🙏🙏 apa timat akita wafa
@willardrajab53829 ай бұрын
Kkkkk mwayamba kuba che mandota 🤣🤣🤣🔥❤️❤️
@user-qd6rd5kg3p9 ай бұрын
Iyi akulu enake anandimenyako 😢😂😂
@faluqmayere9 ай бұрын
May Allah azikupatsa moyo wautali.........inshahllah 🤗 Hahahah che mandota utangaso award this year
@promisemakawa15569 ай бұрын
Chiphunzitso chachikulu, gud up chemandota
@HajimaKhalid17149 ай бұрын
Mamairi anenepatu nzokuba proud of u mandota
@SamuelMainjeni-uh1pf9 ай бұрын
Very educative
@davidwakhokamoto11249 ай бұрын
Kkkkkk ine sindimaziwa kut ndalama ikhoza kubwezedwa ku phone yamwini thaw yomweyo
@hossainsanudi35789 ай бұрын
Lero chakagone nditu mchitolokosi hahaha
@DalitsoSimango9 ай бұрын
Iweyo ndota bas ndiwe number one pa malawi PANO I lavizi you❤❤
@LloydPitros-iu7wp9 ай бұрын
You are the best
@williamsmwale84819 ай бұрын
Eee Koma iweyo mandota umaganiza mwa thinking 😂😂😂 mwali Za Kuno Ife tinasiya zokutumizila mu Fon muli phunziro kwambiri mu episode imeneyi ndaikonda 🎉🎉🎉