This video is talking about Mr Jokes who was staying in a rented house for 15 years, then later he claimed that it's his house, and he can't move out. watch the video till the end.
Пікірлер: 292
@jaybgeorge8540 Жыл бұрын
Please part 2 ,can't wait .love you from 🇿🇲 🇿🇲 🇿🇲 🇿🇲 🇿🇲 🇿🇲 🇿🇲 😊😊
@chrissymasauko5 ай бұрын
Watching live from zomba
@bensonpaul6866 Жыл бұрын
This is a Masterpiece... Jokes ndidolo🙌🙌😁😁🌍🌍🇲🇼🇲🇼
@payobonnie5901 Жыл бұрын
Mwandisiya mmalele, part2 Mr Jokes pls. Beautiful
@mrjokes001 Жыл бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga, osadandaula part 2 ikubwera.
@rashidmtembo6045 Жыл бұрын
Wagani zopereka mimba kwa mwana wa a landlord kuti usatuluke, iwe ndi mulesi kamange yako kkkkkkkkk
@mrjokes001 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂
@piusgoodnewsmkandawire1766 Жыл бұрын
Great work bwana Jokes.... Nice acting.... Koma kukhala ndibook onsewo panja plus kut mkazi atuluke Ndi dress manja was not that necessary the idea was already clear.... Once again great acting.. team mwasankha yabwino
@stevenmponda42984 ай бұрын
This is the best ever keep it up Mr jokes and our own ching'axy
@stanleymakwati5658 Жыл бұрын
Umakwana jokes🔥🔥🔥🔥💯this is beautiful 🙌🏾🙌🏾
@mrjokes001 Жыл бұрын
Ndathokoza kwambiri boss wanga
@festonmlomba4673 Жыл бұрын
Fire mabomba Jokes munabwera kuzakhala🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@mrjokes001 Жыл бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga chifukwa cha Chikondi chanu
@skpbeatz Жыл бұрын
Mwagwira ntchito makosana.. Koma muyambe kuyika ma English subtitles. Mwayi sugogoda. Pa KZfaq pano Pali anthu osiyanasiyana
@mrjokes001 Жыл бұрын
Simukunamadi
@nelsonnyanja178 Жыл бұрын
Now you start to recover,,,,nzeru zinayamba kukokolokat 😂😂😂 Big up,,, nice one
@mrjokes001 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂
@user-rd7wx9un2x7 ай бұрын
Nice one,...mr jokes kulanda nyumba ndikudyaso mwana wa landlord...
@gamammwenye Жыл бұрын
check on your scriptures, play ili bwino kwambiri, komano ikupanga lack realistic content, mwini wa nyumba ndi mfumu amayenera kumayankhula kwambiri upon arrival anali mwini nyumbayo osati a mfumu, and first encounter ija amayenera jokes kupangidwa summoned kwa mfumu kumene amayenera kukawopsezako, then second encounter kukampeza kunyumba kuja iye mkuyitana ma bouncer, and high voice imayenera kukhala ya Jokes and mwini nyumba. amfumu amayenera kubweletsa bata
@mrjokes001 Жыл бұрын
Thank you so much for your feedback
@mbongoboymalawi623 Жыл бұрын
Mulandu ukafika kwa mfumu mwini mulandu sayankhula asanauzidwe kutero😂😂😂😂
@gamammwenye Жыл бұрын
@@mbongoboymalawi623 mfumu sayankhula ma details of the case, iye amamvetsera mbali zonse ziwiri kenako mkupereka maganizo ake. pomwe apapa mfumu imayankhulira odandaula yet odandaulayo ali pompo. zimenezo sizichitika choncho
@user-xi9zt4nj3i4 ай бұрын
Kkkkkkkkk😂😂😂
@teoortecca3 ай бұрын
Mr Jokes mumamatha. Mwakhala mukutisangalatsa kuyambira tili ana😁. Koma we still waiting for Part 2 of this masterpiece, Keep it up. You are the legend 💪🏾
@stevephaka9253 Жыл бұрын
Kkkkk pokutha pa 10 days yooo ndiye mpaka mumpatsa phaaatu kkk
@mrjokes001 Жыл бұрын
Kkkkkkkkk
@thomasmwitiya1447 Жыл бұрын
Amene munkati JOKE'S anantha aja bwerani kuno🗣🗣🗣🗣🗣
@mrjokes001 Жыл бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga
@BrownDen Жыл бұрын
Unali serious YO 😅😂🥇 shoutout Mr jox n ching'aning'ani+ the whole team
@mussanesterkapanda1417 Жыл бұрын
Hahahahaha one of the best Malawian plays I have watched so far.
@stevenmponda42984 ай бұрын
This is the best ever keep it up Mr jokes and our own ching'axy
@duwessmatchaya6699 Жыл бұрын
Kkkkkkkk mwana wamuthira batire mmmm umakwana Jokosi. Ine ndasiriramwe
@mrjokes001 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂
@gregorykandinda5546 Жыл бұрын
Yose bho waiting for part 2, watching from centurion south africa
@user-ou8gs4iw8x27 күн бұрын
😂😂😂😂 Ching'axy!!!!! Am not the man, that someone can play with 😅😅😅😅😅
@wisdomsambuka40 Жыл бұрын
Kkkkkkkkkkkk kulanda Nyumba ndikudyanso katundu wa mwana wao
@mrjokes001 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@stevengulanbandah-wh1rr Жыл бұрын
Iweyo ndiye waza aise, part 2 isachedwe kubwera🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@mrjokes001 Жыл бұрын
Thank you so much boss, we are shooting it now!
@petermitambo9257 Жыл бұрын
Me jokes lodala bele adayamwalo. Kkkk🤣🤣🤣🤣🧎♂️🧎♂️🧎♂️ respect
@mrjokes001 Жыл бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga
@maliriwadi6468 Жыл бұрын
Eya ndaonera ndiye za akubazo basi
@misianguisheraufi4803 Жыл бұрын
Can't wait for part 2🔥🔥🔥
@mrjokes001 Жыл бұрын
Thank you so much for your love, we are now shooting part 2
@joyousmlenga3742 Жыл бұрын
Akuyichedwesa kwambili
@angelmichaelmvula357 Жыл бұрын
I was thinking that jokes saziwa but now I believe it umatha I like it
@chisomochalema8971 Жыл бұрын
😂😂😂 jokes kukhalatu serious ngati zenzen
@mrjokes001 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂
@andrewchikafa7322 Жыл бұрын
Ching'axy ndi dolo
@PatricianosiphKamkuzi-zf8dg8 ай бұрын
Ma percentage anayenda bwanji amfumu ameyenera atikitilepo eish chinganinhani my guy 😂😂🤣🤣🥰
@user-bv3px8ie5n Жыл бұрын
Watching from Durban RSA,ulemu Wako Mr
@lovenesschiliko4486 Жыл бұрын
Cast yonseyi yakwathu. Nice
@mrjokes001 Жыл бұрын
Zikomo kwambiri
@dalitsonewiri3643 Жыл бұрын
Nice work of art just the 42million figure isn't realistic...it means he was pay a monthly rent of 200+thousand....in which in reality that house isn't worth that much monthly.....but still this is nice work.
@alhaj9127 Жыл бұрын
When are we getting another epsod? Make a serie please nkhani iyiyi isathe pompano
@dailesigift4092 Жыл бұрын
This is massive.. i luv this movie.. big up Mr Jokes and the whole team