Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" Episode 2 ( Full Video )

  Рет қаралды 57,428

MR JOKES

MR JOKES

5 ай бұрын

Пікірлер: 278
@mphatsosolomon6789
@mphatsosolomon6789 5 ай бұрын
Kkkkkkk even before I finished watching I've loughed ioi anthu onsewa abwela kudzaonekela kkkkk
@chintemw6439
@chintemw6439 5 ай бұрын
Koma Jokes Adha 😂😂😂🔥🔥🙌🙌..Big Up ..waiting for Episode 3
@user-cm8nw2tg4z
@user-cm8nw2tg4z 5 ай бұрын
Kuonekera mpaka mmudzi onse " Ndimagwa vimbuza" kkkkkk
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@user-je6sg3mz9v
@user-je6sg3mz9v 5 ай бұрын
Komatu sanalakwe😂😂
@DysonDzuwa
@DysonDzuwa 5 ай бұрын
😂😂😂😂 akut a Ras ali mommo, komatu ching’aning’ani
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga
@stevenjosphat
@stevenjosphat 5 ай бұрын
Kkkk koma jokes iweyo ndi number one
@magretphili-un9up
@magretphili-un9up 5 ай бұрын
😂😂😂 jokes don't kille me,kukawonekera paka timu yose kkkkkkkkkkk
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@jamesnixonMw
@jamesnixonMw 5 ай бұрын
Awa mutu wawo unajama aah kupititsa mudzi onse Kwa mkazi😂😂😂misala iyi tsopano😂😂
@user-xr7mk5fv5d
@user-xr7mk5fv5d 5 ай бұрын
At ngaz man iiiii chingaxy undipweteka iwee🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@Mesha540
@Mesha540 5 ай бұрын
Ikanakhala imodzi izipitilira
@user-qk4dc5cr4r
@user-qk4dc5cr4r 5 ай бұрын
Jokes iwe kungomva kt akwanu abwere nde mpka chomcho 😂😂😂
@mikemisuli8113
@mikemisuli8113 5 ай бұрын
Mayiwo ndiye ndi rasta odana ndi barber😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤ mumatha bwana inuyo❤
@jumahphiri-zu6ri
@jumahphiri-zu6ri 4 ай бұрын
😭😂😂 jokes Ali ndi back up😂😂
@stevenjosphat
@stevenjosphat 5 ай бұрын
Ya bwela boh guys good combination
@priscillachanza
@priscillachanza 5 ай бұрын
keep it up mr jokes 😂😂
@elubymtheto1152
@elubymtheto1152 5 ай бұрын
😂 😂 😂 😂 😂 Koma guys
@IliyasaYusuf
@IliyasaYusuf 5 ай бұрын
Jokis Unu ndidolo bas😊😂😂😂
@MadalitsoJackson-ns3vu
@MadalitsoJackson-ns3vu 3 ай бұрын
😂😂😂 yalakwa apa baxi okaonekera onsewo aaaah
@imranmussah-ki7un
@imranmussah-ki7un 5 ай бұрын
Iwe unakalanda yachakhumi uwona ngati ukulola😅😅
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@user-nb7bv6zy8c
@user-nb7bv6zy8c 5 ай бұрын
Koma jokes 😂😂 kokawonekera maka mudzi onse 😂😂
@phillipowenbwanali7082
@phillipowenbwanali7082 5 ай бұрын
Akuti nde ngazi maniyooo kkkkkkk
@Kyou905
@Kyou905 5 ай бұрын
ili bho hvy keep up entertaining us bro🔥🔥🔥
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri boss
@user-fv5vz3vp1u
@user-fv5vz3vp1u 5 ай бұрын
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk km chiphwanya kuwauza nthu ku t avetsele kt umagwa vimbuza 😂😂😂😂😂😂😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@Gautengstanzo
@Gautengstanzo 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 koma inu ndikuona panozi zina zina
@user-qu9iu7hs8k
@user-qu9iu7hs8k 5 ай бұрын
Ndiwe 1 Mr jox
@NuradinaAbrahima-rt9ip
@NuradinaAbrahima-rt9ip 5 ай бұрын
Koma big man inuyo anakomza sure 🤣🤣🤣🤣🤣🧢🧢🧢
@dianna3577
@dianna3577 5 ай бұрын
Kkkkkkkkk kkkkkkkkk chiphwanya ati wakuzomba,chiphwanya simunthu wamba, mkazi unja timutaye basi tipange maganyu tiphe makwacha
@NebotPatrick
@NebotPatrick 5 ай бұрын
😂😂😂Ati ngaz man
@user-jz4kw3ow8w
@user-jz4kw3ow8w 5 ай бұрын
Koonekela mpakana kunyamula mudzi onse 😂😂😂🎉🎉🎉
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa cha support yanu.
@MadalitsoJackson-ns3vu
@MadalitsoJackson-ns3vu 3 ай бұрын
Ati Arasi mmadzi mommo😂😂😂😂 zisilu za anthu izi😂😂😂
@giftchazima5546
@giftchazima5546 5 ай бұрын
Anthu akwanu onsewo adhaa😂😂😂😂😂 nde chakudya chimene anakukonzerani sichikwanatu kkkkkk
@user-ks3uw3pq7d
@user-ks3uw3pq7d 5 ай бұрын
Koma Mr 😂😂 iweyo
@gabrielmaluwa1038
@gabrielmaluwa1038 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 jokes uzikhala serious
@imranmussah-ki7un
@imranmussah-ki7un 5 ай бұрын
Ase jokes😂😂😂 ndayamba kuseka kale apa just in seconds 😅😅😅
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@MalawiBelieversLibrary
@MalawiBelieversLibrary 5 ай бұрын
😂😂 kowonekela chigulu chonsecho
@tzshoppers4471
@tzshoppers4471 5 ай бұрын
Komatu jokes iwe ndi galu kobasi siku lina tizakakuponya ku mental 😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@kidmbappe1120
@kidmbappe1120 4 ай бұрын
😂😂😂😂kaonekereni
@user-mh3vd2oi7s
@user-mh3vd2oi7s 5 ай бұрын
Kokaonekera mpaka mudzi onse😂😂😂😂
@user-cn2mg2ee2p
@user-cn2mg2ee2p 5 ай бұрын
😂😂😂 kokaonekera ndimudzi onse
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Eyaaa😂😂😂😂
@MphatsoLisimba-bb8yf
@MphatsoLisimba-bb8yf 5 ай бұрын
Jokes, zako zotenga khwimbi la anthu ukafunsidwa kukatenga okuimilira zija sunasiyebe etiii?😂😂😂😂 Waiting for Episode 3
@sayidimisessa
@sayidimisessa 5 ай бұрын
From south Africa jox Ali ndiazibale akwawodi eeeee
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@victorsmtseka1574
@victorsmtseka1574 5 ай бұрын
I remember when l broke up with my ex during exam l almost submitted a desk😢😢😢
@zwangezgambo6194
@zwangezgambo6194 5 ай бұрын
😆 😆 😂
@Fullkeyz
@Fullkeyz 5 ай бұрын
Fodya😂😂😂😂😂
@brianloyd7702
@brianloyd7702 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@FRANCISCOALFREDOVARANQUINHOVar
@FRANCISCOALFREDOVARANQUINHOVar 21 күн бұрын
Bo
@emasonchapfunya4255
@emasonchapfunya4255 5 ай бұрын
Iiiih koma jokes mpaka mudzi onse
@DreyAndrew-mb8ql
@DreyAndrew-mb8ql 5 ай бұрын
😂😂😂 ati taona thako
@jumagombeza486
@jumagombeza486 5 ай бұрын
From Dubai jokes umatha
@danielskamchacha9875
@danielskamchacha9875 5 ай бұрын
Top notch
@alickka
@alickka 5 ай бұрын
I suggest you should put English as sub title for more viewers but acting is great 😂
@SobwaJahman
@SobwaJahman 3 ай бұрын
Kupembeza azungu kumeneko koma amalawiso timapusa bwanji
@alickka
@alickka 3 ай бұрын
@@SobwaJahman How many can view this with only chichewa, amene amagula bundle Malawi kuno ndiagati
@user-bt7uh1yk8o
@user-bt7uh1yk8o 5 ай бұрын
Koma jokes ngat ndi chamba 😂😂😂😂😂 anthu akwawo et
@praiseluhanga2123
@praiseluhanga2123 5 ай бұрын
Kugwa vimbuza😂😂😂😂😂😂😂
@user-zi4tw5fv9w
@user-zi4tw5fv9w 5 ай бұрын
A jokes mwabwera😅😂❤
@user-wv3pt9vu4m
@user-wv3pt9vu4m 4 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣Koma inuyo man anakoza
@IliyasaYusuf
@IliyasaYusuf 5 ай бұрын
😂😂😂 jokes umayitha
@abbuhanif4650
@abbuhanif4650 5 ай бұрын
Kumalilo kp koonekela kkkkkkkkk jokes upole moto
@LysonBwanaliMbewe-um1ro
@LysonBwanaliMbewe-um1ro 4 ай бұрын
Mwayamba kutha a Jokes
@isaacchambwinjajr4984
@isaacchambwinjajr4984 4 ай бұрын
Hvy ase
@user-yo4zn6tb9i
@user-yo4zn6tb9i 5 ай бұрын
Ku green malata kwamiyandikira jokes
@user-dv1ik2cv3i
@user-dv1ik2cv3i 5 ай бұрын
Jokes adah 😂😂😂 anthu onsewo
@RodgersKanyasko-dh3cy
@RodgersKanyasko-dh3cy 5 ай бұрын
Jox ndi Ching'aning'ani ndinu zisilu. Kusuzumira azimayi kosamba kkkkkkkkkkk
@jaqxonbanda-pg7ow
@jaqxonbanda-pg7ow 4 ай бұрын
Koma jokes at mchani 😂😂😂🔥🔥🔥
@celinamanuel9017
@celinamanuel9017 5 ай бұрын
Jokes ndi galu kwabasi
@EstherKambale
@EstherKambale 5 ай бұрын
Well done
@jumaandisen515
@jumaandisen515 5 ай бұрын
Jokes 🤣😂😂 You are too much 😂😂😂😂😂😂😂 Okaonekela ku maliro chan
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@user-to2wx4oj2y
@user-to2wx4oj2y 4 ай бұрын
😂😂😂😂 mudzi onse kokawonekera😅
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 this is really mr jokes
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@r45CroH
@r45CroH 5 ай бұрын
Ati nde ngazimani yo 😂😂😂
@Enidok-f7
@Enidok-f7 5 ай бұрын
Iiiiii koma jokess suzatheka aise kkkk mpaka mudzi onse koonekera kkkk
@ChicoKazembe-xs4dr
@ChicoKazembe-xs4dr 5 ай бұрын
Kma jokes ndiwe galu kwabasi 😂😂😂😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@eishmeilakidu3364
@eishmeilakidu3364 5 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Mr jokes you must be serious how can you do that ,mpaka mudzi onse
@seanjacob325
@seanjacob325 5 ай бұрын
😂🤣😂 koma abale onsewo aaaaah no
@user-wk3nk2fo3r
@user-wk3nk2fo3r 3 ай бұрын
Koma ching'ani ng'ani Ndi one😂 ati aras Ali momo😂
@Fullkeyz
@Fullkeyz 5 ай бұрын
Kukaonekela ndi mudzi onse inu amenewo 😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@chigokhalid9420
@chigokhalid9420 5 ай бұрын
Zilibwino kwambir keep it up
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri
@user-kb5fd9iq3m
@user-kb5fd9iq3m 5 ай бұрын
Akwawo mpaka stand ya ndirande yonse
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@austinmpahuwa6552
@austinmpahuwa6552 4 ай бұрын
koma iweo Jokes, umakwanira ndiye nkazi wapezayu Mesa unakatengako ndalama 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@Yolokazi829
@Yolokazi829 5 ай бұрын
😂😂😂mwabwera kuzakhala mikoz
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@chisomokamata9627
@chisomokamata9627 5 ай бұрын
this is nice
@YamikaniDebwe
@YamikaniDebwe 5 ай бұрын
Koma jokes ndwe dolo
@ronexmcdonald8742
@ronexmcdonald8742 5 ай бұрын
Ili bwino koma jokes part yomwe watengayo samayenela azioneka osalala kumeta bwino ngat ozindikira
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu!
@user-lx4by7sk3l
@user-lx4by7sk3l 5 ай бұрын
Kkkkkkk koma ndiye kusokhanotu osati kokawonekela
@JaxyPeter-jr9gt
@JaxyPeter-jr9gt 5 ай бұрын
Plz Mr jokes mudzatipha ndikuseka sapanga choncho gululonselo
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@IdrrissahIshimael
@IdrrissahIshimael 3 ай бұрын
Koma kkkk umakwana❤❤❤
@belemjuliocamblege9609
@belemjuliocamblege9609 5 ай бұрын
Jokes ndi wachabe chabe
@josephykapichi3647
@josephykapichi3647 5 ай бұрын
Amoyoo anthu onsew jokes kwanu ndiwe munthu ndithu
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@user-qv8vr5dq2x
@user-qv8vr5dq2x 5 ай бұрын
Big up Guys
@user-xr7mk5fv5d
@user-xr7mk5fv5d 5 ай бұрын
Azibale ako onsewo heeee🤣🤣🤣🤣
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@raphaelzuze1781
@raphaelzuze1781 5 ай бұрын
Mr jokes 🔥🔥🔥🔥
@ulemumajawa-gw4cf
@ulemumajawa-gw4cf 4 ай бұрын
Jokes sunasiyebe zotenga mudzi onse zija😅😅
@SheriffAbduh-tv8sn
@SheriffAbduh-tv8sn 5 ай бұрын
Ansaaaa😅😅😅😅😅🙌🙌🙌
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@imranjanatu2844
@imranjanatu2844 5 ай бұрын
Koma jokes mutu sugwila ndithu iweyo wuli pa number 1 ku ma comedy wosekesa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga
@user-fl9xy8bk7e
@user-fl9xy8bk7e 5 ай бұрын
😂😂😂 mmakwana km❤
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@ChrispinNyani-ed4nz
@ChrispinNyani-ed4nz 5 ай бұрын
Nthawi yopuma tilibe 🔥🔥🔥
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Ndathokoza kwambiri boss wanga
@user-bq2zb1pc8m
@user-bq2zb1pc8m 5 ай бұрын
Moto kt buuuuu kukaona azimayi akusamba
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga
@dalitsonakutepa199
@dalitsonakutepa199 5 ай бұрын
Ndie ngaziman yo, zomba zomba
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@user-yx7jw1pj2f
@user-yx7jw1pj2f 5 ай бұрын
Zomba yeniyeni😂😂😂
@MarizaAvelino-rs2uj
@MarizaAvelino-rs2uj 5 ай бұрын
kkkkk ese meteu água trouxe o exército todo
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri boss wanga
@HEZEKIAHCHUNGA-ib2hi
@HEZEKIAHCHUNGA-ib2hi 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Kwa mfumu basi
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@imamwali2693
@imamwali2693 5 ай бұрын
Wapita ndi mudzi ose😂
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
@patrickmasa7145
@patrickmasa7145 5 ай бұрын
fire
@jamesbanda3537
@jamesbanda3537 5 ай бұрын
Award tatenga basi Chaka chino,,team Jokes
@bigthellamwechande8641
@bigthellamwechande8641 5 ай бұрын
Watching live from Cape town table mountain 🏔️
@user-hg6ot6vp3f
@user-hg6ot6vp3f 4 ай бұрын
😂😂😂😂 Koma fadah
@user-ql2rk3nq5m
@user-ql2rk3nq5m 5 ай бұрын
Msono athu onswewo🤣🤣
@mrjokes001
@mrjokes001 5 ай бұрын
😂😂😂😂 Zikomo kwambiri chifukwa Cha support yanu
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 3 ( Full Video )
19:26
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 1 ( Full Video )
17:00
마시멜로우로 체감되는 요즘 물가
00:20
진영민yeongmin
Рет қаралды 32 МЛН
Самый Молодой Актёр Без Оскара 😂
00:13
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 9 МЛН
Cat Corn?! 🙀 #cat #cute #catlover
00:54
Stocat
Рет қаралды 16 МЛН
Mr Jokes performing in a street. Why people get married?
28:25
CRUISE 5 WITH THERESA PHONDO
51:44
Zodiak Malawi
Рет қаралды 21 М.
My Mum Movie | Aaron Chambo | A Malawian Throwback to 2014
1:34:14
Jabroma Shots
Рет қаралды 11 М.
Mr Jokes VS Ching'aning'ani, Kuyambitsa Church. @mrjokes001
7:52
Mushroom Shade - EPISODE 1
27:24
Chaz Production
Рет қаралды 518 М.
Mr Jokes Performing live at Mzuzu University, (Full Video)
33:43
RING OF LOVE / AFRICA K!DS IN LOVE
28:18
AFRICA KIDS IN LOVE (AKIL)
Рет қаралды 710 М.
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)
15:12
MR JOKES
Рет қаралды 179 М.