You got my vote 💪 continue being a blessing to others
@user-dt8nr1zx6e8 ай бұрын
Umakwana mandota
@TUDECHABLESSED8 ай бұрын
U are the Tru Talented G .... We konda you to the Max...
@gabrielmaluwa10388 ай бұрын
Tafota zateka che mandota
@littlebrainer8 ай бұрын
Che mandota is the best comedian in malawi who is with me
@costeryusufu95698 ай бұрын
I'm with you
@GiftMunyonga-ko9dz8 ай бұрын
As a matter of fact 😂
@NACNAC-fg5yd8 ай бұрын
Most definitely 😂😂😂😂
@josephkananja-bi8vs8 ай бұрын
Umatha ase ulemu wako
@user-ys3ze7pk9j7 ай бұрын
We are together
@GloriaGunde-xo4rf10 күн бұрын
Our own doctor che mandota, keep the fire burning.olo patient amanva bwino
@markluke19948 ай бұрын
Wow that's great on our way okatengaso award yathu loweruka lino❤️🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-dh7lv2cx9s8 ай бұрын
0:23
@BahatLeman8 ай бұрын
Iweyo mumata mazo awad tatenga nditutu mwaona ,mwaona❤❤❤
@shadreckchipembere35758 ай бұрын
Kodi mumalemera ma KG angati Chemendota😂😂😂😂😂😂 Chifukwatu anthuwa amangokunyamulani2😂😂😂😂😂😂
@HajimaKhalid17148 ай бұрын
Talirapo ambiri mu limbe,18k yanga inapita, inspired 🇲🇼 pa top ndi che Mandota umaphu zitsa ase koma sechedwa kufaaa kkkkkkk
@atCurrentkid5 ай бұрын
I'm a comedian and I wish to be followed by you ❤️
@jonathanmaseko60578 ай бұрын
Che mandota I like the way u have acted this episode.... Waphunzitsa anthu ambiri kuti mu limbe azikhala ochenjera even if munthu sunapiteko ku limbe ukhala ukudziwa kuti kuli okuba .... Komanso anthu omwe amachita mchitidwe obela anzawo atengelapo phunziro kuti akupangazo siku lina azaona polekera ..coz zinthu zikuvuta aliyense nde solution isamakhale kubelana keep it up u deserve masso award
@alickka8 ай бұрын
Yes this video is very educative do more of this type Bro more fire, umatha
@user-bv3px8ie5n8 ай бұрын
Yaaaaa umathadi mr watching from Durban South Africa ❤
@davisonphiri-sm9xe8 ай бұрын
Tili pambuyo Pako mandota,my best comedian in Malawi,umakwana
@Muslimvoicemalawi8 ай бұрын
Mandota iwe ndi 1 maso award mwatenga basi😂😂
@daudcassim16368 ай бұрын
Kkkkk sopano mologeni alikt apa zikukuonekera wekha nzanga
@JosephTembo-hm5yp8 ай бұрын
Mu limbe amwene eeee
@jariamdoka31798 ай бұрын
Big man mudzathera mmanja mwa anthu Inu adzangokuyatsan kkkkkkkkk❤❤❤❤❤ iweyo ndi mbambande taphunzra zaku limbe
@watchmanprayerwarrior95698 ай бұрын
😂😂😂😂 napangidwapo ndili mwana ku chilomoni BT, 🤣🤣🤣
@saifullahalick4078 ай бұрын
Zowona zokha zokha, ine mu Limbe momo anandibera 50 thousand njira yake yomweyo.
@jefreykazembe86918 ай бұрын
😂😂😂😂😂 ndibwere kodi kkkkk n yothawira mbasada.....umakwana king of comedian