Mulungu amatikonda Kwambiri kaya wina afune ky asafune adzakhala nafe mnyengo zonse
@user-yi4oc4xz4v9 ай бұрын
Ayime dad inu
@chrisboyce2299 ай бұрын
Mcp Kwake kwatha basi tiwone Zina
@user-dt8nr1zx6e9 ай бұрын
More fire nkhanga zaona
@AnishaMoosa-ej7yr7 ай бұрын
Mulungu awalange osee 😅😅God help us
@sparkdymon34299 ай бұрын
Nkhanga zaona kkkk tipeleke bushili alibe kanthu
@wysonnamaona64979 ай бұрын
Bushiri aperekedwe basi.. Nyanja sikukhuzidwa
@AleksaWilliams-qc6cn9 ай бұрын
Zuchita kubebatu zikufunika exchange kkkk,ku Mozambique Kaya tisithanisako bakayawo,
@user-sb2qe7ce3t9 ай бұрын
Zandale umachedwa kupanga chitukuko
@lamecknyadani19059 ай бұрын
Nde kuti muzikhalila kupempha basi... Simungakagule mafutawo... Mayikotu akayenda amapita kukapanga trade agreement... Inu mulibe choti mungagulise nde mungopempha basi kkkk hehehehe business yomwe mukudziwa ndiyogulisa alubino 😂😂😂😂😂🤣🤣🤣
@user-qi8xe7qh1e9 ай бұрын
Amaona ngati ochenjenjela
@wysonnamaona64979 ай бұрын
Aprophet apite basi.. That's our last option 😢
@JohnChibalo-wf8gr9 ай бұрын
Ku DPP kuchosedwe anthu onse osokonedza kukhale ntendere nankhati pali ena ofuna upresidernt kudzera mudzina la DPP akayambise chipani chawo.chakwera nkhani waimva ? Nankha palinso upresidernt ❤❤❤❤❤
@user-cg8vg5mr6x9 ай бұрын
Ndipo zosangalatsa kwambir mulungu alemekezeke nd2 ndipo mzosadadwitsa pot ameneyo nde mulungu wa zatheka bwanj
@evancebokati64139 ай бұрын
Is this Limpopo FM or Rimpopo FM?
@0marusuff-oe2xm9 ай бұрын
✍️✍️✍️✍️
@0marusuff-oe2xm9 ай бұрын
✍️✍️✍️✍️✋
@joaquegerman22509 ай бұрын
Mtanyiwa iwe ndi katundu
@frankkaipa89259 ай бұрын
Ndiopusa kwambiri nyanja akayisinthanise
@0marusuff-oe2xm9 ай бұрын
✍️✍️✍️😰😰
@user-cy2db4fs7w9 ай бұрын
Timakunyadilani ayaluseni asamajaile
@CrytonMalunga9 ай бұрын
Eee tili pamoto
@user-nz8mq4ff3e9 ай бұрын
Nkhangaaaaaaaàaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaasaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaàaaaaaaaaaaassssaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaàaaaaaaazaoooooooooooooooooooooooo oooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooozamulibwanji a Malawi anzaga kulikonse kumene muli Lelo 4th October ine ndine mr tanyiwa ndati mr tanyiwa ndati mr tanyiwa ndati mr tanyiwa Limpopo AFM Rodio
@user-ux4ff2bl6y9 ай бұрын
Eeeee nde bushiri yo akufuna mamunangeso?
@user-ub1mw7ce5p9 ай бұрын
Malawians,please tell your papa to resign. We are tired of this nonsense going on. President must resign with immediate effect.. papa! Papa! Papa! Resign wena man