No video

Osamwa Juwisi wa Enjoy!

  Рет қаралды 60,055

Morton Baghaya

Morton Baghaya

Күн бұрын

Muvulaza Ana!

Пікірлер: 297
@user-oc9zn1di7h
@user-oc9zn1di7h 2 ай бұрын
Thanks for sharing.Wofunira moyo wake zabwino apanga chisankho yekha.Enafe ana athu anadwalapo nazo.Timangopanga za local basi
@christophermukaka7403
@christophermukaka7403 2 ай бұрын
The best drink is water or thobwa koma anthu timaona ngati za chimidzi
@romeomhone744
@romeomhone744 2 ай бұрын
Zoona
@AndrewChiponga
@AndrewChiponga Ай бұрын
Ase tizimwa Iya kusiyana ndikudya khono umadya zidya
@charlokapalamula9299
@charlokapalamula9299 2 ай бұрын
Thanks for opening people's eyes. Amene wamva wamva basi....
@situationmalawi3646
@situationmalawi3646 2 ай бұрын
Ndiye mMalawi kumuuza izi aziti ukumupangira nsanje.... you'll hear them saying "if you can't aford don't tell me not to" 🤣
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
bola apeza info...zinazo azipangano akuziwa mbali zonse
@alfordkuyenda2684
@alfordkuyenda2684 2 ай бұрын
I have never like this guy but on this video am 100 % behind him, osangonyoza for the sake of kunyoza but follow the facts. Very good healthy tips!!!
@deborahngwira724
@deborahngwira724 2 ай бұрын
Thank you...ineyo honestly v never thought kuti in the juice wa enjoy muli real stuff, n if you open to see the ingredients you can vomit.
@BrianMandhlopa
@BrianMandhlopa 3 ай бұрын
Malawi bureau of standard is a sleeping cat.....
@ndabaningichisiza9574
@ndabaningichisiza9574 2 ай бұрын
There was a time my Son could not sleep until 1 Am! This juice is bad indeed.......but which cheaper brand is good abale, nanga tingakwanitse kugula series muwiri daily? Lol
@user-vk2ym8ql4k
@user-vk2ym8ql4k 2 ай бұрын
Ine mwana wanga akamwa amadwala chifuwa sizinaoneke
@yamzyboumar502
@yamzyboumar502 2 ай бұрын
Good thing is kumampatsa phala basi apo ayi azidya kwambiri nsima with ndio zothira nsinjiro osati mafuta kwenikweni
@premakiyi
@premakiyi 2 ай бұрын
Are you sure the insomnia was due to a Juice?
@corretabanda7685
@corretabanda7685 2 ай бұрын
Zimvele mtolo. Ofuna kumwa adzimwabe, amene wamvela asiya.
@noelmsiska3692
@noelmsiska3692 2 ай бұрын
Zidyani nokha poisoniyo munthuyu akunena zoona ineyo juice ameneyu ndimamumva irritating throat this guy is right
@KhadijahImedi
@KhadijahImedi 2 ай бұрын
Ever since I stopped giving my baby enjoy chifuwa chake chinachepa eish
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
Wise choice!
@sharodynicier001
@sharodynicier001 2 ай бұрын
Ndizoona akumapangitsa chifuwa 🤔🤔🤔
@innongwenyah
@innongwenyah 2 ай бұрын
No mkulu uyu despite kuti amakonda zotukwana, koma ndi mdala wa mnzeru. Zomwe akunenazo zitha kukhala zothandiza kwa winawake. The best way possible ndiyoti MBS itithandize kupanga regulate ma standards a ma products athu. Ineyo I love enjoy juice koopsya, coz ndimadana ndi zakumwa za gas like achina Coca-Cola ndi Fanta, koma I didn't care kuti what are the ingredients of this juice. Sinayambe ndafatsako kuwelenga, and mwina nkupanga understand ma ingredients wo coz ambiri ndi ma technical terms. But this video is an eye 👁‍🗨 opener ndithu, will consider other ways of supplementing my diet. Let's be positive guys, munthuyu sakupanga de-campagn enjoy juice, no, he's only exposing stuff yosakhala bwino. We'd really love to support ma products opangidwa kwathu konkuno, koma nanga tifa nazo tu tsono. As Malawians 🇲🇼 let's normalise kumapanga ma products abwino that are of international standard. Tisafe coz mwatimwetsa poison tisakufuna please.
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
A great summarize my message, we love local industry but people should know.
@innongwenyah
@innongwenyah 2 ай бұрын
@@mutafire Exactly, anthu adziwe kuti akamwa enjoy juice akumwanso ma chemicals oipa. Ndeno ma guys opanga enjoy nanu, Try to improve ma products wo, otherwise eeeish mutipweteka. Lol 😂
@BinwellMayani
@BinwellMayani 2 ай бұрын
Bwana Morton,pitilizani kutiphunzitsa coz zambr sitikuzidziwa
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 2 ай бұрын
Ndidzowona olo mwana akamwesa enjoy, Chifuwa sichitha ndidzachabechabe.
@user-vk2ym8ql4k
@user-vk2ym8ql4k 2 ай бұрын
Same us mine amadwala chifuwa chandithu
@lindakondowole8021
@lindakondowole8021 2 ай бұрын
Thank you for sharing this helpful information, zinazi timangotsutsa coz ndife amalawi mkukhala kwathu
@bonfesszinkomola6552
@bonfesszinkomola6552 2 ай бұрын
Ndangomaliza kumene kumwa wa tropical
@bnamandwa44
@bnamandwa44 2 ай бұрын
Powerful Boss
@mackwellingsphiri3646
@mackwellingsphiri3646 2 ай бұрын
Thanks for the alert. Information is power; consumers need to understand and not just know what goes into their body and how it affects their health.
@yosefemwansapozimba1027
@yosefemwansapozimba1027 2 ай бұрын
Ndamva iiii thanks for this
@kingstonechisale978
@kingstonechisale978 2 ай бұрын
Ndi chilichonse akulu! Check Sobo simukhala chipatso chilichonse ndi ma flavors okhaokha. Nde musaopsezepo anthu apa 🥱
@twavysibale4751
@twavysibale4751 2 ай бұрын
Much respect boss,do more videos like this,..
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
will do
@mayesokazembe5880
@mayesokazembe5880 2 ай бұрын
Can be true, bola asakusumileni……..
@BMadhlopa
@BMadhlopa 2 ай бұрын
Someone is alerting people about hazardous food /drinks, how can he be mad? Calling him mad is preposterous!!
@ladyb9179
@ladyb9179 2 ай бұрын
Tipilizani kuwatsegula mmaso a Malawi.
@hawabanda-xs5fx
@hawabanda-xs5fx 2 ай бұрын
Izi zoona ine ndinagula cartoon for my son koma pomaliza cartoon ija mwana amadwala kusegula kumangosaza almost 2 weeks mwana paja Ku school samapita ndipo kuyambira pompo sindigulaso
@shongafilms3925
@shongafilms3925 2 ай бұрын
Even chimanga chomwe tikudyachi amakhala ayikako zimankhwala zambiri kuti chidzicha msanga. Palibe infa kuithawa.......zokupha si izi ayi amachita kuzikwelera bus anthu
@kaymikundi7935
@kaymikundi7935 3 ай бұрын
Hmmmm ndazizidwa. Totally mortified!
@LusayoSunga
@LusayoSunga 2 ай бұрын
Wakumva ndewava
@PemphoGwazaJere
@PemphoGwazaJere 2 ай бұрын
Tiyeni tizimwa nthobwa magaye 🤣🤣
@desiremuwawa6978
@desiremuwawa6978 2 ай бұрын
😂
@MikeBanda-cr7ni
@MikeBanda-cr7ni 2 ай бұрын
Zakudya zonse zopangidwa Ku factory ndi poison even nkhuku zachizungu izi sizabwino ayi. Matenda a cancer ankhagwira azungu kwambiri koma pano anayamba kuchuluka Kuno Ku Africa chifukwa timadya ma processed foods tinasiya kudya zakudya straight from farm
@Alien_design2
@Alien_design2 2 ай бұрын
Share more broz eye opener cheers
@emmanuelmwanyali750
@emmanuelmwanyali750 2 ай бұрын
Try zima 100% fruit Juice zija
@user-sm8gx4vf1v
@user-sm8gx4vf1v 2 ай бұрын
Yes ineso ndi mboni chifuwa sichithelapo ayi abale koma yaa
@viollachilemba
@viollachilemba 2 ай бұрын
Not me watching while enjoying enjoy 😉 😅
@veronicankhoma4493
@veronicankhoma4493 2 ай бұрын
😂😂😂
@TachikoMwanamanga
@TachikoMwanamanga 2 ай бұрын
Ndie ma nurse aku central hospital amachita kukakamiza kugulila ana akapangidwa admit 💔 ndinayambanako ndima nurse akundilesa kubweletsa 100% drink akut ndigule komweko enjoy ndiwabwino kwa ana💔😂 sometimes ku Malawi amangobweletsa zithu bola apange ndlama
@EffieMalonda
@EffieMalonda 2 ай бұрын
Thanks longosi I've never seen u serious like this izizi ineyo I will use it..... no more enjoy in my house
@user-gu1wf3vh6v
@user-gu1wf3vh6v 2 ай бұрын
Ana ambiri akupezeka ndi nthenda ya sugar coz of these foods and drinks
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
Exactly !
@user-nb7dp6pr9n
@user-nb7dp6pr9n 2 ай бұрын
Wakunva wanva osanva akhale Morton Baghaya 🔥💪
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
heavy, anthu aziyenda ndi info.
@chemapa
@chemapa 2 ай бұрын
of all the poisonous juices in malawi, the least I expected you cud condemn is enjoy.
@EmmanuelMponda-ig9bm
@EmmanuelMponda-ig9bm 3 ай бұрын
Akusowetsa 😂😂😂😂
@naBEthA
@naBEthA 2 ай бұрын
Kma tamumwa eeesh😢😢😢
@masozibanda7473
@masozibanda7473 2 ай бұрын
Maka anthu opasa Ana enjoy mmaganiza bwa...
@RitaHussein
@RitaHussein 2 ай бұрын
Koma tazimwera come on bro
@BizweckFred
@BizweckFred 2 ай бұрын
Ndiye chiputu chanyatu
@user-bw6uc3dl5s
@user-bw6uc3dl5s 2 ай бұрын
My favorite Juice Enjoy mawa ndimwa mwina I can notice something but if not ndekut ndizimwabe
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
Come back in 20 years.
@ElishaMfune
@ElishaMfune 2 ай бұрын
The best juice to drink its water, take it or leave it but at end you regret for taking these deadly juices
@user-bw6uc3dl5s
@user-bw6uc3dl5s 2 ай бұрын
​@@ElishaMfunendakumva Eli
@christophermukaka7403
@christophermukaka7403 2 ай бұрын
The best drink is water or kumangophika thobwa
@staymotivated1768
@staymotivated1768 3 ай бұрын
Tikudya en kumwa ma chemicals oopsa, nkona ma cancer, ma sugar, ma bp angoti mbwee
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
kooopsaaaaa
@user-sf9di3rq6p
@user-sf9di3rq6p 2 ай бұрын
Ukamaletsa anzako kumwa juice uzinenaso juice amenetiyenela kugula and from your opinion zambiri zomwe tikumwa kapena kudya masiku ano ndizoopsa kumene coz of modern world akupanga introduce zinthu zambirimbiri zinazi tikazitengela mwambiri ndetisiya kudya zambiritu coz since enjoy yekha amene alindi zolakwika zambiri
@Sharongimo
@Sharongimo 2 ай бұрын
Kuwaonongera business anzanu. Mai wina ku Nigeria is in Jail for bad comment on tomato puree
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
you know you are allowed to comment and speak on any issues as long as it is the truth, right? do not fear. Say it if you are sure of the facts.
@chemapa
@chemapa 2 ай бұрын
ZIKUPHA ANTHU A KU AFRICA THESE DAYS SIZIMENEZI.
@gracenalikata1159
@gracenalikata1159 2 ай бұрын
Tamumwa tamumwa enjoy is my favourite
@ElishaMfune
@ElishaMfune 2 ай бұрын
Keeping drinking
@Allieshaibu8612
@Allieshaibu8612 3 ай бұрын
Wayakhula zonad aaaaa
@Justman34_dislike
@Justman34_dislike 2 ай бұрын
I started disliking Enjoy the moment I saw increased list of chemicals on its ingredients. Thanks for sharing
@jimmymakunigondwe7998
@jimmymakunigondwe7998 2 ай бұрын
very informative tawonga
@mikelilemba2104
@mikelilemba2104 2 ай бұрын
Ignorance is a bliss! U've spoil de fun 😂💔
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
that is my job!
@pemphoashani4619
@pemphoashani4619 2 ай бұрын
Great
@veronicasimuka3882
@veronicasimuka3882 2 ай бұрын
Its true siwabwino ine wandidwaritsa kwambiri
@user-qp6qh2dj6l
@user-qp6qh2dj6l 2 ай бұрын
Ndi zoona mukunenazi koma anthu ndi osamva ndi chifukwa chake ambiri akupanga makani apa, zinthu zimenezi ndi zoipa zimapha komanso chifukwa chochuluka sugar munthu umakalamba mwansanga, ma juice onse opangidwa ku factory ndi oyipa ngakhale anene kuti 100% fruit juice, preservative free ndi zabodza, ngati mukufuna 100% juice pangani nokha, osakhulupirira zopangidwa ku factory za moyo wanu alibe nazo ntchito bola iwo akupanga ndalama
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 ай бұрын
Ndaleka kumwa ine
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
wise choice
@chekiamaabdul5083
@chekiamaabdul5083 2 ай бұрын
Osamangodya achule akowo kumeneko bwanji. Chinkhope ngati iweyo.
@HANCENENTERPRISE-yw4mr
@HANCENENTERPRISE-yw4mr 2 ай бұрын
Iweyo man umalikonda dziko lako.
@peggymkandawire-mw9xj
@peggymkandawire-mw9xj 2 ай бұрын
Nde tumizani ndalama kut tizigula ma juice abwino.... Nanga ife tingakwanise ma juice omwe mukumwa Inu?
@Josenkuth
@Josenkuth 2 ай бұрын
Mad man, dont u know almost everything we eat nawadays is harmful. Even masamba enieni akudimbawa are full of very toxic residual chemicals. What about these common processed meats, tinned fish are common too aren't they. Maybe that's far fetched, did u know even bottled water has recently been proved to contain harmful plastic carcinogen particles secreted by their contaners. Nde mukanene za Enjoy. Come on guys, have some sense. Kambaniso za Sobo Orange Squash
@Kamangaify
@Kamangaify 2 ай бұрын
Koditu momwe akukamba za Enjoy mu, sizutanthauza kuti zina zonse zili bwino.
@romeomhone744
@romeomhone744 2 ай бұрын
Bola mwamva zili ndiiwe kunyozela
@MatthewKanyenda
@MatthewKanyenda 2 ай бұрын
Ichi ndi chidziwitso,zili ndiweyo kuzipha Koma langizo ili akuti avoid juice wa enjoy tu. Vuto kusamvetsetsa a Malawi shame on you.
@DinaJere
@DinaJere 2 ай бұрын
😂pepani kwambiri anthu itse
@DinaJere
@DinaJere 2 ай бұрын
😂pepani kwambiri anthu itse❤
@DeborahGowelo
@DeborahGowelo 2 ай бұрын
Ase we have learnt something else
@leonardmalirana7423
@leonardmalirana7423 2 ай бұрын
Kamdzukulu kanga timavutikanako kumangoyendayenda osakhazikika mwina ndi enjoy yemweyo.anthu Ena ngati angakasume basi kungotenga enjoy anachita umboni yekha
@MaudKapakasa
@MaudKapakasa 2 ай бұрын
Hypa, more sugar kids are become crazy eish
@TamandaTikoma
@TamandaTikoma 2 ай бұрын
Zikomo kwambili, nde tithandizeni ndi drink wanji otchipa wabwino oti titha kumapatsa anawa chifukwa dzachulukatu dzamwenyezi. Komanso makambawa tatiuzeni abwino.
@user-xs3nj1es1r
@user-xs3nj1es1r 2 ай бұрын
oOoOO brother ndakhu.mudwa koooopya
@HadijaAsima
@HadijaAsima 2 ай бұрын
Ayi zikomo 🤗 koma anthu tikuzimwela ndinthu
@goldenselenje686
@goldenselenje686 3 ай бұрын
Akusumiranitu che morotoni owo
@goldenselenje686
@goldenselenje686 3 ай бұрын
Miex anahonga kale ku MBS
@DavidIsradoris
@DavidIsradoris 2 ай бұрын
Mutipangileko check Maheu bwanj wakulu?
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
tipanga
@ElizabethPhiri-ky1wm
@ElizabethPhiri-ky1wm 2 ай бұрын
This is a very timely warning .
@user-if4ul9bp3p
@user-if4ul9bp3p 2 ай бұрын
Is true even here in SA some yogurt is not good ana kukhosomola kosatha
@noelmsiska3692
@noelmsiska3692 2 ай бұрын
You can imagine ana kumangokhosomola that's poison. Ndagulitsa mabisiketi ine zaka zambiri koma amwenye tikawabweretsera za expire zomwe abwenza makasitomala amazigayansi kuthira zinthu zawo nkupanga bisikete wina anthu nkumadyabe ndipo zikuchitikabe mmalo ambiri including hotels recycling of food anthu kumangotsekula mmimba ndi ma spices and chemicals koma MBS certified food imagine!
@PatriciaMajawa
@PatriciaMajawa 2 ай бұрын
Zikhoza kukhala zoona coz madokotala anandiuzapo kt ana tiziwaikira madzi mmalo mwa ma juice and anthu ena anandiuzapo kt enjoy iz bad
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
Ndizoona ndithu
@sharodynicier001
@sharodynicier001 2 ай бұрын
This is true 🤔🤔😒😏
@user-ef2lz6fn3k
@user-ef2lz6fn3k 2 ай бұрын
Tizingomwa thobwa basi chete
@MaryTembo-oj6dj
@MaryTembo-oj6dj 3 ай бұрын
Iwe nd katakwe😂 umatichosa umbuli
@fanuelh.ckhuluzah6852
@fanuelh.ckhuluzah6852 2 ай бұрын
It's not juice , it's for those that can not afford real juice.
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 2 ай бұрын
Good job sir
@josephchidwala2697
@josephchidwala2697 2 ай бұрын
Taphunzira, kwakhala tipeze alternative drinks otherwise anawa ativutatu
@PatrickJuma-v5n
@PatrickJuma-v5n 2 ай бұрын
Thats true it's not juice preach on brother
@user-ib3rz9ic8g
@user-ib3rz9ic8g 2 ай бұрын
Well noted and thank you brother
@tinamitunda8420
@tinamitunda8420 2 ай бұрын
Tizimwa thobwa zokonza tokha
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 2 ай бұрын
😂😂😂😂 bakukomenge tu....
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
wamunisanga kochi?
@ireenesthermbisa7200
@ireenesthermbisa7200 2 ай бұрын
Ever since ndinapanga chisankho chosiyitsa Ana kumwa the so called Enjoy .....ndinapuma ku zifuwa zosatha. Ana pano anazolowera kumwa madzi even ku school .
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
wise choice
@thokobanda5983
@thokobanda5983 2 ай бұрын
Eee mukulanga anatu, bola mukanawapezela alternative iii😂😂. Amasilira pa break amenewo
@ireenesthermbisa7200
@ireenesthermbisa7200 2 ай бұрын
@@thokobanda5983 Anazolowelanso, at times amanyamula mkaka koma juice ayi ndithu Ana anapuma zifuwa ndipo aindingabwererenso
@NthambiLipenga-jw5gc
@NthambiLipenga-jw5gc 3 ай бұрын
EEEEh Koma adha ndi mbora game yih
@GriberthaKalulu
@GriberthaKalulu 2 ай бұрын
Wasowa zoika pa net iwe
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 ай бұрын
What about energy drink?
@yamzyboumar502
@yamzyboumar502 2 ай бұрын
So dangerous
@KanyozaMatope
@KanyozaMatope 2 ай бұрын
Everything is poisonous.. it depends the way we take it
@FAB_ONE_PICTURES
@FAB_ONE_PICTURES 2 ай бұрын
Zambiri zimenez timadya zimakhara ndi ma preservatives amwene almost every processed food has these kind of chemicals
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 2 ай бұрын
Zoonadi izi koma tiuzeni za ukwaju pls
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t 2 ай бұрын
Aaah iwe zopenga zakozo upeze womunamiza wanva ine ndamwa enjoy for 7 years now palibe nvuto ndipo moyo wa munthu uli m'manja mwa Mulungu osati mwa munthu nzanga.
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
well, 7 years ndikachani... mudikire mukamafika ku ma 40, muzabwera pa comment iyiyi kuzapepesa
@noelmsiska3692
@noelmsiska3692 2 ай бұрын
Mulungu samatiteteza pomwa dala poison tisamunamizire abale. Juice ameneyu amavulaza pang'onopang'ono 7years zachepa
@ElishaMfune
@ElishaMfune 2 ай бұрын
Soon u will see the results for taking the juice
@lyiemax
@lyiemax 2 ай бұрын
Thanks for the information
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
My pleasure
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 2 ай бұрын
Amaika mankhwala etii? Iiii! Zaphazo ndiye ndizambiri.... No where to run...
@marygoza1205
@marygoza1205 2 ай бұрын
The truth is that these processed foods are not nice at all. May God help us
@MirriamRaja
@MirriamRaja 2 ай бұрын
Nde juice wabwino ndi utiyo? Ti7zeñ please
@user-vk2ym8ql4k
@user-vk2ym8ql4k 2 ай бұрын
Mutichilenso check more
@Justman34_dislike
@Justman34_dislike 2 ай бұрын
Juice wanji wokhala ndi sugar?😮
@NIKSYCHIMA
@NIKSYCHIMA 2 ай бұрын
Enjoy ndiotchipa nanga
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
Ndiyoopsa
@KonzaniZinthu
@KonzaniZinthu 2 ай бұрын
A Malawi musavutike ndi mantha. Chilichonse chopangidwa ku fakitale ndi choopsya komanso ngakhale nsima mukudyayo imayambitsa nkhansa chongofunika ndi kasinthasintha basi. Musadziphe ndi ma 100% omwe dzipatso dzake ndi dza GMO mudwalabe basi.
@leviecashmere7555
@leviecashmere7555 3 ай бұрын
Kmano iweyo umakwana km tiuzeniko juice wa bwino
@mutafire
@mutafire 2 ай бұрын
opanga nokha
@rashidadan2533
@rashidadan2533 2 ай бұрын
We don't have MALAWl bureau of standard ,
@ElizabethPhiri-ky1wm
@ElizabethPhiri-ky1wm 2 ай бұрын
Komatu izi ndizoona ngati simu simikiza pitililani kumwa koma maliyake alike ache ndi ma tenda
MDYANGU COMEDY SERIES 24/12/2022.
28:49
LIKI-LIKI Ladies
Рет қаралды 52 М.
Kubunyula Nkoipa kapena Ndikwabwino?
17:55
Morton Baghaya
Рет қаралды 25 М.
Can This Bubble Save My Life? 😱
00:55
Topper Guild
Рет қаралды 87 МЛН
王子原来是假正经#艾莎
00:39
在逃的公主
Рет қаралды 17 МЛН
Chikondi -  Malawi
0:17
Centre for Human Rights
Рет қаралды 2,6 М.
Apeza Mankhwala a Nthenda ya Shuga
10:24
Morton Baghaya
Рет қаралды 8 М.
Cruise 5 with Msulira Mathews Sapemba Tisatayane
58:13
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 24 М.
VENDA - Episode 163
12:24
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 49 М.
Zigololo, Chikwati ndi Zibwenzi pa China Paja
21:16
Morton Baghaya
Рет қаралды 13 М.
CRUISE 5 WITH ALLELUYA BAND
1:17:41
Zodiak Malawi
Рет қаралды 15 М.