No video

#PROFESSOR_HASSAN_SAID_ZAMBIA

  Рет қаралды 50,630

1islam

1islam

Күн бұрын

Пікірлер: 192
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Ай бұрын
I am proud from Christian to be Muslim ☪️ ❤❤❤
@SUWEDSHAMWKUPE
@SUWEDSHAMWKUPE 14 күн бұрын
Mashallh
@GoldenBarnet-hv3wj
@GoldenBarnet-hv3wj Ай бұрын
Am proud to be a Muslim,Allah is great
@user-ub1vt2kq4s
@user-ub1vt2kq4s Ай бұрын
Allah bless you professor mashalah❤❤❤
@RedsonRichard
@RedsonRichard Ай бұрын
Nthawi yatha amsilamu inu musasokoneze choonadi
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Akusokoneza ndi chani amenepo mmm
@sharifhenderson6982
@sharifhenderson6982 22 күн бұрын
Asokonesa pati 😂😂😂
@AbdulAzeezChapita
@AbdulAzeezChapita 23 сағат бұрын
Chilungamo chakufika mutima mwako
@user-tk6qh9zs7h
@user-tk6qh9zs7h Ай бұрын
Alhamdulillah kuti ndine Msilamu. Ma videos ngati awa adzipezeka ndithu pa KZfaq. In so doing zithandizira uthenga wa Allah kufikira ena omwe ali kutali mosavuta
@SelemanIssahAhmad
@SelemanIssahAhmad Ай бұрын
❤❤❤
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f Ай бұрын
Hohn 14 v 6, Yesu anati ine ndine njira choonadi ndi moyo. palibe munthu adza kwa atate koma mwa ine. Most of theses things brings conflicts among peoople, Palibe mpikitsano pa mawu a mulungu
@mickchiliko2796
@mickchiliko2796 Ай бұрын
Alhamdulillah am proud to be Muslim. May Allah guide me and protect me In shaa Allah.
@ghadaffmoosa7535
@ghadaffmoosa7535 14 күн бұрын
In sha Allah
@user-vn2mz7qd5i
@user-vn2mz7qd5i Ай бұрын
Ndinali msilamu koma ndinasiya Chisilamu nditazindikira kuti YESU ndiye njira yowonadi.
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f Ай бұрын
Mulungu akudalitseni kwambiri, munapanga chisankho chabwino.
@HakeemJossam
@HakeemJossam 22 күн бұрын
munali msilamu koma Osazindikila kungopitako poti makolo Anu amkapita kumeneko
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f 21 күн бұрын
Ambuye akudalitseni chifukwa ndi ochepa amene akumaona patali mu uzimu, ambiri ali komweko chifukwa anabadwila momwemo kapena makolo awo anawasiya mzikiti omwe anamanga, ambuye akuthandizeni in everything especially moyo wanu wa uzimu
@MpondaBanda
@MpondaBanda Ай бұрын
Alhamdu lillah proud to be one hu follows Allah's submission
@EmmanuelstoneyJere
@EmmanuelstoneyJere 11 күн бұрын
Afarisi a lero ndamenewa ntchito yao nkuphwekesa Yesu basi
@promisemakawa1556
@promisemakawa1556 Ай бұрын
Im proud to b Muslim, mpaka imfa idzanditenge ndili msilamu
@UmarAjussu
@UmarAjussu Ай бұрын
Allah akudaliseni ma sheikh nonse
@ghadaffmoosa7535
@ghadaffmoosa7535 14 күн бұрын
Ma sha Allah may Allah bless u sheikh SAID HASSAN ZAMBIA
@ChrispinLunda
@ChrispinLunda Ай бұрын
Zamasiku otsiliza amenewa ndiwo omkana yesu aja zimene munthu udakhazikikamo sikopheka kukusutha amenewa simungawauze za mzimu oyela sangave ndiwo umaulula umazindikilitsa umaphuzitsa ngat ulibe mzimu oyela ungalive baibulo ukamaliva kuthupi mzimenezo zovetsa chison ambuye akuzindikilitsen amen
@tauhidtimba
@tauhidtimba Ай бұрын
Kumva chichewa umafunikira kukhala ndi Zimu oyera kod?
@chiogamata2560
@chiogamata2560 Ай бұрын
Ine anthu inu mmandiwaza apapa Kumva language yako yomwe zufunaso nzimu oyela?? Kukuuza kut iyo ndi kapu yomwela madzi, sumva coz ulibe nzimu oyera?? This thing of nzimu oyera, koma mmaudziwa, mungaufotokoze ndi malemba maumboni?? Concept iyiyi eeeeti eeeeeeish mumadyera guys 🤣🤣🤣🤣🤣
@sharifhenderson6982
@sharifhenderson6982 22 күн бұрын
Mzimu oyelawo anaulenga ndan??? 😂😂😂
@sharifhenderson6982
@sharifhenderson6982 22 күн бұрын
​@@tauhidtimbakayatu 😂
@ALICKMASANGANO
@ALICKMASANGANO 22 күн бұрын
Mmm baba moti ma verse akupereka muthuyu si amu bible
@MussaMalon
@MussaMalon Ай бұрын
Mashallaah Sheikh mulungu akudalitseni ❤.
@blessingsdouglas3
@blessingsdouglas3 Ай бұрын
Aaaaaaa ine saidi Zambia nakhala nayepo ndi tambwali uyu
@dennismachemba9514
@dennismachemba9514 16 күн бұрын
Masha Allah may Allah Grant him jannat firdaus
@SUWEDSHAMWKUPE
@SUWEDSHAMWKUPE 14 күн бұрын
Allihamdulilah to be a Muslim my dad please protect pokhala slamu paka ifa
@FathimaMa2
@FathimaMa2 Ай бұрын
Alihamudulilahi kwaine mpakana kwa asilamu ose pano pa dhunia mashaalhaa
@IbrasyaicheWizyx
@IbrasyaicheWizyx Ай бұрын
Alhamdulillah for choosing me to be a Muslim❤
@KassimIssa-bn3od
@KassimIssa-bn3od 23 күн бұрын
Mashalla Allah ndi silamu ndipo tikuphemba kwa Allah ndizafe ndi silamu
@ngozo07
@ngozo07 Ай бұрын
I'm proud to be a Muslim
@SelemanIssahAhmad
@SelemanIssahAhmad Ай бұрын
❤❤❤❤
@user-ei2yt3kf4x
@user-ei2yt3kf4x Ай бұрын
❤❤❤
@MahometAli-e8w
@MahometAli-e8w Ай бұрын
My lecture Said Zambia you miss me long time no hear you
@mariamhassan6788
@mariamhassan6788 Ай бұрын
Proud to be a Muslim Alhamdulilah ❤
@AfredMbeta-pk1cn
@AfredMbeta-pk1cn Ай бұрын
Ndizomwe timadikilira,go ahead
@HarnetJauma
@HarnetJauma 22 күн бұрын
Am proud to be a Muslim ❤
@muhammadisaid3968
@muhammadisaid3968 22 сағат бұрын
Mashallah
@Chayibujackison
@Chayibujackison 24 күн бұрын
Mashah allah ❤ ♥ 🙏
@BysonBanda-z8q
@BysonBanda-z8q 21 күн бұрын
I am proud to be a Muslim
@user-pw4dv1el3d
@user-pw4dv1el3d 22 күн бұрын
Allahu Akbar. Ma sha Allah. Na am ❤❤😂
@user-lk3ki9hi3k
@user-lk3ki9hi3k Ай бұрын
Nawe hule Zambia ukuziona ngati ndi mngero
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
I am proud to be a muslim , Komafunso langandiloti , Ndichifukwachani Muhammad timamupemphela chikhululuko komanso madaliso kwa mulungu ? Kodi Muhammad ndi azibale athu omwe anamwalila oyenela kuwafunila zabwino kwa mulungu ndindani ?
@JohnstoneMwandira
@JohnstoneMwandira Ай бұрын
Dzina la mtumiki Muhammed likatchulidwa timanena kuti swalalah alaih wasalamah,( meaning , mtendere ndi madalitso amulungu apite kwa iye). Zimenezi even zimachitikaso kwa Azitumiki ena onse . Issah(Yesu) ndiye timati Alaih Salam Wasalatuh(Meaning, madalitso amulungu apite kwa iye). Nde zimenezi zimanenedwa kwa mtumiki winaaliyese akatchulidwa dzina.
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
@@JohnstoneMwandira ok , ndichifukwa chani okhala atumiki a mulungu timawafunila mtendele ndi madaliso , chikhalilenicho anapanga ntchitoya mulungu .
@JohnstoneMwandira
@JohnstoneMwandira Ай бұрын
@@rashidadan2533 Zimenezi akulamula ndi Mulungu akuti mfunireni zabwino mtumiki wanu. Nde Ife ndindani kukanira.
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Iweso sisilamu tachoka apa
@PhiladelphiaManyumba
@PhiladelphiaManyumba 7 күн бұрын
Devil's deception 😢😢 beware my fellow Christian this is one of the last events Aim of this ceremony is to contradict your faith keep watching 😢😢
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z Ай бұрын
Chiweluzo chidzapelkedwa chifukwa Cha zintchito zarhu osati proud to be a Moslem or proud to be a chriastian nzopanda pake
@AlkadoNkundwe-wb3of
@AlkadoNkundwe-wb3of Ай бұрын
Evidence please !!!!
@danielmangalisobanda8356
@danielmangalisobanda8356 Ай бұрын
Mr Hassan munaphunzira koma ndinu mbuli yothelatu kuuzimu ndichifukwa chake mukupembedza wovumbulutsa Quran naganiza ndikukhulupilila kuti mukupembedza Mulungu wamoyo, chonsecho ndiSATANA weniweni adamunamidza muhammad kuti ndiiyeyo adili kuvumbulitsila aneneneli amuBible
@GiftSinalo-ku6zb
@GiftSinalo-ku6zb Ай бұрын
Alhamudulillah to be a Muslim
@khadijailiyasa5315
@khadijailiyasa5315 Ай бұрын
Kodi simungayike apapa dawa yonse please tikuyifuna
@abdul-rasheedsalika
@abdul-rasheedsalika Ай бұрын
Mposo abaleee, nanga kwinako tikakupezera kutiko sono
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 Ай бұрын
Manshaallah brother
@raphicallan5331
@raphicallan5331 Ай бұрын
Proud to be a Muslim
@JUBRANBULAYHl-yb4ke
@JUBRANBULAYHl-yb4ke Ай бұрын
Mwenyezi Mungu, hapana mungu ila Yeye, Aliye hai, Msimamizi wa milele, Amekuteremshieni Kitabu kwa haki, kinachosadikisha yaliyokuwa kabla yake, na ameteremsha Taurati na Injili kabla yake kuwa ni uwongofu kwa watu. Na akateremsha upambanuzi: Hakika walio kufuru Ishara za Mwenyezi Mungu watapata adhabu kali, na Mwenyezi Mungu ni Mwenye nguvu, Mwenye kulipiza kisasi wewe katika Mwingi wa rehema, vipi hakuna mungu ila yeye ni mpendwa, Mwenye hikima ni yule aliyeteremshiwa kwako Ama waliomo nyoyoni mwao wanafuatwa Hawakusema kuwa kila mmoja Kwa Mola wetu Mlezi. na hawakumbuki ila wenye akili, tusipotoke nyoyo zetu baada ya kutuongoza bila shaka Mwenyezi Mungu hatavunja ahadi yake, mojawapo ya makusudio ya surah. Kudumu katika Uislamu baada ya ukamilifu na ubainifu wake, na kukanusha shaka za Watu wa Kitabu, hususan Wakristo Ni surah ya Madina iliitwa Surah Al Imran kwa sababu familia ya Imran imetajwa ndani yake katika aya ya surah. Herufi hizi zilizotengana zimemtangulia mwenzao katika Sura Al-Baqarah, na zinaonyesha kutoweza kwa Waarabu kutoa Qur’ani kama hiyo ingawa inaundwa na herufi ambazo Sura ilianza nazo, na kutoka kwao wanatunga hotuba yao. Mwenyezi Mungu ndiye ambaye hana mungu wa kuabudiwa kwa haki isipokuwa Yeye pekee na hakuna mwingine aliye hai ni maisha makamilifu yasiyo na kifo au upungufu.
@BindulaMtambo
@BindulaMtambo Ай бұрын
Mashallah, please upload some more
@Chayibujackison
@Chayibujackison Ай бұрын
Mashah allah sheikh awuzen ndithu❤❤❤
@peterkinsLekera
@peterkinsLekera Ай бұрын
Kwamuthu yemwe sawerenga ndikutsata za zipembedzo adupha nkhani zonse ndikumangosankha momwe akufuna pokwanilitsa zolinga zanu koma choonadi mukuchidziwa
@user-xu9rh1lm8o
@user-xu9rh1lm8o Ай бұрын
Pelekan lemba nanu
@chiogamata2560
@chiogamata2560 Ай бұрын
Pelekani zomwe mmawelenga inuzooo Ndanga izi zikuchoka mmitu mwao ngat?? 🤣🤣🤣🤣🤣
@Lionelmosse
@Lionelmosse 29 күн бұрын
Allahmdulillah ❤❤❤❤❤❤
@YusufuYunusuSavielMakey
@YusufuYunusuSavielMakey 29 күн бұрын
Masha Allah pondipanga kukhara msilam ❤
@ghadaffmoosa7535
@ghadaffmoosa7535 14 күн бұрын
Ma sha Allah❤
@AbdurashidAhmad
@AbdurashidAhmad 9 күн бұрын
Tiyeni tafunile zabwino zonse makolo athu omwe anayima pakati pachowonadi chisilamu omwe alimoyo mpakana omwe anasogolera kale kumanda mulungu awapatse jan'na please
@ShaibuJackson
@ShaibuJackson 15 күн бұрын
Mashaalla
@martinchimwala
@martinchimwala 25 күн бұрын
Proud to be Muslim
@JazraJeffm
@JazraJeffm Ай бұрын
I'm proud to be a musilim
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f 21 күн бұрын
Anthu timasokoneza pakati pa Mulungu ndi Alla, palitu kusiyana kwakukulu, ndipo mudzadzindikira koma mochedwa kusiyana kwa awiriwa
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 13 күн бұрын
Asilamu olambila mwala wa ku arabia saudi dzipumi biii ngati zoona
@Robson513
@Robson513 Ай бұрын
❤Mashallah
@omarmanduwa4127
@omarmanduwa4127 Ай бұрын
MAA SHAA ALLAH
@HaliJana
@HaliJana Ай бұрын
MULUNGU AKUONJEZELENI MASIKU AMOYO WANU ADALISESO MU MZELU ZANU
@DIMZYRECORDS
@DIMZYRECORDS 21 күн бұрын
Minika ❤❤❤❤
@JohnAsendi
@JohnAsendi Ай бұрын
Dawa koma imeneyo osati zakuti Achibeketi adali mfiti adakuphera agogo ako muzichita Dawa yolimbana ndi amene Sali Asilam timakunyadiran big kep it up
@AKHTARLINGSON
@AKHTARLINGSON Ай бұрын
Anayankhulapo choncho iyeyu?
@tomthompson4429
@tomthompson4429 Ай бұрын
Where is the other part of Seventh Day part? Let's PRAY that each one of us here on Earth meets GOD's Grace and know the truth, I Pray for you my muslim brothers. Amen
@danielmangalisobanda8356
@danielmangalisobanda8356 Ай бұрын
Mulungu wamoyo wovumbulutsa Uthenga wamuBible akuchitileni chifundo kuti mumudziwe.
@user-dx5dc4sm5v
@user-dx5dc4sm5v Ай бұрын
Alhamdulillah
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem Ай бұрын
Ameen thummah Ameen
@UlandaHarjisonstone
@UlandaHarjisonstone Ай бұрын
Allihamdulillah pokhala msilam chonde Allah muzanditenge ndili msilam
@frankkasamala6956
@frankkasamala6956 24 күн бұрын
We need you here at ntonda in ntcheu
@adamuhwaduh1080
@adamuhwaduh1080 Ай бұрын
Ndipepha Allah kut ndidzamwalire kanali silam
@BornwellOtala-dm1zm
@BornwellOtala-dm1zm Ай бұрын
❤Ma shaaAllah
@PatienceNgulinga
@PatienceNgulinga Ай бұрын
Aaaaa Sheik openga uyu kanundu akumupweteka,, mutuwo kukulako ukumulemera
@chiogamata2560
@chiogamata2560 Ай бұрын
Kung'alula zomwe mmazidutsa kutchalitchikoka nde mwadabwa nazotu?? Akutenga zammutu kapena?? Else likunama ndi Bible lotu pamenepoo 😂😂😂😂
@chiogamata2560
@chiogamata2560 Ай бұрын
Kulowa kumoto kulipo ndiiithu 😂😂😂😂
@IssahNgalinje
@IssahNgalinje Ай бұрын
Mashaa Allah sheikh ❤❤
@SABITISABITI-yv9jq
@SABITISABITI-yv9jq Ай бұрын
🕋🕋🕋🕋🕋☝️☝️
@AshrafSaidi
@AshrafSaidi Ай бұрын
Jazakum llah khaira
@user-ky8eq5ek1p
@user-ky8eq5ek1p Ай бұрын
Ma Sha AllAh Amee
@AsanteBilly
@AsanteBilly Ай бұрын
MashaAllah ❤❤
@mramir.s.smkubwa3985
@mramir.s.smkubwa3985 Ай бұрын
Komano kunena chilungamo Alhamdulillah asilamu mulungu anawapasa mzelu ndithu
@YatoRoy-kt4lh
@YatoRoy-kt4lh Ай бұрын
I once met this Saidi Zambia for almost 8 hrs. Anafika pokwiya titamufotokozera zinthu zomwe iye samadziwa za chiyambi chachisilamu ndipo anakwiya heavy. Amene mumamudziwa ask him za anyamata omwe anakumana nawo usiku mnyumba ina ku mangochi. He ended up a failure on that meeting.
@GiftStephano
@GiftStephano Ай бұрын
Chinayamba bwanji tiziwe nao
@cassimmeleka40
@cassimmeleka40 29 күн бұрын
ان الدين عند الله الإسلام
@user-dx3cp1tx5z
@user-dx3cp1tx5z Ай бұрын
Ameen
@OmrahGeraldOmrahGerald
@OmrahGeraldOmrahGerald Ай бұрын
MASHA ALLAH MASHA ALLAH MASHA ALLAH
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj Ай бұрын
Pakut ngat wakhungu alondole njira akukhungu onse awili azagwa mmbuna....mukazaziwa choona choona chizakumasulani
@user-gj7jh1yx7g
@user-gj7jh1yx7g Ай бұрын
Inu chilungamo munachiona bwanji
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
Macha hallah ❤❤
@abhentomwcmwanjeza5771
@abhentomwcmwanjeza5771 Ай бұрын
MaShaallah
@user-sb8hi8vc9w
@user-sb8hi8vc9w Ай бұрын
Ma shaallah
@MarthaChizi-h1u
@MarthaChizi-h1u Ай бұрын
MBULI ZA ANTHU NDIPO PALIBE CHIMENE MMADZIWA
@SwaibaMussah
@SwaibaMussah Ай бұрын
Mashaallah
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 13 күн бұрын
Asilamu nonse ndi ma judger ndekha nonse moto ma vindictivist shupiti
@AbgirlChinheya
@AbgirlChinheya Ай бұрын
Alihamudulilah❤
@AbdullahRight-ld2vv
@AbdullahRight-ld2vv Ай бұрын
Ma sha Allah ❤❤
@danielmangalisobanda8356
@danielmangalisobanda8356 Ай бұрын
Ndikudziwa chimene ndikunenachi and i Challenge you
@IssahNgalinje
@IssahNgalinje Ай бұрын
Sheikh musiponya zambili kuti tizinva zambari chonde chonde ❤❤
@KelvinMangwengwe
@KelvinMangwengwe Ай бұрын
Ma sha Allah ❤
@SaymonMawaya
@SaymonMawaya Ай бұрын
Maashallah
@MariamJaffali
@MariamJaffali Ай бұрын
Ma shaa Allah
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g Ай бұрын
Masha Allah ❤❤❤❤❤❤
@ZainaJolozagunda
@ZainaJolozagunda Ай бұрын
Allah Akbar
@MussaLameck
@MussaLameck Ай бұрын
Alihamdulilahi
@masebermsanga7623
@masebermsanga7623 Ай бұрын
Masha Allah ❤
@GiftTwaya
@GiftTwaya Ай бұрын
Allah akbr
@MadalitsoWillson
@MadalitsoWillson Ай бұрын
❤ mashaallah
@JafaBulhm
@JafaBulhm Ай бұрын
Masha Allah Allah Akibari
@ThokozaniChadza
@ThokozaniChadza Ай бұрын
Mashaa llah
@YusufuUsumani
@YusufuUsumani 29 күн бұрын
1 muslim
@user-du4ng6gx3o
@user-du4ng6gx3o Ай бұрын
Salaam aleykum...video muzimalidza osamayidula
@KassimShaibu-f6h
@KassimShaibu-f6h Ай бұрын
Machalawu
@UseniMailosi
@UseniMailosi Ай бұрын
Mashaah Allah
SAID ZAMBIA
1:18:45
AWUZENI KUTI MEDIA PRODUCTION CREW
Рет қаралды 120 М.
Nurse's Mission: Bringing Joy to Young Lives #shorts
00:17
Fabiosa Stories
Рет қаралды 5 МЛН
MILANDU PA OKALA....Episode 24
11:54
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 278 М.
TIPANGE  DAWA  SAID ZAMBIA
58:39
AWUZENI KUTI MEDIA PRODUCTION CREW
Рет қаралды 142 М.
Rev Alexander Kambiri preaching at the funeral service in Malomo Ntchisi
30:23
Rev. Alexander Kambiri
Рет қаралды 90 М.
Professor Said Hassan Zambia
3:17
CheNaNaNaH Visuals(Poet Kinanah Jannah)
Рет қаралды 1,3 М.
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Malawi News Update
Рет қаралды 196 М.
ANGANGA AFICK AND MOFOLO LIVE PERFOMANCE AT BT LODGE
15:45
Red Apple Visuals
Рет қаралды 39 М.
Akuchita kusankha anthu omanga; Chilungamo kulibe ku police
10:42
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 69 М.
CCAPYUM SERVICE
42:33
MVAMA CCAP NKHOMA SYNOD (Rev. Yassin Gammah)
Рет қаралды 214 М.
Nurse's Mission: Bringing Joy to Young Lives #shorts
00:17
Fabiosa Stories
Рет қаралды 5 МЛН