UTM Musapusitse A Malawi Lero Bon Kalindo

  Рет қаралды 88,414

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

2 ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo Says UTM should not come and lie to Malawians that they have nothing to do with how Malawi is being run becuase they are part of the problem as long as they are part of the Tonse Government.
Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo Wati UTM isabwere kudzanamiza Amalawi kuti alibe chochita ndi momwe dziko la Malawi likuyendetsedwera chifukwa iwo ndi mbali yamavuto bola ali mbali ya Boma la Tonse.
#malawi

Пікірлер: 133
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 2 ай бұрын
tili mmavutowa chifukwa cha UTM ndi amene anapangisa 54 percent ndikulowesa MCP m'boma, Chilima wadya ulele misonkho yathu, watidyela ndithu koma osayigwirirla tchito ndalama yathuyo zoona? ndakulila kwabasi
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp Ай бұрын
God bless you 🙏🙏
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 ай бұрын
Alan ngumuya anamugwilitsa ngati ndondocha, anathamanga ma campaign koma osamuganizira udindo ulionse or wakuchipani 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@BambordKabambe
@BambordKabambe 2 ай бұрын
Allan ngumuya😂
@nickmumba2131
@nickmumba2131 2 ай бұрын
Wafa Wafa Kalindo oyeeeee ❤❤
@juliochiwalo
@juliochiwalo 2 ай бұрын
Iwe ukunyoza Kalindo ndiye kuti sugar sopo mafuta a galimoto ndi katundu yense ukugula motchipa 😅
@hamiducassim5724
@hamiducassim5724 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 kkkkk kkk akuluwa amalakhula chilugamo kma bvuto amalakhula ngat aledzela
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Chilimaoto 🔥... Even how much you can talk chilima fire fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥. Tigwere uko kalindo, chitsiru
@ChimwemweAsifa-wh4mf
@ChimwemweAsifa-wh4mf 2 ай бұрын
Iwenso uli nd mavuto amuubongo
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n Ай бұрын
kkkkkkkk Koma the DC.. alibe manthadi. 😅😅😅😅😅🤣🤣🤣
@user-hn8sr9oc7k
@user-hn8sr9oc7k Ай бұрын
Kalindo siiwe dolo chifukwa ukanakhala kuti ndiiweyo dolo sibwenzi pa mgwirizano paja utapezekapo tsono iweyo ndiamene unalinso patsogolo kumuuza chilima kuti akapqnge mgwirizano lero ukumublemanso chilima why?
@user-uh1bs6cx1d
@user-uh1bs6cx1d Ай бұрын
Koma nayenso anari komweko anangomumana udido bas anapenga 😂
@mauricetayali8041
@mauricetayali8041 2 ай бұрын
The DC, always justice is penifull. Chulungamo chimapweteka
@omarajibu860
@omarajibu860 2 ай бұрын
They can't be forgiven, you have miserably failed.
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Umbuli basi aliyese, kusayenda yinu kuno ku SA popita ku chipatala you have to carry id or any identify document
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 2 ай бұрын
Ife ndiye DPP wooooyeee
@ThokozaniBondo-em9fr
@ThokozaniBondo-em9fr 2 ай бұрын
Awuze Bon sakuziwa kuti ife wathu umatiyimilira
@MadalitsoGreen-bj1np
@MadalitsoGreen-bj1np Ай бұрын
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤
@user-uv7yq1fx4r
@user-uv7yq1fx4r 2 ай бұрын
Kkkkk kunena chilungamo osanamiza anthu kuti mwapusitse kachikena ai
@LastenWesele-wq8jh
@LastenWesele-wq8jh Ай бұрын
Kkkkkkkkk kalindo wati chani magalimoto a utm ngati mabokosi amalilo
@MarthaBonongwe
@MarthaBonongwe Ай бұрын
Kip it up the good work
@royGovender-vl9on
@royGovender-vl9on 2 ай бұрын
Born kalindo good guy..... Don't scared
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 ай бұрын
Zoonadi ndithu.Sitikusowa kupepesedwa.Apitilize kudya ndalamazo
@EssaPindani
@EssaPindani 2 ай бұрын
Koma uku wina alira 😢
@ShadreckPhiri-er2nb
@ShadreckPhiri-er2nb 2 ай бұрын
Mpaka chilima aaa koma kusowa zochita
@DanielBonfaceadungaz-rx4sm
@DanielBonfaceadungaz-rx4sm 2 ай бұрын
ichi sichimanva ichi 😀😀😀😂😂😂
@NdloAphe
@NdloAphe 2 ай бұрын
This is realty ❤
@MysonDiverson
@MysonDiverson 2 ай бұрын
Mmakwanira boss
@user-op3nx5qt4q
@user-op3nx5qt4q 2 ай бұрын
UTM inapita kukaziyipisila mbiri ku MCP Chakwera ndipo UTM ikuzinamiza sidzawina or atani
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 2 ай бұрын
galimoto ngati bokosi lamaliro la utm😆😆😆😆🤣
@PeterMoloko-lr3wq
@PeterMoloko-lr3wq Ай бұрын
Voice imeneyi ya kalindo?
@user-jv3fk9be7p
@user-jv3fk9be7p 2 ай бұрын
Iwe ndi munthu ongofuna kuti zanu ziyende ngati Mtambo.
@SamsonLynfordmpnda
@SamsonLynfordmpnda Ай бұрын
Ndipo zoona
@Patgregorymanyumba
@Patgregorymanyumba 2 ай бұрын
Kkkk wina alira ❤❤❤❤ the DC
@AngelManda-vk1nc
@AngelManda-vk1nc 2 ай бұрын
Iwe umayimandi pachilungamo 🔥🔥
@BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr
@BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr 2 ай бұрын
Amaona ngati ndi abwemzi koma osadziwa kuti a nzake amamupondeledza ayisomva
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 2 ай бұрын
Eya!, takumvani a President athu, sitingakhulupilire mcp and utm kkkkkkkkkkk infact sitinaivotele wonse alliance kuyambira 2019
@NditajiMaxwell-cz8ir
@NditajiMaxwell-cz8ir 2 ай бұрын
Kkkkkk mtezawo ndiwamanu
@AhamadiAlifu
@AhamadiAlifu 2 ай бұрын
Kkkkkkk olo uzipita kwanu ukulila kulankhula kwabwanj
@AdoreNgoleka
@AdoreNgoleka Ай бұрын
Mphangala ya ife iweyo born kalindo
@user-qj3db4lu7c
@user-qj3db4lu7c 2 ай бұрын
akungofuna ma vote chongowavotera azasinthanso mawanga UTM ndi MCP no vote for him ndimbamva zokhazokha
@KimmuMatola
@KimmuMatola Ай бұрын
Koma tisaywale zoomwe akanena bon kalindo lelo chilima wamwalila woosese anakwela ndege amwalila
@AnafiRGRajabu-me9ki
@AnafiRGRajabu-me9ki 2 ай бұрын
Komanso chilimayu waba ngalama dzatu Ali vice president imagine akatenga u president sazatiba matako 😢😢😢😢😢?? Vote imeneyo ingakhare ngati chimozimozi kutenga mkono wako kuocha mwadala ndithu
@zanganation8415
@zanganation8415 Ай бұрын
Akuti ku 30 sawopako😂😂😂😂😂😂😂😂😂 adzamuboola thako ndi screw driver uyu ohooooo
@KristenMaly
@KristenMaly Ай бұрын
😂😂😂😂😂
@amosnyongo6565
@amosnyongo6565 2 ай бұрын
UTM 😢😢
@RuthChipojola
@RuthChipojola Ай бұрын
Chilungamo chiyende ngat madz
@Meleka.X
@Meleka.X 2 ай бұрын
Kalindo pangani zogwilisana musange chipani chabwino Kuti mutitukule
@arabisaidi4768
@arabisaidi4768 2 ай бұрын
president bon kalindo auzen akuona kut pot munali ku UTM akuona ngat muyikila kumbuyo president waphawi sakupanga zandale koma akuimilila amalawi osat chipan
@stanbanda
@stanbanda 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂❤❤❤
@ManenoKanyika
@ManenoKanyika Ай бұрын
Ukunama iweeee upeze ena oaputsitsa
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 2 ай бұрын
Kung'alula basi Dc
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 2 ай бұрын
Kalindo tangopita ku dpp uzikapha nawo albino agogowo usakhale wanzelu ndiwe wekha chilima siwomsewelesa ndipo munthu sali ngati iwe galu wouwila adpp chosilu
@user-op3nx5qt4q
@user-op3nx5qt4q 2 ай бұрын
Iwe ndiwe opanda nzelu satana moti malawi ili pamamvuto sukuwona wekha Galu iwe ukatelo umati inapita ku school 😢😢😢 ndikukumvela chisoni kwambiri kuligalira abale ako akumvutika kwambiri chifukwa cha iwe ndi MCP Chakwera
@labsonwisick7057
@labsonwisick7057 2 ай бұрын
Yabayatu imwani panado
@InnocentChiwaya-qw7zu
@InnocentChiwaya-qw7zu Ай бұрын
Thank you Bon kalindo.iweyo ndi more.waiwala anyamata awa.pitala ndi mphatso anyamata anagijima awa koma mmmh kungowataya.
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di 2 ай бұрын
Nde tizavotela Yani poti akumbuyo onsewa nde worse chifukwa pano tinapenyatu
@CharlesTambala-zn2bd
@CharlesTambala-zn2bd 2 ай бұрын
Mr Kalindo... I thought that you were an activist? you have a political element... ..
@RenardYono
@RenardYono 2 ай бұрын
Auzeni apepese azi kazao bas
@SildaKatundu
@SildaKatundu 2 ай бұрын
Kupepesa kulibe nthawi ngayi tchimo kwa Mulungu
@MacmillanMakombe-sz4iy
@MacmillanMakombe-sz4iy 2 ай бұрын
Palibe zimenezo Mukakhala ndizimaganizo zoti kupepesa kulibe nthawi mupitirira kunamizidwa NDI andalewa, Uku dziko likulowa pansi Be serious
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 2 ай бұрын
Inu akalindo unakukanikani u MP ndiye musamalakjure ngati anzeru
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Umbuli wakumenyani kwambiri akalindo utm mote Moto
@ChimwemweAsifa-wh4mf
@ChimwemweAsifa-wh4mf 2 ай бұрын
Mbuli yaikulu ndwe
@FiscaniCasambara
@FiscaniCasambara Ай бұрын
Born kalindo pick it up ' chilungamo
@PaulvinMhango
@PaulvinMhango 2 ай бұрын
Born kalindo ndi mbuzi
@user-op3nx5qt4q
@user-op3nx5qt4q 2 ай бұрын
Iwe ndi Galu wachabe chabe satana ndipo Uyambe ku pita ku church Galu
@BrightonStorey
@BrightonStorey Ай бұрын
Zaziiiii
@BrownMatonyola-xi3lb
@BrownMatonyola-xi3lb 2 ай бұрын
Uyu nde akufinisher tonse manyaka
@SamsonLynfordmpnda
@SamsonLynfordmpnda Ай бұрын
Chamba uyoso chimapweteka chitsilu cha munthu
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 2 ай бұрын
Zoona the DC
@NumeliKambo
@NumeliKambo Ай бұрын
Kuyankhula zoona. Zokha zokha
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 2 ай бұрын
Mbambande the DC
@ChimwemweAsifa-wh4mf
@ChimwemweAsifa-wh4mf 2 ай бұрын
😂😂😂
@ShadreckPhiri-er2nb
@ShadreckPhiri-er2nb 2 ай бұрын
Mpaka utm
@pempheropharaohphiri3634
@pempheropharaohphiri3634 2 ай бұрын
😂
@SemuJali
@SemuJali Ай бұрын
Ine ndibanja ranga sitidzavotaso
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Umbuli wakumenyani kwambiri akalindo
@alliimraan3985
@alliimraan3985 Ай бұрын
Kkkkkkkkkk 0 per ten!!!!!
@williamjuliuskitha4861
@williamjuliuskitha4861 2 ай бұрын
This charlatan must not be anywhere near UTM.
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el 2 ай бұрын
umakwana iwe President wanthu wawumphawo
@ronaldbysonchisale2110
@ronaldbysonchisale2110 Ай бұрын
Apatu nduvera atamwalira Chilima
@user-vh9oy9io8n
@user-vh9oy9io8n Ай бұрын
Iwe ndiye opusa kobasi Mulungu wake uti okumva zopusa zakozo, satanic iwe
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 2 ай бұрын
Utm ndye chaniso onse ndiolephera bas chilima kape ngati ameneuja
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 2 ай бұрын
Time Up, no Points earned!!, iwee kalausi chilima, usatitenge amalawife ngati zitsiru wamvaa?, we don't need your apology ok, your apology hasn't been accepted, you failed us!
@MaxwellSakwata-wb8ep
@MaxwellSakwata-wb8ep Ай бұрын
Kalindo please don't change to the wrong chanel
@FlechaChipeta
@FlechaChipeta Ай бұрын
Kalindo ukarankhura chilungamo
@YinomiyaEko
@YinomiyaEko Ай бұрын
Bono kalindo ndiwe m,banga
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Galu wena, zoyankhula za ziii
@user-qu9ww1cd1y
@user-qu9ww1cd1y 2 ай бұрын
Mutu sukugwira
@owenmulemba5347
@owenmulemba5347 2 ай бұрын
Kupepesa kulibe nthawi, munthu amatha kupepesa nthawi iliyose
@stanleysaiwa9120
@stanleysaiwa9120 2 ай бұрын
koma ngati kupepesako kwafika muthawi yosayenera kumakhala kolakwikwa
@oscarnamirecah5386
@oscarnamirecah5386 2 ай бұрын
Bagamoyo
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 2 ай бұрын
Auze amvesese
@user-ls5hh8lb5f
@user-ls5hh8lb5f 2 ай бұрын
Kape winiko wa DPP
@VincentMpokosa
@VincentMpokosa 2 ай бұрын
Dc ndi mamuna,sagawa kamba
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 2 ай бұрын
Kalindo ife timakunyadila
@ClementinoAnerio
@ClementinoAnerio 2 ай бұрын
Kalindo ng,alura boma lakuba iyi
@user-nc6cz4jn9r
@user-nc6cz4jn9r Ай бұрын
Apa sipopangira ma drama
@MwizaChavula
@MwizaChavula 2 ай бұрын
Iwe ulindi vuto kalinda
@MsondaBanda
@MsondaBanda Ай бұрын
Kalindo please please
@user-vh9oy9io8n
@user-vh9oy9io8n Ай бұрын
Wamisala uyu
@innocentbanda-zc6zf
@innocentbanda-zc6zf 2 ай бұрын
Awa ndachitsiru
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 2 ай бұрын
Chitsilu ndiwe
@amourvido8027
@amourvido8027 2 ай бұрын
Achitsiru awaaa, za ziiii
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 2 ай бұрын
A chitsilu ndiwe
@amourvido8027
@amourvido8027 2 ай бұрын
@@user-jn9tz3li3v oky
@DooksyYasidu
@DooksyYasidu Ай бұрын
Eiich kuli znthu
@MusaMKaunda
@MusaMKaunda 2 ай бұрын
Kuswa
@WhytedMary
@WhytedMary 2 ай бұрын
Aaaaaaa
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Kalindo galu of land
@SildaKatundu
@SildaKatundu 2 ай бұрын
Kalndo umayankhula za nzeru koma iyi yokha nde wapala, wanama .Vote yanga ndi SKC basi
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 2 ай бұрын
Asa ungotaya tym yako ase uzapindulan
Donald Trump Addresses Republican Convention After Assassination Attempt
12:24
Good Morning Britain
Рет қаралды 116 М.
This is not my neighbor  Terrible neighbor! #funny #zoonomaly #memes
00:26
УГАДАЙ ГДЕ ПРАВИЛЬНЫЙ ЦВЕТ?😱
00:14
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 3,7 МЛН
ZODIAKTV CRUISE 5 WITH MRS MARY CHILIMA
41:54
Zodiak Malawi
Рет қаралды 94 М.
Microsoft | Outage sparks chaos - Nick Harper shares more
9:23
SABC News
Рет қаралды 1,4 М.
SIHI Uganda Fellowship Program
6:33
Social Innovation in Health Initiative
Рет қаралды 434
MAI JANE ANSAH (TIPPEX) part TWO-02
53:34
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 20 М.
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 138 М.
A Kalindo Musalimbikitse Umphawi - Shaffie Hassan
18:36
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,6 М.
This is not my neighbor  Terrible neighbor! #funny #zoonomaly #memes
00:26