We miss you bakili muluzi tv, it's been two days without you😢
@jogechawa6192Ай бұрын
I hope he is okay asatipheleyi
@abisalomchunga6695Ай бұрын
Timuikize mumanja mwa ambuye
@Homeofpeace321Ай бұрын
Amene simunva chitumbuka akuti, Chakwela ndi Chule, Chilima Ndijoka
@MacmillanMakombe-sz4iyАй бұрын
😂😂😂😂😂
@harrymicah6140Ай бұрын
Kakakakak mmmm
@raytavares2256Ай бұрын
Bodza akuti iwowa abusa MM anali mkati mwakasupe wamadzi koma ukakamiza chule akuthawa mmadzi mom amakhala ataona njoka mmadzi mom, he means that he him escape the serpent. Tell people the truth.
@BrownMainje-sh7hjАй бұрын
Kkkkk inbox me please
@user-yb1nt9te7fАй бұрын
We need back our guy 😭😭😭
@YabwataАй бұрын
Please 2025 vote for pm plz kuzabayizika yayo plz kumupoto kwi2 uko plz ,Only pm can rescue us, and plz brother tell us about vote here in SA how didi it go ,I wish DA could win.
Bwana wathu kodi mulikuti imfe tiri wodandawula kwambiri sitikuwona video new one😢😢
@McfrankJacksonАй бұрын
Voice ya bigy zkutibwaaaa
@AuffiPillo-cf9rnАй бұрын
Best TV ever
@HappyAbyssinianCat-xt2bmАй бұрын
Km ine ndili ku south Africa chaka cha mawa ndkubwera kuzavota kumalawi ndpo chakwera uyu sindkumufuna ndizavotera adad tikufuna nsima ife feterez ndamene timafuna❤
@LysonMtalika-tb6fkАй бұрын
Powerful!!! 💪
@juliochiwaloАй бұрын
Mmalawi wa nzeru uyu
@abrahammwekinda9605Ай бұрын
Hie Mr new presenter. Mukanakwezako mawu kuti tizimva bwino. My phone is at maximum volume but still am struggling to hear clearly.
@kingsleyhopematchaya5184Ай бұрын
Ndiye ku Zambia Mozambique Tanzania anakweza ndi chakwera kod tiziti ndivhiyani mumanganiza athunu or apm akanakhalapo akanakwera anakwera dziko lapasi
@honourablemcgregorysc97tvАй бұрын
Best Ever TV
@RazarusmbavachakweraАй бұрын
Guys I miss bakili muluzi tv 📺 where is our best journalist it's been a while
@chigokhalid9420Ай бұрын
Lero akulankhulayu nde uti?
@UNIMAMOMENTS123Ай бұрын
amene akuyankhulayu sakukumesa aaaaa
@AustinChiyembekezo-cx4mzАй бұрын
Dzika yokhuzidwa
@sebi2439Ай бұрын
Boss tapangani check in mukusowatu, muli kutiko
@Kay-racle_mwАй бұрын
Best TV
@jogechawa6192Ай бұрын
BM tv takusowani koma muli bwinobwino?
@isabelmartin7567Ай бұрын
Bakili muluzi please come out we need you this time please 😭😭
@user-ud6qc9mw7bАй бұрын
Where is our man bakili muluzi tv we miss you too much
Ndipo even chilima asakunamizeninso amalawi anzanga tiyeni ku DPP
@user-pn7cj9hb3tАй бұрын
Awuze
@hastingsmunthali4298Ай бұрын
Even panopa ku Jon kukuwawa chifukwa chachibwana awa akutcha apuledetiwa e.g fertilizer in 3 ago 100 thousands amagula 4 bags koma pano just the period of 3 years zikufunika kutumiza 500 zowawa kwambiri.
@user-dk6nk7hx5qАй бұрын
Koma akuluwa alipo sathatu 2days opanda video ananjatidwa kapena 😢😢😢
@christophergondwe6562Ай бұрын
8 days bro mwatiyiwala2. daily. bundle timagula bcouse ov u bro
@peterjim6810Ай бұрын
No any updates for 6 days now are you arrested?
@AffickChaonaАй бұрын
Ulendo uno anthu avota malingana ndi zimene aona osati kunva Best TV in Malawi bakiri Muluzi TV
@davenchimadzi6529Ай бұрын
Kodi mwini voice mulipo big? Kapena akupezani a MCP aja😢