Koma tu palibe munthu angawongole phazil lake akamayenda zonse munena apa nonse ndinu akuba okha okha
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Kkkk ukamati akuba tokha tokha meaning what?
@demsterenason73985 ай бұрын
Amkanyoza DPP
@harrymicah61405 ай бұрын
😂😂😂😂 koma ya osapya ntima ayih
@tisuhmakhwah70855 ай бұрын
Kk kali mwalatu
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Thanks boss
@christophergibson724 ай бұрын
Osapita kukawauza live pa maso bwanji zamkutuzo
@user-sh5wq4uf6r5 ай бұрын
Mmmmmm koma
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Osakayika kkk
@ZephaniaJoseph-zq8jj5 ай бұрын
Inu abwana ayakhula kuti izi
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Adayankhula in 2019 boss
@Allan-bk12 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 eeeesh
@greychizaka40885 ай бұрын
Chilimatu ndi shasha😂
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Kwabaxi 🤣
@Razzaq20105 ай бұрын
Shasha opoila
@greychizaka40885 ай бұрын
@@Razzaq2010 maybe you just hate him but ifeyo timauona udolo wake
@Razzaq20105 ай бұрын
@@greychizaka4088 palitu udolo Nde pali udolofe ,chilima ndi dolofe
@LukeshadrickShadrick5 ай бұрын
Mauwa analankhuladi akuluwa angopanga edit
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Anayankhula ndithu boss
@LukeshadrickShadrick5 ай бұрын
Koma ndale za kumalawi zogwebana basi
@user-oo5bx1rl3j4 ай бұрын
Mwatha inuyo ada ndimiyambi yanuyo MCP yakumalizani afana oganiza booooo. no chance for you my brother again in Malawi. For now you're finished completely finished on your career. I think the best way you must give up to the Malawians. Beacuse for now you have know words to tell the Malawians. So how can they trust you again? beacuse ur just keep quiet like nkhuku ya Mikolongwe
@lucianojames75555 ай бұрын
Koma kuli zinthu kkkkk
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Tikonzekera next year campaign
@tingamasi1065 ай бұрын
Thats not his voice thats the exactly voice of chilima. Achita photoshop
@honourablemcgregorysc97tv5 ай бұрын
Aaaa inu you don't know what you are talking about, I can't come here posting my videos of high Government officials oti sanayankhulepo. Do you know kuti ndi mlandu or I can say ndinakatha kumangidwa