Ndinkangomva kung'alula km uku ndimapeto a kuswakuswa ❤❤❤
@user-mi3fw1zg8bАй бұрын
More fire Chihana komano ngati mukufuna vote yanga mukampepese APM kaye pa zomwe mudapanga in 2019 mkuchiika chigawengachi pampando
@user-gr5zt6kw3sАй бұрын
This is awesome speech, we have someone who was part of the signing. Glory to God, no one can play God. Thank you sir
@AlexKaunda-ny2egАй бұрын
Munamupusisa nzanu mwaona tsopano chakwera ndi chigawenga😢😢
@TaweniChavulaKamwendoАй бұрын
Eeee simbi yakalipa 😂😂
@PreciousBandah-l2rАй бұрын
Kkkkk waukape iwe chakwela awinabe
@lindananthalo5327Ай бұрын
@@PreciousBandah-l2rmukaberatu ungrateful pastor God is watching
@limbikanil.i.mmtewa759529 күн бұрын
MCP really, idzawina bwanji@@PreciousBandah-l2r
@KENETHMAJASA-ud5eeАй бұрын
Uli bhooo Enock, keep the fire burning
@chrisboyce2Ай бұрын
Simbi ya moto🔥🔥💪 AFORD + UTM + DPP My vote💙
@JacobMphandeАй бұрын
Iyi ndiye tonse alias ina kkkk
@PreciousBandah-l2rАй бұрын
Km mcp iwinaso wava
@SamKaposa-i5cАй бұрын
Plus udf
@temwarachaelkhonje3733Ай бұрын
I like aford and Enock....the party cloth is also beautiful...
@wittinessnkhokweАй бұрын
But similar to dpp interms of colour
@KennedyPhiri-h9hАй бұрын
To all Malawians tiyeni tidzuke and fight for this country pls chakwela ndi chingawenga chachikulu 😢
@JuvenileDebwe-bv8owАй бұрын
Wodana ndi izi ndi mfiti Malawi tonse ndife banja ngati wina akulakwitsa tidzudzule basi bravo Chihana
@kilt_la-flame265Ай бұрын
uyuyu ndi deal, no matha and straight forward leader🙌
@PhillipJoseph-kp1glАй бұрын
Okuba ndichincho awine tione ma fruits ake
@GodfreyWhayo-hh1dmАй бұрын
This is rare courage .With a free and fair election ,MCP can't win an election .To people's surprise MCP is already claiming a land slide victory with 70% . Let's wake up and check out what they are relying on to determine election results before polling.
@EmercianahKasiku-en6hlАй бұрын
Kampeni sinayambe nkhani ilipano mdziko muno ndi ya Chilima zafundo azakamba nthawi ya Kampeni ikakwana mumva mbembe munapha Anthu osalakwa
@PatrickBondo-ur2plАй бұрын
Munamuphetsa mwana osalakwa
@abdulhameed7808Ай бұрын
Okuchenjezani analipo Koma inu kusamva. MCP will never change. Amenewa ndimawu a former president Dr Bakili Muluzi
@EmmanuelMoyo-hy5niАй бұрын
Kusamvera akulu akale
@user-zl8qr7vr2eАй бұрын
Muudzeni munthu waononga dziko lamalawi uyo mmm amalawi zavoteni mwanzeru mwamva mmene chihana wayankhuliramo presdent wanzeru chihana more fire
@lorainemponelaАй бұрын
This calibre of leadership is what we need: Leaders who are activists/fighters at heart. They rebuke whenever it calls for rebuke. They praise when you deserve a praise. Viva ✌🏿AFORD.
@DysonUmaliАй бұрын
Malawians keep your anger and vote to remove the tyrany.
@cassimyusuf668329 күн бұрын
We need people like you in Malawi , MCP asatibwezerese ife ku 1 party system.
@ChamelionJonesАй бұрын
We need asogoleli olimba ntima like you osati kumangosekelela we are on your back fad skc tikumulilabe
@GraceZumazumaАй бұрын
Mmanja mwanu a Chihana kuyankhula mosanyengelera muuzeni chikangawa mfiti wakupha okondela odya maliro kupanda chilima akamnamvotela ndani ameneyo
@shadreckphiri1799Ай бұрын
There's no government. For as long as UTM is no longer in alliance,then Malawi must go for elections.
@saintjoseph6572Ай бұрын
Which constitution? As a country we do things in line with the constitution not with mere agreements that are not constitutional bound. If Tonse alliance agreement is constitution bound, then we can go for elections but if not, let's wait for 2025😅
@KENETHMAJASA-ud5eeАй бұрын
What a strong leader he is
@JohnConar-kq4hiАй бұрын
Chihana is back
@iangondwe6857Ай бұрын
i respect the president of malawi coz the bible said so zinazo God will judge at the end but God help you mr president
@CeniaMayeni29 күн бұрын
Stupid statement from a stupid person
@user-hh4wn4vf9eАй бұрын
😂😂😂😂 koma ndaseka lne akut mulemba chani 😊😊
@CharityMsyaliАй бұрын
eti eti😅
@MafunaseKamotoАй бұрын
Ipatse moto mwana wa simbi ...iyi ndiye timati democracy osati autocratic rule ili Leroyi
@EdwardKamangaАй бұрын
Well done speech without fear
@dexzimba4082Ай бұрын
Very good msg am a tumbuka pangan volongosoka tiliwakali kuno ku south Africa palije vote pala mukapwekesa because apa tili pa vipan 3kupatula mcp
@fleshar-j6iАй бұрын
Moto ngat uwuwu nd omwe ufunika kuuyatsa, keep it up.
@user-ok7bq9es3yАй бұрын
Kodi abale inu over my died body, Afford ingalowe boma? Zomwe akunena a Chihana kunyoza president and MCP ndi chimodzimodzi kunyoza achewa. Ndipo akunama kwambiri Chihana, MCP sichipani cha mu suitcase ai.muzane nonse
@ChamelionJonesАй бұрын
Ukunama ase kwanu konko mcp
@lindananthalo5327Ай бұрын
@@ChamelionJoneskwao konkodi
@user-un6qv6sj3hАй бұрын
Akulemba bodza coz muli live ndithu osaopa osafooka osapepesa ❤❤❤
@mortonmsukwa2125Ай бұрын
Koma kulankhula kwa Chihana kopusa kombwambwana. Ati kufuna mavoti. MCP my vote.
I speak on behalf of the fell Malawians about your secret politics .guys we are tired of being cheated. Achihana and your friends where were you when you became across the fact that chilima ndi mbava and let him lead Malawians cruetly. Now that we are one year behind elections ndiye mukufuna muoneke wabwino. Think about anthu amene Akhara akuzunzika ndi njala since we voted you pple. Munkati DPP was wrong of which DPP eversince pple never suffered at this far. Ndinu anthu oipa guys. Munali anzeru before Lero mukuwukirana yet you know palibe chomwe mwachita
@RaphiqueYusufАй бұрын
Ng'ona ndi Ng'ona anthu aMCP ndi mbabva , tikumana 2025 a Malawife sitikusangalala ndi momwe mokuyendetsera boma
@ElliotNkoko29 күн бұрын
Bwana tiuzeni teopano nfundo zoti tikuvotereni,komanso mavuto ali mu dziko lino angathe bwanji
@KuhuniChopi29 күн бұрын
This not the time boss osasokoneza zinthu
@PhillipRoyMsiyaАй бұрын
Achihana muzlankhula mfundo osati manosensi
@Nomsa77Ай бұрын
Amen mulungu awakanthe achakwera
@EnockBwailaАй бұрын
Let's be considerate just tolk what makes people to vote for you dzina la mwana uja silopangila ndare
Mwapeza zoyankhula pa campaign Anyway tizavota koma
@GraceLuwemba21 күн бұрын
Akut ngat tikufuna jona ,kumwamba mulungu alipo
@EliasKawuwaАй бұрын
Tell us what you will for Malawians, not za Maliro ,nthawi imene Malemu analipo, mumamunyizaso pamodzi ndi Chakwera, nde Saulosi musiyeni,mudzingonena zomwe mudzachitire dziko la Malawi
@lindananthalo5327Ай бұрын
Azanena pa campaign ife tikulira achilima ndipo mtima ukuwawa
@Justman34_dislikeАй бұрын
Great speech
@user-uj4oi7xv6eАй бұрын
Baseless points
@robsontyg3928Ай бұрын
Mbuzi za anthu
@user-vx5kv8dz3dАй бұрын
Tawazuseni anyamata apange za Kenya . Inu president asamakhale above the law. Presidential immunity tichose basi . Komaso ndalama sichoke ku account number one zipite ku ma district
@ahhobebamw7365Ай бұрын
Kubudura ndiwo zagulu 😂😂🎉🎉🎉🎉
@user-jk8sh7fh2d28 күн бұрын
Vuto ndale za kwathu apa amayankhula ngati atakhala pampando apanga zanzelu aaah ziko langali ai zikomo
@GersomChingani29 күн бұрын
We want zinthu zomwe mupange ngat Aford not maliro a SKC ngat campaign tool.
Pondani moto fada,MCP sizasintha mpaka muyaya basi. Ndipo komwe aliko ayiwale zoti azalamulilanso 😢,mwakhetsa misonzi ya nzika za ku Malawi mokwanila.
@AR-l-YАй бұрын
We are waiting for 20 days from Mr chakwela to tell us the results
@evahkaendera7755Ай бұрын
Mzimu wa Chilima uwuse mumtendere 💐💐
@AlexHenere-r6lАй бұрын
Tithokoze eeee abwana apa mwayankhula pitilizan koma nthawi isanathe chitani changu pangani mgwiriza DPP UTM ndi AFORD fundo zanu ndizabwino
@KenRobert-j1yАй бұрын
nice zinali pat zimenezo
@UPPERROOMWORSHIPCENTERTVАй бұрын
Ndale za ku Malawi sizidzathandiza a Malawi ngati inu anthu andale simungasiye kuchedwa ndi kutukwanizana mmalo moliuza dziko zomwe inu mudzachitire anthu mukadzapambana, Maliro chi chinthu chopangira kampen ayi Chitani manyazi
@AlexKaunda-ny2egАй бұрын
Koma abale zikhale ng'oma nduna Koma ndi minyama yadziko abale😢😢
@KennedyPhiri-h9hАй бұрын
😂😂😅😂😂 koma inu kkkk
@jonas-xh4hzАй бұрын
waphalirani boma ili latigongowesa kweniso latondeka likupulikaso yayi malango likupokera kweni no kupulika yewo
@LouisAndrew-jr1yjАй бұрын
Keep fire burning 😂😂😂🙌
@user-cz8dc9ik5y29 күн бұрын
Well spoken mr Aford president but we expected you to said this long time ago when things turn wrong. You were waiting for skc to die first and then be active ?
@user-mw3kj4qz7b29 күн бұрын
Even us from Zambia we want answer s how the the eroplan crushed
@user-nw6ie3xx8bАй бұрын
Fundo apa palije nganya
@kilt_la-flame265Ай бұрын
Apaso si thawi ya campaign ndi thawi yopanga attack
@LimbikaniBanda-q7s28 күн бұрын
Kampeni wachaka chino mwakoza zoti muzingoyakhula za ifa ya chilima
@TiyesNayumaАй бұрын
Tell Malawians why we should vote for you osati mukunenazo ayi we need solutions to malawi problem not attacking pipo.
@ChikondiKwengwereАй бұрын
This is what we want to hear boss ndipo we expected a beautiful speech like this
@lindananthalo5327Ай бұрын
What is wrong with this speech....we want the truth about SKC
@TiyesNayumaАй бұрын
@@lindananthalo5327 after you knw then what ? We need speech with merit.