Nkhani ikhale UTM , AFORD ndi UDF apange alliance, president achoke ku UTM ndekuti azapeza ma vote Ku north , central pang'ono koma ochuluka ku southern nde kuti azaiphula bho bho
@AnthonyPhiri-qp8fn26 күн бұрын
Mr bon kalindo thanks live on zambia Lusaka
@KhalideNerve-mu1eq26 күн бұрын
Mission possible
@user-iz3qr1gu9d26 күн бұрын
UTM welcome back to DPP family
@mishasjambo479326 күн бұрын
Eeeh ndine bon ...... 😂😂😂 Kuipatsatu fireee
@Yuze_Matukula26 күн бұрын
Boooooooooon Kalindo!🔥
@OmecxKondwan-dx7do26 күн бұрын
Mr DC hohoho🔥🔥🔥
@user-wh6zp4vx1n26 күн бұрын
Chikati hahahaaa Ndipo chimaseka modelela Chi Born Kalindooooo
@chrisneySwanepoel-yu5vd26 күн бұрын
Born kalindo ndakamuna
@IssahAluba26 күн бұрын
So good 👍
@McDonaldMakina26 күн бұрын
Pangolini tsopano
@daudinussah223226 күн бұрын
Ubwino wake ovota ndife, and kalikonse kochitika pansi pathambo Mulungu amachionetsa poyera
@GogoKasiketi25 күн бұрын
God first
@PemphoSmart24 күн бұрын
Propaganda at its peak. Ife anthu osauka takana kuti ndiwe president wathu
@InnocentSayenda25 күн бұрын
Mmakwanila big
@GeorgePhiri-ub2of25 күн бұрын
Pakhala mabvuto olimbilana utsogoleli APA ifee phee Ku MCP basi
@AlbertNambwale-sm9qe25 күн бұрын
Well did L
@user-wi9pe2hz7e25 күн бұрын
Mawu a Bon sapita pachabe nd Yosef mwana wa maloto😅
@desmondshugar458526 күн бұрын
Good
@PeterJanga-wv9nz25 күн бұрын
Born kalindo akamuna bambo
@Africanbwoy18525 күн бұрын
Uthenga ukupita kwa Michael Usi aka Manganya
@AlidiMdala26 күн бұрын
Munyengo yong'alula🔥
@RuthChilobwe26 күн бұрын
UTM ISAPHATIKIZANE NDI DPP CHIFUKWA MKAZI WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POTHAWA MOTO KU SODOMU..PAMENE NGELO WA AMBUYE ANAWAUZA KUTI ALIYENSE ASAYANG'ANE MBUYO. KOMA MKAZI WAKE WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POGANIZIRA MOWA WAKE WOMWE ANKAPHIKA KUSOMUKO NKUMAGULITSA. IYEO ANASANDUKA CHULU CHA MCHERE. SO UTM NSO MUKAPHATIKANA NDI DPP MUSANDUKA CHULU CHA MCHERE.MUKHALA STUCK AND DORMANT DEAD WOOD .!!!
@EdisonNgolomibanda26 күн бұрын
Carry on pangolin
@SteveGemini26 күн бұрын
This is boooooooorn Kalindo🤣🤣🤣💯🔥
@ChifundoNinje26 күн бұрын
This is the truth utm plz bwererani ku dpp
@raymondlupiya26 күн бұрын
Ichichi chinabwera🔥🔥🔥.
@Yungjoe78625 күн бұрын
Pangolin iweyo the DC
@LDeeNdilimunjila-zs1qh26 күн бұрын
Born!!!!!!!!!!!! Kalindo!!!!!!
@heavenpromotions26 күн бұрын
Akuti anzanu wo anavota kale😂😂
@YusufujohnSeruweke25 күн бұрын
Chilungamo kalindo
@RuthChilobwe26 күн бұрын
And madam Patrucia Kaluati being the leader of utm presidential.candidate.cos she is has got experience of leadership.by profession she is a teacher and again she has experience of political leadership.she was in dpp .wurh Bingu wamutharika and peter mutharika
@user-xn5jl3sp6d26 күн бұрын
Born💥💥💥
@MarkTembo-ut9sv26 күн бұрын
Ku dpp tikataniko? Chilima anatulukako ndipo sanabwelere mpaka kufa kwake ndiye ife tufuna mufuna mzimu wake utikanthe?
@MosesNjanje26 күн бұрын
Ndeee kupusako do you think kut utm payokha ingagwetse mcp yotiiii ili m'boma inuyo dziko lanu simulikondayiiii amkolo chilima ananena yekha kut ku dpp anachokako analibe vuto lililonseee ndee inu ndare simuzidziwa Bola mungokharah chete ngt muganiza kut mungazawine panokha kuchotsa chipan cholamulachi
@franciskameko258626 күн бұрын
A UTM panokhs simungalamule dziko ndpo position yanu izingokhala 3 or 4... Koma chifukwa chot ndinu okulamtima mumadzimva ngat muli nkuthekera... Kachipani ka ma MP 4 koma matama thooo🤣🤣🤣
Musiyeni Manganya asangalale ndi mdalitso wake, ndi Mulungu adalola kuti akhale pa mpando umenewo. Sizoti iyayi wa UTM weniweni apange resign, kuti chani? Kulephera kwanu musade nako anzanu amwayi.
@inessmsiyambiri851725 күн бұрын
Hehehehehe kweeee ulira sunati
@MEDSONMZUMARA26 күн бұрын
zoona kalindo chilungamo
@user-de9nx7ts2d26 күн бұрын
kung'alura
@isaacpiyo679226 күн бұрын
We are not going for coalition again
@franciskameko258626 күн бұрын
UTM chipani cha pa social media🤣
@christopherpetro-pen367826 күн бұрын
Komatu ndiye kuli kung'alula🤦
@chisomogareta195826 күн бұрын
Uyusotu amangolubwa
@richardkuwani364726 күн бұрын
Chayankhula bwinotu
@HarryKumwenda-jm1df26 күн бұрын
Utm
@SwazzyCassium-u9n25 күн бұрын
😂😂😂
@itzfazmuslimah26 күн бұрын
Uyuyu ndi 🔥🔥🔥
@RuthChilobwe26 күн бұрын
Correction utm has vast followers so let utm.stand alone..and its gonna win with the majority.nos
@EvyEvy-my9mj26 күн бұрын
😂😂😂😂
@gideonnyasa25 күн бұрын
A Kalindo zindikirani ichi dziko la Malawi ndi latonse, is not about resignation of its members in government positions. Stop misleading people, eg Usi won't resign cos he is serving Malawians not MCP.