No video

Zomwe wayankhula Michael Usi Lero atangofika mu Mzinda wa Blantyre

  Рет қаралды 21,157

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 125
@benardisaac1986
@benardisaac1986 Ай бұрын
Nyengo ndizosintha manvuto sankha moyo wose wamunthu koma Dr usi all the best
@user-zs6qc9dx8s
@user-zs6qc9dx8s Ай бұрын
We all know kut anthu omwe avala makaka a UTM nd a MCP. Eni eni a UTM sitikupanga nawo zopusazo.
@JonesSiliya
@JonesSiliya Ай бұрын
Zoona akufuna kupusitsa
@JonesSiliya
@JonesSiliya Ай бұрын
Chilima nzake amane amakambilana naye ndi ndani nanga nthawi imene amakusekani pakamwa ndindani
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 Ай бұрын
Manganya ndi wa MCP kuchokera kalekale
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 Ай бұрын
Michael usi is a matured intellectual who doesn't entertain nosense.
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 Ай бұрын
Wachepa nao u vice president.waiwala imfa ya skc.
@LukeKalima
@LukeKalima Ай бұрын
@@paulnyondo7572 aaaaaaaaaaa imfa ya skc ndiyotani anthu samamwalira kodi kapena munamuphera dala kuti muzipangira ndale imfa yake, kodi maliro akwanzanutu amaphweka chomchi akadzakhala akwanu zidzakuwawa kuti anthu azidzaseweretsa dzina la malemuwo
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 Ай бұрын
Ndimaona ngati adziyankhula zogwira mtima
@moyowrobert3331
@moyowrobert3331 Ай бұрын
zoti akumanga thumba ngati Mphaka sukuziwa
@hastingskalambo8502
@hastingskalambo8502 Ай бұрын
Ndekuti zoti UTM yatuluka ku alliance iyeyo sakudziwa
@JacobKasalika
@JacobKasalika Ай бұрын
UTM ndimaikonda komano tikudzibalalitsa yokhatu.Uyu ndinthu ndinyamata wa SCK
@LukeKalima
@LukeKalima Ай бұрын
Wandisangalatsa usi sakupanga nawo za mtopola ena achita manyanzi kumeneko ndiye kulankhulatu ambuye akudalitseni dr usi
@sanddaniweck2703
@sanddaniweck2703 Ай бұрын
Zangongole ife tilibenazo ntchito nkhani musise zinthu zakwela kwambili coz za Neef zo anthu ena akumamizi kwina salandila koma mukasisa zinthu anthu onse athandizika
@FrankSpison-o7o
@FrankSpison-o7o Ай бұрын
Mbuz yamunthu iyi yudasi ife a Utm zopusazo ayi sitikupanga nawo
@LeviBlackson
@LeviBlackson Ай бұрын
Anthu sakumudziwa Kodi ku Blantyre kapana amapanga sewero
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j Ай бұрын
Ngongole imeneyi udzabweza ndiwe . Fataleza udula konseko
@samchibenene4458
@samchibenene4458 Ай бұрын
Seriously
@Jane-qb5qf
@Jane-qb5qf Ай бұрын
Amalawi look sharp amalawi tilindivuto akati uku komweko uku komweko lekani timapemphera kukhala ndi chiganizo chokhazikika zimandimvesa chisoni kwambiri tisinthe mindset plz plz tizagwa chagada ndikati ndione amazayesa zida kuti kuli bwanji uku aaaa kaya Malawi
@SifatiMoses
@SifatiMoses Ай бұрын
Muli mbali iti kodi Fada
@user-nu1dj3jh7b
@user-nu1dj3jh7b Ай бұрын
Palibe azalande m'dalitso wamunthu, Dr usi ndiodalitsika muzonse komanso olimbika.
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi Ай бұрын
Koma bwanji sanavale makaka
@footballhighlightsofficial7248
@footballhighlightsofficial7248 Ай бұрын
​@@FrancisNyayiamugula a MCP
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 Ай бұрын
​@@FrancisNyayitikufuna chitukuko osati makaka
@user-dv6rt6vb6e
@user-dv6rt6vb6e Ай бұрын
Kusangalalila imfa ya mzawo
@joeldaniel-pc3ij
@joeldaniel-pc3ij Ай бұрын
Mwapatsa anthu a MCP ma uniform a UTM kuti aziti chani?
@LeniaJosophat
@LeniaJosophat Ай бұрын
Mukutipatsirazi ndizabwino zeedi koma you need to fix the sound kuti zizikomabe( this is the VP)
@user-vb1iq5un5p
@user-vb1iq5un5p Ай бұрын
Kodi Usi ulimbali iti?. Koma umphawi luMalawi ukupepeletsa azibambo...
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane Ай бұрын
Mudyelen bambo wasikono akabwela osadziwa kuyankhula odvala madiresiyo
@JuniorKalipinde-gy7dx
@JuniorKalipinde-gy7dx Ай бұрын
Usaone ngati ndi bugwe LA adla limenelo akupweteka
@johnbakali27
@johnbakali27 Ай бұрын
Kodi iwe ukumenyera kampeni ya mco kapena UTM?
@user-hh4xg4hf2k
@user-hh4xg4hf2k Ай бұрын
Enafe tisayankhire
@JonesSiliya
@JonesSiliya Ай бұрын
Mwachedwa ndi chilima simunapange chifukwa chiyani
@FrankidEugenio
@FrankidEugenio Ай бұрын
Ndale zayambika,Malawi ayiwale zambuyo.😂
@user-dv6rt6vb6e
@user-dv6rt6vb6e Ай бұрын
Umbuli suzatha anthu munayambila kunamizidwa muja zilero changamukani
@constancemkandawire7378
@constancemkandawire7378 Ай бұрын
You can't say that you love God if you don't love your nearby that's a total lie.You have failed to come together with your fellow utm members mukuti phala lomwe likudumpha mu mpoto lidumphe meaning you don't care ,ayi zikomo
@user-ni4nw1ee2f
@user-ni4nw1ee2f Ай бұрын
Mwschedwa nayo ngongoleyo bwana kkkkkkk nyimbo ikhale ya mpaka malilo vinyo watha
@user-yq1mc3nm1f
@user-yq1mc3nm1f Ай бұрын
Dziko la Malawi lafika pa uchitsiru weni weni
@JuniorKalipinde-gy7dx
@JuniorKalipinde-gy7dx Ай бұрын
Ndipo live
@CHRISSYBALALIKA
@CHRISSYBALALIKA Ай бұрын
Tasisani fertilizer zinthu zisike agalu inu muona muwina mosavuta
@RossanaMitha-tl9in
@RossanaMitha-tl9in Ай бұрын
Kodi akuti kwabwela ndani ?😂😂😂😂
@lumbaninyirenda8223
@lumbaninyirenda8223 Ай бұрын
tamangopitani muzikapanga ma drama,mfundo palibe apa
@ChrisjuZiyaya
@ChrisjuZiyaya Ай бұрын
Chizindikiro choti Usi siwa utm onani zomwe zavalidwazo , zomwe Malemu Sks sadapangepo. Tikufuna m'tsogoleri wa serious not this gys.
@user-kg5lf6bd1g
@user-kg5lf6bd1g Ай бұрын
Lelo akunamizila chilima lelo ndi mbuzi yamunthu
@genesismbewe
@genesismbewe Ай бұрын
genius
@jedoforsure2842
@jedoforsure2842 Ай бұрын
Umakwana us
@joekamphulusa4767
@joekamphulusa4767 Ай бұрын
Chitsilu chenicheni ichi watenga athu a mcp kumati a utm 🚮🚮🚮
@footballhighlightsofficial7248
@footballhighlightsofficial7248 Ай бұрын
Missing Chilima Already😢
@MlecheFatch
@MlecheFatch Ай бұрын
A manganya mmmh
@enockharry8039
@enockharry8039 Ай бұрын
koma izi wina aziona
@joma5327
@joma5327 Ай бұрын
champhamvu kopasa kale kuthanthauza chani
@KondwaniNdobvie-f4v
@KondwaniNdobvie-f4v Ай бұрын
Komatu adzake afanazo
@user-qu9ww1cd1y
@user-qu9ww1cd1y Ай бұрын
Anamizana zokuti akope Southern Region
@ellahmvula
@ellahmvula Ай бұрын
Hahaha awa a mcp achina Eliza avala za utm
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Ай бұрын
Wakupha iwe manganya
@AbdulrahimoMassamba
@AbdulrahimoMassamba Ай бұрын
Satan ndiyemwe ali kutsogolo kwakoyo
@RobertChisenga-ci2mq
@RobertChisenga-ci2mq Ай бұрын
BT chitsilu2 paja
@MerySaid-uw3cm
@MerySaid-uw3cm Ай бұрын
Tikufelanji
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 Ай бұрын
Iweyo ukuti ukufuna ulongo sole, ndimaesa UTM yatuluka mungwirizano ukufuna kupusisanso Wanthu
@user-rs7vx6hc1k
@user-rs7vx6hc1k Ай бұрын
Basi tizingokhalira ma handouts mpaka liti abale?
@NkosDysonNkosDyson
@NkosDysonNkosDyson Ай бұрын
Tangotsitsani fertilizer muonanso mudzawina mosavuta ife amalawi sititichedwa kuiwala
@charlesmasauko4651
@charlesmasauko4651 Ай бұрын
Wosokoneza uyu
@macdonaldchaonekera834
@macdonaldchaonekera834 Ай бұрын
Kodi akupanga sewero la tikuferanji et?
@frankwilliam9844
@frankwilliam9844 Ай бұрын
There's contradictory in his mind,chomwe amalawi akufuna singongole,tsitsani zinthu,chepetsani kudalira ngongole za IMF...koma ndithu 60yrs independent Malawi yukanikabe kudalira payokha pa nkhani ya zachuma? so sad...Kodi maiko amzathuwa amatani Kodi ..adatukuka bwanji atalandila ufulu???
@NELSONMULIMAH-fv6ub
@NELSONMULIMAH-fv6ub Ай бұрын
Zauchisilu zaziii
@user-lu8px7td6p
@user-lu8px7td6p Ай бұрын
Aaaaaaaaaaaaaaaaaaa chitsiru mbuzi garu nyani mfiti iwe
@jeymulima9664
@jeymulima9664 Ай бұрын
Zaziiiiii
@user-kg5lf6bd1g
@user-kg5lf6bd1g Ай бұрын
Anthu 4 okha bs
@florenceharawa519
@florenceharawa519 Ай бұрын
Uku wapita uku wapita punsi anagwa chada😂😂😂😂
@user-rs7vx6hc1k
@user-rs7vx6hc1k Ай бұрын
Koma zimenezi zitithandiza izi????
@user-ep7gu2td6y
@user-ep7gu2td6y Ай бұрын
Sakudziwa zomwe a makawi akukumana nazo ....,
@MuhammadNyambalo
@MuhammadNyambalo Ай бұрын
😅😮😢😅😅😅😅😂 patumbo pako iwe nyo
@NathanMaunda-dz8gc
@NathanMaunda-dz8gc Ай бұрын
Awa sakuyankhula zotigwira mtima kodi nd wa chipani chanji ameneyi
@LottiAffati
@LottiAffati Ай бұрын
kod akuyankhula kut chan apa guys aaaaaa, komanso amalawi ngoputsadi ndithu
@MarthaChintolo
@MarthaChintolo Ай бұрын
Aaaaaa chifukwa chani Chilima unalakwitsa ee
@AbdullCassim
@AbdullCassim Ай бұрын
Iweso ndiye kayatu
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Ай бұрын
Ayakhura ali pat?
@chikondiyovita7210
@chikondiyovita7210 Ай бұрын
My data hu!
@Vascomw
@Vascomw Ай бұрын
Ïn̈ë n̈d̈ïm̈än̈g̈än̈ïz̈ä k̈üẗ äÿäk̈ḧür̈ä z̈äz̈ël̈üüü k̈m̈ ääää b̈ün̈d̈l̈ë ÿän̈g̈ä amayo
@momuumro
@momuumro Ай бұрын
Situfuna kunva zimenezo Ife tufuna nkhani yotuluka mu tonse alliance
@charlesmasauko4651
@charlesmasauko4651 Ай бұрын
Akufuna kugulitsa UTM KU MCP
@user-lu6nq9bs6w
@user-lu6nq9bs6w Ай бұрын
Nde ku MCP' ko akuti chani kkkk 😂😂😂
@elizabethnkhata3438
@elizabethnkhata3438 Ай бұрын
It's lik people are not happy
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh Ай бұрын
Ndimwana uyu alibe fundo
@QuotienieMw
@QuotienieMw Ай бұрын
Tikufilanji episode 10
@user-ou4md5ud1u
@user-ou4md5ud1u Ай бұрын
Sizikuveka ai komas sizikugwilizana ayi
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh Ай бұрын
Kupusa
@SifatiMoses
@SifatiMoses Ай бұрын
Palibe kunyengelerana ndi ngongore nbuzi za anthu.
@ElizabethMwakamogho-x7j
@ElizabethMwakamogho-x7j Ай бұрын
Sukuziwa make awo find alimbe
@user-zl1xz9kt5s
@user-zl1xz9kt5s Ай бұрын
Amalawi mitu sigwiradi sure
@Vascomw
@Vascomw Ай бұрын
Hhhhhhh
@user-lu8px7td6p
@user-lu8px7td6p Ай бұрын
Palibe chanzeru waywnkhula
@FysonKaliba
@FysonKaliba Ай бұрын
Kod ati Ali Mbali iti??????????
@SmithLikoswe
@SmithLikoswe Ай бұрын
Zamasewelo bac
@jeymulima9664
@jeymulima9664 Ай бұрын
Kkkkk ngabule moyo,thetsa,uthetsa suthetsa kkk yathayi kkk
@WindowSomanje
@WindowSomanje Ай бұрын
Za ziii
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Ай бұрын
Km malawi ndfe anthu opusa kwambiri tinakali kuvutika
@smartchitimbe2450
@smartchitimbe2450 Ай бұрын
Za ziii tu
@MECChiona
@MECChiona Ай бұрын
wamisara uyu 😂😂
@NATASHAChimtolo
@NATASHAChimtolo Ай бұрын
Opepela uyu malemu amavala makaka achipani chake
@RighteousMhone
@RighteousMhone Ай бұрын
Shimeyi atukwane😂😂😂
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j Ай бұрын
Emeneyi si dyera koma
@ChrisNkhoma-i8m
@ChrisNkhoma-i8m Ай бұрын
Mcp BOMA labwino kwamunthu woganiza mwazelu tiwone komwe tachoka .
@user-px6kt8rx2p
@user-px6kt8rx2p Ай бұрын
Yes
@user-uq4hn4rp2j
@user-uq4hn4rp2j Ай бұрын
Nice
@thokofodya1583
@thokofodya1583 Ай бұрын
😢
@user-hl3vl9nt1b
@user-hl3vl9nt1b Ай бұрын
Aaaa zazi bas
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko Ай бұрын
Sanje bac amalawi eeee
@FlorenceKamtema-kw5ru
@FlorenceKamtema-kw5ru Ай бұрын
Jealousy siumuna
@sonkieleymanni6312
@sonkieleymanni6312 Ай бұрын
ndiopusatu awawa,,,,,,,,,,,,,,,palibepo chanzeru anena apa
@LukeKalima
@LukeKalima Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 mumafuna akanamanyonza kuteroko mwakhaula mindset change ikufunika ndithu
@LukeKalima
@LukeKalima Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 mumafuna akanamanyonza kuteroko mwakhaula mindset change ikufunika ndithu
@SiphiweTonnyChidumayo
@SiphiweTonnyChidumayo Ай бұрын
Anthu sakusangalaratu😂😂
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 Ай бұрын
Ndizawo zimenezo komanso musawapangire Zochita anthuwo . ngati inuyo simukusangalala basi
@SiphiweTonnyChidumayo
@SiphiweTonnyChidumayo Ай бұрын
@@ancientnkhata1137 eh eh iwe im commenting according ndimmene zuonekera nsiye ine
🩷🩵VS👿
00:38
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 24 МЛН
ПОМОГЛА НАЗЫВАЕТСЯ😂
00:20
Chapitosiki
Рет қаралды 30 МЛН
My Cheetos🍕PIZZA #cooking #shorts
00:43
BANKII
Рет қаралды 27 МЛН
Bony Just Wants To Take A Shower #animation
00:10
GREEN MAX
Рет қаралды 7 МЛН
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
🩷🩵VS👿
00:38
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 24 МЛН