A Chakhaza mwàchita bwino kucheza ndi mayiwo ndamvetsera bwino. Koma mbali yomwe simunakhuze kwambiri ndi banja lawo, chidwi changa ndimafuna ndimve kuti amuna awo akutani ndikuwonjezera zomwe mungathe kuwonjezera za amuna awo.
@LamzyZiphah21 күн бұрын
Munthu wansangala❤
@OFG-th3st23 күн бұрын
Nthata za njala😢
@wangamusicofficial244324 күн бұрын
Rest well big
@user-sm8gx4vf1v24 күн бұрын
Abwino sakhalitsa
@GraceLimani-zw7dx24 күн бұрын
Uwuse
@GraceLimani-zw7dx24 күн бұрын
Mzimu wanu ukafuse mu mtendere Bishop kapenga mwalimba a nalo dziko kupereka uthengawo wa Mbuye kuti anthu tive za ufulu wakumwamba ambuye akusamalireni zimu wanu
@LeeroyKambale27 күн бұрын
😂😂🇲🇼🔥🇲🇼 interview ya bwino
@OviousSili-th5mk27 күн бұрын
❤❤❤
@bugadada575228 күн бұрын
Bon kalindo 🔥🔥🔥
@parcamkanda9629Ай бұрын
😂😂dolo
@bwenguking3894Ай бұрын
I support the court decision
@user-jc5tf8jl1mАй бұрын
Zoonadi Abishop
@MtenjeHassanАй бұрын
Ka sound ka mdyangu.....
@JuliusMandalaАй бұрын
😭😭😭😭😭😭😭
@isaacnkhambula6514Ай бұрын
🙆
@MoiNagaManuAseАй бұрын
Thank you so much for honouring the legend Chalamanda. Lots of love from India.
@user-hl5tk4ze1uАй бұрын
Zoona bishop we used to call you big Sunday powerful
@ChiyembekezoPhiri-sv8nwАй бұрын
Kumalawi athu amzeru alipo ndithu, vuto ndi ndale basi
@temwanyirenda7123Ай бұрын
Apostle misheck you have the message keep up the good work. Good understanding its vital than memorizing. You are doing good work Mr misheck you really understand may the good Lord bless you and give you wisdom