Alhamdulillah taphunzira kwambiri brother Allah adzikutsogolerani ndi kukutetezani inshaallah
@user-dl9hv8un5i4 ай бұрын
Zikomo kwambiri brother taphuzila nawo may God bless you 🙏
@mussanesterkapanda14177 ай бұрын
This is a welcome development Doc. Nanga mpaka free consultation? You were born to serve and not to be served. Keep it on!!!! Next topic idzakhale ya mauka. I guess anthu akusautsika nawo matendawa.
Dr. Chikakuda, ine ndikumangonda kuiwala maka kudzimitsa data ndie ndikufunika kuyedzetsa mwina ndi matenda omwewo 😂😂😂😂😂😂😂
@pscvideoz7 ай бұрын
Kmano kukayezetsa syphilis voluntarily ananiuza kt sapanga wamba ku KCH,they said unless I'm referred to "the test" by the doctor after the doctor has seen or discovered that some of the signs and symptoms I'm showing are related to syphilis. So you can see kufuna tinali Nako km tinakanizidwa access to voluntary syphilis testing at the KCH as big as it is 😢😢 Don't know what to do know,,, kaya what can be your say doctor??
Apa tikupangani address Ngati Doc sopano osatinso Che Mandota. So next one should be Hepatitis....I think ndika silent killer nako kameneka
@wilsonrajab16507 ай бұрын
Ndazikonda
@user-qw2vo4xh4q7 ай бұрын
Zikuveka kwambili a doc❤❤❤
@OsmanKassim-ec1hu7 ай бұрын
Munyao opusira ziyan kunena ayaove, 😂🎉
@user-js9op1xi8r7 ай бұрын
That's perfect may you explain about diabetes
@samuelmabulesse12677 ай бұрын
Zilibwino kwambiri malume
@shanlaljith53897 ай бұрын
Clear thanks
@user-ls4ct4qg3y7 ай бұрын
Pitilizani kutiphuzitsa achimwene
@user-jh8kq6uw2n7 ай бұрын
Kuleka zausatana bas kkkk koma mandota zikomo potikumbutsa ambuye akudalitse
@isaacfesani23577 ай бұрын
Powerful
@Mbozo_tv_20026 ай бұрын
Kodi munthu wamkulu pa nkhani yokhuza masturbation kd zimakhala ndi effect yotani kuma sex organs and kt uzisiye zimatani plz help me l've been m*** for 5 yrs now l found that l have penile disfaction wht is the connection? Plz help me plz
@mayah_kandoje7 ай бұрын
zikomo
@andymisempha8487 ай бұрын
Umakwana
@muhammadackleen24877 ай бұрын
Thanks ❤jameer😊
@liki-likiladies---lilongwe69637 ай бұрын
Doc tazakambani za nthenda ya gas ikusautsa nowadays😊
@lloydsimioneseveriano74967 ай бұрын
Yah zoonadi
@enockmsakatiza16837 ай бұрын
Zili bwino kwambiri tamvetsera mwachidwi. Next time dzakambeni za gas
@JosephNanjala7 ай бұрын
Nambalayo sikuoneka
@jamesedwin49687 ай бұрын
Thanks chemandota ndiyamba kusamala
@AhyamieChiwanda-zd1on7 ай бұрын
Doc ineyo Maka pankhani ya tizilondato tinandipangapo ndinagonana mosaziteteza and mapazi mate matentha ndeno ndingathandizidwe bwanji boss