Apa simungakhale che mandota ayi koma Dr chikakuda thanks alot
@vitumbikonkhonjera71786 ай бұрын
Mwabwera inuyo 🔥
@magretphili-un9up6 ай бұрын
Thanks for information doctor ❤
@JosephTembo-hm5yp6 ай бұрын
Doc doing what he knows best
@MickheyButison6 ай бұрын
White coat ineyo bola isazandigwireko kuchipatala kumandiopsa..... Keep it Dr. TIKUPHUNZIRA ZAMBIRI
@chikondikazembe26145 ай бұрын
Thanks Doc,may you please talk about ulcers if possible
@alexmajanja31796 ай бұрын
Zilibwino
@giftblack76906 ай бұрын
Thanx Doc zambili tikudziwila kwayinu
@user-nx2su4yr1l6 ай бұрын
Big up Mr chikakuda
@Clyne_Phiri_2656 ай бұрын
it's a nice move sir, we really appreciate this for the topic, but try not to be too technical for easy understanding,
@shakilasaid7056 ай бұрын
Thanks very much Dr
@ishmaelhamisi4 ай бұрын
Tell me more about angina and how to prevent it
@user-ug6ox9rf7c6 ай бұрын
Kodi nanga ungaziwe bwanji kuti uli ndi nthenda ya chizonono Pali zizindikiro zanji
@richardmolande6 ай бұрын
Following mwachidwi doctor pitilizani kutipasila uphungu wabwino.
@lucifrexmbungo21066 ай бұрын
Good explanation
@user-rm8oc7me8l6 ай бұрын
Thanks Dr chikakunda ❤❤❤
@stevenhonde106 ай бұрын
Please ngat nkotheka tidziwitsenkoso za Hepatitis tidziwekoso zambiri za Hepatitis nthenda yomwe ikumpha anthu mwa chinunu
@DuduNanchinga6 ай бұрын
Thanks so much bwana god bless you
@charniakayulayula62806 ай бұрын
Next ikhare ya asthma plz
@fatsosmart42956 ай бұрын
Inuyo mwabwela doc🥳🥳🥳🫴 we needed this
@user-kg5mb9ss7m6 ай бұрын
Taphumzilapo ndithu doctor
@haroonabdulahadulodala54756 ай бұрын
Thank you very much, the next topic should be for tb
@josephchidwala26976 ай бұрын
Thanks Doc. Taphunzira koma how do we overcome some of the side effects of BP drugs?
@user-qu9iu7hs8k6 ай бұрын
Za mphamvu Doc mandota
@trellixnazeer21916 ай бұрын
❤
@magamwagomba97216 ай бұрын
is there a range for "normal pressure" or whatever it is called?.. nanga ma pressure readings akakhala on the lower side, ndi zokhazokha mwakambazi?
@nerrcejngulube6 ай бұрын
Amuye akudaliseni aboc tikuphuzila zambili
@siskanyirenda6 ай бұрын
Zikomo kwambiri Doctor koma ndili ndi funso (FUNSO LANGA NDI ILI) Ine ndimati ndikhakhala pa mtima panga ndikhala ngati kuti chinthu China chakundiphwinda kenako ndimayamba kuvutika kupuma ndima banika kwambiri ndiye chimakhala chili chani please Doctor thandizeni