Akulu Akulu Achipani Cha UTM Kuyankha Mafunso Pa Hanifa tv

  Рет қаралды 12,279

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

Akulu Akulu Achipani Cha UTM Kuyakha Mafuso Pa Hanifa tv

Пікірлер: 94
@talentfreshfoods4607
@talentfreshfoods4607 2 ай бұрын
Ngakhale Satana Ali ndi omutsatira
@LesterKalipinde
@LesterKalipinde 2 ай бұрын
Aaaa,,nonsenu ndnu akuba,,mabuku ake ATI amene munenawo,,ndpo akweni nthaw yanu inatha bas munapangako mbali yanu asyen ena apangeko osat tizngomva zainu tangoyambani kutumikra mulungu osati mpaka mumwalile muli mu ndale ,,mukupitako mtendere kulimbe lapan lapan mulungu akukhululukiren nthawi ndyomwei
@FrankKambwani
@FrankKambwani 2 ай бұрын
Ndinthawi yoti a Malawi akudyereni ino,anthu oyipa kwabasi zoona mukanene kuti munatipatsa thobwa pomwe ife ndi thobwa lomwero sitinaliwone.Katundu wakwera mitengo inu mulimuboma momwemo.
@HassanTayubu-li3tm
@HassanTayubu-li3tm 2 ай бұрын
Amazing inu nzelu mulibetu koma zowona zimenezi
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 2 ай бұрын
Mwayamba maboza enatu kkklll😂😂😂😂😂😂😂
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e 2 ай бұрын
Zina ukamva 😂😂 mwauponda malawi wake ut
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 2 ай бұрын
Izinso ndiye ayitu.....APM MY VOTE
@MaliGomani
@MaliGomani 2 ай бұрын
Mbuzi za anthu abalaba inu 😂😂😂inuyo simungasithe kanthu mbuli
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 2 ай бұрын
Zachamba bas😮
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 2 ай бұрын
Tatopa ndi bodza inu aaaaa
@Favor.2023
@Favor.2023 2 ай бұрын
Mphuno ngati bwato mamaka atolskhani inu mukulimbilisa zompusa mulimbani kupanga zimafuso athu osa muziwa mulunguwo
@ZinenaniPetrol
@ZinenaniPetrol 2 ай бұрын
😂😂😂 Km kumeneko
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 2 ай бұрын
Kodi mukuti akuyakha fuso kapena akuyambana ndi atola nkhani kkkkkkk
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 2 ай бұрын
Chilima nde mbuziyo
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Mbuziyakensotu yamano kunsi
@chikumbutsomarch4484
@chikumbutsomarch4484 2 ай бұрын
Za ziiii, manyazi mulibe?
@ZinenaniPetrol
@ZinenaniPetrol 2 ай бұрын
Waditu kungoti alibe zimu owapanga control ntchimo lawo😢
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 2 ай бұрын
SKC my vote ❤❤❤❤
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 2 ай бұрын
Utm yu will never rule this country
@patisonlufan2823
@patisonlufan2823 2 ай бұрын
My vote
@paulmakaula4937
@paulmakaula4937 2 ай бұрын
Anzeruwo ali chipani chiticho??? Pajatu UTM sitinayiyesepo tidikile kaye
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Inu musapusise anthu musapusisa kale Kodi amayakhula zokudya katatu Mesa adali chilima ? Lero wapangapo chani Ngat vice President zaziii Musapeperese anthu inu simuvoteredwa mwasocheresa anthu akulira lero mcp ndi UTM foseck
@Misasi19
@Misasi19 2 ай бұрын
Azungu oyela okalambakalamba pamtumbo pako KALIATI
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 2 ай бұрын
Ndipo anthu inu a UTM musanamizenso anthu kawiri mwalelephera kuyendetsa BOMA ndi chakwera ndi chilima wanuyo tsppano musabwere ndi boza Lina pomwe mwaona kuti nthawi yatha tikupita kuzisankho palibe Pano angamukhulupile chilima ndi wonama kwambiri
@GeradiPhilip-hl9do
@GeradiPhilip-hl9do 2 ай бұрын
Bodza limenelo tidatopanalotu Lonenakuti =kudya katatu patsiku=feteleza ochipa mtengo" pezanilina bodzalo
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 2 ай бұрын
Nthaw yosei munali kt amalawi tikufa inu mkujoya ndiye pano mukubwera nsi zomwe zija aaaa nthata zanjala izi
@jamesgama5489
@jamesgama5489 2 ай бұрын
Abwere kuno ndi miyambi yakeyo tayisowa ma push ups atisenzere fertiliser afana oganiza bowa tambwali wa munthu chilima
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 2 ай бұрын
Ndipo galu wachabechabe
@ChimmsRichardOrden
@ChimmsRichardOrden 2 ай бұрын
Akweni this time around Musatipusitsenso anthu tikuzunzika ife chifukwa cha Mgwilizano wanj ndi MCP
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Aaa chilima olephela adzafa ndi mtima watsanje nde chifukwa ananthandidza MCP kuti udzitidzuza ife amalawi chotsangalasa ukutidzudza ife amalawi iyetso yakwapulaso ngati mwana otsamva kkkkkk
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 2 ай бұрын
Iwe kaliat osatinamize apa tinadya katatu kt chiloweleni boma inu ndachakwela wanuyo.
@EllizaEmmanuel-pz3pr
@EllizaEmmanuel-pz3pr 2 ай бұрын
Iwe napathako ukakhuta uzicheza ndizidzukulu zako oputsa yehova anaipidwa Nanu mukazawina ndizanyera kukamwa
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 2 ай бұрын
Akaliati bodza musanasiyebe mpaka lero,mulibe manyazi ?anthu munawanamizabe ,siyani kapangeni Zina izi mungodzitaitsa nthawi
@FaroukMdala
@FaroukMdala 2 ай бұрын
Mmayi uyu alibe Manyazi,aChilima Mbuzi,amayi Kaliati mbuzi,UTM yonse mbuzi mbuzi mbuzi
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 2 ай бұрын
MCP idutsa moyera cause sizikuyana chilima akatenga mavoti ake ikahalabe patsogolo nankhumwa atenganso ache MCP patsogolo zotsatira DPP mavoti a chepa in short chilima and nankhumwa athandiza MCP kugwetsa dpp poyima paokha
@user-nj3gn5xq2s
@user-nj3gn5xq2s 2 ай бұрын
Zaa ziiiii>
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 ай бұрын
Akweni ifetu a Malawi sindife zitsiru ayi. Kodi mubweranso ndi THUMBA pa Phewa? Kodi andale umakhala usatana chani? Inu mpaka lero kumalimba mtima kuyankhula mbwelerazo.
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 2 ай бұрын
Utm 2025 BOMA ❤❤❤❤❤
@innocentkandulu2825
@innocentkandulu2825 2 ай бұрын
kkkkkkkkk amene atakakuvote;eni inuwo ndiopusa okha basi
@owenmoses9434
@owenmoses9434 2 ай бұрын
Mwatitolamo mzikomuet zakuchiphwisi bas
@patrickmoffat9609
@patrickmoffat9609 2 ай бұрын
this lady I full nonsense chilima alibe leadership
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 2 ай бұрын
Chanel chotukwana ichi..too much ma comment Mamphuzo😂😂😂..Kaliati wakalamba please sitidzakuvotelani..
@ThomNkhoma-no5rt
@ThomNkhoma-no5rt 2 ай бұрын
UTM ❤ 🔥🔥🔥🔥
@user-gg6uh2wo4x
@user-gg6uh2wo4x 2 ай бұрын
Kapumeni mwakalamba chonde
@Yabwata
@Yabwata 2 ай бұрын
Vote for your own risk iyaaa , APM basi ❤
@user-tr4fv6ry9q
@user-tr4fv6ry9q 2 ай бұрын
Kweni kuphoda,ndizozola zake zozolesa malirozo,mbuzi za anthu
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 2 ай бұрын
Musavutike aliyense ali ndi Kukonda kwake SKC 2025 BOMA inu kavotereni agogo anuwo azikukambilani nthano
@user-tl1jq2gc5b
@user-tl1jq2gc5b 2 ай бұрын
Manifest amenewo mukapangira mnyumba mwanu
@user-qj3db4lu7c
@user-qj3db4lu7c 2 ай бұрын
ndipo amalawi Ngati amvere izi aaaaaaaa ine ayi
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 2 ай бұрын
Zauchitsiru zauhule zaumbava fotseki
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 2 ай бұрын
Chipani cha utm mwadzadza mbuli manyaka
@GidionJonas-sr4zr
@GidionJonas-sr4zr 2 ай бұрын
Aaaa km nde nthobwa leni leni mbala inu
@user-fl7br3dw4h
@user-fl7br3dw4h 2 ай бұрын
Akweni pumani bas tchito munagwila kale apa mwatenga malonda okanika ambamva
@user-xd6hq1pp4d
@user-xd6hq1pp4d 2 ай бұрын
Mumatitenga ngati ife zisilu mwauponda agalu
@greychizaka4088
@greychizaka4088 2 ай бұрын
power🎉
@user-th3yy1ku2n
@user-th3yy1ku2n 2 ай бұрын
Ndiyabodza akubawa
@mustafailanga2585
@mustafailanga2585 2 ай бұрын
Hule kulibe zonamizana unya galu iwe
@MAPAGASTUDIOS
@MAPAGASTUDIOS 2 ай бұрын
Mmayi opusa kwambiri iyiuze mbuzi yakeyo mapushup ake akapangire kwawo mwina
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
Anthu abodza awa, akutaya nthawi, bola APM basi, za ziiiii! Zikuwakani apa.
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Chilima has word to talk during Champaign because he was out of office for many years, But I will DPP to ask mpinganjira to represent the party, honestly I don't have problem with DPP but honestly I hate Peter muthalika. Uyo kwa ine ayi
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 2 ай бұрын
Iweyo hule chilimayo Ali kunjabkwa Boma nonsense MCP ..UTM nonsense out
@user-tj5bp4sk4m
@user-tj5bp4sk4m 2 ай бұрын
Zomvetsa chisoni
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Anthu woyipa inu, zonse zomwe mukukambazo ndi dzabodza
@user-nj3gn5xq2s
@user-nj3gn5xq2s 2 ай бұрын
Zamanyi
@user-ur8fq6ht5u
@user-ur8fq6ht5u 2 ай бұрын
Good people in a wrong place
@ThomNkhoma-no5rt
@ThomNkhoma-no5rt 2 ай бұрын
❤🔥🔥🔥🥤🔥
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 2 ай бұрын
Osasokoneza amalawi oyayi agaru.inu aboza
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 2 ай бұрын
Uchitsiru basi mwadyelera mwatibera apa mudzilankhula mopusa fokofo musatibowe
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Zopusa et
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Anthu akuba inu anthu atayananu chikhulupililo
@patrickmoffat9609
@patrickmoffat9609 2 ай бұрын
Malawi wake up Mayi uyu chisilu
@patrickmoffat9609
@patrickmoffat9609 2 ай бұрын
musamumvere
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 2 ай бұрын
Izi xopenga mbava izi chatap
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Koma mulibe manyazi
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 2 ай бұрын
Kodi mumasuta fodya wanji?
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 2 ай бұрын
No more UTM anthu a bodza inu
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 2 ай бұрын
Apa mizimukanila chakwera kut ndamene waononga pomwe inu munali mommo mukhaula this time
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 2 ай бұрын
Chilima boma 2025
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 ай бұрын
Kodi inu andale, simumatopa ndi bodza etie????2019-2020 mumanena zomwezo mwakanika kupanga ndie mukufuna mutipasenso 5yrs ina yozunzika???? Stupid
@EllenLuwanika-tl5ck
@EllenLuwanika-tl5ck 2 ай бұрын
Kkkkkkk Mwayi kwakwana mwava dziko Lathu mukuti tipitekuti
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Koma inu olo Ulesi mulibe aaaa mudziti chani koma?? Shame on you guys..
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 2 ай бұрын
No vote 4 u guys 4get it now
@bayanimponda8746
@bayanimponda8746 2 ай бұрын
Chilima my vote
@estonmnthali3719
@estonmnthali3719 2 ай бұрын
Nonsense
@zakeskamoga1291
@zakeskamoga1291 2 ай бұрын
🤮🤮🤮
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 2 ай бұрын
Kukhala ndi mabukhu ndikukhala ndi nzeru nzosiyana .komanso kumalawi kuno oziwa ndale sinu nokha.posilinza zophodazo ndi mdyelekezi wenwen
@mphatsojuliostandy4918
@mphatsojuliostandy4918 2 ай бұрын
Uwu ndiufiti, ngakhale manyazi osakhalanawo
@user-rd8vw1pc4b
@user-rd8vw1pc4b 2 ай бұрын
Zozolazolazo kukowa kukoweka 😂😂😂😂
@liki-likiladies---lilongwe6963
@liki-likiladies---lilongwe6963 2 ай бұрын
Make up is expensive and by choice
@ThomNkhoma-no5rt
@ThomNkhoma-no5rt 2 ай бұрын
yes 🤝
@ThomNkhoma-no5rt
@ThomNkhoma-no5rt 2 ай бұрын
live from. Lilongwe
@ThomNkhoma-no5rt
@ThomNkhoma-no5rt 2 ай бұрын
machine ❤
@Yabwata
@Yabwata 2 ай бұрын
​@@liki-likiladies---lilongwe6963 useless sis, ma make up doesn't make you beauty be naturally uyu gogo wakujinaga waka vazii asaa.. just coz you do it also that's y ur saying it ma nonsense tiyeni uko ndichipani chanu agogo uhule basi ..
🤔Какой Орган самый длинный ? #shorts
00:42
Cool Items! New Gadgets, Smart Appliances 🌟 By 123 GO! House
00:18
123 GO! HOUSE
Рет қаралды 17 МЛН
Задержи дыхание дольше всех!
00:42
Аришнев
Рет қаралды 2,4 МЛН
Patriotic Alliance holding its campaign rally in Cape Town
20:50
Chegutu : Ruvimbo wekuurairwa $100 onzi opfuka asati avigwa
1:03:06
Икболгула кунте бданша даказат кардем
13:04
FARUKHI NURZOD Official
Рет қаралды 22 М.
Tchad : portrait de Mahamat Idriss Déby Itno
3:28
TV5MONDE Info
Рет қаралды 531 М.
Lwasa afunye sente bupya,aguze benz ne rangerover
30:52
Kasuku Live
Рет қаралды 39 М.
ZOMWE ZACHITIKA KU ESCOM YAKU BLANTYRE🙌🙌🙌🔥
20:54