Mabvuto Kokhwima
10:36
Ай бұрын
MCP Kumangochi Yayaka Moto
10:08
2 ай бұрын
Nawo Achinyamata A MCP Akulira
14:00
Пікірлер
@DevisonHala
@DevisonHala 9 сағат бұрын
Kkkkkkkk
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 13 сағат бұрын
Atha kukhala hule
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 21 сағат бұрын
Osamakhalira kuikira kumbuyo aneneri abodza, taikani chidwi chanu kwa Mulungu, siyani kupembedza anthu pembedzani Mulungu masiku ano kulibe aneneri, amene mukuwaona ndikuwamvawa ndi anthu a satana munthu wa Mulungu sakhuzidwa ndi mirandu yakuba,ngati sanali olakwa anathawa chani iyaaaaaaa
@AllanChingwazala
@AllanChingwazala Күн бұрын
Ndimafunisisa utazakhara president malawi ikhoza kukhala yopambana ngat wakwanisa kumanga ndalama zayekha kulibwanji athakhala president buchiri ndimakufila kuzakhala president ndizabwerera kumalawi
@alomuddin8801
@alomuddin8801 Күн бұрын
Bola ife PA jozi pano timalandila ndalama zimalowa m matumba mwathu kmso TiKAFUNA kubwelera timapita no vuto
@StellahChikupira
@StellahChikupira Күн бұрын
Kulakwa 😢
@jacquelinemagwera155
@jacquelinemagwera155 3 күн бұрын
Eti osawaonetsa?
@ZefaniyaWelios-e5y
@ZefaniyaWelios-e5y 4 күн бұрын
poop?
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
Chinali chiwanda
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
Eh
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
Iweyo easy come ndonwe imakupwwteka kusavera lamulo la Mlungu loti udzadya thukuta lako umafuna kudya mofewa motsatulutsa thukuta (ulesi)apo waiwala Mlungu size yako
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
Ku mpoto nde kuli ufiti wa serious akapha akapha anthu aphabasi tsamauka ku manda pamene kumwela amauka kumpoto kuli ufiti oyipa!anthu ambiri kumwera akumauka ku mpoto zero🙄
@AndyGama-m3u
@AndyGama-m3u 5 күн бұрын
Ayi wachitola chikwama Nanga ma million onsewo pajatu ndalama zilimunyasi
@IshmaelSaidi-f8l
@IshmaelSaidi-f8l 6 күн бұрын
Chiwanda chimenecho
@AngelaMhango-c2i
@AngelaMhango-c2i 6 күн бұрын
Izooo
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 6 күн бұрын
Chakwera ndiwe wakuba pa thako pako, niwezgere ndalama Zane nkhuyiwona ya passport yane
@Aisha-db6ds
@Aisha-db6ds 6 күн бұрын
Atsogoleli ake opanda mfundo
@YONA-v5o
@YONA-v5o 7 күн бұрын
Nde inuyo aku banja munthu woti mmakhalanaye simnamu fananitse ndamene anamwalilayo
@YONA-v5o
@YONA-v5o 7 күн бұрын
Nde inuyo aku banja munthu woti mmakhalanaye simnamu fananitse ndamene anamwalilayo
@tiwongehojaney5873
@tiwongehojaney5873 7 күн бұрын
Tangomugululabi mpezi ameneyo
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 8 күн бұрын
koma dzikoli ndi lanthu olemeradi et? mpaka munthu kuba chinthu cha office ya boma mpaka kurephera kumulanda???? mukutiseweretsatu makosana😂😂😂😂😂
@MatumeMkhondo
@MatumeMkhondo 10 күн бұрын
Mzimu wawo ukawuse mutendele
@HassanCharle
@HassanCharle 10 күн бұрын
Mbambande amalawi mumakwana
@HassanCharle
@HassanCharle 10 күн бұрын
Km sili bwino Pamenepo galu ameneyo achijapulapo chifukwa chakwera ndi mbuzi galu yachabechabe
@LovenessLester
@LovenessLester 10 күн бұрын
That's a great city for many Malawians let's learn how to appreciate this our man of God 🙏
@CatherineDesire
@CatherineDesire 11 күн бұрын
Lazy people lovers of miracle money will always have negative minds against trueth👹👺👿
@CatherineDesire
@CatherineDesire 11 күн бұрын
,,,😂😂mzimaiyo akunama amafunanso nae amagwilidzana naeso akufuna chipepetso eti 😂😂😂😂🤸🤸🤸🤸🤸
@ChikondiKwengwere
@ChikondiKwengwere 4 күн бұрын
Sinzimayitu
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 11 күн бұрын
Inuso asilikari musati bowe manyi anu mulibe chisoni ndi Amalawi
@KimamboPk
@KimamboPk 11 күн бұрын
Zam'Zam'masiku omaliza no wonder
@JosèFelixsailessFelixsailess
@JosèFelixsailessFelixsailess 11 күн бұрын
Zoipatu zimenesi
@JosèFelixsailessFelixsailess
@JosèFelixsailessFelixsailess 11 күн бұрын
Zoipatu zimenesi
@BarnabeMacuane
@BarnabeMacuane 12 күн бұрын
Ndikupemba mamba ya profit ine Kuno ku mozambiaue
@ChadichadinjanjeNjanje
@ChadichadinjanjeNjanje 12 күн бұрын
Zohona anaphedwa ndi nzake amene Ana mukongola mavoti yake
@DorrahBanda
@DorrahBanda 12 күн бұрын
Osauka tilipamavuto mabwana ndimfulu olo atalakwa chotani samamangidwa km mulungu nfiye mwini zonse
@FatimaRehemah-gi4mp
@FatimaRehemah-gi4mp 13 күн бұрын
ma gay achimwenye🤨🤨🤨
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 13 күн бұрын
Kupusa bwanji samakadandaula ku ma bungwe ndi opepera
@GeraldJairos
@GeraldJairos 14 күн бұрын
Zochitika m'masiku otsiriza machenjera amdyerekezi Osakhulupira kwa tonse owerenga tiyeni tikhale mmaso,wakufa sadziwa kanthu bii
@GeraldJairos
@GeraldJairos 14 күн бұрын
Kodi inu bambo osapeza mkazi wina,ndikupemphera ,ngati mutachita bwino nkudzakumana ku ulemerero wa mulungu
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 14 күн бұрын
Ndipo chitukuko chikuwakanika akurimbana nikupha anthu
@user-rc8ze8do7e
@user-rc8ze8do7e 14 күн бұрын
Kkkkkkkkkkk sister laz ndwe kangenge
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x 14 күн бұрын
Kkkkkķkk km ku malawi kokoma😂😂
@HamzahBandah
@HamzahBandah 14 күн бұрын
Mundipaseko nambala ya aprophert akulilongwe ndikuwafuna aprophert andithandoze
@IdrissahSadick
@IdrissahSadick 15 күн бұрын
That's just jiin
@user-kk5br9vm9u
@user-kk5br9vm9u 15 күн бұрын
Nyimboyi ikunena zoona ndipo munthuyo sakunama koma nkhani ndiyakuti billy ponena bakili anaikapo nkhope yake naeso ngati amafuna kunena achakwela akanaikaso nkhope yake
@OjesYahaya-zl4rx
@OjesYahaya-zl4rx 15 күн бұрын
Athu akumwalila zimpatalamu kamba kosowa Panado ndiye Muthu mozi ndalama zosezo kusonyeza kuti miyo yanuyo ndiye yofunikila mumwalilabe mutisiya aphawife mulungu sowona chuma
@fredlemani
@fredlemani 15 күн бұрын
Anali yemweyo kapena ayi? Nkhope imasiyana bwanji? Mprothet ameneyo anamutumiza Mulungu kapena ndani? You and your prothets are fools and you don't know God.
@EthelLimited-bo5ey
@EthelLimited-bo5ey 15 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@HellenGondwe-d1g
@HellenGondwe-d1g 15 күн бұрын
Mpaka Chaka kumalorera zimenezo mavuto ake amtundu wanji
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 15 күн бұрын
.musiyen waimbayu Ali ndi luso.nyadilan bro billy
@user-qb2lt6qj1p
@user-qb2lt6qj1p 16 күн бұрын
Palibe chomwe chikuveka
@user-ot6jv1gj9w
@user-ot6jv1gj9w 16 күн бұрын
Nkhani sikunvekatu ife timaona ngat muli ndi umboni kuti anayenda bwanji.