No video

Amalawi ndi mbuli, asiye kudzudzula Chakwera;

  Рет қаралды 66,953

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Күн бұрын

Пікірлер: 479
@yusuflifa2923
@yusuflifa2923 3 ай бұрын
Palibe TV ingapose Bakili muluzi TV ku Malawi kuno. Bravo for giving us real history.
@BenissoneErnesto-eh6zs
@BenissoneErnesto-eh6zs 3 ай бұрын
Kumalawi tikapuma kumwamba basi Chaka chino chobisika chilichonse tikaona ndiponso tikanva watching from Mozambique 🇲🇿 never give up bg brother timakunyadirani kwambir potiwululira zisisi zambavazi
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 3 ай бұрын
Muthu salephela kukhala ndi zofooka koma peter athu tikumulila anali muthu osese mulungu amupatse moyo wautali peter muthalika
@ThomasShuga
@ThomasShuga 3 ай бұрын
Amen 🙏🙏
@user-sh5wq4uf6r
@user-sh5wq4uf6r 2 ай бұрын
Amen
@user-ne7rn4ki3c
@user-ne7rn4ki3c 3 ай бұрын
My favourite T V Bakili Muluzi yooo! My brother keep on updating we love you from the heart may Allah protect you from the evil like chawezi and the tonse government including Chakwela the big evil
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 ай бұрын
Chakwera is big mbavament of Malawi mbuzi yeniyeni ndithu ntheradi
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 3 ай бұрын
CHAWEZI PANYA PAKO.....ULIBE NZERU...I HAD respect for you..koma with what u said..aaaaaa iweyo ngati ukunjoya ndi boma la chakwera ndiweyo ndi apa banja pako
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 3 ай бұрын
Good job bakili muluz tv
@user-Grant260
@user-Grant260 3 ай бұрын
Watching from Venezuela in Caracas paboma 🇻🇪
@user-gf9di3fc2g
@user-gf9di3fc2g 3 ай бұрын
Chawezi tisamusekerele mbole yamako ase 🚶🚶🚶
@websterkausiwa8919
@websterkausiwa8919 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@tyolosbakili8272
@tyolosbakili8272 3 ай бұрын
kkkk
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 3 ай бұрын
Mmmm Chawez ndye ndaniso mbudzi yamtola nkhani ngat imeneyo
@innocentkapachika6591
@innocentkapachika6591 3 ай бұрын
Musalimbane naye ndi kape uyu.
@nadiahPhiri
@nadiahPhiri 27 күн бұрын
Mungomva dzina chawez kkkk chauleledi galu kwabs
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 3 ай бұрын
What shall we give back to you Sir, for the commendable job well done? We just say long live and stay blessed 🙏
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 3 ай бұрын
HE IS AN INCOMPETENT journalist....chonsecho ali mbuuuuu ngati bakayawo
@blandinabonaventure
@blandinabonaventure 2 ай бұрын
Ndiye
@mayamikochikafa2239
@mayamikochikafa2239 12 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@augustMag
@augustMag 3 ай бұрын
You are the one true speech go ahead bro Chawezi akavotera MCP iye ndi banja lake koma kuda ali biiiiii ngati amakasamba nyanja ya mchere Chawezi limbikira kutothoza Amalawi ife akupasa nthumba la ndalama kuti mwina usambeko ungafe udakali mphawi
@JusticeGonani
@JusticeGonani 3 ай бұрын
Mumakwana big keep it up
@allamalbertbeza2679
@allamalbertbeza2679 2 ай бұрын
From north of Malawi, Chawez must wake up in his dream we are not stupid as he thinks ,he can be bribed but we know what is happening on ground we buy things at high price
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 3 ай бұрын
Kulilila malawi ambuye mulungu mtioneniko iyeana anu kuchiliseni kumalawi ambuye tichozeleni zatana mudziko mwntu chonde chonde ambuye 🙏🙏😭😭😭
@ThomasShuga
@ThomasShuga 3 ай бұрын
Inu ndakatundu omanga ndimawaya keep it up br ❤❤❤
@cephasnkhoma2301
@cephasnkhoma2301 18 күн бұрын
Gati akutsusa abwele ndi umboni (na'o). Ife bakili TV the best.
@DeviLinya
@DeviLinya 14 күн бұрын
❤❤❤ iwe ndiwann !!!!!!
@isaaczuze
@isaaczuze 3 ай бұрын
Koma munthu uyu amandiyankhulila bwino koopsa ndipo amanena zoona zokhazokha .....bwana pitilizani kuwaiza agaluwa zoona .... Anthu opanda chisoni ndipo aononga ziko ili
@MussaMalon
@MussaMalon 3 ай бұрын
Watching live from Cape town South Africa.
@user-fd7fg1bx4y
@user-fd7fg1bx4y 3 ай бұрын
you are a star brother keep it up
@JimmyGeorge-ot7zh
@JimmyGeorge-ot7zh 3 ай бұрын
Mbudzi yamuthu ameneyo yaaa big up Bakili Tv
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 3 ай бұрын
Komatu mbuli akuzinenazo ndizomweso zidavotela MCP yoh . Tiwonana mu 2025 , Viva Bakili Muluzi TV
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 3 ай бұрын
Good job Mr and l salute you
@JohnPetro-vv3er
@JohnPetro-vv3er 3 ай бұрын
Well done Bakili tv , ndikakhala ine ndiye ndamuuza kale kuti mbuli ndi chawezi banda
@jonathanmunthali8500
@jonathanmunthali8500 3 ай бұрын
We’ll done brother watiyankhulira wamva chawezi mburi yomphuzira kkkk
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 3 ай бұрын
Bakili muluzi tv You're truly a freedom fighter
@dontreybanda278
@dontreybanda278 3 ай бұрын
Mumakwana big boss
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba 26 күн бұрын
Osaopa bakili muluzi tv 📺 our best TV in country timakudalilani madala . Musaope munthu .
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 3 ай бұрын
Thanks boss for this have told chawezi that chakwera has failed because mulusu recovering plan, gwengwe recovery plan, cuthiola recovering plan and chakwera recovering plan but to no avail
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 3 ай бұрын
Good message Bakili Tv ❤
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 3 ай бұрын
Ndinewakumpoto but i like this guy
@CharityGondwe-bw9gs
@CharityGondwe-bw9gs 3 ай бұрын
Mumakwana boss
@yusufjonas5088
@yusufjonas5088 3 ай бұрын
❤I love your contents
@FosterChilumba
@FosterChilumba 3 ай бұрын
Watching from Cape town big up
@papelariareis.e.
@papelariareis.e. 3 ай бұрын
That's amazing 😂🎉🎉🎉 I love the bakili tv
@makomberodgers3791
@makomberodgers3791 3 ай бұрын
Your number one bg
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 3 ай бұрын
M'makwanira abwana m'manja mwanu👋👋👋👋
@user-sr6hc3pv8o
@user-sr6hc3pv8o 3 ай бұрын
Eeeh koma iwe aseeh uzangosowa komaso usazasowe chifukwa tizakusowa😂😂😂
@maulidisaidibugudadi4091
@maulidisaidibugudadi4091 3 ай бұрын
Watching from Bagamoyo pa Boma Live
@Justin_Nano
@Justin_Nano 3 ай бұрын
Kkkkk 😂😂😂ndaseka bro umakwana.🙏🙏🙏
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@abisalomchunga6695
@abisalomchunga6695 3 ай бұрын
Good work boss
@tisamulangala5570
@tisamulangala5570 3 ай бұрын
Watching from Scotland
@mikekhamusi1807
@mikekhamusi1807 3 ай бұрын
Sindinaonepo president ngat amenei, ndipo kuchokela 1994 mene ndinabadwa, ngat pali zaka zomwe ndinava kuwawa ndi za apre amenewa
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 3 ай бұрын
Muxiganiza chawezi is best journal in Malawi speaking honest
@websterkausiwa8919
@websterkausiwa8919 3 ай бұрын
Yea ndiwabwinodi komano sanayankhule bwino tivomelezee...kuyankhulaa mopusa kmene kujaa
@shideshidex5679
@shideshidex5679 3 ай бұрын
Who Is This You Call Chawezi Banda Ndiwakutiko Amatani Iyeyu Kufikana Poyankhula Motokosa M'kwiyo Waamalawi Thanks Broo Potidziwitsa Izizi 🙏 Keep It Up May God Bless Amd Guide You My Brother
@edonellzrmw
@edonellzrmw Ай бұрын
❤❤❤long live bwana DPP yomweyo 2025 🎉🎉🎉🎉 zinazi ziwone kolowera timadana nzopepera😂ife simburi Chawezi asatinyase ndopusa
@MichealKumikanthu
@MichealKumikanthu 3 ай бұрын
True story chawezi banda ndi mbuli yeniyeni
@Pangolinimw
@Pangolinimw 3 ай бұрын
Best TV 📺
@user-le8jh3st8b
@user-le8jh3st8b 3 ай бұрын
Muma kwana brother best tv in Malawi l four you
@ashikalam8616
@ashikalam8616 3 ай бұрын
Imeneyi mbuli etiii chawezi Banda nyawu yachabechabe
@user-mo4tv5eu5y
@user-mo4tv5eu5y 3 ай бұрын
Ameneyu yu anyapulidwe
@user-zg7iw8kq4r
@user-zg7iw8kq4r 3 ай бұрын
Zoonadi pofunika kumuyendela
@kotking-jn5us
@kotking-jn5us 3 ай бұрын
keep it up boss
@user-hg8zy8pt5b
@user-hg8zy8pt5b 3 ай бұрын
Ulemu Wanu big ❤❤❤
@james-zd2nz
@james-zd2nz 3 ай бұрын
Watching from JHB CBD
@LukaAron-el5qh
@LukaAron-el5qh 3 ай бұрын
Osayakhula za ma passport, fertilizer, sugar waduyi nkhumba ya mwana wamunthu iwe wayamba kumwa mowa wamabotolo wasiya wasese wamundilande nde wati uyambe kutukwana amalawi kuti ndi umbuli garu wamunthu,nkhumba yachabechabe kukamwa ngati matako anyani ukuyenela kuwapepesa amalawi garu iwe
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 3 ай бұрын
He is right, serious kukavotera galu Peter
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 ай бұрын
CHAWIZI BANDA AZIYENDA MOSAMALA AMENE MUNGAKWANISE KUMUPASA UTHENGAU MUMUUZE CHONDE ASATI NDI TSOKA ZIKAMUGWERA PANOPO MALAWI WAKWIYA NDIPO ATHYOKEDWA , WINANSO NDI MWANA YEMWE WATUMIDWA NDI MCP KUTI AZI HAKA MA NETWORK AWANTHU , AFERA ZA ENI ENOUGH IS ENOUGH 🎉🎉
@MikeEdwardChitopa
@MikeEdwardChitopa 3 ай бұрын
Muudzeni akasambe chaweziyo am with u my brother ❤
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 3 ай бұрын
Wadya money chawez azisanza
@AndrewNkhoma-ek8xk
@AndrewNkhoma-ek8xk 3 ай бұрын
We love u brother, bakili muluzi tv reporter
@user-pt1fy3qg4u
@user-pt1fy3qg4u 3 ай бұрын
Never give up bro❤
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i 3 ай бұрын
Mtola nkhani wa dyera uyu, he will never find a descent job😂😂😂😂😂
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 3 ай бұрын
CHAWEZI....U HAVE TO KNOW THIS...WE ARE STRUGGLING UNDER THIS PRESIDENT.DURING PETER MUTHARIKA DZIKO LINALI BWINO ILI
@CatalinaLupiya
@CatalinaLupiya 2 ай бұрын
Your number one Bakili tv
@IsmailJimmy-mr3kp
@IsmailJimmy-mr3kp 3 ай бұрын
Best tv
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 3 ай бұрын
The whole world because of COVID things went wrong, don't blame Chakwera zinthu anawononga ndi galu wakoyo Peter muthalika
@user-dh8ho2qt4h
@user-dh8ho2qt4h 2 ай бұрын
❤❤❤❤ zoona chakwerq is doing favor. He doesn't like North side. Anyway it happens. But for sure, chakwerq is a greedy Man 🎉
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 3 ай бұрын
Chawezi ndi mwana opanda khalidwe, ndipo ndikachitsilu, kamachita kumwa chamba , osati kusuta ai. Ndicho chifukwa si kakhalitsa pa ntchito, kachitsilu aka.
@DicksonJere-dc6qm
@DicksonJere-dc6qm 2 ай бұрын
Mbuli ndi iyeyo Chaweziyo, iyeyo akuona ngati kukhala announcer wa TV ndiye kuti Ali ndi nzeru.
@user-sv7od9ms7p
@user-sv7od9ms7p 2 ай бұрын
mzimba Mtwalo Lord Dpp
@user-ub1vt2kq4s
@user-ub1vt2kq4s 3 ай бұрын
Timakunyadirani brother, number one channel
@jamesgama5489
@jamesgama5489 3 ай бұрын
Mumatiyimirila man keep it up
@ThomasChiwaya-qx9mf
@ThomasChiwaya-qx9mf 3 ай бұрын
Acha wezi atiyakhe bas
@GSMWINDOWS
@GSMWINDOWS 3 ай бұрын
Mmakwana broo
@user-jq1ug8lq9h
@user-jq1ug8lq9h 3 ай бұрын
Freedom fighter
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 3 ай бұрын
Ndipo ndamuva mwanayu sindikuziwa chomwe anadyaa koma mbuli ndi amache omwe anamuswaa osati ifeyo
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@user-uw8gu4tc1y
@user-uw8gu4tc1y 3 ай бұрын
Big up bro
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 3 ай бұрын
Good voice and speech
@WedieKaseka
@WedieKaseka 3 ай бұрын
Bakili Muluzi tv you are genius
@Cosmassaiwa
@Cosmassaiwa 3 ай бұрын
Chawezi bwera pano umve zoona Chawezi mbuzi ndipo mkamva zomwe umayankhula dzulo lija umafunika imfa
@neusajoaolevenileveni2672
@neusajoaolevenileveni2672 3 ай бұрын
A Malawi nanunso ndi anthu osayamika olo pang'ono..chomwe ndikudziwa ine ndichakuti ingakhale atabwela winanso kudzalamulila adzakhala oipa mudzatiso bola Chakwela..inu anthu ovetsa chisoni
@mosesnyangato4900
@mosesnyangato4900 3 ай бұрын
Ndirindi chikhulupiro kuti achitsiru omwe akumayamikira za mbuye wao Chakwera wo salimdzoko muno ayi, ngati ali mdziko mommuno ndiye kuti ndiakhungu sakuona
@Blessings31
@Blessings31 3 ай бұрын
Ka page Ka uchitsiru aka..palibe chomwe mungapindule..wakupwetekani Chawezi
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm 3 ай бұрын
Chawezi banda M'Maso mwako chitsiru Mbuli ndi iweyo
@user-nn9mx5tt6d
@user-nn9mx5tt6d 3 ай бұрын
Bro your the king of the king I love you long live
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 3 ай бұрын
Above all, respect is important
@DannielOnions-fy3dc
@DannielOnions-fy3dc 3 ай бұрын
Keep GOING brother
@EvanceMponda
@EvanceMponda 3 ай бұрын
Kumuyang'ana chawezi bandayo Ali mbuuu uchitsiru shupiti
@ibrahimmeemzy9754
@ibrahimmeemzy9754 3 ай бұрын
Mumakwana❤❤❤🎉🎉
@mcdonaldgerard9707
@mcdonaldgerard9707 3 ай бұрын
Chawezi ngati alimtola nkhani, palibepo chimene akudziwa pantchito yautola nkhani. Chimene akudziwa iyeyo ndimowa wake omwewo, koma osati kutsata chilungamo chamunthu. Kachiwili iyeyo kwao amalima fodya sangathe kuona momwe mabvuto akukhalira mum'dziko lamalawi, mbuzi yamunthu imeneyo.
@user-fd4dw6bs4q
@user-fd4dw6bs4q 3 ай бұрын
Chawezi Banda palibe chomwe akuziwa ndi mbuli number 1 chifukwa chake Dziko la Malawi liri lo sauka chifukwa cha anthu a mamina mutu ngati chawezi Banda chitsiru cheni cheni.
@noordeenmsamu6652
@noordeenmsamu6652 3 ай бұрын
Bigy up bro💪
@Rizikfarms
@Rizikfarms 3 ай бұрын
Big mumatha❤
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 2 ай бұрын
Chawezi mburi ndiwe mapazi ako tamangomwa kachasowako uyo
@mkhokholasamuzonda5094
@mkhokholasamuzonda5094 3 ай бұрын
chawezi pa nyini pa mako nzeru ulibe, wadya banzi ndipo mfundo zako zopanda phindu
@user-vj6jt2df3e
@user-vj6jt2df3e 3 ай бұрын
Chawezi banda iva izi mbulili yoyamba ndimayi ako ndi bambo ako chifukwa nawoso ndimalawi ukamayakhula uziyamba waganiza usanayakhule
@user-oq7ub3yg8x
@user-oq7ub3yg8x 3 ай бұрын
😂😂😂😂 ndiyemwati analedzela kkkkk
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w 3 ай бұрын
Zikachitika ndinutu mumatiziwisa ulemu wanu bakili tv
Bony Just Wants To Take A Shower #animation
00:10
GREEN MAX
Рет қаралды 7 МЛН
Zombie Boy Saved My Life 💚
00:29
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 29 МЛН
Meet the one boy from the Ronaldo edit in India
00:30
Younes Zarou
Рет қаралды 19 МЛН
Malema addresses Gauteng EFF members
1:25:51
SABC News
Рет қаралды 270 М.