Ulemu wanu bambo aife mwatilela zambiri talandila zaulele moti nyengo ya makolo athu samakwanisa kugura respect for you our father and thanks Brian potionesa atcheya
@user-do2cs8nf4b2 ай бұрын
Atcheya tsopanoooo!!! timakunyadirani president wamsangala odziwa kuseka, osakhala zinazi aaaah
@user-he7bu2tp8z2 ай бұрын
Well spoken Dr Bakili Muluzi atsogoleri azitero tikufunilani moyo wautali pamodzi ndi family yanu Mulungu azikudalisani nthawi zonse
@rashiddeula57152 ай бұрын
This man! Ayayayay.....the humour is just great. Brian on a lighter note question eish.....ayayayay ndaseka mpaka misonzi. Mpaka odziponyaponya eti? 😂😂😂😂😂
@AdamSteven-ne9hg2 ай бұрын
Nantahala ife muthawi yanu long life atcheya
@JoshusMbewe2 ай бұрын
Long live Dr. Bakili Muluzi Abwanawa ndi munthu wabwino
@DonaldBanda-qi7ywАй бұрын
That's true His Excellence Dr Bakili Muluzi could stop just to give someone a lift in his Ministerial Car. For example is my Father (Late Stephen Eliya Banda) and myself, His Excellence the Former President gave us a lift in his Official Car while he was the Administrative General of the Mighty Malawi Congress Party.
@user-qe2lz7mx7u2 ай бұрын
Bakili knows how to choose but bingu was the best ayao simuziwa economy
@ImraanYaseen252 ай бұрын
This man his is another level just hear his voice 😊
@EddieBakali2 ай бұрын
Quran on shelf mashala habibi
@jaydee12362 ай бұрын
The great man 🎉❤
@WellieManonga2 ай бұрын
Achalume kuchitekete God be with you
@magdalinemafunase24402 ай бұрын
We will always Love you a chair.❤❤ Long live.
@FrankFrancis-ch3xv2 ай бұрын
Watching live from SA Durban KZN
@tiongegondwe72192 ай бұрын
Great man
@SwidiqLameck2 ай бұрын
I like his voice
@user-mz8nw6nx6p2 ай бұрын
Kuti enafe tisakhuzidwe ndi nkhaza za chipani chimodzi for that time Achair,,,munatinvetsa kukoma mu nthawi yanu❤❤❤❤❤
@mtangaJumbe2 ай бұрын
Munthu amene anapangitsa Malawi kukhala owawa kwambiri panopa. Chomwe ankagulitsira ma company kwa amwenye sichikudziwika
@atanasioestevao97072 ай бұрын
Long live atcheya❤
@ibradaglass86462 ай бұрын
Pa town kumachenjela ❤❤❤achalume
@user-cw6jg6xg7h2 ай бұрын
Long live achair!we love u!
@user-yk7gj1sl2z2 ай бұрын
Allah akudalitseni a chair
@richardmadaka2872 ай бұрын
Anamva mtunda ukufotokoza, anamva zonsezo ( I remember Mkasa's song. A Chair ndi mtunda)
@ChristopherKalonga-jt8iz2 ай бұрын
Nice
@victorzakeyuzimba77422 ай бұрын
Long live Muluzi
@stewart.mwamughunda2 ай бұрын
Malawi ndi dziko lokhalo lomwe mapresident opuma akumva kukoma. Ulemu wanu a Chakwera. Taonani a Muluzi,mayi JB, Khumbo, APM, Chilupha n ena.
@jeffchikwapata69332 ай бұрын
Big man ever
@salimmkumakumakitombi-yc7pw2 ай бұрын
Kholo pa ndale
@CumbuNgoma2 ай бұрын
A Gama we love you,long live
@shakajudahTV2 ай бұрын
Much respect to our granny mumakwana 🎉🎉🎉🎉
@MonicaMbwera2 ай бұрын
Big man tsopano ❤❤❤
@RobertLuka-wy9cl2 ай бұрын
Achair Allah bless you ❤❤❤❤❤
@user-ub1vt2kq4s2 ай бұрын
Ulemu wanu acheya timakunyadirani kwambiri potibweretsela ufulu Allah bless you more
@user-hx8rr1mq7u2 ай бұрын
Watch live from Nyambadwe
@darlingtonchimutu83902 ай бұрын
The most likeable PULE of Malawi kuseka continuous
@user-ud6mz3pf7x2 ай бұрын
Big man
@WisikiBlack-gj4gu2 ай бұрын
Simungathe kusangalatsa aliyese koma ndinu big man muthu wa bwino kwambili
@cristovaoherculano86622 ай бұрын
Government doesn't run a business. It should create atmosphere for people to do business. Ndani wamva zimenezi bwinobwino?
@dannymangawa75112 ай бұрын
Ine ndinamva, tcheya si munthu wamba baba anakonza
@geoffreyNkhomah2 ай бұрын
umenewu ndi ntondo endeed
@user-nj5vu8cd5l2 ай бұрын
Bakili vuto linapo ndi umbuli komanso business yake o i hope anali kupikulitsa bonya. Nfi masamba
@user-ud6mz3pf7x2 ай бұрын
Achakulungwa wachiyao
@aureliojose7632 ай бұрын
kuntunda 🔥
@osmanwanja37332 ай бұрын
Atcheya woeeee!
@imranshaibu15772 ай бұрын
Ku machinga Kwa chikweo ndiye kwathu 😂😂😂
@Oraterbadri2 ай бұрын
putin waku malawi bakili
@JustinPhiri-kq2bb2 ай бұрын
Sizaiwa former President pa free education primary sizophweka
Sitinaone nawo utsogoleri wanu komabe timanyadira chifukwa Cha zithu zochepa zomwe tinapeza kamba ka utsogoreri wanu taona ma k50 opanda mitu ife ndalama mumkatigaira ndi manja Anu akulu inu osati zinazi
@chawezichipeta53262 ай бұрын
Kumtunda
@BashielSalade2 ай бұрын
M,tunda wa m,ndale
@rtqwtetohedron2 ай бұрын
A Chair palibenso
@user-ud6mz3pf7x2 ай бұрын
Byson mwaona
@ElijahHarah2 ай бұрын
10:20
@chinielstailoring-ro9lu2 ай бұрын
professor
@harrispheleni22052 ай бұрын
Kungogulitsa ma company a boma basi ndalama kupochera achalume anali ochenjera
@user-nd8zg6ni7l2 ай бұрын
Tionele zimenezi
@YasinMusa-ym8lp2 ай бұрын
Kungocho kela kuchalichi kuvuna udndo ngamti chakwera
@user-fh5yn8xk2k2 ай бұрын
Awa anali adindo
@DanMhone-iw6xg2 ай бұрын
Tate wokondeka
@ElijahHarah2 ай бұрын
Bigy...
@user-xg2ks9nw5q2 ай бұрын
Uyu ndi amene anayamba kugwirisana ndi amwennye nkhani yobera amalawi
@abdulrasheedsuleiman68912 ай бұрын
Achisilu inu
@user-xg2ks9nw5q2 ай бұрын
Mbava iyi ndi yomwe inaononga zuko lamalawi
@abdulrasheedsuleiman68912 ай бұрын
Achisilu inu you know not
@waxyamidu56382 ай бұрын
Umbuli Owononga sukumuona
@user-xe3xo5mu9k2 ай бұрын
Achalume🥸
@OscarChizula-qr4bi2 ай бұрын
munali munthu
@imranshaibu15772 ай бұрын
Munthu wamkulu ❤❤
@AllieKaisi-je6rm2 ай бұрын
Munthu wamkulu
@patrickyakobe96852 ай бұрын
By mentioning Late Chikufwa Chihana he was being honest, that name contributed a lot to Malawi democracy!