Boma lapanga hayala asilikali a Rwanda ndi Zimbabwe kuti adzagwire Bakili Muluzi TV

  Рет қаралды 34,815

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Ай бұрын

Пікірлер: 484
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Ай бұрын
Bakili muluzi TV KZfaq channel Never arrested I'm telling you this is home land we are democracy now🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Dat's true bro, we're in a democratic society and noone lemme repeat noone can come and intimidate us in our own country!, Bakili Muluzi tv is a genuine freedom fighter and He's a Hero and watever is saying or talking is the truth!, mukuleka kusakana ndikumangana nokhanokha am'boma inu amene mukutionongela misonkho yathu, pano mwagundika kupanga hire kapena kuti hayala mbava ndizigawenga zimzanu zaku Zimbabwe ndi Ruanda kuti zithane ndi anthu olankhula chilungamo, for wat!, shame on you zikhale ng'oma and mozesi kumukuyu, shame on you!, . Bakili muluzi tv will Never ever be arrested and if u'll try to do dat, we'll fight each other!,
@LetsSeePlaces43
@LetsSeePlaces43 Ай бұрын
Kodi kukukumbutsani bodza lomwe munkatisambitsa nalo 2020 lija kukhaleso mulandu?? Mukuba ndipo aliyense akuona komaso Akudziwa kukuwululani ukhale mulandu??? Viva Bakili muluzi Tv ❤❤❤❤
@LuundoJohnkabage
@LuundoJohnkabage Ай бұрын
Ndipo inu ati tidzisangalala ngt zukomela tose kma Mulungu alipo ndipo ndimwini chitetezo ameen
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w Ай бұрын
We love bakili muluzi tv than chakwera
@MsondaBanda
@MsondaBanda Ай бұрын
Amaphoyisa bophani yonke uyathuka Mulungameli , bayadelela laba banthu
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Keep it up bakili muluzi TV ziyaluke mbamva zimenezi
@serakillo8668
@serakillo8668 Ай бұрын
Nkukuyu phwala lako ndithu osakungwira iwe unapha alani witika bwanji bolo yako kuphatikiza zinkhale ng'oma ndi chakwera nose bolo zosadulindwazo zozaza madeya muuzane ❤❤ bakili muludzi channel tsimupata munyera manyi onukha
@emiliaumali8360
@emiliaumali8360 Ай бұрын
Akumangatu iwe 😂😂😂😂😂
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i Ай бұрын
Palibe, we love bakili muluzi tv....osati tv ya muluzi..😂😂😂😂😂
@CharlesTambala-zn2bd
@CharlesTambala-zn2bd Ай бұрын
Kodi..uwu wa mutu ngati nkhonkhwe mmati ndani... ? Kunkuyu ..akunama kwambiri.... My brother, you are opening the minds of vulnerable Malawians. Keep it up...afa ndi mtima
@Allan-bk1
@Allan-bk1 Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
😂😂😂😂😂, wamutu ngati chikwele cha nkhunda kkkkkkk
@mussasamuel774
@mussasamuel774 Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@braveglorymwanzagolah4899
@braveglorymwanzagolah4899 Ай бұрын
Mutu ngati dukwa leave muluz alone😢
@user-et5nz4vz2v
@user-et5nz4vz2v Ай бұрын
We love Bakili muludzi tv best TV ever
@AhmedPhillip
@AhmedPhillip Ай бұрын
Machende achakwela ndi agalu azake osavinidwa am here Durban lamontville ngati akufuna andipeze viva bakili muluzi 📺 we are behind you
@rashidlamos3403
@rashidlamos3403 Ай бұрын
God protect bakili muluzi channels tv
@LemanJackson
@LemanJackson Ай бұрын
Mitu siukugwila kulimbana ndianthu Malo moto akonze ziko
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
Akutaya nthawi Yao zangamupeze ameneyo Chakwera must go
@user-ug6bq4ou9x
@user-ug6bq4ou9x Ай бұрын
Long Live bakili muluzi tv 🎉🎉
@jameschibisa1433
@jameschibisa1433 Ай бұрын
Mphwanga iweyo ndi akatundu police ya ku malawi yakukanika 😂😂😂😂😂 kenako akunena zosemphana brother keep it the fire burning one year left
@HarryNtanga
@HarryNtanga Ай бұрын
Bakili muluzi tv osafooka ndip osaopa Pali chilungamo sipakhala mantha kip it up love you more
@MathewsMynus-ow6no
@MathewsMynus-ow6no Ай бұрын
Aaaa koma ana inu mwasowa zochita et wa bakili muluzi tv Mulungu amutezera
@OZIELBLESSINGS
@OZIELBLESSINGS Ай бұрын
Ndakayika ngat angazikwanise akuziyambazi, people loves you boss and I'm one of them ❤
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Akuyiyambayi ndi ndewu ya nkhondo
@user-zl9vj6hc6y
@user-zl9vj6hc6y Ай бұрын
Malawi police kukanika kugwila munthu wamba ndiye angagwile zikale ng'oima homeland security wakubayo 🤣🤣🤣
@AmandaConstance-fx8cr
@AmandaConstance-fx8cr Ай бұрын
The angles of God will be always around you protecting you where ever you are sir Mr bakili TV 🙏❤❤❤❤
@ishaqyassin5001
@ishaqyassin5001 Ай бұрын
Koma Mwapanga ko note kuti WA Bakili Muluzi TV kuti ziiiiii?
@PatiencejonasiAustin
@PatiencejonasiAustin Ай бұрын
Agalu anenewa asagwila mbava zikuba ndalama boma
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Komadi inuu eish
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Viva bakili muluzi tv 📺 ♥️ viva, bakili muluzi tv woyeeee ku nkuli kwereko kuchitekete.
@mathewsphiri5779
@mathewsphiri5779 Ай бұрын
No worries we are together atigwira tonse
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka Ай бұрын
Kuliufulu Mani tsitsani suger soap ndi Xina musiyeni muthu
@user-rk3gq7gd8f
@user-rk3gq7gd8f Ай бұрын
Paja kalindo amawuza kuti ndilipano mundimange amamuopa asamakuopsyezeni ameneo thawi Yao yatha akupita ameneo
@user-ou5vj2uc3p
@user-ou5vj2uc3p Ай бұрын
Mukapanga masewela tiyambisa gulu lazigawenga tithana namwe sitingakuopeni ayi
@HassanCharle
@HassanCharle Ай бұрын
Ndine mosi kwa andu amene amasapota Bakili muluzi TV sikomo amalawi asanga
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Ай бұрын
Yesani kumumanga muwone ngati mukuganiza kuti timakuopani. Mukuona ngati ndinu amuyaya inuyo eti. Nafensotu mifuti tilinayo
@patrickscott9086
@patrickscott9086 Ай бұрын
Uyu2 amanena chilungamo mugwile mbava zili m,boma nanga mpaka kulimbana ndi mwana ngat ameneyo. Pangani zina
@user-zd9js7qx1i
@user-zd9js7qx1i Ай бұрын
Muchoka chaka chamawa inuyo ndipo simumukwanitsa wa bakili muluzi
@DicksonBlack
@DicksonBlack Ай бұрын
Akamupeza chakwela azankhala wamuyaya bolezamawo muonaso Kodi bakili muluzi ndiye ikugwesa kwacha iiiya zausilu basi
@user-hy7kw6mm8n
@user-hy7kw6mm8n Ай бұрын
Mbuzi za wanthu mmalo mothana ndi mavuto awanthu ndalama muzionongela kumanga munthu
@user-ko2yv4gi5y
@user-ko2yv4gi5y Ай бұрын
Komanso nkulu ameniyi akuti nduna yanji sichidakwa chimenechi
@Moses51
@Moses51 Ай бұрын
Keep up bakili muludzi best TV in Malawi 🇲🇼💯
@emmanuelchavula7144
@emmanuelchavula7144 Ай бұрын
Zaziiiii nduna zina zomwe zilizopandq zeru zimenezi
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Pepe kale kod uuzitenga ngat ndiiwe wamuyaya et ediot Nkukuyu mbuz
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Useless politicians
@IbrahimDailes
@IbrahimDailes Ай бұрын
Tchito kulimbana ndi anthu azanu si kukweza kwacha we love this guy bakuli TV mo 🔥
@EddieBakali
@EddieBakali Ай бұрын
We stand with bakili muluz
@injesimadera1313
@injesimadera1313 Ай бұрын
Stay safe my brother!!! We love you and we wish you a long life
@innocentissah2636
@innocentissah2636 Ай бұрын
Imeneyi ndiye nkhondo, mukuona ngati chipani chanuchi ndi chamuyaya eti
@HarryKabambe
@HarryKabambe Ай бұрын
Muuzeni galu was kaunjikayo kuti its not TV ya muluzi Bakili, it's TV on its own
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef Ай бұрын
Mitu yanu simagwira. Malo mokoza mavuto amene akukumananawo a Malawi
@user-yi4bs3cd7w
@user-yi4bs3cd7w Ай бұрын
Mcp kupumila ku nkhwapa chifukwa cha bakili muluzi tv munya agalu inu ndi corruption yanuyo bakili muluzi inabwera kuzakhala pano ndipo sizasitha
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Mbuzi ya munthu president ameneyo kuchita kuwopa bakili muluzi Mesa kubako achina mapwalanu
@user-bw2cv9sd7x
@user-bw2cv9sd7x Ай бұрын
osaopa ndi agaluu amenewo chilungamo chikuwawawa
@user-wv4nt9zt3u
@user-wv4nt9zt3u Ай бұрын
Zisilu iizi zosowa zochita mmalo mokodza ziko ndiye munakula bwanji
@user-jl6od3qr5b
@user-jl6od3qr5b Ай бұрын
Kukula mutu koma zeru zero basi tamaendani mmidzimu koma muende opanda ma guard ok
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Ayelekeze kukumanga Ku Malawi kuvuta ndithu
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 Ай бұрын
anthu akuba awa ndipo mayazi zitsilu izi zichoke boma zikuba kwambiri
@SPAGHETTI313
@SPAGHETTI313 Ай бұрын
Ana achepa Bakili muluzi tv is our bold Best whole Malawi
@EvansPhiri-ug4oz
@EvansPhiri-ug4oz Ай бұрын
Chakwela ndi cabinet yake zisilu
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga Ай бұрын
Zitsiru za anthu izi Mwavomereza kuti akunena zowona Mulungu amutetezere B muluzi ❤❤❤
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 Ай бұрын
Zimapanga hate akubanu, pomwe ife osawukafe timanjoya ndi bakili muluzi TV kuposa chilichose
@saidichirwa5456
@saidichirwa5456 Ай бұрын
Sitikuopa ,mukudana ndi chilungamo inu.mukufuna kumaba opanda okudzudzulani.Brother usanyumwe nawo makapewa.
@augustMag
@augustMag Ай бұрын
Mmmmmhu mpaka asilikali akuja akuchedwa brother Bakili Muluzi TV 🔥 iwowatu ai Mulungu ai ndbwino kuti azingopanga zoti adyeretu chifukwa nthawi yawathera 2025 ulamuliro wao ukutha monga momwe MULUNGU anawatulusa Aisrae ku Egypt ifenso ku Bagga moyo tikutulukako ndithu Mulungu wamphamvuzonse apitiliza tchito imene anayamba mwa Inu Ndipo azikutetezani 🙏
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s Ай бұрын
Kkkkk koma azikhale mwangokula mutu koma ulibe nzelu bakili muluzi tv simungamukwanise ameneuja ndipatali ife tithane ndinu sopapano agwape inu
@MaIikhiziDawood-lm7mg
@MaIikhiziDawood-lm7mg Ай бұрын
God BLESS You Appreciate TE You AND RESPECT You DEFINI TELY For You
@Nathkala997
@Nathkala997 Ай бұрын
Bomba sakhalisa chifukwa likaphulika silibisika
@tisamulangala5570
@tisamulangala5570 Ай бұрын
Bakili tv God bless you ❤❤
@FonexLackson
@FonexLackson Ай бұрын
Zisilu izizi Bakili Muluzi TV. Musakhotese nkhan pamenepo akuti TV ya abakili mapazi ao anthu okuba inu
@user-nb7dp6pr9n
@user-nb7dp6pr9n Ай бұрын
Mulungu atithandize ameneyi asamupeze ndithu, mwaiyeyi tikudziwako zinsisi zambiri🙏
@Nelsonmacken
@Nelsonmacken Ай бұрын
Koma kusowa zochita boma ili aaaaa koma kuputsa kwenikweni uku
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba Ай бұрын
Boma lopusa kwambiri satana amadana ndichilungamo ziwanda izi
@milliambandah1939
@milliambandah1939 Ай бұрын
Mmalo mosaka zakudya anthu akufa ndinjala ndiye kumaononga ndalama kusaka wa tv mbuzi zanthu
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 Ай бұрын
Koma zoona bomali ndalama azionongela zachibwanaziii
@user-ek7ny9wi4g
@user-ek7ny9wi4g Ай бұрын
Akulu ife tidzalowelera serious tidzapanga mademo coz palibe zimene mukhoza kumagwidwila mudziko la democracy
@saidichirwa5456
@saidichirwa5456 Ай бұрын
Iyi ndi tv #1 kumalawi
@MisheckAselo
@MisheckAselo Ай бұрын
Mungoonanga ndalama zaboma a zikhale ng'oma Pangani za minster of finance ija ndinu agalu kwabasi
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 chimimba ngati finye Ifeyo we Love ❤️ Bakiri muluzi TV
@zephasibanda4462
@zephasibanda4462 Ай бұрын
Kodi aboma mulibe zina zochita kuma offece anuwa mwatikwanatu pano bakili muluzi simavuto athu ife tikufuna ma passport agaru inu kodi mukufuna anthu atani
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
😂😂😂😂😂, amenewa siagalu ayi koma imbwa za dogs
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o Ай бұрын
I love bakili muluzi tv,, Mcp nthawi yanu koma chaka cha mawa tionana
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
Zikhale ng'ona musamadana ndi chizuzulo zikalakwika zalakwika
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Awuzen agulewa
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Pa mtumbo pake Chakwera ndi anzake
@user-mz4tk1pw3f
@user-mz4tk1pw3f Ай бұрын
Ali ndi chibwana kwambiri Moses kunkuyu
@MwanaRosario
@MwanaRosario Ай бұрын
Mmalo motenga ndalama ineyo kuthandizira ana a masiye, não zawo za ziiiiii
@felixsaidi6715
@felixsaidi6715 Ай бұрын
Osawopaa ndi mbavaa izii. Akuwopa
@andrewmtendere3167
@andrewmtendere3167 Ай бұрын
Koma agaru amenewa asowa zochita et bwanj akumuopa born kalindo
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 Ай бұрын
Asa azibambonakulu akulu ngati inu mpaka kusaka bakili muluzi TV ASA kuwopa chilungamo koma azathu mwalemelatu ma tissue ndindalama
@owenmoses9434
@owenmoses9434 Ай бұрын
Komatu God is watching what u are doing guyz nd mcp yanuyo
@GeoffreyShariff
@GeoffreyShariff Ай бұрын
Zomvetsa chisoni kumalawi bwanji
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v Ай бұрын
Komatu inu mpando muliwo oyamba siinu ndiye zinazi bwezi mukuganiza inutu ngati simukupeza ma bakili muluzi mutafe ndinu mufa imfa uya zisilu
@EnockMuyaya
@EnockMuyaya Ай бұрын
Kuru owe tisave Kuru mwamupha sizoophwezana ai sithawi ya win pat
@ChipieMabulets
@ChipieMabulets Ай бұрын
First viewer of this video
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d Ай бұрын
Best tv ever in Malawi ❤❤❤
@Ocean20020
@Ocean20020 Ай бұрын
That will not happen
@user-zl9vj6hc6y
@user-zl9vj6hc6y Ай бұрын
Kodi akuti chani namachende ameneyu Mutu ngat mwala
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v Ай бұрын
Sizoopsesa anthu mdziko muno ali mu democracy
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 Ай бұрын
Boma lazaza ndi zisilu mwava
@marshacee8315
@marshacee8315 Ай бұрын
Koma guys nduna ziwiri kukanika kugwira ntchito za Boma nkhani koma Bakili muluzi tv zoona?😂😂😂
@ibrahimmeemzy9754
@ibrahimmeemzy9754 Ай бұрын
Number one tv❤❤❤🎉🎉
@maccussim1079
@maccussim1079 Ай бұрын
Sangakwanise,ndipo aphesa asilikali ayeni.....ndikakhala ine yanga ndiyo loader kale plus plus 100 more extra
@usherjamson174
@usherjamson174 Ай бұрын
Inuyo ndi one big cabinet yose uli busy kusaka munthu olakhula chilungamo
@Misasi19
@Misasi19 Ай бұрын
Alibe nzeru ndiapumbwa koma sangakupezeni biggy ndi ana
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 Ай бұрын
Kodi inu azikhale ngoma Kodi iyeyu walakwa chani ....tiuzeni poyera Achakwera akukana kut wina aliyense Ali ndi ufulu olankhula zoona nde inu mukuti bwanji...koma mumaopa Mulungu? Kapena mwasanduka Mulungu inuyo
@samsonthukuta5713
@samsonthukuta5713 Ай бұрын
Ya wa dinya pa liwombo tv imeneyi sure Kkkkkk
@AhmedHchipelesa-zm8oe
@AhmedHchipelesa-zm8oe Ай бұрын
Imagine the whole government now it's against bakili muluz tv chilungamo baba munya
@user-lb5gt4uv3s
@user-lb5gt4uv3s Ай бұрын
Bakili muluzi TV ❤❤
@patricksamson4852
@patricksamson4852 Ай бұрын
Kuzakhala mademo a phwee muterekeze
@FosterChilumba
@FosterChilumba Ай бұрын
We are in a democratic country mbava inu masiku opyezana anatha ndi dictator Kamuzu ndiye inu ziduswa Za Hestings mutiuza chiyani
@mussasamuel774
@mussasamuel774 Ай бұрын
Ife ndye bakili muluz tv yo😂😂😂😂 paja amat chilungamo nd mwano😅
LIVE: President Biden delivers speech to Nato summit
1:16:46
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 7 М.
That's how money comes into our family
00:14
Mamasoboliha
Рет қаралды 11 МЛН
Incredible magic 🤯✨
00:53
America's Got Talent
Рет қаралды 78 МЛН
Was ist im Eis versteckt? 🧊 Coole Winter-Gadgets von Amazon
00:37
SMOL German
Рет қаралды 39 МЛН
Atikumbutsa Samora Machel wa ku Mozambique
10:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 30 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 168 М.
Sky News host brutally takes down Joe Biden after he lies in interview
12:22
Sky News Australia
Рет қаралды 1,9 МЛН
Akusaka mtolankhani ndi kusiya Paul Mphwiyo ndi Moses Khombe
7:29
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 107 М.
Who killed Evison Matafale?  Adaferanji Evison Matafale?
21:20
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 146 М.
That's how money comes into our family
00:14
Mamasoboliha
Рет қаралды 11 МЛН