Bon Kalindo Response To H E Chakwera's SONA.

  Рет қаралды 38,338

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

5 ай бұрын

His Excellency the President Dr Lazarus Chakwera was at Parliament in Lilongwe to make his State of the Nation Address (SONA) and here is what Bon Kalindo had to say about it.
Olemekezeka a President Dr Lazarus Chakwera anali ku Nyumba ya Malamulo ku Lilongwe kukakamba nkhani ya boma la dziko lino (SONA) ndipo izi ndi zomwe Bon Kalindo ananena pankhaniyi.
Note: We Apologize, we mentined in the intro that Bakili Muluzi TV had a copy of the but it turns out they too do not have the full copy. Tikayipeza we will post it or tikupatsani Link kuti nanunso muyimvele.

Пікірлер: 120
@nyasavoicebox
@nyasavoicebox 5 ай бұрын
Note: We Apologize, we mentioned in the intro that Bakili Muluzi TV had an Audio/Visual copy of the SONA but it turns out they too do not have the full copy. Tikayipeza we will post it or tikupatsani Link kuti nanunso muyimvele. If you would like get the PDF version please email us at nyasavoicebox@gmail.com and we will make that available to you.
@ChrispinMpando
@ChrispinMpando 5 ай бұрын
😊😊😊😊😊
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 5 ай бұрын
Ine ndiye chakwera wandikwana😮😮
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 5 ай бұрын
Ndipo opha, chakwera pano angakhale herooo
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 5 ай бұрын
Empty brain
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 5 ай бұрын
Koma analidi m'busa uyu ? Fuso zikupeleka pic yanji ya azitumiki achauta. This is are bad people not all 90%bad 10 are good.
@ephraimkadamika
@ephraimkadamika 5 ай бұрын
Mwana owopsya kwambiri ❤❤ the Dc
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 5 ай бұрын
Ine ndye saname president uyu amandinyasa zed since kulowa boma mbudzi
@GRACIOUSKENAN
@GRACIOUSKENAN Ай бұрын
The king master, the DC bon kalindo
@BunayaJafali
@BunayaJafali 14 күн бұрын
Bon!!!!! Kalindooooo 🔥🔥🔥🔥🔥
@Bkathira
@Bkathira 5 ай бұрын
Nice one Mr DC waiting ma Demo
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 5 ай бұрын
Thank you Mr kalindo
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e 5 ай бұрын
❤❤❤❤❤ Bon kalindo Mawu amenewo
@MphatsoDuncan-gh2vc
@MphatsoDuncan-gh2vc 5 ай бұрын
Fire
@charlurquhart5788
@charlurquhart5788 5 ай бұрын
Akanakhalako anthu ten kumalawi ngati born kalindo pano kumalawi kutasintha akapange kwa mache ximenezo galu ameneyo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 5 ай бұрын
❤❤❤❤❤ mr bon kalindo
@oliviamphande1900
@oliviamphande1900 5 ай бұрын
Waiting ma demo Mr bon kalindo
@HildatoweraMhango-et4mz
@HildatoweraMhango-et4mz 5 ай бұрын
Pa campagn ndi chilima anatiuza kale kuti adzamanga airtell yabwino
@user-xo5mq7wl7t
@user-xo5mq7wl7t 5 ай бұрын
A KALINDO KEEP IT UP
@TiyaMtete
@TiyaMtete 5 ай бұрын
❤❤❤❤Mr bon kalindo
@user-xv5pr3ji6w
@user-xv5pr3ji6w 5 ай бұрын
A chakwera zikufunika musazike ndithu inuyo nthawi yanu yatha,.. ine patrick nampota, South Africa
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 5 ай бұрын
Sure kkk
@user-pu3sb2xw6z
@user-pu3sb2xw6z 5 ай бұрын
❤❤❤Kalindo
@charlurquhart5788
@charlurquhart5788 5 ай бұрын
❤born kalindo ndikukanika kupta kwathu kumalawi chifukwa cha Boma iri mmm ai
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 5 ай бұрын
Ngakhareso ine mmm galu uyu
@dingim1234
@dingim1234 5 ай бұрын
Those who don't value their words, will never value your wishes.
@IsaacPhakaya
@IsaacPhakaya 15 күн бұрын
Mwanaa opsa kwambili Bon kalindo
@user-jp2qg2ww7r
@user-jp2qg2ww7r 5 ай бұрын
Dc❤❤
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 5 ай бұрын
The DC ❤
@user-ec3xh4pc6t
@user-ec3xh4pc6t 5 ай бұрын
Wawa ambwiye
@user-mk7fh5ml8s
@user-mk7fh5ml8s 5 ай бұрын
Umakwana DC❤❤❤
@user-oo5bx1rl3j
@user-oo5bx1rl3j 5 ай бұрын
Nkhani yaikulu a bwana president Boni Kalindo monga athu amene mukutiimilira ifeyo anthu osauka. Ndimaona ngati kuti akawakana mai Mary Navitcha kuti akhale leader of opposition; ndimaona ngati kuti inuyo ndi gulu la Malawi First. Mungopita ku court kukatenga injunction chifukwa MCP ikuwadelera a Malawi kwambili. Kulibwino parliament imeneyi ingoimitsidwapo. Chifukwa anthuwa akuwatola a Malawi ngati alibe tsogoleli monga inuyo bwana Boni Kalindo. Thanks mr President Boni Kalindo
@user-xm5bg9qi6b
@user-xm5bg9qi6b 5 ай бұрын
Mau amphamvu
@thefather007
@thefather007 5 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉the dc!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Umakwanatu
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 5 ай бұрын
DC ndimunthu wachilungamo anthu wotere ndi amene akufunika ku parliament
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 5 ай бұрын
Koma chakwera amalingalira kt azafa ndikukakuman ndi fum ya mafum?mm koma ukuxuza ndithu
@PreciousHenderson-qc1hq
@PreciousHenderson-qc1hq 5 ай бұрын
God guide malawi🎉❤
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 5 ай бұрын
Dc plz come tulusa ndodo
@ThandieWaMalungaseda-rd1bg
@ThandieWaMalungaseda-rd1bg 5 ай бұрын
Chilungamo chenicheni
@user-qw4pk7wj8i
@user-qw4pk7wj8i 5 ай бұрын
Ndithandizeni guys liu lot DR wakuti limatanthauzanji anzathu mumatha kuona dictionary
@user-to8pv7ph9g
@user-to8pv7ph9g 5 ай бұрын
It stands for Doctor, mainly used in health field like physician,or with phd.just an abbreviation like, Mr which stands for mister.
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 5 ай бұрын
Tidya chizungu chachakwera chaka chino
@HappyMwase-w7f
@HappyMwase-w7f 20 күн бұрын
szilimbino dzikolawola
@AllanCharlesNgona-wm5xs
@AllanCharlesNgona-wm5xs 5 ай бұрын
Mr kalindo ❤❤❤😂😂😂😂😂😂😂😂 neco
@PrinceMapemba-fn4cw
@PrinceMapemba-fn4cw 5 ай бұрын
One day will bath together at state house 😎😎😎
@AlickNdeketeya
@AlickNdeketeya 5 ай бұрын
Ku gaza
@BrightNkhoma-xz4bg
@BrightNkhoma-xz4bg 10 күн бұрын
Kod .mesa anat akalephera 2 years azatula pas udindo?? Tinenekut akukwanisa kusatula pasi udindowu?
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 5 ай бұрын
Chakwela mulungu adzamulanga kwambili chifukwa athu akuzuzika ndipo athu akufa ndi njala
@abdulirichard260
@abdulirichard260 5 ай бұрын
viva D.C. ❤❤❤
@PreciousHenderson-qc1hq
@PreciousHenderson-qc1hq 5 ай бұрын
Viva malawi Viva malawi
@johncassimu5433
@johncassimu5433 5 ай бұрын
Ine chakwela ai ndi mbudz
@josephMandala-hk4xs
@josephMandala-hk4xs 5 ай бұрын
Kodi a Boni K Alindo ndiotani ?Is he a Malawian or Mozambican
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 5 ай бұрын
Achakwela tikufa ndi njala komwe tikupita basi musala nokha
@user-qy5sh4di7t
@user-qy5sh4di7t 5 ай бұрын
Iya
@user-ny3it3jp9l
@user-ny3it3jp9l 5 ай бұрын
Hy
@custommantchombe-rn1oo
@custommantchombe-rn1oo 5 ай бұрын
The kalindo DC ....Umatha
@tiunzanenganimunomwaafrican
@tiunzanenganimunomwaafrican 5 ай бұрын
🎉 Ndiye wina aliyese😂akulira naye❤ chakwela olo kufusa mwana amangotu kwana kuti ansavele virus ya chakwela ayenda ndi kurangura zonsa kwana Oro kakebe ka feteresa.🎉😂❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂Ndipo aliyense anadi akudana naye Akumamutukwana coz chaufiti wake
@eliasmgala8469
@eliasmgala8469 5 ай бұрын
Akuluwa ndale zawalowa kwambiri. Angokhala leader of opposition basi
@peterkuliyanimbewe
@peterkuliyanimbewe 5 ай бұрын
Moto kuti buuuuuuuuu kalondo yemweyooo
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 5 ай бұрын
Chakwera kukamwa kobwafikako
@user-qw4pk7wj8i
@user-qw4pk7wj8i 5 ай бұрын
Kod uyu chidzungu chake chakut bible courage yomweyi kkkkkk Kom chisoni kobs
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 5 ай бұрын
Satanic, imamusintha munthu mu zambiri ndipo English yi ndi silang ya pansi pa nyanja
@BrazioBauleni-sq9pu
@BrazioBauleni-sq9pu 5 ай бұрын
The DC more fire sonayi ndi manyaka
@user-qd2uy9fp9v
@user-qd2uy9fp9v 5 ай бұрын
Bwana kuyakhula kumeneko kwa nzeru awawa akufunika ku pita koko atulukeko si ana ife
@user-gh1yc3mu5r
@user-gh1yc3mu5r 5 ай бұрын
Umakwanira the DC
@user-pe7lo1fe9b
@user-pe7lo1fe9b 5 ай бұрын
Tikufera chizungu
@yusufhuseyin2039
@yusufhuseyin2039 5 ай бұрын
For sure
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 5 ай бұрын
Nyengo yakutswakutswa
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 5 ай бұрын
Mumaona Ngati achimwene aakulu ndi wazisuzo munya muona
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 5 ай бұрын
Kwa ine zomalandila ndalama za ulerezi si zabwino kwen kwen, chifukwa zimapwetekesa anthu ozilimbikila pa okha chifukwa ndi pamene misonkho imakwela kwambili ovutika amakhala ozilimbikila uja olandila za ulere sadandaula coz nzaulele. Program imenei ndingakhale osangalara itakhala only okalamba bsi not aliese and big problems amalembana pa chibale anthu ake ndi omweomweo choncho nzosakoma.
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 5 ай бұрын
Ndipo chakwera palibe chilipo ine ndie wa kwa gwanda chakuambayo ndi bodza kwathu sanaikeko nseu DPP ndi lomwe idzakonze nseu
@georgemponda
@georgemponda 5 ай бұрын
Speech yagalu uyu(chakwera) its copy and paste speech ya president wa South Africa 🇿🇦 😂😂😂😂
@evansevas119
@evansevas119 5 ай бұрын
Kalindo asakupusitseni amalawi choti mudziwe palibe chingasinthe mavuto wabe adzapita patsogolo chimene akufuna born kalindo ndichakuti boma limene likubwelalo lizamuganizile udindo winauliwonse akadzatelo simudzamuwonaso wapita basi mavutowabe adzati tsalila yinu ndiyene
@storytambala6088
@storytambala6088 5 ай бұрын
Chakwera usanamize anthu kuti, ungamange njanji yoti sitima iziyendera magetsi. Pakalipano, ikulira boma la south africa anthu atadula mawaya onse a copper mu njanji ikutha 3yrs pakali pano madera ena kulibe sitima zonyamula wanthu. Ndiye ukawanamize anthu lero, tamawopa Chakwera kumwambaku kuli mulungu udziwe kuti, unayamba bwino koma tsopano utha udyo.
@AlickNdeketeya
@AlickNdeketeya 5 ай бұрын
Chakwera ndi batile linja lizigona Pa charge basi
@fridaymtembo1304
@fridaymtembo1304 5 ай бұрын
Akafuse nyamilandu akati azamanga 5star hotel mu nthawi yowonjezela zimene akayesa kuti Malawi wa lero ndi wa zana anthu ndiwokwiya ndi anthu opusa onga wawa
@lawrencetenthani5547
@lawrencetenthani5547 5 ай бұрын
Or iweyo Kalindo ndichani unapangako uli MP kwanuko. Leave Chakwera alone tidamuvotera tokha
@IdritsaHanudan-dg3gi
@IdritsaHanudan-dg3gi 4 ай бұрын
Ndpo chaakwela sukunya sunny wako
@ronexmcdonald8742
@ronexmcdonald8742 5 ай бұрын
The DC
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 5 ай бұрын
Mbewu iyiyi ya Chakwera yi isazabwerenso yatizunza ngat tili mu chipani chimodzi.
@charlurquhart5788
@charlurquhart5788 5 ай бұрын
Cionse akulandila machende ache galu amenei achoke bs
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e 5 ай бұрын
Kod inu amalawi muli pati paliposo mukangonyoza zili zonse mwatan kod nanuso mitu yanu sikugwira ntchito pitani uko ndi chakwera wanuyo machende ake, bon kalindo ndi katundu payekha ife tili ndi abon kalindo
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 5 ай бұрын
Dikila ndi wa tukwaneno zenizeni, mboli zanu,machende anu,nyini zanu, mikongo yanu ,kuda ngati kuseli kwa tchende nonse otsutsana ndi bon kalindo ,chakwela galu wa munthu, nankhumwa mwana wa mbuzi okakamila kuyamwa galu chakwela koma munya campaign ikayamba mpamene muone mkwiyo wa a Malawi,,,,,machende anu nonse ! Chakwela kukamwa ngati mpheto, mkazi wako kukamwa ngat kumtumbo agalu inu mwatizunza kwakwana manyi anu
@georgednthala-wh3pf
@georgednthala-wh3pf 5 ай бұрын
Kuyanba kuwapatsa150k simwano, bcoz amadikila apange budget through parliament bcoz thy needed a gud amount of money. Iwe ili ndi nsanje whatever speech angayankhule u criticize it bcoz u want to deal with the president posakupatsa udindo m'boma
@user-fs1ox7ou1b
@user-fs1ox7ou1b 3 ай бұрын
Chisilu ichi
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 5 ай бұрын
Chakwera inachuluka ndi jerasi nkhwidzi kupangira APM koma kunena zoona walephera kusogolera wanthu
@MathewsKamphambe
@MathewsKamphambe 5 ай бұрын
Komatu amene akudyelela misokho yathu ni azathu akumwela koma izi anena ABorn Kalinndo nizosaveka kodi anapeleka Fredy ndi a boma ? anthu amafa ninjala ninali boma liti ?inu mukulimbana mokho ku DPP kwanuko .ukuwuzani kuti mukakhale kwina mukana kuzolowela kundila zawulele
@user-mk4lo7bd6f
@user-mk4lo7bd6f 5 ай бұрын
Iwe ukusowa zolakhula kagone nichamba cakocho
@davietembo7935
@davietembo7935 5 ай бұрын
Don't talk about Kalindo for everyone here in Malawi is able to see .Ifetu ndi anthu akuluakulu tikuona zonse bwana though mukusapota manyaka
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 5 ай бұрын
timayembekeza kut tikumva kuti akalindo athandiza anthu 50 pakuwagawila chimanga aaa zokamba ulibe mbava yamunthu
@user-kr1kg5hy9l
@user-kr1kg5hy9l 5 ай бұрын
Zokotani mfumu.
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g 5 ай бұрын
Abonikalindo akachoka achakwera chakachamawa amene abwereyo simudzayimililanso nkuyamba kutukwana ndikungokuonani mulungu akadzatisunga tidzakusekani
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 5 ай бұрын
Iwe ndi chitsilu eti! Bon satukwana koma kutsuka bodza la boma
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g 5 ай бұрын
@@user-qv4ko6ps4j tachenjera ndiweo mudamuchotsa apm lelo mukulankhula zachakwera mukusonyeza kuchenjera kodi kumuitana munthu kuti mbuzi sikutukana?
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 5 ай бұрын
@@user-nc4vi1jt5g chokaaaaaa iweso mbuzi
@nellikkmwenda7087
@nellikkmwenda7087 5 ай бұрын
Achakwela ndi aboza
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 5 ай бұрын
Chimangoziwa kuyankhura chisiru chi boza basi mbuzi ya munthu. Nthawi yako yatha basi.
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 5 ай бұрын
A kalindo even u mp unakulephelani anakuchosan mukanakhala kut anthu akwanu mumawathandiza bwenzi sanaku choseni pa u mp leave our president alone ,jealous lakuvutan mumafuna unduna
@PSTPerivoli-xd1ot
@PSTPerivoli-xd1ot 5 ай бұрын
kodi umangosusa zilizose basi? ziyamikilani zinazi akulu ifet tikuonako ubwino winawake
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 5 ай бұрын
IMF, world bank, European union komanso the whole donor community is fully behind the president's economic policy... Anthu amenewa sapanganawo zandale so give credit where its due. Iweyo Kalindo what do u know about economy? Your audios are just a source of entertainment basi osati muzinamapo apa 😅😅😅
@lawrencetenthani5547
@lawrencetenthani5547 5 ай бұрын
Kusokoneza Parliament ukalowera kuti ndipo khomo lake litilo.
@user-rk3uo5fs6g
@user-rk3uo5fs6g 5 ай бұрын
Am failing to get your argument. U trash the SONA and same u recommend the SONA to the extent kuyitchula yokongola and mwayichekenera kuti can induce maiko akunja kuti apange support. Nkhani ikukambidwayi Ndi commenting on SONA is totally different. I expected you analyzing the SONA and isolate issues of great important and bring alternatives that can help to shape the situations. Waste of precious time
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 5 ай бұрын
Kalindo has nothing and doesn't know anything chitsiru Cha chabechabe
@user-xs3pk1vp8i
@user-xs3pk1vp8i 5 ай бұрын
Kalindo chilichonse kutsutsa mmmm asatipusitse mutu wake sulibwino akuluwa
@user-xs3pk1vp8i
@user-xs3pk1vp8i 5 ай бұрын
Kalindo ngwakufuntha akufuna ndalama wakavuka uyu zaziii
@robertharawa9203
@robertharawa9203 5 ай бұрын
The most useless guy in Malawi is Bon Kalindo after realising whatever problems the Malawi are facing what have you done to the people of you area to areaviate some of these problems do you really see what your friends like Bushiri are doing to help the poeple of this country but they have never been here to talk the nosense you talking about here
@PSTPerivoli-xd1ot
@PSTPerivoli-xd1ot 5 ай бұрын
i think bon kalindo you just opposes for the sake of opposing!! see things with positive lens! akulu kususa kwanu nkopanda nzeru
@lawrencetenthani5547
@lawrencetenthani5547 5 ай бұрын
Ndipo ine amandikwana Winiko wanuyi
@user-og3dp9di7e
@user-og3dp9di7e 5 ай бұрын
Kalindo mmmmm kumangotsutsa zilizose, ulire ndiweyo ,chifukwa chakwera akuwinaso,
@johnchicoti
@johnchicoti 5 ай бұрын
Bon kalindo adazowela kubwebweta kungomuzolowela basi alibe ninzelu zomwe ngati iweyo Ali plasntent wawanthu osawuka bwanji suwathandiza anthu osawukawotu
@user-cw8ue6qp8w
@user-cw8ue6qp8w 5 ай бұрын
Kod inuyo a born kalindo ndiy tivotele ndan koz mukutisokonedza ndiy mwina muine inuyo
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 5 ай бұрын
Akalindo ndiwopusa komaso chamba chamvuta
@user-lc9bm6li6z
@user-lc9bm6li6z 5 ай бұрын
Ndiwopusa kwambiri uyu
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 5 ай бұрын
Nasongoleyi ayende byake biiiiii
@peterkuliyanimbewe
@peterkuliyanimbewe 5 ай бұрын
Moto kuti buuuuuuuuu kalondo yemweyooo
Nastya and SeanDoesMagic
00:16
Nastya
Рет қаралды 15 МЛН
THEY made a RAINBOW M&M 🤩😳 LeoNata family #shorts
00:49
LeoNata Family
Рет қаралды 43 МЛН
SONA 2024 | President Ramaphosa's State of the Nation Address 2024
1:40:37
A Opposition Mwafatsa Kwambiri   Bon Kalindo
14:08
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 748
CrowdStrike: How an IT outage caused worldwide havoc
7:48
Channel 4 News
Рет қаралды 129 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 185 М.
Nastya and SeanDoesMagic
00:16
Nastya
Рет қаралды 15 МЛН