BON KALINDO WAMANDIDWA TAMVANI

  Рет қаралды 70,118

FRANCIS MTAWAYA TV

FRANCIS MTAWAYA TV

11 күн бұрын

Пікірлер: 170
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 9 күн бұрын
Mulungu nthawi zina amalolera kut zichitike ,Mulungu akuziwa choona coz anthufe tikuvutika, koma siku lina tizayimba nyimbo uzakhala umbon,long live Bon kalind and Kamulepo kaluwa coz sikuti mumàtukwana ayi koma chilungamo
@babranzima8120
@babranzima8120 9 күн бұрын
Achakwera ndichisiru kwanose inu mkumbaliri yachakwera mulimbuli mmangokonda kudyanaye mukuzuzika zanu akudya bwino zisiru zikungoombera manja mkuti bon kalindo ndiolakwa sanalakwepo I support my brother bon odana ndi bon afonyika yekha
@user-gm9xj1wc2m
@user-gm9xj1wc2m 4 күн бұрын
😢😢😢😢😢😂🎉besrs
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv 9 күн бұрын
We should just pray for bonkalindo not be killed
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 9 күн бұрын
No Democracy under Chakwera leadership but they said Malawi is the free country.
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 9 күн бұрын
Chakwela you mast go watikwana walephela
@NACNAC-fg5yd
@NACNAC-fg5yd 9 күн бұрын
Akapita tisankha inuyo mukhale president.
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d 8 күн бұрын
Okey
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 9 күн бұрын
Pan apanga puran akumusamusa bon kalindo ku police yomwe anakasekeredwa akupita naye mbali zin ,koman sakafik apanga prn kt amuponye pasi galimot ikuthamanga ndicholinga,azit bon kalindo wafa polupha mugalimot
@LameckGamah
@LameckGamah 9 күн бұрын
Ndiye mwawamanga imagine mwat iyyy ndiye best way kut Amalaw osawuka akhare mu umbuli be eet inuu mukuchita manyii Boma😂
@user-zv3cy2xj5p
@user-zv3cy2xj5p 7 күн бұрын
Zofuna izi, president sakhala busy ndi accident koma a civil aviation ndi army aviation
@joicemumba3608
@joicemumba3608 9 күн бұрын
Ndiye mumanga tonsetu, ife tikubwerezanso kuti chakwera wapha chilima
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 9 күн бұрын
Ndi akunja omwenso
@GilbertKuchipinda
@GilbertKuchipinda 9 күн бұрын
Abweletu wamoyo kumeneko
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 9 күн бұрын
Asampase poison kumeneko,a police chenjeran ndife abale Anu.
@alicehananiya
@alicehananiya 9 күн бұрын
Ndipo abweledi wamoyo chifukwa anthu amcp afika poopsaletu
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 9 күн бұрын
Zoonadi we don't trust mcp at all
@MercyNyachi
@MercyNyachi 9 күн бұрын
But guys why can't we be like south Africans this too much chakwera wazolowela guys but why we Malawian we don't act guys akati boma ndife tomwe anthu onse akumalawi
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 9 күн бұрын
Ndizomwe ndimaganiza ine nane big amatitola
@SteveChirwa-ne9nt
@SteveChirwa-ne9nt 9 күн бұрын
Chimwendo Mkaka Mangano Chakwera Uyo wapha saulos chilima osapanga anthu olira.zitsilu inu .nanunso apolice ndinu zitsilu Zeni Zeni zosaganiza panyo Pani nonse pamodzi general inspector wanu
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 9 күн бұрын
kkkkk azake akulowa boma iweyo akulowa kundende chifukwa chopusa kkkk
@FlywellDamalekani-f2k
@FlywellDamalekani-f2k 2 күн бұрын
Mmm zokamba kamba ndizambili mulungu simunthu ngati ndiyifa yochokela mulungu adakoza kuti zidzakhala choncho ifesitingalanditse, kwatsoka amene adayikapo dzanja chifukwa adakolola zimene sadadzale.
@GRACIOUSKENAN
@GRACIOUSKENAN 9 күн бұрын
Ameneyo ndi kavuluvulu sangamutheee ohoo,atangophesa ana ayen akeee
@LuckyKalonji
@LuckyKalonji 9 күн бұрын
Kalani chete amalawi inu ngati mwaziwa chilungamo mwapangapo chani mugo lubwalubwa basi azeru akukuhuzani mwango kalachete osa aphatsa olo support amalawi simzateka dzaka 10,000,000.
@user-lw4wt2lo5o
@user-lw4wt2lo5o 8 күн бұрын
Kachilungamo kabwanji aka ,kakuwawa bwanji
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 9 күн бұрын
Even a smallest child knows the truth
@DavieChikumba-kl5tt
@DavieChikumba-kl5tt 9 күн бұрын
We don't know the power of Jesus Christ, thats why akumaphana😢😢
@davidbulla5128
@davidbulla5128 9 күн бұрын
The Voice of The People. Saulos not around to protect Bon...Let him Go Zachitsamunda Izi
@user-fi2by2ui9o
@user-fi2by2ui9o 9 күн бұрын
Tukwanani nyozani tikudziwa kuti ndinu ma kadeti simungayankhulepo zanzeru yense amene akulankhula zopanda nzeru kumalawi kuno ndi kadeti
@user-wt3ol5je4v
@user-wt3ol5je4v 7 күн бұрын
Amutulutse ngati sakufuna mademo
@MaryMary-dz2th
@MaryMary-dz2th 9 күн бұрын
Komatu anthuwa sanatukwane amanena chilungamo...ndikuti bon ndi Mr kamlepo abwereko amoyo
@joemlelemba6572
@joemlelemba6572 9 күн бұрын
Koma chilima ndizamulira mpaka kale
@ExcitedCornflowers-nw9oc
@ExcitedCornflowers-nw9oc 9 күн бұрын
Chigewengaaaa chigewenga,chakwera
@BrianBanda-mr2iu
@BrianBanda-mr2iu 7 күн бұрын
Osayipitsa Chakwera Apa; aMalawi kodi tizasinthaliti kumanyoza President aliyense angakhale pampando m Malawi..???? Mkutibowa kwambiri Mkanyoza Munthu Osalakwa, Tonse Tikankonda Mr Chilima, koma OSAYIPITSA Munthu. Anthu 9 basi Onse Anawapha Chakwera....?? Fursekkkkkkk, .Mmenyeni kundendekoo Bon iyoo, Akhale ndikhalidwee labwino LA Umunthu.
@dankopland-dp3vx
@dankopland-dp3vx 9 күн бұрын
PANO Chakwera Ali busy kuba ndalama ZATHU kuti adzalipire maloya akadzayamba kuzengedwa mirandu yake
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 8 күн бұрын
Amumasule bon kalindo and kalua mukhalidwe omangana mopanda zifukwa zenizeni ndiopepera
@PatriciaSemu
@PatriciaSemu 9 күн бұрын
Mmmm Koma athuwa akufuna Kodi chikhale chipani chimodzi ndale zachimidzi basi zaazingongo
@user-tm8eg3fd1f
@user-tm8eg3fd1f 9 күн бұрын
Nanu anthu andalewa amakuphimban maso..angofuna. Zao ziyere...
@MorrisMapiri
@MorrisMapiri 8 күн бұрын
If the gvt is just should let people to express their mind. This is democratic time where people should speak their concerns.
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f 6 күн бұрын
Aah.Singozi chabe ija.
@HappyNkhatha
@HappyNkhatha 7 күн бұрын
Kamulepo wafume pls muzengeko yayi kumpoto
@Cathy-oc7vd
@Cathy-oc7vd 8 күн бұрын
Tivomeleze kuti ija inali ngozi ngakhale kuti recently zimaoneka kuti issue ya presidential candidate wa 2025 imasokonekela. Chifukwa cha ichi pakukhala maganizo olakwika pomwe ndi ngozi ndithu.
@AufiThera
@AufiThera 9 күн бұрын
Ndalam zakoma kukanika kupanga rizine Mmmmmmm mudye bwino
@Moses51
@Moses51 9 күн бұрын
Kundale kulibe ngozi kom imankhala planning
@marryphili5419
@marryphili5419 9 күн бұрын
Wunenesko anthu aku mzuzu akunenadi chocho.kuti dege sinafike ku mzuzu amangonamiza anthu
@PempheroAlufandika
@PempheroAlufandika 9 күн бұрын
Akumangira chani ndikuyesa kuli democracy oyakhula a mcp inu simulibwino mwaoneka
@felixsaidi6715
@felixsaidi6715 9 күн бұрын
Mmalo mofufuza zangozi. Ali busy kumanga anthu omwe akuyima pachilungamo. Bwanji osakamanga anthu aja amkamukuwa chakwera ku ntchewu kuti waphera mngoni.
@davidkasisi7490
@davidkasisi7490 8 күн бұрын
Zolozana zalazi plz tatiyeni tizisiye pano tidakalila ndindani yemwe imfa imeneyi angasangalale nayo
@giftmingo9293
@giftmingo9293 8 күн бұрын
Chakwera cannot resign chifukwa cha Kalindo. Dikirani 2025. Only God knows zangozi.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 9 күн бұрын
Koma guys panopa Malawi ufulu watha basi chakwera asaonengati akhalapo mpaka muyaya ayi komatu bon abwereko wamoyo apapandiye muwaziwa a malawi
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f 6 күн бұрын
Audioyo akunena dzowonadi. Ife sitikuona chalakwika
@HEZEKIAMajuta
@HEZEKIAMajuta 8 күн бұрын
Only God knows what was happening 😂😂😂😂😂😂
@FrankKambwani
@FrankKambwani 9 күн бұрын
Chakwera dzoti ndiwe m'busa akudziwa ndi satana kukamwa kophotchokako.
@moyo77777
@moyo77777 8 күн бұрын
MCP yatha bas kkkkkkk or akumumanga bon
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 9 күн бұрын
Komatu Chakwera udzaziona
@arabisaidi4768
@arabisaidi4768 9 күн бұрын
Kma agalu inu a MCP mukampanga chipongwe bon kalindo tionesaka agalu inu machende anu nose a MCP Shat up
@MsondaBanda
@MsondaBanda 9 күн бұрын
Vajumpha pakulila wanyake, ndipo ufulu waujumpha, kutuka mbufulu yayi ,kulije ufulu wakutuka
@dorothykalanda1742
@dorothykalanda1742 7 күн бұрын
Kupha ndi kumanga anthu, kodi ndale zimenezi bwanji kodi? Tilibe mu nthawi ya kamuzu 😢
@StevenTembo-mb7rm
@StevenTembo-mb7rm 9 күн бұрын
Mr chakwera and your government bring back our freedom that our fathers and grandfathers fought for
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 9 күн бұрын
Then Malawi timayenera kupanga mademo osausa koopsa zedi
@Malani41
@Malani41 9 күн бұрын
He is a great comedian
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 9 күн бұрын
Koma iwe chakwera bonikalindo usamupheso ngati mumene wachita ndi chilima uyambisa nkhondo midziko mo galu iwe
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 9 күн бұрын
A chakwera ndi MCP yake sakudziwa kuti ku maiko ena anthu amamuuza President pamaso kuti itule pasi udindo. Tsopano a Malawi Bon Kalindo ndi Kamlepo Kalua kungolakhula choncho amangidwe! Aaaaaaaaah, useless government.
@dunganyamwela7266
@dunganyamwela7266 9 күн бұрын
Matsurani anthu, ndipo mumanga angati amalawi tonse tikuti a map mwapha chilima
@AfricanKingdom-uv1qb
@AfricanKingdom-uv1qb 8 күн бұрын
But chakwelayo anthu amene akuwamanga akulakwisa coz pano oziyipisilathu mbili munthu sazakhalaso president
@GeraldineSnyman
@GeraldineSnyman 8 күн бұрын
Komatu chotiuziwe iwe chakwela kenakoutasowe ndi iweyo sikalenso ayi
@trevorkasabikalyangu9255
@trevorkasabikalyangu9255 9 күн бұрын
Please Release them. Peace
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 9 күн бұрын
A yalukatu sanat mcp muona 2025 mutanosenu
@HappyAutumnTrees-cd9ye
@HappyAutumnTrees-cd9ye 8 күн бұрын
Chonena ife tilibe 😭😭😭😭
@MathewsChitsulo
@MathewsChitsulo 9 күн бұрын
Chakwela ndi wakupha. Kodi nanga ndichifukwa chiyani akufuna kutseka anthu pakamwe by Force? He must not force us to keep quiet for the murder. How many people is he going to murder and how many times is he going to stop us looking for what killed Chilima and 8 others. He can do whatever is doing but he must remember that no matter how dark the night is, the don is still coming
@AubreyKadzuwa
@AubreyKadzuwa 9 күн бұрын
Kd bomali ndi chan komatu a bwere wamoyo kumeneko
@AnnieBanda-rb2dk
@AnnieBanda-rb2dk 8 күн бұрын
manyi ake chakwera galu iwe chakwera ndeno oro umange anthu ukuona ngat oro umange anthu ndeno ukuwona ngat uwina galu iwe kachakwera, ubwereso kuno ku nkhotakota uzamange ine wava galu iwe ineso ndikumalengezaso kut wapha chilima ndiiweyo ndipo suzapeza voti kuno ku nkhotakota and nkhatabay galu iwe ubwereso kuno uzamange ine wava? galu opanda manyazi iwe l think inakubereka ndi ntchentche mayi wako ndi ntchentche ubwereso kuno uzamange ine galu iwe mayi anakubereka manyi awo galu iwee fiti yamunthu , ndikut oro umange anthu koma ndikubwerezaso unapha chilima ndiwe galu iwe chakwera ndikut wanapha chilima ndi chakweraaa
@MisheckAselo
@MisheckAselo 9 күн бұрын
Mumatero kumumanga akamanena chilungamo eee koma MCP, ameneu ndiye mutopa naye chifukwa mau achilungamo saopa gulu mutuluka Mr DC osaopa 🙏
@CatherineDesire
@CatherineDesire 9 күн бұрын
Akatero akufuna akampheso fiti dzachabe chobe
@chitchohistorical1036
@chitchohistorical1036 9 күн бұрын
Malawi wanga mayooo 😭😭😭
@lonjebinga5920
@lonjebinga5920 8 күн бұрын
Akangopereka maumboniwo basi. They know the truth mesa?
@ahamadulmbishana6629
@ahamadulmbishana6629 9 күн бұрын
Km Kalindo sanalakwe
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d 9 күн бұрын
Eti inu, nthawi ya campaign ino kumaopsezana?
@jamesgama5489
@jamesgama5489 9 күн бұрын
Osawopa timatelo nthawi ya mademo kuti mcp ilowe mboma lero zatembenukanso tiyambe kuwopsyezedwanso ayi zikomo.
@ChristopherUmari
@ChristopherUmari 9 күн бұрын
Kodi nanga amalawi asayakhule zoona, boma lanji limeneli
@Dickies-mk8cd
@Dickies-mk8cd 9 күн бұрын
MCP magazi mmanja muzasamba liti😭.
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v 9 күн бұрын
Anthu ambirimbiri alankhula nde chomangila kalindo ndichani? Mwapezerapo Mwai munkamufuna kale Bon please amasuleni anthu osalakwawa
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 9 күн бұрын
Mulungu dziwonetsereni nokha pa kumangidwa kwa Bon kalindo ndi kamulepo kaluwa
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 9 күн бұрын
God help our country malawi by the stuesion we have for give us our sin
@HaneefInnocent
@HaneefInnocent 9 күн бұрын
Amen
@user-gt6gd1er6s
@user-gt6gd1er6s 9 күн бұрын
Km tikuuze chakwera watitopesa wava
@user-gr5zt6kw3s
@user-gr5zt6kw3s 9 күн бұрын
Where is freedom of speech & expression?
@flytonenkunika-pi9dn
@flytonenkunika-pi9dn 8 күн бұрын
Bon kalindo utuluka kumeneko
@MsondaBanda
@MsondaBanda 9 күн бұрын
Boma lamanga wachikulile Bonface
@MaryMary-dz2th
@MaryMary-dz2th 9 күн бұрын
Abwere wamoyo borne otherwise pavuta pano
@JosephTembo-g6d
@JosephTembo-g6d 9 күн бұрын
Amasulidwe
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq 9 күн бұрын
Chonde Kalindo musamuphe mukatero mubwelesa ziwawa
@winfredyerikobanda4732
@winfredyerikobanda4732 9 күн бұрын
When people say, MCP will remain that is according to the MCP we as Malawians know from the those old days when police cruisers were still in black painted colour with an eagle 🦅 mark on the left. Don't forget, with them killing is an inborn behaviour that they can't help it.
@AufiThera
@AufiThera 9 күн бұрын
Tizaima pachilunhamo ngat born kalindo pls don't killed him
@user-gi1gh9ry6h
@user-gi1gh9ry6h 8 күн бұрын
?????? Boni kalindo asalakhole zowonadi kwa malawi 😂😂😂😂😂 shemu chakwela ndi mcp madafaka
@jomochirwa
@jomochirwa 9 күн бұрын
Ndiye kuti dpp ikutuma chilima ?ndiye kuti dpp sikufuna u.t.m kuti iyendeso limodzi ndi mcp? Means dpp ikufunitsitsa kuti iyendele limodzi ndi utm.woooo!zovuta ,mama akweni alipo ndipo akhale pasi.esh tchito ilipo .kkkk
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 9 күн бұрын
Let God be God
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 9 күн бұрын
Democrancy ya kumalawi ndi ya uchitsilu ufulu wake ukhare otukwana,
@Dickies-mk8cd
@Dickies-mk8cd 9 күн бұрын
Bon K amanenna zoona kwambiri.
@AngellaWitiness
@AngellaWitiness 9 күн бұрын
Abweleko ameneyo wamoyo
@dankopland-dp3vx
@dankopland-dp3vx 9 күн бұрын
Koma ulamuliro ukatha Chakwera adzamuteteza ndani?
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 9 күн бұрын
Ndipo amanga angati? Angomanga Malawi yonse chifukwa olo achewa anzke sakumufunanso pano akulila
@AstonJackson-rw8su
@AstonJackson-rw8su 8 күн бұрын
Akudana ndichilungamo why?
@BobcosterVassilatos-sd4so
@BobcosterVassilatos-sd4so 7 күн бұрын
Mmmm guys I dont think ngat angabwele wamoyo it's there chance
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 8 күн бұрын
Koma abale athu amangidwawa abwerako amayo kumeneko??? Pafika dziko lathu zafika powawa
@MirriamKambale
@MirriamKambale 9 күн бұрын
Akudziwa kuti ndi iyeyo galu ameneyu awamasule mthakati ameyu akufuna aphe angati? Kodi afiti kumalawi anatha? Nyawu imeneyi zimafunika kuilodza ndithu isanatithe tonse
@ShareeffJAjiluShareeffJAjilu
@ShareeffJAjiluShareeffJAjilu 9 күн бұрын
And maganizo anga kuno ku mudzi kuno kulibe anthh azelu monga ngat momwe apanga zo fufuza za imfa y chilima ku pe mpa sadic kuti alowelerepo zomwe zikuchitika kumalawizi zandi kwana zed
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d 9 күн бұрын
Koma boma iri nkhanza zake, anthu akamati MCP ndi nkhanza ndi kupha adzikana? Anthu akanike kuyankhula mudziko la democracy? Mmmmmmmmm leading people with anger and emotions? 😅
@harryphiri9020
@harryphiri9020 9 күн бұрын
Malawi is going to be like Zimbabwe no freedom at all becareful guys
@LukamanuelFisi-kx7dy
@LukamanuelFisi-kx7dy 8 күн бұрын
Koma Bon akangomupha ,, tiona
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 9 күн бұрын
Ukafotokoza komweko
@EphaciePhiri
@EphaciePhiri 9 күн бұрын
Chakwela ndigalu kwa basi
LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA 1 JULY 2024
49:58
Club Junta
Рет қаралды 23 М.
Hanzi "Tatumwa NaPresident" 😲
15:20
Dj Lenon TV Show(The World of Latest News)
Рет қаралды 13 М.
OMG😳 #tiktok #shorts #potapova_blog
00:58
Potapova_blog
Рет қаралды 3,9 МЛН
Was ist im Eis versteckt? 🧊 Coole Winter-Gadgets von Amazon
00:37
SMOL German
Рет қаралды 13 МЛН
터키아이스크림🇹🇷🍦Turkish ice cream #funny #shorts
00:26
Byungari 병아리언니
Рет қаралды 27 МЛН
ZIZINDIKILO IZI, ACHILIMA ANA CHITA KUPHEDWA..
8:42
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 221 М.
Wakatolika uyuyu Amutapa posachedwapa😂😂🤣😂😂
14:40
Malawian Cameras
Рет қаралды 54 М.
ANTHU AYANKHULA ZOSAOPA AWA 🙌🙌🙌
27:38
HOT 265
Рет қаралды 91 М.
CHAVUTA NDICHANI KUTI MWENDO UDULIDWE??? (DZULO PA 6TH NOVEMBER) TAMVANI
8:20
SILIKALI KUWULULA ZA IFA YA ACHILIMA 😭😭🙏
9:06
COLLINGS MW
Рет қаралды 17 М.
Hwindi kuita bonde nemukadzi wemunhu Ku back seat?
26:43
Manass-Chibanda
Рет қаралды 21 М.
EXPOSING MALAWI FAKE PASTORS
10:10
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 17 М.
ZIFUKWA 7 ZIDAPANGITSA CHAKWERA KUSATULA UDINDO PANSI
8:13
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 21 М.
Көктемге хат
3:08
Release - Topic
Рет қаралды 198 М.
Saǵynamyn
2:13
Қанат Ерлан - Topic
Рет қаралды 2,6 МЛН
Say Mo - LIL BIT & 1 shot 2 (Waysberg Music Remix)
2:43
Waysberg Music🇰🇿
Рет қаралды 108 М.
V $ X V PRiNCE - Не интересно
2:48
V S X V PRiNCE
Рет қаралды 856 М.
Duman - Баяғыдай
3:24
Duman Marat
Рет қаралды 109 М.
QANAY - Шынарым (Official Mood Video)
2:11
Qanay
Рет қаралды 264 М.