Limpopo FM yomweyo galu iwe Ntanyiwa kufotokoza za anthu 7 omwe anakamaliza a Chilima ndi anzawo

  Рет қаралды 48,410

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

14 күн бұрын

Пікірлер: 134
@giftwankhama9914
@giftwankhama9914 12 күн бұрын
Stay safe comrade. May the God in heaven keep u safe my brother.u the only source of true information to us.
@user-kr4wb2th9i
@user-kr4wb2th9i 12 күн бұрын
❤❤❤❤more fire 🔥🔥🔥 ndipo titemana serious muno oky mungoti pheee anthu amenewa asazayerekeze kubwera kumangochi serious azaona ngati akufuna kuti azalembe book la history lomkuzana anthu akumangochi 2024 yelekezani kubwera kuno , zimunezo kulilongwe komweko kwa anthu aganiza mwauchitsiluwo try to come here in Mangochi try
@Hudhayf
@Hudhayf 12 күн бұрын
😂😂😂😂 Mangochi m'bomamo
@peterlowole7841
@peterlowole7841 12 күн бұрын
We are great to have you comrades
@user-ph3zy9ox7d
@user-ph3zy9ox7d 12 күн бұрын
From South Africa all i have is a protecton prayer for you my brother ,, may God protect you from these anacondas for not swallowing you Amen
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Tikuziwa zisisi zambiritu mmm
@augustMag
@augustMag 12 күн бұрын
Tili pano kudikira Chilungamo chioneke ndi Limpopo FM radio 🔥♥️
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 12 күн бұрын
Kunena zowona paziko rapansi pano paribe chinsinsi sure nyimbo ikhare ya grace chinga ndizaurura tchimo rimazunza orichita sure 🥱🙆
@sulleahmnyimbili1362
@sulleahmnyimbili1362 10 күн бұрын
Thanks alot comrade, May God protect u so that a Malawi tipitilize kuziwa zoona zenizeni
@jacquelinecunningham363
@jacquelinecunningham363 12 күн бұрын
Limpopo 🎉🎉❤❤🔥🔥🔥🔥🔥💯
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 12 күн бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose adziwa yekha chochita nximu wanu uuse mumtendere bwana chilima
@PetroMatias
@PetroMatias 12 күн бұрын
Chakwerao osangomuombera bwanji watikwana kwambiliaaa
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Ndipo inu mmm
@eliasnyilongo4865
@eliasnyilongo4865 12 күн бұрын
My redio in malawi
@MustapherDavie-su3nk
@MustapherDavie-su3nk 12 күн бұрын
Tili pa mbuyo panu
@ShyreenMbwana
@ShyreenMbwana 12 күн бұрын
Chidanti Malunga wako uja amusankhadi kukhala VP monga umanenera dzulo lija
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Anaisintha game
@RachelNkhoma-vn2jo
@RachelNkhoma-vn2jo 12 күн бұрын
Umunthu alibe mphamvu ya satana basi,ngati opemphera koma Satana weniweni ineso ndi mchewa koma awaso aonjeza
@WilliamKapungu
@WilliamKapungu 12 күн бұрын
❤❤❤❤ More fire comrade ntanyiwa
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 12 күн бұрын
Mbuzi zawanrhu zukanika kulamulira dzko
@user-qg4it7my9n
@user-qg4it7my9n 12 күн бұрын
watching from cape town limpopo no: 1
@JamesKakhome
@JamesKakhome 12 күн бұрын
Comrade mtanyiwa! Chamzelutu apa kunali kungotulusa zinthuso coz mukat mwatulusa olo report mudikilalo sangatuluseso n mukhoza kumacedwa conco then kaya nditsokaso akusowetsan sibas zizakhala kut mwatidikilisa pachabe umbon muli nawowoso mwapita nawo! Tulusan chabe zomwe muli nazozo mukucedwa mukucedwa
@user-pj9rs6vj8x
@user-pj9rs6vj8x 12 күн бұрын
Umboni alibe awa chomwe akukanikira kutulutsa ndi chani?monse muja
@user-mq7ou5xp5m
@user-mq7ou5xp5m 10 күн бұрын
Chabodza ichi
@yassinn5634
@yassinn5634 12 күн бұрын
Magalimoto adutsa ku Lunzu?
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 12 күн бұрын
Viva Limpopo FM
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 12 күн бұрын
Magalimoto amene mukunenawo mungovutika amene aja ndi alendo ongudusa amachoka ku nacala port adusa ku Moçambique mpaka zimbabwe
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w 12 күн бұрын
More fire
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 11 күн бұрын
Watching from limpopo province in lephalale town
@LuciousKotamu-dh5uq
@LuciousKotamu-dh5uq 8 күн бұрын
Keep on inform us good work
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r 12 күн бұрын
Emusipi Chipani Cha Nkhanza komanso chakupha
@eunicesaiti
@eunicesaiti 12 күн бұрын
Following.... Limpopo 🔥 🔥 🔥
@ChawingaMwaseteza
@ChawingaMwaseteza 12 күн бұрын
Wina aziphe kumene agalu amenewa sangatiphele adzibale athu motelo
@ModesterMkawa
@ModesterMkawa 11 күн бұрын
More fire comrade kusatira ndi chidwi
@user-mh5xw5xu9w
@user-mh5xw5xu9w 10 күн бұрын
Number one Limpopo FM more 🔥
@user-pf5hu2pd2b
@user-pf5hu2pd2b 12 күн бұрын
This is true station
@babranzima8120
@babranzima8120 12 күн бұрын
Ndizisiru chakwera watha basi South Africa
@AliceGeorge-il6ig
@AliceGeorge-il6ig 12 күн бұрын
Bravo bravo achimwene,be safe plz
@YatoRoy-kt4lh
@YatoRoy-kt4lh 12 күн бұрын
2025 they will be no votes. Dziko lonse lapansi kukhala Climate Lockdown(NWO) mufufuze zimenezi
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Kkk
@BarnettWitness
@BarnettWitness 12 күн бұрын
Ipanse Moto tiziwe zoona zen zen
@emmanuelalbertbotolo
@emmanuelalbertbotolo 12 күн бұрын
More fire Mr muthanyiwa
@chrisboyce2
@chrisboyce2 12 күн бұрын
Limpopo ❤🔥🔥🔥
@WilliamKapungu
@WilliamKapungu 12 күн бұрын
Amfumu akabudula 😂😂😂😂 muziti Chan? 😂😂😂😂
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 11 күн бұрын
Viva Limpopo FM ❤❤🔥🔥🔥🔥🔥
@user-wg8tp8in1v
@user-wg8tp8in1v 12 күн бұрын
Koma mathelo a nkhani izi ndi Otani?
@ZelipaMalanda
@ZelipaMalanda 12 күн бұрын
Katundu akudula chifukwa cha kugwa kwa Kwacha yathu. Kwacha yathu ikugwa pafupipafupi chifukwa chosowa forex, forex ikusowa chifukwa chochepa kwa export; amalawi tachulutsa ma import osati export. Amalawi tiyeni tilimbikire kugwira ntchito zomwe zitha kutibweretsera katundu yemwe titha kutumiza mayiko akunja kuti forex ilowemo yambiri muno.
@paulinekayuni1621
@paulinekayuni1621 10 күн бұрын
Vuto ndiloti report yanuyi sikhala official zomwe zikuoneka zabodzazo ndizomwe zizamveke makutu a anthu ambiri. Koma tingopemphera ngati zanuzi zili chilungamo zizakhale official and anapanga azazengedwe mlandu
@ZelipaMalanda
@ZelipaMalanda 12 күн бұрын
Munthu akuyankhula za achewayu wangoonetseratu umbuli waku wonse kuti za democracy sazidziwa. Democracy imabwera ndi ma condition ake. Boma lingapereke ku ma company angati ndi ufulu wa pa malonda omwe ulipowu? Muli ma company angati m'Malawi muno kuti boma lingakwanitse kuperekako ndalama? Taganizirani za fetereza wotsika mtengo momwe zikuyendera, akupindula ndi amphawi kapena anthu andalama? Zomwe zikuchitika ndi fetereza ndi zomwe zikhoza kuchitikanso ndi sopo kaya ndi sugar kaya ndi mafuta ophikira. Omwe ali ndi ndalama zambiri akhoza kumakangozikokololako zonse nkumagulitsa ku amphawiwo modulabe.
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 12 күн бұрын
We are very angry we want to given us good information,we are not joking, Chakwera,Chakwera, Becareful., you will flee and Leave Malawi One Day,zida wagula zija ndi zathu tizazi tenga zonse tiku ziwa Chakwera Ufa ngati Nazombe Malawi uyu ndiwa sopano Siwa Kale munapha uja Chirima ndiye Anali bwana wanu,siku limodzi ma ofesi a MCP aza pshya tsiku ndi limodzi Osati Ndi chipani,Gulu la anyamata liku konzeka wenatu Alípo secret soldiers Malawi an there's is outside, Asirikari mukama gwiri sidwa ntchito Ndi MCP zizakuvutani yang'anirani Amalawi,Os militar não tenho partido, tem dereito para defender população ouviu Malawiano Malawiano não pode deixar Chakwera para vingar cidadão malawiano quidado Chakwera
@user-qg4it7my9n
@user-qg4it7my9n 12 күн бұрын
kkkkkkk ooooh ndodo itulukedi basi
@TryceMagombo-sh7kb
@TryceMagombo-sh7kb 4 күн бұрын
Big up big more and more imfo
@samchibenene4458
@samchibenene4458 12 күн бұрын
Mo fire Limpopo FM
@francismlilima
@francismlilima 10 күн бұрын
Koma mukuchulikitsa gagadiwa...go straight to the points
@LazaroSinerioSineiro
@LazaroSinerioSineiro 10 күн бұрын
Mcp omse ndi amagazi manja agalu Eni Eni mbuzi za wanthu
@RichardMphopheya
@RichardMphopheya 12 күн бұрын
more fire limpopo
@KeltonKapanda
@KeltonKapanda 5 күн бұрын
May God keep you safe comred
@user-pj9rs6vj8x
@user-pj9rs6vj8x 12 күн бұрын
Iwe osatulutsa lako lowonalo bwanji?hahaha mabodza awa
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 12 күн бұрын
Bwanji ya nzungu wamathanyula sunafune kuti tiyikepo maganidzo
@IssacMateyo
@IssacMateyo 12 күн бұрын
Sangave samadikila kuti amuuzeko ena kkkk
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 11 күн бұрын
Ife tupanga kaye za ifa ya Malawi nzathu, akanakhala Chakwera wafa ifa yotere ifeso sitikanakhala chete tikanafuna chilungamo chioneke
@partmaulidiPatrick
@partmaulidiPatrick 12 күн бұрын
Adahinuyo makwana
@BrightNyoni-yd4ip
@BrightNyoni-yd4ip 12 күн бұрын
Am watching you from Lusaka zambia
@CheMass-05
@CheMass-05 12 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥
@jonas-xh4hz
@jonas-xh4hz 12 күн бұрын
mumakwanira a mtanyiwa
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 12 күн бұрын
awa ndachisilu sanena zobveka amakonda bodza uzanamiza alomwe azako
@JulietKamanga-t5n
@JulietKamanga-t5n 5 күн бұрын
Ndipo ndimsona Ngati fm'yi ndiyakujonitu🤣🤣🤣🤣pa Malawi ayi ndithu
@ZelipaMalanda
@ZelipaMalanda 12 күн бұрын
Alimi afodya asangalala chaka chino musanamizepo anthu pamenepo inu a Limpopo FM. Ifenso alimi achimanga tikusangalala panopa chafika kale 750 per kg osati za 150 zija tinkaona mmbuyo zija ali, zomathandiza alesi osalima, olima nkumangolira. Kazingokhalani kumeneko anthu osowa zochita inu.
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 11 күн бұрын
150 mukuinenayo and imagula feteleza 18000 matumba awili zingafanane ndipano 200000 matumba awili
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx 7 күн бұрын
Are u a member if MCP or are u from central region u show your evil and dirty mind here better no comment if u not interested with him
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx 7 күн бұрын
Its not home of debates
@CathyYassimin
@CathyYassimin 12 күн бұрын
Kumatu muli phwete achimwene
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 12 күн бұрын
Mesa mumati asankha a chidati malunga inu mungodziwa kunamiza a malawi basi
@JoyceChimphwika
@JoyceChimphwika 10 күн бұрын
Ulosi wa grace chinga umandikumbusa kwambili chipani chamwadzi ichi mulungu achite nawo ndithu
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@AhmedKjuma
@AhmedKjuma 12 күн бұрын
❤❤😂😂😂 Koma kuthawadi
@EdwinMabviko
@EdwinMabviko 11 күн бұрын
Inu ndabodza,anthu akumayakhula bwanji sakuwamanga?
@rashidadan2533
@rashidadan2533 12 күн бұрын
Kagwedwe ka ndege tilibenazo ntchito , kubedwa kwa black box yamu ndege izo tilibenazo ntchito , Mufunilanji umboni wina chonsecho tikudziwa kuti chakwela ndi nduna zake ndizomwe zinapanga plani yogwetsa ndege yomwe inapha anthu 9 kuphatikizamo V'P Claus chilima .
@christopherchikankhen
@christopherchikankhen 12 күн бұрын
Limpopo Yayamba Kunamiza Anthu, Munatiuza Kuti A Chidanti Malunga Ndiomwe Adasankhidwa Ukhala Wachiwiri.
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 12 күн бұрын
Kkkk
@KennethChagunda-gn8kg
@KennethChagunda-gn8kg 12 күн бұрын
Uyuyu ndiwa bodzadi akulu
@ChristopherNikola
@ChristopherNikola 12 күн бұрын
Zilengwalengwadi eee
@PatriciaIron
@PatriciaIron 12 күн бұрын
Sanati amusankha chidanti koma amati ndizomwe akukambirana ndye nzosadabwitsa kuti ayitembenuza pamenepo
@user-pj9rs6vj8x
@user-pj9rs6vj8x 12 күн бұрын
Mmmm anati amusakha osabakira mveraninso mwina simunamve bwino
@KennethChagunda-gn8kg
@KennethChagunda-gn8kg 12 күн бұрын
Ndykt iyeyu amatiuza zopanda umbon
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Anaisintha game
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
​@@KennethChagunda-gn8kgkoma zimaphelezera akulu sikuti amanama ayi
@PililanilikomwaLuwesi
@PililanilikomwaLuwesi 10 күн бұрын
😢😢😢😢ok Malawi
@OwamThoko
@OwamThoko 12 күн бұрын
Zero ya bwino pofuna kukamiza chakwera kuti asiye anthu onse Malawi asiye lupita muzintchito dzeko lonse mabungwe ,aboma,amwenye asilikali,apolisi,mabusi,matekesi,mbc,wina aliyese,magurd ,capita muzintchito,palibee kanthu muvutike koma mawa muzasangala,dzeko lonse liyime paka achoke.mukuina bwanji amalawi
@OwamThoko
@OwamThoko 12 күн бұрын
Yah mzeru yabwino,achoke basi ameneyu,
@EdwinMabviko
@EdwinMabviko 11 күн бұрын
Asilikali aku Malawi amasunga mwambo,uyu ndiwabodza simsilikali!
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 12 күн бұрын
Its better kumakamba zinthu ndi umboni coz pamawa uzayankha brother
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
La 40likwana one day is one day
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 12 күн бұрын
Limpopo iweyo umakwanila ndipo mulungu azikudalisani ndikupasani moyo wautali
@SolomonAmon-bu5qc
@SolomonAmon-bu5qc 12 күн бұрын
Koma yaah
@ZelipaMalanda
@ZelipaMalanda 12 күн бұрын
Mabodza anuwo akutsalirani makape inu. Mwakonzekeratu zodzatsutsa lipoti powanamiza amalawi. Muchite manyazi.
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 12 күн бұрын
Lelo akuluwa zolakhula khalangati zasowa
@KennethChagunda-gn8kg
@KennethChagunda-gn8kg 12 күн бұрын
Ndiwa bodza inu munthu uyu. Kd iyeyu akudziwa bwanji zonsezi munthu ali ku SA??
@ZelipaMalanda
@ZelipaMalanda 12 күн бұрын
Wokhulupirira mabodza a Limpopo mutu wake sugwira. Ndani adatuma anyamata achipani kukafufuza za ndege? Muzichita manyazi ndi propaganda yanu makape inu.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 10 күн бұрын
Ndichifukwa chiyani osangomuchoseratu pompano chakwerayo? Apatu zikuonesakuti before 2025 kukhala kutafa anthu ambiri chakwera salibwinoyi
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 12 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥 Limpopo umakwana
@oathbilliot
@oathbilliot 12 күн бұрын
❤❤❤❤Limpopo
@LazaroSinerioSineiro
@LazaroSinerioSineiro 10 күн бұрын
Usiyo chiwembu chomwe anafera chilima uja akuchiziwa
@user-mz8nw6nx6p
@user-mz8nw6nx6p 11 күн бұрын
Vutoso la inu ndi la propaganda,,, Zikanakhala kuti mumangotiuza nkhani kuti tinve tidziwe mmene zinthu zikuyendela Koma mumapangaso campaign kuti anthu anvotele yemwe inu mukumufuna this is no sense
@KennethChagunda-gn8kg
@KennethChagunda-gn8kg 12 күн бұрын
Koma kodi iweyo ngati ukudziwa chulungamo bwanji osangonena?komanso ngt unkadziwa chomwe chinkachitika udatan iweyo kukawapulumutsa?? Komanso apa unanena kt Vp asankha Chidathi Malungo now is Usi ndy anthu tikukhulupilira bwanj kt umanena zoona??
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 12 күн бұрын
Limpopo number one
@gremarmbewe9906
@gremarmbewe9906 8 күн бұрын
Following
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 11 күн бұрын
Ndiye akugwesa kwachayo ndindani mesa ndichisilu chanucho
@Emmanuelisraelsimbi
@Emmanuelisraelsimbi 12 күн бұрын
Why unati kut chidanti ndi amene akhale vice president lero tu ndi Usi
@KennethChagunda-gn8kg
@KennethChagunda-gn8kg 12 күн бұрын
Uyuyu ndiwa bodza akulu akungofuna kumatipatsa uthenga wabodza
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 7 күн бұрын
Anaisintha game kkk
@lloydmushali-dw2td
@lloydmushali-dw2td 12 күн бұрын
Limpopo FM❤❤
@DanielErnest-ez1qw
@DanielErnest-ez1qw 5 күн бұрын
No comment
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 11 күн бұрын
Prophet mbeweyo Ndie ayiso aaaaaaaa athu opephela siawa akutiliza apawa
@AllanKasalu
@AllanKasalu 12 күн бұрын
comrade Ntanyiwa woyeeeeeeeeeeeeeee
@user-pj9rs6vj8x
@user-pj9rs6vj8x 12 күн бұрын
Hahaha wailesi yabodza iyi dzulo imatiuza bodza kuti vice president ndi chidanti malunga lero alengeza kuti ndi manganya hahaha ndinkana social media sindimaikhulupirira
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 11 күн бұрын
Chakwera evil 😈
@asayileernestsapao
@asayileernestsapao 12 күн бұрын
Ndayamba kukukayikilani
@KennethChagunda-gn8kg
@KennethChagunda-gn8kg 12 күн бұрын
Uyuyu atisokoneza mitu aaaaa
@AbbeyJere
@AbbeyJere 10 күн бұрын
26:58
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 12 күн бұрын
Nzunguyo amafunika kuti akadzike nayo chakwera 😂😂😂 wakupha
@user-bz4dw6vy7w
@user-bz4dw6vy7w 6 күн бұрын
Maloza ndithu
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 12 күн бұрын
Kkkkkkk achewa koma nyawu basi mukhaula munya
@CvgGgbnb
@CvgGgbnb 12 күн бұрын
Wabodza uyu bwanji osamuchula munthu ndimozi yemwe
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 12 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼💕✔️
@user-lg2ws2ki3d
@user-lg2ws2ki3d 12 күн бұрын
Koma mbuli iyi aaaa
LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA USIKU WA 2 JULY 2024
26:38
Club Junta
Рет қаралды 20 М.
Heartwarming: Stranger Saves Puppy from Hot Car #shorts
00:22
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 9 МЛН
터키아이스크림🇹🇷🍦Turkish ice cream #funny #shorts
00:26
Byungari 병아리언니
Рет қаралды 28 МЛН
Получилось у Вики?😂 #хабибка
00:14
ХАБИБ
Рет қаралды 6 МЛН
THEY WANTED TO TAKE ALL HIS GOODIES 🍫🥤🍟😂
00:17
OKUNJATA
Рет қаралды 12 МЛН
Wakatolika uyuyu Amutapa posachedwapa😂😂🤣😂😂
14:40
Malawian Cameras
Рет қаралды 56 М.
Tsatane  Tsatane wa Nkhani ya Anthu Amene Akanilirana kwa Wilisoni
17:42
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 122 М.
Funeral Ceremony for late Rt. Hon. Dr Saulos Klaus Chilima
5:24
Dr Lazarus McCarthy Chakwera
Рет қаралды 8 М.
NKHANGA ZAONA - ANTHU ANGOPHEDWA NGATI NKHUKU PA MALAWI
33:47
TIDZIWE TV
Рет қаралды 25 М.
Political Prisoners in Chakwera's Police State
11:11
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 74 М.
Nancy vs Che Nkope - Impi Biyeni Ause Muntendere
26:03
CHE NKOPE
Рет қаралды 13 М.
Heartwarming: Stranger Saves Puppy from Hot Car #shorts
00:22
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 9 МЛН