Pepani angoni, zikundinvekela ngati Biyeni wangotichokela Kaye pakati pathu akukacheza Kaye Ku dziko lina like abwelanso😭😭😭😭😭😭
@CharlieCoster-nr6on5 күн бұрын
.
@FatimaLuwembe4 күн бұрын
😅😊😊😂❤ti❤ku😊😊😊😅❤😊l😊i❤❤la
@FatimaLuwembe4 күн бұрын
A😊vice p❤😅😂resi❤de❤n😊t❤❤❤
@Byayerayera5 күн бұрын
This just proves how great SKC was. May his soul rest peacefully and may God comfort his family
@Yusufu-Daudi6 күн бұрын
Kuswa kuswa bas nthawi yonyengelera inapita
@j.colman31135 күн бұрын
Angon satha onse
@sylvesteralfred83555 күн бұрын
Zinangovuta nthawi yoti chakwera achoke pampando ndiyomweyi ino, kodi aMalawi tidzachangamuka liti let's all go Kuma Demo pa 10 pano kuchotsa Chakwera ndipo ma Demo amenewa akufunika continueos mpaka atachokapo
@leoleonard21036 күн бұрын
Apart Afumu mudapalamula ndipo imfa yanu mudzafa ngati galu wachiwewe pazomwe mudapanga pa Achilima 👌🏽☝🏽️🙏🏽
@TriciaLupoka5 күн бұрын
Ngati bodza asaulosi chilima.munatisiya mitima itasweka.mulungu achitepo kathu koma 😭😭💔💔
@FortunePhiri-kl7oe6 күн бұрын
Pa 10 pansewu bas enough is enough
@user-uc1pd1tc2x5 күн бұрын
Ndipo Fortu nkhani ndiyomweyo ❤❤
@BlessingsBanda-pr3dw5 күн бұрын
Watching from united Kingdom 🇬🇧, am pure Ngoni from Ntcheu. Viva Viva All Ngonia
@user-si7po9sd5i6 күн бұрын
We are watching from the united kingdom
@MosesNanchinga5 күн бұрын
T/A kwataine kungoying'amba Mwamba ukuchitikira pa old depot eti home is best always Proud to be Ngoni ❤
@dondamissonchdziwe39586 күн бұрын
Angoni from south Africa,osangonja,ndizi tsiru za MCP dzi achewa zakupha.Angoni Ndi Wanthu wozi sungira Ulemu Chilima wachita kuphedwa, koma adali Munthu wozi chepesa kumu manga kumunyoza koma iye wosayankhula kanthu mpakana kuphedwa Ndi Chitsiruu Chakwera mbuzi ya munthu pakana khala Kuti nkale,pakada khala chinkhondo chowopsya Ndi A Chewa komanso Angoni tonse takonzeka A Chewa asati zolowere yayi,unkhontho phambili,nkosi kwata ine
@edenngoma82145 күн бұрын
Iwe ndiwe chitsiru kwambili . Chifukwa chani ukuphatika achewa ndi MCP . Siyanitsani pakati pa Chipani ndi Achewa . Mapwala ako ndithu
@user-uc1pd1tc2x5 күн бұрын
@@edenngoma8214mesa big inuyo achewa Ndi apa central Ndipo mumakonda MCP chipani chokuphachi. Ndinkana iyetu watero coz anthu aku Lilongwe mukumaona kuti dziko likuonongeka koma mukumapopabe MCP big. Ndie sizokuti mutukwaneyi onani Malawi wanunkhiramu boss😢😢😢
@edenngoma82145 күн бұрын
@@user-uc1pd1tc2x braz koma mwayiwerenga bwinobwino statement yake walemba galu ameneyi ???? Akunyoza achewa kungokhalangati achewa onse ndi a MCP . Chitsiru ameneyi kwambili
@user-uc1pd1tc2x5 күн бұрын
@@edenngoma8214 Big pakunyoza achewa ndikulakwitsa tisalimbaneyi Ndi Ntundu komano tilimbane ndiulamuliro oipa okuba, okupha ulipowu boss. Apopo basi khululukani ingozisiyani ndithu braz
@FikiriAsani5 күн бұрын
Olira salakwa
@user-sh6gi5uq3l5 күн бұрын
Many who are encouraging us to take action on this are in the diaspora please let's be careful indeed it hurt and its difficult to bare but let's trade carefully
@user-nx7me7ds5u3 күн бұрын
While I understand the concerns about acting,,,it hurts and is difficult to bear, but caution shouldn't be an excuse for inaction,ululu wachuluka ndikusavesa
@spargomw6 күн бұрын
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Dr SKC and other 8, forever in our hearts 😭😭😭😭😭 Ambuye atonthoze Mitima ya aMalawi😭😭😭😭
Awanso muwamanga???? Zamanyazi iziii mzimu wa chilima uuse mwa ambuye
@gracemaluwa46745 күн бұрын
Mposo inu
@WisikiBlack-gj4gu6 күн бұрын
Zimu wawo unused mutendele . Koma apa chakwela anapanga chipongww
@SameKaposa6 күн бұрын
Ndipo mistake
@user-un4pm4yt5i5 күн бұрын
Ine chilima bodza inu anamulakwira kwambiri
@MonicaChirwa-l4b5 күн бұрын
Well speaking king 😎
@festonkabowa88705 күн бұрын
Angoni sife zitsiru .one day you will see. Anthu amafika potopa
@user-do2cs8nf4b5 күн бұрын
Osatopa, osafowoka, tidzafera mbendera SKC mmhh😭😭 ngati bodza ndithu may his soul rest in internal peace, and including the other souls may there soul rest in internal peace😭
@user-uv5rf4zt5q4 күн бұрын
Angoni olimba mtima inu tikulilira limoza saulosi chilima was a great leader was killed by jealous people.
@wondermsibe17086 күн бұрын
Tililimozi SKC moto ambuye ndiwachifundo SKC kufa Ngati galu akulu akulu po mwe ana Gona abwana omwe anati sithila boma mwampavu 💔💔💔💔💔😭😭😭😭
@EnetChiombaКүн бұрын
Pepani angoni amzathu zowawa izi watching from dedza tikulira limodzi😢😢
@user-sh6gi5uq3l5 күн бұрын
We need peace not igniting civil unrest otherwise who will suffer are women and children malawi need unity not tribalism say no to tribal conflict
@francissumbulero22915 күн бұрын
When peace fails use what?....
@frankjolijo5 күн бұрын
Peace cometh, where there is justice.... A grand revolution is coming ☀️🔥💪✨
@sylvesteralfred83555 күн бұрын
Ngati pakuchitika zauchitsilu zikufunika ma Demo kumene no justice no peace ✌
@user-vm6of8ox3w5 күн бұрын
Next time you must think before casting your rubbish ok?we the ngoni we will do what ever we can
Kuswa kuswa bas madala amwela mazi mwa nkhwiyo awa
@LameckLubani6 күн бұрын
Am following this all the way from SA
@IvyMadumuse6 күн бұрын
Rest well skc
@BrotherPaul-ln2ld6 күн бұрын
Angoni to the world. Yob 13:13
@AlexZanda-e5i6 күн бұрын
Polenii sana amalawi
@sukiemapemba40945 күн бұрын
Tili limodzi angoni zikhale ng'oma ,Moses mkukuyu,chimwendo,nkaka ndi chakwera akufunika zikwanje basi kuphakupha
@EmmanuelGasiten-fo5dr5 күн бұрын
Gogotu walira uyu, R. I. P BIYENI
@Macrina-vv3us5 күн бұрын
Forever in our hearts Dr SKC
@user-px1rq6sj9t6 күн бұрын
Angoni atopa
@GraceLimani-zw7dx6 күн бұрын
Ife tamva kuti ago mani agulilidwa nyumba ku 43 ndi mcp ndi azi mfumu wonse amu ntcheu analandira ndalama ma 10 mita zikomo po kumbukila mzimu wa biyeni
@user-uu6ki3nm6m5 күн бұрын
Aaaaaa asithana ndi moyo wa chilima
@eliffagondewe82146 күн бұрын
😭😭😭Ndipo nde talira amfumu 💔💔💔
@HusseinAdamLidezo5 күн бұрын
Kuyankhula kwa nzeru kwambiri kms continue working hard 💪 👌 👏
@collinschikonde52176 күн бұрын
Its really sad
@GiftSimbi-cv6kl5 күн бұрын
Uyu wadya ndalama koma aja alakhula poyamba paja ngachilungamo
Ndimakhala odandaula kwambiri ndikamaganizira za ifa ya a Chilima mpaka pano zimandivuta kukhulupilira kuti kuti mr SKC anatisiyadi ngati bodza ndinthu
@JulianaMwale-db1ge6 күн бұрын
Sitikuopa🔥🔥
@NEBERTMVULA6 күн бұрын
CHAKWERA, CHIMWENDO BANDA, KUNKUYU, MKAKA, ZIKHALE NG'OMA, CATHERINE HARA be careful Malwians are watching your footsteps! Be very very careful. MCP is ended!
@frankjolijo5 күн бұрын
❤
@PaulKachule5 күн бұрын
Forever powerful mssg from SKC in my heart, mind Osaopa, Osafooka,osatopa .more fire the Ngoni's Watching from South Africa