KWACHEMERATU KUSERIKU/ Achakwela VS Aku Blantyre 😱😱😱

  Рет қаралды 52,565

HOT 265

HOT 265

5 ай бұрын

Пікірлер: 107
@nyararaishumba9288
@nyararaishumba9288 5 ай бұрын
Ife sitikumufuna Kuno Ku ndilande chakwera wanuyo tizamupha ndthu asamale
@Wyson-bo3sp
@Wyson-bo3sp 5 ай бұрын
Kutsalemekeza msogoleli adayambitsa ndi ndi omwe akulamulilawa. Chomwe umadzala ndi chomwe umakolola. Andele muphunzilepo kanthu. Zilibe kanthu koma president ayenela adzikemekezedwa. Zidachitikadzi zidalakwika
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 11 сағат бұрын
Koma iyi nde the best discussion,,bravo Wonder and a Bishop osaiwala state Brian
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 5 ай бұрын
Ndipo Chakwera akuyenera kupeza mavuto oposa awa,, APM anapangidwa zipongwe zoposa izi,, Chomwe anabvala ndi zomwe akukolora lero,, Ndipo I think let's expect more violence between this Government of Chakwera.
@tasmania527
@tasmania527 5 ай бұрын
Musatinyase apa ndi APM wanuyo. You are glorifying APM as if he changed Malawi in his 6 yrs of power. That old man was sleeping on his job, and the only new thing he can bring into government assuming he is given the mantle of leadership, is enriching fools that have surrounded him- the likes of Chimwemwe Chipungu, Namalomba, Chaponda, Mpinganjira Junior, Chisale, and APM's wife. Ask Liberia; they are regretting electing an old man for president. Why are some Malawian minds still stuck in the past? People have really lost their minds to think APM can change malawi's economy. I think our tribalism and regionalism are making us poorer and poorer. A nation that lacks factories to produce things for export can not transform even if it changes 10 leaders in 10 yrs.
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 5 ай бұрын
@@tasmania527 I think you have a point but I want to assure you that even APM is old but he's better than Chakwera the Fake Pastor,, People are dying every day with hunger,, and the price of commodities is going up each and every day,, Chakwera is the worst President we never had before.
@emmanuelsambo1158
@emmanuelsambo1158 5 ай бұрын
The principle of sowing and reaping. APM adagendedwa ku Ndilande. Mchitidwe uwu chonde usapitilire, respect the presidency
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 5 ай бұрын
Anayambitsa wokha mcp thawi yomwe amapanga campaign 2020 now kukolola anthu a ayankhulana koma amkazitenga zopanda tchito bola mulowe mu boma lero ndizimenezi. 🔥🔥🔥
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 5 ай бұрын
Ndipo Chakwera akuyenera kuphedwa basi akangopitanso ku Blantyre
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 5 ай бұрын
Abishopu ndagwilizana nawo abusa oyamba ndi osiliza kukhala president zithele pa chakwelayu
@user-hf4xb5ij3o
@user-hf4xb5ij3o 5 ай бұрын
Apm my vote
@kestenlemucha8316
@kestenlemucha8316 Күн бұрын
Bishop-yi waybaponso kuzipangila campaign apa
@amoschataika1284
@amoschataika1284 5 ай бұрын
Big up Brothers.
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i 5 ай бұрын
Imfa isanafike pakhomo....ngakhale mphaka, amasowa😢😢😢😢...lero Ma Congo angofa mosadziwika..ntsogoleri kukuwizidwa..azimai kugwidwa ku Cocain...iiiiii.... koma 2024 ithabwino???
@homeremedys3748
@homeremedys3748 5 ай бұрын
Security yamalawi ili very weak, army comanda akuyenera kutula pansi udindo, izi zikusonyeza malawi defence is very bad, zigawenga zitha kukudilizani mukukanika anthu amaliro opanda nfuti what more zigawenga?
@user-ir4ph3mp7f
@user-ir4ph3mp7f 5 ай бұрын
Zinthu zina zimangofunuka strong power achakwera aaaaa alibe nzeru za usogoleri ife amalawi tikulira mokweza 😢😢😢
@VincentAndrew-jz2gf
@VincentAndrew-jz2gf 2 күн бұрын
Kagwireni tchito pls Fokofo
@HildatoweraMhango-et4mz
@HildatoweraMhango-et4mz 5 ай бұрын
Achakwera chonde apeweko ku ndilande zoona akudzala zomwe anakoloradi koma mulungu watembenuza flag adziwe zimenezo awa aphaso anthu achakwera chifukwa chokalandira chimanga asabwereso ku 24
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 5 ай бұрын
Vuto anthu omwe ali mbali mwawo akumva kukoma ndiye kut awauze APRESIDENT zoona zimawavuta
@OustinYusuf
@OustinYusuf 4 ай бұрын
Inu Kodi malirowo ndi apulezidenti anuwo chomwe chinali patsogolo ndichani aaaaa?????
@user-gp7wh9in3m
@user-gp7wh9in3m 5 күн бұрын
Osanye ngelera amalaw alibezeru.
@CostanceLalli
@CostanceLalli Күн бұрын
Ine chakwela akundibowa ameneyu mulungu achitepo kanthu mulungu aowonetse mphanvu zake
@jameschibwana2751
@jameschibwana2751 5 ай бұрын
Chitsanzo ku Malawi kuno cha mtsogoleri yemwe samazolowereka kuti lero kucha bwanji, kawirikawiri samafuna kunamizidwa, even omuzungulira amamuopa, anali Bingu Wa Mutharika, MHSRIP.
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Chalwera usiye kupita ku blantyre anthu sitikumufuna olo .pang,ono pomwe .....uzalandila chipongwe osakhala masewela kutsogoloku ...galu iwe munthu wokuba
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 5 ай бұрын
Here in blantyre we don't need him now ........😢😢😢we are crying now
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 5 ай бұрын
Ulemu umapita kwaozipasa ulemu
@MasautsoPatrickKalulu
@MasautsoPatrickKalulu 5 ай бұрын
Inu mkuona ngat muligo umene ummayezara mzako anthu amakuchira chimozmoz 😮
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 4 ай бұрын
Chakwera usogoleloli wake waumbava
@ChristopherTsakamile
@ChristopherTsakamile 4 ай бұрын
Uzisiya
@CrytonMalunga
@CrytonMalunga 5 ай бұрын
Mthawi ya APM mumati Brian ndi wa MCP lero muzitinso DPP ayi iye amangoima pa chilungamo
@user-vx5st6my8i
@user-vx5st6my8i 5 ай бұрын
Chakwera zamudera ngat alindinzeru awone pamenepa
@MakalaSchool
@MakalaSchool Күн бұрын
The president was not wrong but atidyenawo
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws Күн бұрын
NOT APM KOMA ENOCK CHIHANA 2025 BOMA
@JafaliAjusa-zg2xi
@JafaliAjusa-zg2xi 5 ай бұрын
Bishop mukunena zoona kwambili BG up
@user-jq5oz7cf7k
@user-jq5oz7cf7k 5 ай бұрын
Bigu amapanga zimenezo osat tym iliyose pangan chakut
@user-qq3ln3qr6x
@user-qq3ln3qr6x 4 ай бұрын
Tikuyenda ndi mikwiyo kwabasi 😂😂😂😂😂😂 asatinyasepo chakwera
@lupakishomalangaelix6606
@lupakishomalangaelix6606 5 ай бұрын
Uja amati Aide De Camp
@user-xo8ms5wh2s
@user-xo8ms5wh2s 5 ай бұрын
Timalemekeza munthu wanzeru nanga Achakwera nkulemekedwa aaa
@BarnetMwanyula
@BarnetMwanyula 4 ай бұрын
Anthu akundilande sagawa kamba awa azathera manja!? Ubwinowake anaziyambisa okha time ya muthalika
@GiftMteteka-f5e
@GiftMteteka-f5e 2 сағат бұрын
Koma yah
@user-dq9oe8sp8k
@user-dq9oe8sp8k 5 ай бұрын
Abusawo ndee ayankhula za nzeru Ndirande sinama akamfunse APM
@fraiserkapito-yb2ob
@fraiserkapito-yb2ob 5 ай бұрын
Mukanazuzulanso nthawi yomwe anam'genda Pitala ija
@marthaBisani-vm8ig
@marthaBisani-vm8ig 5 ай бұрын
Alendo 6 aku DRC amwalira anthu 6 amwalira kolandila chimanga zikutani apa? ?
@AlexMwalec
@AlexMwalec 5 ай бұрын
The good thing with democracy is that aliyense amayankhula zimene akufuna
@user-wl4nd7ic1s
@user-wl4nd7ic1s 5 ай бұрын
😂😂😂 Wamalizadd busa uyuuu
@user-wl4nd7ic1s
@user-wl4nd7ic1s 5 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥 Yanyamukaa
@user-xc2zm9bu1i
@user-xc2zm9bu1i Күн бұрын
Ife ku ntcheu kuno asadzapondeso mfiti ameneyu
@user-ir4ph3mp7f
@user-ir4ph3mp7f 5 ай бұрын
22:02
@ConfusedAtv-bs4gc
@ConfusedAtv-bs4gc 5 ай бұрын
Wina wopepela ndi nkaka Mesa Amati sizinachitike paja Mesa amakana Kuti sizinachitike paja ndiliti mumamufunsa nkanka
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 5 ай бұрын
Ndilande ikalankhula zavuta basi ili ngati ntcheu. Watenga ntcheu pa masankho wawina basi
@VincentAndrew-jz2gf
@VincentAndrew-jz2gf 2 күн бұрын
Chakwera Walakwa Chiyani
@user-hf4xb5ij3o
@user-hf4xb5ij3o 5 ай бұрын
Alibe umunthu amenewo
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 5 ай бұрын
Komatu bwanano aumva uthengawu eeeeee
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 5 ай бұрын
Kkkkkk naye bishop adalowa mu program yoti siyauzimu ulendo wa ku gahena uyu
@ChristopherTsakamile
@ChristopherTsakamile 4 ай бұрын
Chitsilu kumangonaza anthu sabuside bola bakilimuluzi analidolo
@user-je8yo3zy3y
@user-je8yo3zy3y 5 ай бұрын
Pachikhalidwe a Malawi timalemekeza Malilo A Chakwela ndi MMalawi
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 5 ай бұрын
Watizuza kwambili chakwela sitikumufunaso
@user-du8cy6uj5m
@user-du8cy6uj5m 5 ай бұрын
Atulutseni namalenga awakhululukire
@imranhabibu1743
@imranhabibu1743 5 ай бұрын
Koma nthawi ya Chakwelayu tiona zinthu
@AnnieNamalanga-bk8mj
@AnnieNamalanga-bk8mj 5 ай бұрын
Anger is disappointed love
@Phill-nh8ru
@Phill-nh8ru 5 ай бұрын
Malilo akuyenela kupasidwa ulemu osati apresident
@user-xf8xb2iq9i
@user-xf8xb2iq9i 5 ай бұрын
Zoona wakhale umaliza m,busa wasakharaso wina oramulira dziko mwanena zoona
@SteveBalakasi-qu5cn
@SteveBalakasi-qu5cn 5 ай бұрын
Intelligent Conscious (IQ) loooooh kkkkkkkkkkkkkkk
@OptimisticTrain-vt9fj
@OptimisticTrain-vt9fj 5 ай бұрын
President wamalilime ayi
@lewisdicksonmlozi130
@lewisdicksonmlozi130 5 ай бұрын
Inu andemvu zamwayi inu akulu akulu mumatha president siworakwa worako ndi athu amene amayenda ndi president
@mphatsosadiki4983
@mphatsosadiki4983 5 ай бұрын
Painful truth 😂😂😂😂
@user-gu3mp8uv3y
@user-gu3mp8uv3y 5 ай бұрын
Fertilizer mk4500 kuti mpaka lero
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 3 ай бұрын
Ndi anthu opanda experience anatenga agule okha okha
@PrecioushpZawanda-mm2xf
@PrecioushpZawanda-mm2xf 5 ай бұрын
Muzikamba chirungamo ndinu okondera sadzayenda
@user-el6kv3uj4p
@user-el6kv3uj4p 5 ай бұрын
Kkkkk Malawi
@DelightfulComputerChip-rp8gj
@DelightfulComputerChip-rp8gj 5 ай бұрын
Mukulankhula bwino kwambiri
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 10 сағат бұрын
Ndipo.asiyedi.kubwela.kuno.
@OptimisticTrain-vt9fj
@OptimisticTrain-vt9fj 5 ай бұрын
Malilime adawapweteka kwambiri
@user-fs3wc8ue8b
@user-fs3wc8ue8b 4 ай бұрын
😢😢😢😢😢😢 kape
@godfreysingini1508
@godfreysingini1508 5 ай бұрын
Kupepuka basi Kuonesa kuti panopo presdent akunyasa bola kusamala malilo
@user-gu3mp8uv3y
@user-gu3mp8uv3y 5 ай бұрын
Achoke ameyu
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 5 ай бұрын
Ndirande ikakwiya u president watha sudzawinanso
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 5 ай бұрын
Ukunamatu iwe ukuona ngt udzavota wekha
@ThabisileKanyoza-sr4fz
@ThabisileKanyoza-sr4fz 5 ай бұрын
Zovuta kumvetsa apule zikuwavuta ndithu
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 5 ай бұрын
Koma kuli zinthu yama 2 sau heeeee
@Clyne_Phiri_265
@Clyne_Phiri_265 5 ай бұрын
90% ya apolisi ku Malawi kuno ndi ma savage
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 4 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 5 ай бұрын
Umunthu alibe
@faithkamlongera5128
@faithkamlongera5128 5 ай бұрын
@Michael-yf1tq
@Michael-yf1tq 5 ай бұрын
Wafawafa
@user-wl4nd7ic1s
@user-wl4nd7ic1s 5 ай бұрын
Inde viwathu vina zopanda mzeluu
@marryphili5419
@marryphili5419 5 ай бұрын
Borani waziwa kuti amalawi sakumufuna enough is enough tatopa chilulowere muboma palibe cholozeka mavuto Okha Okha 😭😭
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 5 ай бұрын
Makosana inu mumayakhula zazeru chilungamo chanu mulungu ayelese
@ChristopherTsakamile
@ChristopherTsakamile 4 ай бұрын
Ganizani bwino achakwers
@ChristopherTsakamile
@ChristopherTsakamile 4 ай бұрын
Buzi ikakodwa amalonda alipafupi
@user-ld1js7dt3b
@user-ld1js7dt3b 5 ай бұрын
Adazala ekha mbeu yoipa muthalika adamutelonsotu mwaiwala?
@alubisabili5188
@alubisabili5188 5 ай бұрын
Wachibwana uyu
@MosesNjoloma
@MosesNjoloma 5 ай бұрын
Ghetto sitikumufuna chaimayo asamale
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 5 ай бұрын
Zathapo basi😊
@TiyaMtete
@TiyaMtete 5 ай бұрын
Vote for adad
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 22 сағат бұрын
Chakwela mutu kt buuuuu 2030
@mchipengule
@mchipengule 5 ай бұрын
Zitsilu ndi inuyo pamenepa mumakolezera zinthu zopanda pake. Kodi mulipo angati inuyo? Mwachepa inu ka. Zigwirani ntchito za office. Kodi ndinu andale a Brian Banda? Tulukani mu office. Mumalimbana ndi President bwanji?
@Yusufu-Daudi
@Yusufu-Daudi 5 ай бұрын
Silute 💪💪
@user-nm8gp1du2m
@user-nm8gp1du2m 5 ай бұрын
Chakwera kodi ndi kanyama kanji??
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 22 сағат бұрын
Opusa iwe
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 5 ай бұрын
Kkkkk akuti lebosaya kkkk malilime
@user-zn8bl9ic6x
@user-zn8bl9ic6x 5 ай бұрын
Sizidalakwike mesa APM ananyozedwaposo ndipo Nthaw imene ijayi zinari bwino kumbari ya MCP kuyiwara kut mbeu yoyipa yazaridwa lero ndi zmenez😅
@user-xs3pk1vp8i
@user-xs3pk1vp8i 5 ай бұрын
Brian ndi wa DPP
@MakalaSchool
@MakalaSchool Күн бұрын
Ndizabodza zimenezo
@hopembendela
@hopembendela 5 ай бұрын
chakwela ndi chipani cha mcp adziwe izi khoswe akakhala pa plazima saphekaaa apa ndilandeyi yamutuluka basi
@user-vz6lk1lc7s
@user-vz6lk1lc7s 5 ай бұрын
Kutchyaya kugwetsa Brian moto kuti buu
@johnkambala692
@johnkambala692 5 ай бұрын
Zinazi kumaganiza maguys kodi zoona tiziyendela za wena apa tinene zoona communication panalibe
BON KALINDO  APA NDE WALANKHULA MOTO KUTI BUU |
17:59
DZIWE TV
Рет қаралды 3,7 М.
Каха и суп
00:39
К-Media
Рет қаралды 1,9 МЛН
He sees meat everywhere 😄🥩
00:11
AngLova
Рет қаралды 11 МЛН
Always be more smart #shorts
00:32
Jin and Hattie
Рет қаралды 47 МЛН
TIKUDZIWENI - 13 AUGUST -  ABITI MANICE WILLIAM DAUDI
28:46
Times 360 Malawi
Рет қаралды 40 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 156 М.
BON KALINDO 10 JULY 2024 MWANA OOPSA PA WEDNESDAY
16:36
Malawi Trends TV
Рет қаралды 1,9 М.
Shocking News! Anthu 6 from DRC  amene anabwera ndi Chakwera amwalira.
7:04
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 28 М.
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 36 М.