KWATULUKA NKHANI YACHISISI YOMWE ILI MU KALATA

  Рет қаралды 43,089

HOT 265

HOT 265

4 ай бұрын

Пікірлер: 28
@user-cp4qt9hs8w
@user-cp4qt9hs8w 4 ай бұрын
Ndeno ndalamazo zipita kt afuna kuthila mthumba mwake chakwerayo
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 5 күн бұрын
Kkkk
@IbraheemclassickmahmoodIbrahee
@IbraheemclassickmahmoodIbrahee 4 ай бұрын
Kuchosa ndalama zimenezo potengera ndi mmene dziko lilili,palibe vuto chifukwa chonena kuti ma MP amalandila ndalama zochuluka ndi kale, zomwe zikuoneka kuti akulandila ndalama pa ntchito zomwe akugwira
@user-qe2lz7mx7u
@user-qe2lz7mx7u 4 ай бұрын
Ndichifukwa amangotukwanako akafika ku parliament osaganizilanso za wanthu chikhalilenicho akudziwa kuti ndilandilapo kawiri bingu ananena kale izi maphungu ambili Ali ndi ulesi mudera lawo chifukwa cha maalawasiwo Kodi iwowa angadwale bwanji pomwe Ali ndi ma self doctor fotseki
@EvelynL.Chisale-co8zz
@EvelynL.Chisale-co8zz 3 ай бұрын
Tilipano kukumvetselani tiona 2025
@patricgama4788
@patricgama4788 4 ай бұрын
komatu akuluakulu inu andale musamaeonengati dzikoli ndiyanu nokha ayi panopa tikufunano adzunguno abwelele adzatilamulile mwina dziyenda aguinu tatopananu kwabasi kumalawi ko ife tatopa ndalama mudzingonya nokha koma kumamidzi mumayenda ana amayi amangokhala ngati amitsala ganidzani bwina akulua akulu
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 4 ай бұрын
Very good chilima ❤
@user-mq3nw3mb1d
@user-mq3nw3mb1d 4 ай бұрын
Malawi yhaaa😂
@IbraheemclassickmahmoodIbrahee
@IbraheemclassickmahmoodIbrahee 4 ай бұрын
Company imatha kupungula ndalama kumene kwa ogwira ntchito awo if things are not oky,
@user-jo3nz3gn6m
@user-jo3nz3gn6m 4 ай бұрын
Wawa thawi izakwan
@user-jo3nz3gn6m
@user-jo3nz3gn6m 4 ай бұрын
yasala pang'ono aona
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 4 ай бұрын
Kuchema
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 4 ай бұрын
Ndichifukwa amadana naye chilima ndiopoira kwambiri .
@user-og1nx7en7j
@user-og1nx7en7j 4 ай бұрын
Following
@lenzophiri
@lenzophiri 4 ай бұрын
Akadwala munthu amapita ku chitala ndipo ndi ulere osati kugula aspirin
@JerryChain-cz8ru
@JerryChain-cz8ru 4 ай бұрын
Nkhani yabwino imeneyo
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 4 ай бұрын
Ndalama olo zitatelo mesa mcp idzingodzitapabe. Zopoyiyila
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 4 ай бұрын
Paja Ali target a mcp
@duncainjimmy
@duncainjimmy 4 ай бұрын
Zimenezi akufuna kulanga otsutsa oonse ,poti akudziwa kuti omwe alim'bomawo adzidziwa mowapasila mwake allowances awo . Komanso zimenezi zachita link mwadala ndi cholinga choti nkhani ya passport tiyiwale kae
@KambewaKenikeni-bz2se
@KambewaKenikeni-bz2se 4 ай бұрын
Watulusa report ndi chakwera ndi mcp kufuna kuipisa chilima
@lusungumsiska2293
@lusungumsiska2293 4 ай бұрын
Timva zambiri
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 4 ай бұрын
Nkhaniyo ndiyonadi ndipo zitheke kuti ndalama zizigwila ntchito zoyenela mchitukuko cha dziko,,,,, Mp akukatsegulila bridge ku dela lake ndie asainile allowance ndipo mwexi ukatha alandilenso salary. Kodi ntchito ya MP ndi yanji? Ngati ntchitoyo akukagwilila ku dziko lina apo mpomvekadi kusainila allowance koma osati adzilandila allowance chonsecho MP akugwila ntchito mdziko lake lomwe iye adasangalatsidwa kutumikila mnzika zake ndie please cancel allowance for MPs
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 4 ай бұрын
Nanunso inuu.kodi munabadwira mwa munthu koma.Kodi ndalama yo akayambe kuchita save pano aMCP atabaiba ndalama yochuluka??? Ndiye pano azikaoneka ngati ndi anzeru po saver ndalama podula ndalama ya aphungu.It will never change kuti dziko alikonze awa awononga kwakukulu
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 4 ай бұрын
@abdulrafiquekalembo469 walankhula maganizo ako ndipo ndizoonadi potengela ndi mmene MCP yaonongela chuma cha dziko koma phunxilaso kulemekeza maganizo anxako osati za mwano zakozo ! Ukati mnabadwila kwa munthu kodi? Ndi njila inaso yotani yomwe munthu adaenela kubadwila kupatula kunyeredwa ndi ku nyini?
@user-er7gm1ez3t
@user-er7gm1ez3t 3 ай бұрын
mulibho ahot 265
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 4 ай бұрын
Achita bwino
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 4 ай бұрын
Iyaaaa zopeka chabe ndikuona choncho
@sibubrightcmasulanphiri3652
@sibubrightcmasulanphiri3652 4 ай бұрын
Koma yaaaa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Malawi VP attacks president, quits ruling party
1:37
africanews
Рет қаралды 99 М.
Vivaan  Tanya once again pranked Papa 🤣😇🤣
00:10
seema lamba
Рет қаралды 33 МЛН
ОСКАР ИСПОРТИЛ ДЖОНИ ЖИЗНЬ 😢 @lenta_com
01:01
NKHANI ZALERO 9 July 2024.
23:37
HOT 265
Рет қаралды 4,6 М.
Candida Nankhumwa #AgShares
0:28
Agrilinks
Рет қаралды 37 М.
MZIMU WA (SOJA LUCIUS BANDA)UUSE MU NTENDELE
1:45:51
Jimmy
Рет қаралды 10 М.
KU NG'ALULA KWA BON KALINDO LERO PA 8 JULY 2024
16:10
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 156 М.
ABDULL..CHIPANI CHOLAMURA UK CHAULUTSA ZISANKHO
12:53
Club Junta
Рет қаралды 8 М.
Nkhani ya ku Bisesero ikumukhudza bwanji Zikhale Ng'oma
11:25
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 42 М.
Vivaan  Tanya once again pranked Papa 🤣😇🤣
00:10
seema lamba
Рет қаралды 33 МЛН