LIMPOPO FM ..usiku wapa 12 June thawi ili 9 koloko

  Рет қаралды 35,227

Club Junta

Club Junta

Ай бұрын

Пікірлер: 140
@ToothyWebb
@ToothyWebb Ай бұрын
Ine ID yanga ikangopanga expire ulendo ndingosaka kolowela. Malawi wandikanika🙌🏾
@chimwemwekamwana787
@chimwemwekamwana787 Ай бұрын
Sindizasiya kumvera limpompo... Kumvera bakili muluzi tv.. born kalindo....❤❤❤❤
@vincentgerald9172
@vincentgerald9172 Ай бұрын
Inense
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Ай бұрын
Chakwela amasankhila dala achewa maudindo aku army ndikupolisi kuti amuthandize kupha chilima, zonsezo tikuzidziwa
@DannieChimenya
@DannieChimenya Ай бұрын
Limpopo Fm 🔥🔥🔥🔥ndipo timakutsatilan kwambili pitilizan kutiwuza zoona tililimodzi
@IsaacTsinde
@IsaacTsinde Ай бұрын
Amenewa alawa kulamula komaliza...
@stelliamkupa693
@stelliamkupa693 Ай бұрын
Ing'aluleni basi
@JamesChiphwanya-tb3tq
@JamesChiphwanya-tb3tq Ай бұрын
Inetu ndikuti ndikanakhala banja la vice president sindikanalola kuti boma litengepo mbali maliro amenewa komaso Malawi zukani iyi sikhani yokhala chete
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Ndipo simukunama ndithu palibe chifukwa chokhalira chete.
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 Ай бұрын
You are right.
@ChaloseMoyenda
@ChaloseMoyenda Ай бұрын
Ndimaona ngati tisadzavoteso kungomutenga peter kumuika pampandopo basi galu ameneyu achoke basi😢😢
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Koma achilima aphedwa maliro owawa chifukwa cha mpando 😭😭😭
@ToothyWebb
@ToothyWebb Ай бұрын
Tipite ku zambia konko tikawathothole bwanji?
@MphatsoWilliam-dh5ou
@MphatsoWilliam-dh5ou Ай бұрын
Ulemu Boss mtanyiwa osaopa
@JimmyKapunza
@JimmyKapunza Ай бұрын
May you God please protect this guy of Limpopo FM
@braveglorymwanzagolah4899
@braveglorymwanzagolah4899 Ай бұрын
Kung,galula basi osaopa
@stelliamkupa693
@stelliamkupa693 Ай бұрын
Ipondeni fadah
@garnetphiri
@garnetphiri Ай бұрын
I support you Mtanyula that Chilima and others are just killed even the the speech of Nankhumwa mmene amakhazikisa chipani chake anati ,akulu akulu ena asogoleli azipani anati agwesa athana nawo ndipo sadzaima pachisankho cha 2025
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr Ай бұрын
Tinkangonva mbuyomo Kuti MCP ndichipani chakumpha Koma tazionela ndimaso
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Ayitu mcp imkapha ija ndiyakale kkkkkkk mcp yalero ndiya anyamata oganiza Booo kkkkkkkkkkk chakwela oyeeeeeee
@ManganiStanley
@ManganiStanley Ай бұрын
MCP ingothesedwa basi panyapanu a MCP
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 Ай бұрын
MCP isakatengeso mbali ku masankho
@LouisChipanda-ux9dz
@LouisChipanda-ux9dz Ай бұрын
Mcp sizasintha !!chipani Cha magazi koma dziwani kuti mwazi uwu mulangidwa ndi mulungu
@modestamhango611
@modestamhango611 Ай бұрын
Ndipo alangidwadi aputa wolakwika.
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 Ай бұрын
Mau awa a Saulos is vry heart breaking, MTSRIP 🌹😢, mulungu yekha atithangatila,dziko lathuli tizindikize mmapemphero
@stevenfrancism3638
@stevenfrancism3638 Ай бұрын
Maganizo chabe,kukanankhala kotheka zipani zonse zotsutsa zigwilane manja against mcp kuti ichoke mosavuta olo atapanga zobela ma vote
@CharlesTambala-zn2bd
@CharlesTambala-zn2bd Ай бұрын
Ndipo sukunama because MCP mmmm ikazawinanso dziko lino mtendere udzasowa
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h Ай бұрын
Osaopa osatopa osafooka ndipo sitigonja tose atimalize
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Limpopo ndi khan zina ❤❤ We're following big
@CatherineKamsare-cy3yo
@CatherineKamsare-cy3yo Ай бұрын
Ther is no peace for the wicked,RIP Chilima
@ZionekaMember
@ZionekaMember Ай бұрын
Long live Limpopo FM
@user-mv8vy3ht3n
@user-mv8vy3ht3n Ай бұрын
Limpopo l love you
@stephancommercial580
@stephancommercial580 Ай бұрын
I'm following
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z Ай бұрын
Mulungu azikutetezerani kwa Adani chifukwa dziko limadana ndianthu achilungamo ngati Inu alimpopi FM mumatinvesa kukoma kobasi
@MesiyaChazinga
@MesiyaChazinga Ай бұрын
Tikumbukile za udasi chinamuchitikila ndichani yudasi atagulisa yesu anasowa ntendele mapeto ake anadzimangilila yekha mulungu sanyozedwa
@ToothyWebb
@ToothyWebb Ай бұрын
Zikomo comrade mtanyiwa.
@IsaacTsinde
@IsaacTsinde Ай бұрын
Nkhondotu iyi
@amosbula1249
@amosbula1249 Ай бұрын
Mbendera yathu ndi imeneyi. Dead but lives on.
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
The best Radio station in central Africa
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp Ай бұрын
Athu ngati inu dziko lingayende bwino bwanji
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
Big up brother ❤❤
@TracyTomu
@TracyTomu Ай бұрын
Koma Kwa kalindo alimbetu Amasamba mankhwala chimasanduka chilombo kkkkkk
@user-mc1ig1ex4v
@user-mc1ig1ex4v Ай бұрын
The closure of Israel embassy, is the best solution for Malawi. We are at risk of loosing our identity as Malawi. Comrade Ntanyiwa, the DC and other activitis have opened all the hidden corners exposing the ruling government to have captured the state using Israel and Rwanda of course. Malawi wake up and get things done
@RobertChisenga-ci2mq
@RobertChisenga-ci2mq Ай бұрын
Thawi imeneo akulimbana ndi Peter muthalika,mau a chilima Osaziwa chakwela ndiye fisi wake adaziyamba yekha
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 Ай бұрын
Mwaona mmm dziko 🙌
@SolomonBewula
@SolomonBewula Ай бұрын
Osaopa
@PatrickMailos
@PatrickMailos Ай бұрын
Chakwera wapha chilima 😭😭😭 umboni ulipo
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Ай бұрын
Ululani big Man. Ayaluke anthu amenewa
@user-jn4wu3ii5n
@user-jn4wu3ii5n Ай бұрын
Limpopo . Go ahead. Umakwana ntanyiwa
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula Ай бұрын
Tingoyambisa nkhondo basi tatopa ndi mcp tisatile chilima
@peternashyo9850
@peternashyo9850 Ай бұрын
MCP paulendo, timaona ngati za achina Gadama zija anasiyatu, ooooh!.
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
Mmmmm MCP ndiyoipa kwambiri
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 Ай бұрын
Timakunyadilani big man
@collennyadile8179
@collennyadile8179 Ай бұрын
Peter muntharika akufuna azamuphe tikamayandikila ku mavoti cholinga anthu azasowe mtengo wogwira tiyeni tidzuke MCP ndi chipani cha magadzi
@VictorChiwaya-sb6tg
@VictorChiwaya-sb6tg Ай бұрын
Ndisaname zinthu zimenez mzoipa kwambili,, munthu akudalisen ndkukutetezerani nonse alimpopo fm
@user-zf7xk8fk5s
@user-zf7xk8fk5s Ай бұрын
Taonani lero zatigwera kumalawi end mumaiika patsogolo israel kuipang support ikamapha ma palastine ikuchit bwino lero ndi iziii
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Ай бұрын
MCP ali very happy now kuti akukhanso m boma next year, mpando wakomela akuphela nawo anzawo.
@leviecashmere7555
@leviecashmere7555 Ай бұрын
Limpopo🔥🔥🔥
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko Ай бұрын
Mcp ndiyakupha ndithu😢😢
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Koma anthu enanu muzachangamuka liti?
@alicembetewa5151
@alicembetewa5151 Ай бұрын
speechless kwathu ndikulira bas😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o Ай бұрын
Ayalusen maiko awaziwe kt ndi.akupha mwina maiko angalowelele amuchose garu qmeneu chakwera
@farooqjamus
@farooqjamus Ай бұрын
Limpopo
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
boma lolamula zigawenga ili ndi mbava zokha zokha amabisara mu ubusa mbuzi za anthu
@user-mj2te7vl6p
@user-mj2te7vl6p Ай бұрын
Mufunirani umboni wina please
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Lipopo fm 1 Anthu analakwisa kwambiri amene anavotera mcp ndipo tivutika ngati kale. Anthu ena anavutika kutichosa mukamwa mwa ng'ona 1994 koma kupupuluma ife amalawi ndikuvotereso ng'ona
@Zamwano
@Zamwano Ай бұрын
This is comred muthanyiwa on lipompo fm
@JustinLipipa
@JustinLipipa Ай бұрын
Crocodile party MCP
@user-gr2vr6yw8b
@user-gr2vr6yw8b Ай бұрын
Ndikutsatila ndithu😭😭😭
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Komato MCP akamwalila muthalika ndi DC kalindo.iiiiiii kaya malawi apa ifa achilima mwadziyika pamoto nde muphetso aaa nkhondo imeneyi chakwela iwe ndi galu nsono police adzichita kulondola anthu kuti ayankhula chiyani ndikuwona ngati ma Israel nde mulungu wanu aaa mulungu wamoyo sagongo GOD BLESS MALAWI
@StellaMike-og3wf
@StellaMike-og3wf Ай бұрын
Ife tili pano kutsatira chilungamo dziko ndilatonse ili
@EnetChiomba
@EnetChiomba Ай бұрын
😢😢😢 eee koma nkhani zake zovuta
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 Ай бұрын
Mcp sizatheka... Malawians made a huge mistake
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Pafupi ndi tower kmso mudzi anthu akuona km akuti kasakeni mu nkhalango zomvetsa chisoni kwambiri. 😢😢😢
@mlomwegomiwa1223
@mlomwegomiwa1223 Ай бұрын
Ife tizigona pompano bas
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Koma nde kundende kudzaza but we are in democratic country we are not in one party system
@user-zc4wl5pc3m
@user-zc4wl5pc3m Ай бұрын
😮😮
@marthansaliwa7732
@marthansaliwa7732 Ай бұрын
Mwazi wa Abel umulilire Kain. There should be no peace in the camp of the enemy
@user-ct9dx7mw9o
@user-ct9dx7mw9o Ай бұрын
Following
@RaphaelJordanNyirenda
@RaphaelJordanNyirenda Ай бұрын
This world
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h Ай бұрын
By public demand tiyeni a Malawi tisawope tisafooke tiyen tipange zothela amutuluse wa police ameneyo
@georgednthala-wh3pf
@georgednthala-wh3pf Ай бұрын
Mukutunyasa kwambiri anthu opanda nzeru Inu, mutirole tilire Kaye mtsogoreli wanthu mwantendere, tikaika marilo tilipo mutiuza nkhani zanuzo
@user-kj6qj1md5e
@user-kj6qj1md5e Ай бұрын
Mmmm km chakwela chakwela udzafa ifa yowawa
@samueljacksonmatickmatick8360
@samueljacksonmatickmatick8360 Ай бұрын
Koma ku malawiko 😢😢😢
@modestamhango611
@modestamhango611 Ай бұрын
😭😭😭😭😭😭😭😭
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Amalawi wake up chakwera atitha ndithu amanena zoona Kuti chikomekome chakhuyu mukati Muli Nyerere chakwera khope mawu achikoka Koma ndi fiti yotheradi shame on you chakwera
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 Ай бұрын
waboza iwe ndege yagwera pafupi ndi tower ya chikangawa malo otchedwa nkhunga not pafupi ndi mizi ayi
@ERICBISHOPJERE
@ERICBISHOPJERE Ай бұрын
It doesn't matter nawe. What matters is there were people next to what the whole thing happened. So someone should know exactly on what has happened.
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Ай бұрын
Shut up,ndiye wqpangapo chqni with your information? Ukufuna Anthony asalankhule?
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Ай бұрын
Chakwera sitikukufuna uchoke
@wypatrickdakankhoma9655
@wypatrickdakankhoma9655 Ай бұрын
Khazulani zikhale poyera chipani chakupha ichi, eish 😢😢😢😢😢😢😢
@RaphaelJordanNyirenda
@RaphaelJordanNyirenda Ай бұрын
Put it in writing and use international language
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda Ай бұрын
Agalu awa
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Komadi zovala amawavula ndindan eish
@MosesChipala
@MosesChipala Ай бұрын
Ipondeni fadah tiye nazo limpopo
@OliviaIssah
@OliviaIssah Ай бұрын
Ang'alureni bas 😂
@EvanceSungani-cv9jk
@EvanceSungani-cv9jk Ай бұрын
Ikan poyera ndthu nkhan ija ndthu😂😂😂😂😂
@user-ds3po9ub7d
@user-ds3po9ub7d Ай бұрын
🥱🥱aaa chimwene angadziwe kuti pangatalike bwanji naoso tsiku ili lidzafikilaso nawo
@user-gx3xc9lk8x
@user-gx3xc9lk8x Ай бұрын
Mcp ichoke chipan chakupha ichi
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda Ай бұрын
Mau ndlbe kwanga nkulira
@ImeedFranck
@ImeedFranck Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂kuribe wambewu padziko
@FLETCHERBANDA
@FLETCHERBANDA Ай бұрын
Crocodilians
@user-sr6hc3pv8o
@user-sr6hc3pv8o Ай бұрын
sogolo lowalalija mayooo😭😭😭😭
@lovenesskampira
@lovenesskampira Ай бұрын
Mudziyankhulaso mchizungu azungu adzimva nawo
@GiftHalord
@GiftHalord Ай бұрын
Ndendende zomwe zikuchitika
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q Ай бұрын
MCP ndiyakupha
@hardworkkayuza6353
@hardworkkayuza6353 Ай бұрын
Ndlipo inu😢😢
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
LIMPOPO FM umakwana
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp Ай бұрын
Ululani chungamo sanong,ona
@gospelselengu21-cf2lp
@gospelselengu21-cf2lp Ай бұрын
Ine ndufuna zithuzi zija zandidutsa
@marthansaliwa7732
@marthansaliwa7732 Ай бұрын
Satanism yeniyeni
@Rose-zv2ut
@Rose-zv2ut Ай бұрын
Rest in peace chilima
@user-yl5gk4od3s
@user-yl5gk4od3s Ай бұрын
Watch ilikuti nanga ling ilikuti
@user-jn4wu3ii5n
@user-jn4wu3ii5n Ай бұрын
Tingochokamo mu dziko Muno. Shaa not gud. Imfa yowawa kwambiri
Amazing weight loss transformation !! 😱😱
00:24
Tibo InShape
Рет қаралды 67 МЛН
Это реально работает?!
00:33
БРУНО
Рет қаралды 4 МЛН
ЧУТЬ НЕ УТОНУЛ #shorts
00:27
Паша Осадчий
Рет қаралды 10 МЛН
Spot The Fake Animal For $10,000
00:40
MrBeast
Рет қаралды 197 МЛН
KU MCP ZINTHU ZAVUTA NKHANI YA CONVENTION YAFIKA POSAUZANA
36:05
BON KALINDO AMAFUNA KUPHEDWA KU PARLIAMENT
38:53
TIDZIWE TV
Рет қаралды 67 М.
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Jimmy
Рет қаралды 50 М.
TAMVANI ZA IMFA YA CHILIMA IJA
10:10
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 213 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke// PART 2
27:18
MALAWI TODAY
Рет қаралды 49 М.
За девочкой гонится бандит😳
1:00
Trailer Film
Рет қаралды 3,9 МЛН
Кто из девушек быстрее печатает?
0:58
Parkour failed !
0:12
Mash_Edits
Рет қаралды 10 МЛН
THE FLOOR IS LAVA 🌋🔥! Blippi Watch Out! #blippi #shorts
0:55
Blippi - Educational Videos for Kids
Рет қаралды 22 МЛН
family is everything 🥺❤️ #shorts
0:16
Pop it GO
Рет қаралды 23 МЛН