Malemu Raisi alowa mmanda mawa ataphedwa pa ngozi ya ndege

  Рет қаралды 52,078

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Ай бұрын

Пікірлер: 277
@YusufNkubwa
@YusufNkubwa Ай бұрын
Big man ukamalankhula ngati usasiye koma mvuto mumachepetsa mphindi..anyway we proud of you may almighty Allah protect you
@dicksonhangiwa7847
@dicksonhangiwa7847 Ай бұрын
Ndimaona ngati vuto limeneli ndi ndekha, ndimangofunabe aziyankhula ,,
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Dat's true bro, amandiwelengela bwino kwambiri and he deserves to be a Journalist, osati ma Journalists enawa ukamawelenga khala ngati ali mmadzi or m'botolo , nthawiyo nde imachepadi Biggy pangani zoiwonjezela ndithu izifikira kuma 25 mnts please
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Journalist olimba mtima uyuu, big up Mr Biggy, amalawi tonsefe tili pambuyo panu kuphatikizapo tonse alliance yonse timakukondani
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Keep it up Mr BK tv, mumuphunzitsenso chawezi banda how to be a Journalist, azisiyanisa kukhala mtolankhani ndi politician, he doesn't differentiate a word between JOURNALIST and POLITICIAN
@HopefulCoralReef-tx4vx
@HopefulCoralReef-tx4vx Ай бұрын
Zoona zake man
@NicholasJames-cb7du
@NicholasJames-cb7du Ай бұрын
Mumativetsa kukoma kwambiri pitilizan watching from port Elizabeth RSA
@FelixMcDonard
@FelixMcDonard Ай бұрын
Bakili muluzi ndi number one we all love ♥️♥️ you
@user-tn5eq9fp2z
@user-tn5eq9fp2z Ай бұрын
Best tv Ever and not only in malawi but the whole world ❤❤ keep it up big man and fear nobody
@maggiekamphinda5699
@maggiekamphinda5699 Ай бұрын
Osamasewela ndi Israel
@chigokhalid9420
@chigokhalid9420 Ай бұрын
Inna Lillah wa Inna ilayih rajiuna
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Ай бұрын
Wina ndiye aziti timange bakili muluzi TV
@LongiMtimabii
@LongiMtimabii Ай бұрын
Ndipo Anya akamange kunkuyu okupha komanso mbava
@StevoZimba
@StevoZimba Ай бұрын
Kutumpa uko
@DjAmfumu
@DjAmfumu Ай бұрын
eti sichamba chimenecho nsanje basi ngati alephela osangosiya dziko bwanji, ndinanso angathe zomwe Bakili muluzi TV IKUPANGA or ku bomako ngati ali anzelu bwanji osatsegulanso channel yawo bwanji
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Ай бұрын
Chocho azit akumangen azitiwuza nkhani ngat zimenezo ndi ndan
@patrickphiri5334
@patrickphiri5334 Ай бұрын
Imagine ayi
@patrickphiri5334
@patrickphiri5334 Ай бұрын
This is the only channel I get the news yodalilika
@innocentchirombo2073
@innocentchirombo2073 Ай бұрын
Ipondeni fadah ❤❤
@JamesbhekiGama-gt5oe
@JamesbhekiGama-gt5oe Ай бұрын
We understand we enjoyed for everything what your saying and thank very much keep it up your big man
@JAMESZIMBIRI
@JAMESZIMBIRI Ай бұрын
Ineso amandisangalatsa mkuluyi
@jameschibisa1433
@jameschibisa1433 Ай бұрын
You are the best baba continue with the story we love you bakili muluzi tv for life
@user-eb7px2ex2q
@user-eb7px2ex2q Ай бұрын
Mwayankhula monveka ngt Aljazeera big up
@AjeliMw
@AjeliMw Ай бұрын
Bakili muluzi tv we proud of you ndipo zomachepetsa mphindizi zimangoona kuchitika koma mmene ndimanvela kukoma mkamanvela nkhan zanu ngat zisamathe
@user-lz4kc5ob1t
@user-lz4kc5ob1t Ай бұрын
Watching from state house malawi ulemu wanu bwana
@user-Grant260
@user-Grant260 Ай бұрын
Watching from Venezuela in Caracas 🇻🇪
@iqrapalelo1191
@iqrapalelo1191 Ай бұрын
Asala awawa.athuwa azingoti belu belu zizamuonekela
@janenkhoma6447
@janenkhoma6447 Ай бұрын
Koma nkhan nduona ngat mwatisiyila malele Mr, kipt up
@MorrisMapiri
@MorrisMapiri Ай бұрын
I like people who make their presentation based on their opinion, without any exaggeration like you.
@abdullalajabu5871
@abdullalajabu5871 Ай бұрын
mumakwala big man koma mutawonjezelako 30mis kuti izikhalako yayitali mokuphepani big
@user-fr9jh7zz1b
@user-fr9jh7zz1b Ай бұрын
Watching from cresta south Africa ineyo i respect u
@alannyirenda588
@alannyirenda588 Ай бұрын
Number one tv in the world
@VickChamasowa
@VickChamasowa Ай бұрын
Iwe Nd dolo ase....keep on updating us ..
@ireenmusende9527
@ireenmusende9527 Ай бұрын
Watching from Dubai middle East
@Josephmwangosi
@Josephmwangosi Ай бұрын
Very pathetic. May his soul rest in peace. Thanks Leader for being so informative and educating us
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 Ай бұрын
Thanks for the update on the video and the analysis
@CharliePaulelic
@CharliePaulelic Ай бұрын
I’ve been since yesterday thank you so much big boss
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj Ай бұрын
Mmakwanisa Ngozo....anthu okusani aja abwela afika dzulo komabe sangakupezeni Mulungu alinanu..ana achepa
@malvinhusted6245
@malvinhusted6245 Ай бұрын
Akufa anthu akutali mmalo moti zimuonekere chakwera kuno, ndipemphero langa day and night
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
Kuyankhula kopusa uku, usamayankhula mopusa pagulu chonchi.
@francis12fombe54
@francis12fombe54 Ай бұрын
Osati iweyo chonde ufe iweyo
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
​@@francis12fombe54 Ubulutu wake umenewu dziko silingatukuke.
@malvinhusted6245
@malvinhusted6245 Ай бұрын
@@francis12fombe54 ndife ineyo unamva kuti ndinabadwa kale?
@melmarsberg6960
@melmarsberg6960 Ай бұрын
Watching from Krugersdorp south Africa
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga Ай бұрын
Ulemu wanu brother ❤❤
@papelariareis.e.
@papelariareis.e. Ай бұрын
Great channel ever
@MBOGEZMuhammad
@MBOGEZMuhammad Ай бұрын
Inu ndi Big ❤❤❤❤❤
@butikhumaro5168
@butikhumaro5168 Ай бұрын
Am your big fan yes ofcourse but today i would like send some special respect always stay safe and strong 💪
@user-et5nz4vz2v
@user-et5nz4vz2v Ай бұрын
Respect boss Best TV ever
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i Ай бұрын
Mkammanga wa Bakili Muluzi tv ife tizanvera kwa ndani? Ameneyu si mnthu wamba ndiye amaunika zomwe zimachitika paziko lapansi. Ulemu wanu boss tiri pano ife kumvera kwa Inu zikachitika tiponyereni .the best Tv in the world not zinazi
@tisamulangala5570
@tisamulangala5570 Ай бұрын
Watching from state house Malawi 🇲🇼
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v Ай бұрын
Nde wina wazimphonongolo mphuno aziti aseka Bakili Mulauzi TV
@StevoZimba
@StevoZimba Ай бұрын
Ubupuba fye baku Malawi 🥳🥳🥳
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera Ай бұрын
Chakwera ndikunkuyu nawotso amayembekezela kuti avekonawo m'mene zakhalira moti panopa asukanawo makutu😂😂
@jamestsabola1376
@jamestsabola1376 Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂mulakhula bwanji akulu? Nanusotu mukhala mu gulu la most wanted wachiwilitu😅😅
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera Ай бұрын
A mcp zizawatengela 20 years ➕ kuti azamuziwe nyamata wa bakili muluzi ngakhaletso american imaziwazoti kumalawikuno kulimunthu m'modziyekha yomwe amaziwa kufuvuza kuposa afuvuziwo ndiyeno akunkuyuwo angozisungila ulemuokha apobi ayalusidwano mfanawake siyu
@user-lu8sv8rk7e
@user-lu8sv8rk7e Ай бұрын
Thanks for update
@samdiverson9733
@samdiverson9733 28 күн бұрын
Machine bakili mulizi tv
@StevoZimba
@StevoZimba Ай бұрын
Bakili Muluzi VT ndi number one enawa ali ngambwi ngambwi ngati chingambwe🥳🥳🥳🥳
@user-ch6pw6mf3l
@user-ch6pw6mf3l Ай бұрын
Mukukamba zoonad America imachita zinthu zonyansa kwambiri... komanso kuchokera ku mbumba ya Muhamud sikutanthauza kuti anali munthu wabwino, Muhmad anali wa khalidwe loyipa imagine kukwatira mwana wa dzaka 6😢😢😢😢 Utolankhan m'mausatad big👍
@noordeenmsamu6652
@noordeenmsamu6652 Ай бұрын
Our history major💪
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
Umakwana m'bale wathu okondedwa mwa ambuye wathu YESU khristu
@EddieBakali
@EddieBakali Ай бұрын
Best tv sukumangidwa iweyo
@ChikondiKasondo
@ChikondiKasondo Ай бұрын
Zabwino sidzinkhalitsa ndawonela pa president wa ku Iran 🇮🇷 almighty allah provides you 🙏 ❤️ Bakili tv 📺
@ShahmeerBullah
@ShahmeerBullah Ай бұрын
Allah amuike chifundo chakee
@shakilasaid705
@shakilasaid705 Ай бұрын
Watching from RSA Pietermaritzburg
@MartinMsimuko
@MartinMsimuko Ай бұрын
Big man we love you 🎉
@cephasnkhoma2301
@cephasnkhoma2301 Ай бұрын
Here in Zambia woching
@StevoZimba
@StevoZimba Ай бұрын
Same here KU chawama kuku
@cephasnkhoma2301
@cephasnkhoma2301 Ай бұрын
@@StevoZimba here Lusaka West old mubwa Rd.
@michaelkhunga3676
@michaelkhunga3676 Ай бұрын
We are behind you
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
Palibe amene wamupha nthawi yangokwana Palibe zomanamizana
@chipiliromalola6380
@chipiliromalola6380 Ай бұрын
I love this TV ❤❤❤
@SamsonMtengula-fl6yl
@SamsonMtengula-fl6yl Ай бұрын
Big up brother mumatha,zoonanadi amaziiti akuchokela kubanja lamtumiki Muhammad saw but they are lier.
@DerickBushiri2000
@DerickBushiri2000 Ай бұрын
I have been waiting for 2 days
@jaffergaffer2560
@jaffergaffer2560 Ай бұрын
Respect best TV ever
@user-ky8eq5ek1p
@user-ky8eq5ek1p Ай бұрын
Brother inuyo AllAh akupatseni mowautalindithudi Ifekwathu ndikumangayamikati Amewo apita kwawo kwatha ndatsalainendiinu Popeza chamochilinse chadzamwaliabasi
@daniedaniel8992
@daniedaniel8992 Ай бұрын
Iyi ndi AYAO TV
@issahmdala8876
@issahmdala8876 Ай бұрын
I also lo Bakili TV ndi ower wake paukadaulo wake maka kufufuza khani ndikudzieisa mtundu wa a malawi
@user-ng7re9sp1g
@user-ng7re9sp1g Ай бұрын
Watshing from durban
@user-mz4tk1pw3f
@user-mz4tk1pw3f Ай бұрын
Inna lillah Wa inna ilayih rajiuna ulem wanu big koma ndadandaura imfa imeneyi kwambiri
@JamesbhekiGama-gt5oe
@JamesbhekiGama-gt5oe Ай бұрын
Mfwentu syabonga kakhulu akuwande Tina e RSA Siti thank you
@staceycossam5933
@staceycossam5933 Ай бұрын
Kkkkkkkkk
@staceycossam5933
@staceycossam5933 Ай бұрын
Awe my bro
@staceycossam5933
@staceycossam5933 Ай бұрын
Number kkkkkkkk
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
❤❤❤❤💪💪 my best tv
@user-pt1fy3qg4u
@user-pt1fy3qg4u Ай бұрын
Never give up bro ❤
@user-to5of3ks3g
@user-to5of3ks3g Ай бұрын
Nice story bro
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba Ай бұрын
Tamatiuzani zimenezi osati Zija zomalimbana ndi boma anthu andale asakugilitseni tchito ndi anthu oipa kwambili
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
Raisi amasokoneza mtendere padziko lapansi, amathandiza magulu azigawenga, lero zinthu zadula padziko lonse chifukwa cha gulu lake la Houlthi limene lasokoneza the Red sea route. Asilamu ndi anthu osafunika padziko.
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 Ай бұрын
Ine pano pheeee kumbetsela inuyo big man ipondeni fadah ulemu wanu
@wilsonsawasawa3794
@wilsonsawasawa3794 Ай бұрын
Good narration
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Zoonadi ABWINO sakhalitsa 😢 Kusiya wathuyo kuno kuti azingotibera bas kaya ameneyu ikumuphonya pati anakapitaso naye ife tipume kumudzi kuno..
@user-dh8ml4bv4w
@user-dh8ml4bv4w Ай бұрын
Kkkkk
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z Ай бұрын
WANING TO CHAKWEL NAYESO ONE DAY ITS ONE DAY TSIKU LAKE LIKUBWEL
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr Ай бұрын
Big up fadah
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Uyuyu ndi dolo timaziwa zambiri indeed
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v Ай бұрын
And I like where you say, magazi a Mohammed
@HakimKasende
@HakimKasende Ай бұрын
Osati ataphedwa ayi,koma kuti atapanga ngozi ndiye ukati ataphedwa wamupha ndi ndani.ma report odzimangisa
@JamesbhekiGama-gt5oe
@JamesbhekiGama-gt5oe Ай бұрын
Sya cela ustshele indaba zausuku
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 Ай бұрын
Home of history I see kkķkkk
@Resterzambasa
@Resterzambasa Ай бұрын
Muli self madala osaopa pitilizani kutipasa nkhani zabwino ngati zimenezo
@KennethKilembe-ex5ro
@KennethKilembe-ex5ro Ай бұрын
Big up bro
@user-bh4zb7ji3o
@user-bh4zb7ji3o Ай бұрын
Unabwera iweo taziwa zambili kamba kaiwe
@user-sh4jz7hs3x
@user-sh4jz7hs3x Ай бұрын
Keep pushing bro...
@johnmiselo2230
@johnmiselo2230 Ай бұрын
This is what I was waiting for
@melmarsberg6960
@melmarsberg6960 Ай бұрын
Thanks big timakunyadilan kwabas 1:10
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e Ай бұрын
Iweyo anakoza umatha mpaka kudziwa zaku Iran mmmmmmm ndakumva
@user-bt3qi1gt8b
@user-bt3qi1gt8b Ай бұрын
Umatha bale agoyerekeza kugwira awona za president wa iran
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 Ай бұрын
Inna lillah wa inna ilayihhi rajiuna❤❤❤
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Ай бұрын
Yes father!! We are together!!
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg Ай бұрын
Kukuyi mapazi ako ukudana nd munthuyu iwe bwanji sunatiwuze ize
@mikekhamusi1807
@mikekhamusi1807 Ай бұрын
Bakili muluzi tv fire kuti buuuu
@AbduhHamza
@AbduhHamza Ай бұрын
Tapangani kakatali big man 😂😂😂😂😂
@LouisAndrew-jr1yj
@LouisAndrew-jr1yj Ай бұрын
Our own lovely TV ever ✌️
@user-tu8yx2on1r
@user-tu8yx2on1r Ай бұрын
Ipondeni fadda ❤🎉
@ayanlerage1989
@ayanlerage1989 Ай бұрын
Allah u nahresoto lbrahim Roohan
@daniedaniel8992
@daniedaniel8992 Ай бұрын
Kumuchemelera president wa new amwene
@HarmzahDaniel
@HarmzahDaniel Ай бұрын
Very sad 😢
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Ай бұрын
Akulu tikumva kuti akugwilani kuzela pa tik tok? Please update us
@user-qq3ip1od6i
@user-qq3ip1od6i Ай бұрын
Great job
@SildaKatundu
@SildaKatundu Ай бұрын
Palibenso jonaulist wanzeru,wakutha ngati wa Bakili Muluzi sure
@martintivalenji320
@martintivalenji320 Ай бұрын
Tiye nazo osawonetsa kugonja🔥🔥🔥🔥🔥
@kingnavitcha6243
@kingnavitcha6243 Ай бұрын
Chakwera idzi akusemhana nadzo Kuti ndikukonda kwake kuyendayenda Ku ?
@user-ik6tr1qi1e
@user-ik6tr1qi1e Ай бұрын
Matiimilira bro
@Oraterbadri
@Oraterbadri Ай бұрын
koma zot nd mbumba ya prophet muhammad achimwene nd zonama mbumba yamu hammadi ili ku saud arabia
Water cannon, arrests in Nairobi as Kenyans protest tax hikes | AFP
1:18
HOW DID HE WIN? 😱
00:33
Topper Guild
Рет қаралды 45 МЛН
路飞被小孩吓到了#海贼王#路飞
00:41
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 72 МЛН
LIVE: President Biden delivers speech to Nato summit
1:16:46
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 7 М.
NKHANI MADZULO  APA 17 JULY 2024 |
19:46
DZIWE TV
Рет қаралды 7 М.
Atikumbutsa Samora Machel wa ku Mozambique
10:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 30 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 168 М.
Karanganda TV ZIMUNYA FAMILY PART 2 MUKOTSANJERA
47:57
Karanganda Tv (Waiyepo ere ?)
Рет қаралды 21 М.
HOW DID HE WIN? 😱
00:33
Topper Guild
Рет қаралды 45 МЛН