Misonkho yakwera ndi Chakwera; Azibusa olandira ma envelope ayambapo kulankhula.

  Рет қаралды 36,150

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

15 күн бұрын

Пікірлер: 352
@BernardoHonorio-ir2io
@BernardoHonorio-ir2io 13 күн бұрын
Kanyimbo kameneka, Zikhale Ng'oma kamapweteka kwambiri. Mumaitha big!!
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 12 күн бұрын
😂😂😂😂
@petertukula1649
@petertukula1649 12 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 12 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@MovableSoundSquad
@MovableSoundSquad 11 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂Ndipo Kamamunyasa
@user-lj4rn7pl5e
@user-lj4rn7pl5e 13 күн бұрын
Ambuye chonde mutengeni chakwera ndi zikhale Ng,oma dzikoli atopa nalo
@marthablessings1314
@marthablessings1314 12 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@MisheckAselo
@MisheckAselo 13 күн бұрын
Mumatiimilira munthu wamkulu wakumva amamva, ndiponso onyozela amanyozera koma ine ndingoti big up, ❤
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 13 күн бұрын
Pomwe palankhula mnthu wankulu sipamasowa l respect you B.M tv. Ndikuziwa tikayonveraso ku Limpompo fm kkkk
@user-my4gr1pv8h
@user-my4gr1pv8h 12 күн бұрын
Pano amabelatu ambli kk
@HusseinMachemba
@HusseinMachemba 12 күн бұрын
This is Malawi we don't know what we want but God bless bakili muluzi TV
@WilliamNuludin
@WilliamNuludin 13 күн бұрын
Munasowa Bakili Muluz 😊
@giftfrank9126
@giftfrank9126 13 күн бұрын
😂😂😂
@ChimwemweStima-ht5ty
@ChimwemweStima-ht5ty 13 күн бұрын
❤❤❤ ka sound akaka anakonza ena ake kwina kwake sakugona nako turo😂😂
@PeaceNkhoma
@PeaceNkhoma 13 күн бұрын
😂😂😂😂..zoona
@LuundoJohnkabage
@LuundoJohnkabage 13 күн бұрын
Ndipo ati ka sports-tu mr zikhale😂😂
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 13 күн бұрын
Ka sound kameneko ndi diru amwene zikhale ng'oma samapuma Nako bwino kkkkk
@dartweedzmdawali5063
@dartweedzmdawali5063 12 күн бұрын
We getting a knowledge from this TV 📺 and we are proud of this BM Tv is only one that we trust
@jamesbanda5709
@jamesbanda5709 13 күн бұрын
We're here for you brother ❤️❤️❤️ much love for you never give up
@mikephiri4092
@mikephiri4092 13 күн бұрын
Akangonva ka sound ka sports amasegula mmimba , amaziwilatu kuti ijaonso waphenduka
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 13 күн бұрын
😂😂😂😂Ndipo brother 😂😂
@martintivalenji320
@martintivalenji320 13 күн бұрын
This is what I was waiting for 💃🏿💃🏿💃🏿💃🏿💃🏿💃🏿💃🏿💃🏿💃🏿
@user-yb1nt9te7f
@user-yb1nt9te7f 13 күн бұрын
👏👏👏👏👏
@user-vu4cz1mt4f
@user-vu4cz1mt4f 13 күн бұрын
Always be with bro and Mulungu azikuteteza Kwa Adan ako popeza chilungamo chimawawa Yesu adat asanamwalire ( atate mwakhululukire onsewa chifkwa zomwe andichitiraz sadziwa Kuti ndizoipa ) izi chakwera akudziwa
@anifoiuene6301
@anifoiuene6301 13 күн бұрын
Mzimu wa Chilima ndi mizimu ina yonse inali mundegemu iuse muntendere ( Ameen)
@user-dj5hd4ys3n
@user-dj5hd4ys3n 11 күн бұрын
The best tv mumakwana big timakunyadilani heave
@ayamijackson1443
@ayamijackson1443 13 күн бұрын
Just 20 minutes more than 84 comments we love you bakili muluz tv zimuwawayo aphulika
@user-hy9ge8tw3r
@user-hy9ge8tw3r 13 күн бұрын
Ndi boma la dzinyawu limeli uncle 😂😂😊respect my brother osawopa
@sheila5812
@sheila5812 13 күн бұрын
Koma President wativuta uyu hmmm😢
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 13 күн бұрын
More 🔥 osawanyengelela big. We salute you from Mozambique.
@MandalaChaona
@MandalaChaona 13 күн бұрын
Never give Up Mchimwene. Akuyenera kuuzidwa anthu Adyera amenewa osaganizira za Mavuto a anthu mdziko
@stevenchirwa5028
@stevenchirwa5028 13 күн бұрын
Keep it up My TV for life
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 12 күн бұрын
Best KZfaq channel here 🇲🇼
@JahmeilKIbrahimu
@JahmeilKIbrahimu 12 күн бұрын
Much appreciated bro continue to update us
@dontreybanda278
@dontreybanda278 13 күн бұрын
Good massage boss
@samdiverson9733
@samdiverson9733 13 күн бұрын
Much respect to bakili mulizi tv
@Pangolinimw
@Pangolinimw 13 күн бұрын
My best tv 🎉 chakwela ndi galu kobasi
@CatherineDesire
@CatherineDesire 12 күн бұрын
Mayo ineeee🤔palibedi chabwino pa dziko lapansi eish ndrama inagulitsadi Yesu,adzibusa !!!aiso ndithu palibe olungama padziko
@hopesato
@hopesato 10 күн бұрын
I love Bakili Muluzi tv
@MosesKalenge
@MosesKalenge 7 күн бұрын
Good news mr big up🎉🎉🎉
@user-wx7pw8xg6x
@user-wx7pw8xg6x 13 күн бұрын
Keep updating the nation
@petermanMitambo
@petermanMitambo 12 күн бұрын
History is the best teacher long live BMTV ♥️
@CharlesTambala-zn2bd
@CharlesTambala-zn2bd 13 күн бұрын
May God bless and protect you.
@user-dd1qq5xq1k
@user-dd1qq5xq1k 12 күн бұрын
Bakili Muluzi TV, Umatiimilira.❤❤
@SimonChirombo
@SimonChirombo 13 күн бұрын
$😂😂😂😂😂😂Malawi chikangawa party😂😂😂😂 yah intelligence at it's best
@Dinalamakanjira
@Dinalamakanjira 13 күн бұрын
Ulemu wanu big brother
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 13 күн бұрын
Pantumbo pake chakwera ndi azibusa omwewo ndithu 😢
@user-sy8oq1sf1r
@user-sy8oq1sf1r 12 күн бұрын
You are a general brother
@user-ne7rn4ki3c
@user-ne7rn4ki3c 13 күн бұрын
Best and only TV ever
@PatrickMailos
@PatrickMailos 13 күн бұрын
My best TV never leave you alone ❤
@user-yv3jp3it2t
@user-yv3jp3it2t 12 күн бұрын
Ine chakwela sindimadana naye but zomwe akuchita ndi cabinet yake akupangitsa kuti amalawi ochuluka azivutika wina aliyese yemwe Ali Mmalawi dzikoli agogo ake anatungila madzi so dziko la athu ochuluka asangalala azikhala ochepa cabinet iyi ndi ya athu oputsa okha okha koma mulungu atimenyela khondo and we win it
@Moses51
@Moses51 13 күн бұрын
Best TV in Malawi keep up update 💪💪🇲🇼🇲🇼
@AbuMussah-wi7gb
@AbuMussah-wi7gb 13 күн бұрын
You arevery true man.100%
@MacmillanMakombe-sz4iy
@MacmillanMakombe-sz4iy 13 күн бұрын
Best TV Tithana nawo soon
@LameckLubani
@LameckLubani 13 күн бұрын
Keep it up the good work bro
@YONA-v5o
@YONA-v5o 13 күн бұрын
My best tv 👍🔥🔥🔥
@LamieTiger
@LamieTiger 13 күн бұрын
Mawu omvekabwino boss chakwera ndi athuake onse mituyawo simagwira ngat simitsala ndekut alipo mu mcp amene alindizithumwa zot chakwera azionangat ziko likuyenda bho iwo akusolora dola kwinaku
@DennesAaron-q4p
@DennesAaron-q4p 12 күн бұрын
Malawi we was loose our target 2020 until now so we'll see more than wht we see, respect Big
@malikoezala
@malikoezala 13 күн бұрын
Chakwera anakoza enanu mukuva kuwawa kwabiri ❤❤❤❤❤❤❤
@Moseskhutse
@Moseskhutse 12 күн бұрын
Mbuzi za azibusa pamodzi ndi mbuzi yanu chakwera chikangawa chinyau moyenda president oputsa kwabansi
@KhalideNerve-mu1eq
@KhalideNerve-mu1eq 13 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ watching from South Africa
@AchinaKellz
@AchinaKellz 13 күн бұрын
Olo kumwera ndi kumpoto titapanda ku voter olo pakati sangawine😂zosekesa kaya kampeni aziti chani😂
@powercharios2087
@powercharios2087 12 күн бұрын
Chakwera is one of useless president nonsense president, Thank you bro you always give us true story
@tisamulangala5570
@tisamulangala5570 13 күн бұрын
Watching from state house Malawi 🇲🇼
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 13 күн бұрын
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏 Ndipo Malawi chikangawa party yatikwna
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 13 күн бұрын
Keep it up brother and we ❤❤❤❤
@osmankachepamangame4965
@osmankachepamangame4965 11 күн бұрын
Mmmm Malawi wavuta kwambili ndithu
@AdamMwanza-rf6pd
@AdamMwanza-rf6pd 13 күн бұрын
Mudzikhudzakoso ku Zambia wez
@JamesKumphanje
@JamesKumphanje 12 күн бұрын
Ndimakonda kuvera bakili muluzi tv
@EmmanuelMoyo-hy5ni
@EmmanuelMoyo-hy5ni 13 күн бұрын
Praise team umatiyimilira
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 13 күн бұрын
Tv mbambande 🔥 keep it up
@PeterMasangano
@PeterMasangano 12 күн бұрын
We know more about this TV respect
@user-mz4tk1pw3f
@user-mz4tk1pw3f 13 күн бұрын
Ulemu wanu big ❤❤❤ anthu amenewa alibe manyazi
@VinsentMwapabwe
@VinsentMwapabwe 12 күн бұрын
Yes azuzulidwe chakwera chifukwa awononga ziko
@mikemakamo7360
@mikemakamo7360 13 күн бұрын
Chakwela achoke palibe chomwe wapangapo mavuto akupita chisogolo 😢 pasipoti ndi feteleza kuliziiiii uyundigalu
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 13 күн бұрын
Fertiliser umalima iwe kod mesa ukudikira Lilongwe kt ikupatseni chakudya ulendo uno titseka pa dedza kusapiteso chimanga tione azuzike ndi ndani
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 13 күн бұрын
Am still sad kupita kwa chilima 😢😢😢😢
@user-nr1xo1nw3z
@user-nr1xo1nw3z 13 күн бұрын
Aaaaa 😭😭😭😭😭💔💔😭😭 midzimu yao idziusa muntendere mwina ndidzakhala kulibe ndaneneratu Andikwana heavy 🪨😅
@user-px1rq6sj9t
@user-px1rq6sj9t 8 күн бұрын
Mbava za MCP zimenezi. Auzeni inu a Bakili Muluzi Tv. Ana achepa 🤱
@charlesnota
@charlesnota 13 күн бұрын
😂😂 Malawi chikangawa party....koma zoonadi
@UsherWilliam
@UsherWilliam 13 күн бұрын
😢 koma dziko lathuli ashi boss just come with solution amalawitu tilipo gulu we can change malawi for better place again to live
@jameschibisa1433
@jameschibisa1433 12 күн бұрын
Bakili muluzi tv will never end the best ever
@AishaKatunga
@AishaKatunga 13 күн бұрын
Zikhale ng'oma samamva lelo ndamuonaso Ali pa 4n kumaliro 😂😂😂😂😂
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 13 күн бұрын
We are waiting to hear from you chief Lucian banda anaferanji
@user-gt6gd1er6s
@user-gt6gd1er6s 10 күн бұрын
Komatu gayez munthu amayakhula zoona zokhazoka tiyeni timuchose chakwera chifukwa dziko tikapanda kusamala tonse tikhala wosauka paka kale kale ok
@JafarAustin-zj6rj
@JafarAustin-zj6rj 13 күн бұрын
Yaah Malawi chikangawa party 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 12 күн бұрын
Azibusa awo ndi anthu opusa ngat alandira ndalama nanga ndalamazo anthu onse akumadya nao anthu amulungu adyera asiya kumutunikira mulungu ntchito ndi kuba
@juliusidaho3262
@juliusidaho3262 13 күн бұрын
Salute ❤
@user-sh4jz7hs3x
@user-sh4jz7hs3x 13 күн бұрын
Keep pushing bro...
@rashidlamos3403
@rashidlamos3403 11 күн бұрын
Zikomo kwambili brother for news
@Littlefair7
@Littlefair7 13 күн бұрын
Kumalawi sikunakhale la makhuluku ngati ili, akudziwa kuwatseka anthu pakamwa ndi makobidi😂😂😂
@yamikanichirwa9787
@yamikanichirwa9787 13 күн бұрын
Big man salute
@yankholemucha4138
@yankholemucha4138 12 күн бұрын
tiyen mademo
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 12 күн бұрын
Komasotu azibusa mulungu adzakulangani kwambili inu mukumalandila ndrama za magazi nose mulandile chilango pamozi ndi chakwela wanu yo ndithu
@GIFTMkandawire-nz9ke
@GIFTMkandawire-nz9ke 13 күн бұрын
lets as wait and see
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 13 күн бұрын
😂😂😂 Malawi chikangawa police 🙌🙌
@MikeEdwardChitopa
@MikeEdwardChitopa 12 күн бұрын
Your my lovely brother ❤❤❤
@JamesKhudze
@JamesKhudze 13 күн бұрын
❤❤❤ best television
@CharliePaulelic
@CharliePaulelic 13 күн бұрын
First watching first comment 💪🏻
@AlexOsman-pi4tv
@AlexOsman-pi4tv 13 күн бұрын
Auzeni ndipo aziwe zoona zenizen azibusa opusawo 😊
@MikeMerecah
@MikeMerecah 12 күн бұрын
Keep it up bro 🎉🎉🎉🎉❤
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 13 күн бұрын
chakwera ndi chigawenga pamtumbo pa make chitsiru boma la zigawenga zokha zokha
@patricktembo1160
@patricktembo1160 13 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@chitchohistorical1036
@chitchohistorical1036 13 күн бұрын
Big man mutipangire video ya ku Israel ndi Lebanon tikufuna tidziwe kuti zikutha bwanj mbali yakumeneko
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v 12 күн бұрын
Chilungamo chake chakwera ndi muthu osadziwa chimene akupanga bola azikakumba Manda akakhala ndi dzeru
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v 13 күн бұрын
Blessed is your mother who bore you Bakili Muluzi TV Keep up
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e 13 күн бұрын
Kulibe azibusa kumalawi km kuli atsogoleli andale mipingo ose kumoto km but fire is under pasipompano azalangidwa zd akunamizila ubusa ali mikango church
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 13 күн бұрын
Mwayamba kukangana ndi anthu amulungu owoooooo
@CosimassShyman
@CosimassShyman 13 күн бұрын
Bakili muluzi imeneyi idabwera kuzakhala kuziko pofuna kudzudzura kuulura ndi kuonetsa ziko dyera la ma ulamuluro wamakonowu
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 13 күн бұрын
We are always following sir 🙏
@FelixKachera-je4yk
@FelixKachera-je4yk 13 күн бұрын
tikapuma kumwamba basi
@FelixKachera-je4yk
@FelixKachera-je4yk 13 күн бұрын
tikapuma kumwamba basi
@BamusLucky
@BamusLucky 12 күн бұрын
😢😢😢 abale malawi yafika pamoto
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe 13 күн бұрын
Big nde mwati Malawi chikangawa party
@SameKaposa
@SameKaposa 13 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 Ndimaona ngati ndamva ndekha
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 13 күн бұрын
Nziko lanthu likusokenekela chifukwa chazi Busa Kut ziko sili kuyenda bwino Iwo akuyikila Boma kumbuyo anthu akayankhula ndikumatiopya
@MosesKalenge
@MosesKalenge 7 күн бұрын
TV NICE ONE 📺
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q 13 күн бұрын
❤❤❤❤timakunyadila man kwambiri
@user-Grant260
@user-Grant260 13 күн бұрын
Much respect elder ❤❤always you stand for us
Can the Conservative party survive defeat? | FT Film
25:04
Financial Times
Рет қаралды 108 М.
Does size matter? BEACH EDITION
00:32
Mini Katana
Рет қаралды 18 МЛН
ТАМАЕВ УНИЧТОЖИЛ CLS ВЕНГАЛБИ! Конфликт с Ахмедом?!
25:37
DO YOU HAVE FRIENDS LIKE THIS?
00:17
dednahype
Рет қаралды 105 МЛН
Atikumbutsa Samora Machel wa ku Mozambique
10:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 30 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 22 М.
Gotani Hara ali pa chikondi ndi Nankhumwa chifukwa chani?
8:31
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 61 М.
KAMLEPO KALUA KUYANKHULA MOSANYENGELERA
29:23
HOT 265
Рет қаралды 40 М.
Chakwera wayamba nkhondo yolimbana ndi social media
7:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 79 М.
M'busa Yasin kularika mwa mphavu pa maso pa Chakwera ndi anthu onse
9:54
Does size matter? BEACH EDITION
00:32
Mini Katana
Рет қаралды 18 МЛН