Mumanga Anthu Angati? - Samuel Lwara

  Рет қаралды 8,964

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

2 ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara asks how many social media commentators the Malawi Government will arrest. He is saying this after Honorable Minister of Information Moses Kumkuyu said they are after the administrators of the KZfaq channel Bakili Muluzi TV.
Pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara afunsa kuti Boma la Malawi limanga anthu angati pa social media. Akunena izi nduna yolemekezeka Moses Kumkuyu atanena kuti akutsata ma administrator a kanema wa KZfaq Bakili Muluzi TV.

Пікірлер: 73
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Yes we enjoy with bakili muluzi t v
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 2 ай бұрын
Nice talk munthu amene uja sakulakwisa
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 2 ай бұрын
Bakili muluzi channel always for the truth even not only malawi histories we listen from other countries stories y don't blame him too so y only chakwela government this government must be evil guys sitingapempheze mafano just because u are in power
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 2 ай бұрын
Awuzen kut iwo si Mulungu.Anthu anakana kalero kupembedza Farawo amene samapita Ku toilet mpaka amazitcha kut ndi Mulungu
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 2 ай бұрын
Bakili muluzi TV KZfaq channel Never get arrested here we love this channel 🇲🇼🇲🇼🇲🇼✊️✊️✊️✊️✊️✊️
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 2 ай бұрын
Very good...Mulungu Ali pamodz ndi anthu olankhula zoona ..olemekeza Iye ngkhale sakumuona .Palibe chimene mtolankhaniyu amalakwitsa .Amalankhula chilungamo ndipo Ife amalawi eni ndimboni chifukwa zikuchitikadi
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Malawi aliyense okhala kunoko sangadzunguzidweyi ndi munthu aliyense waku Malawi, kuno ndi dziko loopsa tizatchuta ndimifuti anthu akewo abwelera mitembo yokhayokha wait n c ndipo ife tonse kunoko sitilora imeneyo ndi nkhondo
@user-qu9iu7hs8k
@user-qu9iu7hs8k 2 ай бұрын
I agree Malawi muphesa ma saidi kuno kur mifuti atha kuphedwa tyen nazo
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 ай бұрын
A CID Amenewo Aombeledwa Ku South Africa kuno, Kuno Sikumalawi
@ANTHONY-cq3up
@ANTHONY-cq3up 2 ай бұрын
True the guy is very genius and we like him.. Kunkuyu ndi mbuzi ya munthu
@JoyMphika
@JoyMphika 2 ай бұрын
Akungofuna kuphetsa ana aeni ake
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 2 ай бұрын
Powerful message and well spoken my brother.
@user-ev4or2kg4z
@user-ev4or2kg4z 2 ай бұрын
Bakili Muluzi TV ndiyabwino kwambiri please andinu zigqirani ntchito zina olo fasani kupanga Kaplan obera
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Ku South Africa aphetsa onsewo ayerekeze sakudziwayi south Africa amenewo
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 2 ай бұрын
ine kupanda Bakili muluzi channel sindingakwanitse🤣🤣🤣🤣
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 2 ай бұрын
Bakili Muluzi tv journalist is the best journalist in malawi please don't arrest him guys,,what wrong has he done for that.
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c 2 ай бұрын
Very much appreciate nice one
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 2 ай бұрын
Good message Bakili Tv is good
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 2 ай бұрын
You have spoken well bro, tell them
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Apita ku holiday amenewo sangamupeze BKtv.
@MajotiMpandasoni
@MajotiMpandasoni 2 ай бұрын
Ayambe kumanga ntambo iwowonso analowa mboma kamba ka mademo anapha anthu anawononga katundu mabusines awanthu mamilion awanthu kupha wapolice apolice kugwililidwa lero mukukana kuzuzulidwa zoona??
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 ай бұрын
Amene akuwatumizawo adziwika ndipo kukhala kusakana wina pa mdima wina powala awine ndani asamale kwambiri Jones simaseka
@MosesWitness
@MosesWitness 2 ай бұрын
Muwabwelese tiwaponye mumigodi yakale
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 2 ай бұрын
A kukuyu aphesa anthu a ena ake sakuiziwa south Africa funso mkumati muzikamusaka pati munthuyo? waste of resources mulekeni munthu ife we love him and he is protected by the blood of Jesus
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 2 ай бұрын
Dziko lomvesa chison
@adamkudzala186
@adamkudzala186 2 ай бұрын
Bakili muluzi tv is the best
@amiduclement2142
@amiduclement2142 2 ай бұрын
Kukhuyu sanapuzire
@user-po6ir6eh4z
@user-po6ir6eh4z 2 ай бұрын
Samukwanisa ngat akumulephera Bon kalindo
@dytonmoyo4629
@dytonmoyo4629 2 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥
@jennyx6914
@jennyx6914 2 ай бұрын
nzomvetsa chisoni kunkuyu ithink magazi awiltika akumuzunguza mutu serious here in RSA chili chonse chimachitika chimene ukufuna ndiye ngati bakili tv akufuna amugwira kufuna kwake koma its not easy ngati ulube mfuti kuno R200 yeni yeni umagula anthu opha anthu so idont know bt may Hid protect bakili guy he is he atrue guy
@morgansilungwe
@morgansilungwe 2 ай бұрын
its not bakili muluzi tv but bakili tv dont mix the two.bakili ndi dzina la wina aliyense ..
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 ай бұрын
Awuuzen akuona ngat kuno south Africa kosewera afako kumeneko Ndipo bakili muluzi TV samukwanisa
@amiduclement2142
@amiduclement2142 2 ай бұрын
Tayesani kutumiza joz athuo tawaonese
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 2 ай бұрын
Kodi mesa naye ali ndi mulandu wakupha alani wititika athu anu ndi aja akukhapa athu koma bwanji osawamanga
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Well spoken💔💔
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 2 ай бұрын
We love BM TV
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 2 ай бұрын
mzimu wa witika ukumudzunza ameneyo
@user-yu4np2wq4s
@user-yu4np2wq4s 2 ай бұрын
Ndipo Kuno athu samawelenga Moyo wamuthu amaopa kupha zinyama ndani amenewo akhutawo abwele aziona mukamangovomela Zina zilinzonse chifukwa chandalama muzipwetekesa Ngati mwakhuta bwelani
@user-hm1ys8vd4i
@user-hm1ys8vd4i 2 ай бұрын
Mwauuze ngati amaukonda moyo asabwele kuno sikumalawi ayi
@EuniceLipenga
@EuniceLipenga 2 ай бұрын
Ulumu wanu munthu wamkuluyu amenewo mawu ngati aliakumva amve
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Abwere ndipo agwilira patipo ma said awowo azimve kunukha magazi ndipo afaaa muphesa anthu inu
@user-ld1js7dt3b
@user-ld1js7dt3b 2 ай бұрын
Ndiposangamupeze
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 2 ай бұрын
Chili chonse chili ndi mathelo tiziona tizimva
@user-ib7ig3xd2h
@user-ib7ig3xd2h 2 ай бұрын
Apatu mwalankhula zanzeru atsibwen
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 2 ай бұрын
Mposo Kunkuyu waganiza bwanji kutumiza ma detective ku dziko Loopya ngati ili?
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Aaaa koma MCP ulamulilo wachikale dzedi malo molimbana ndimamvuto anthu kumawononga ndalama akasake anthu ku south Africa bakili maluzi tv ndumunthu emwe amanena chilungamo kwa amalawi nde mukufuna ulamulilo wachipani chimodzi uja tinaukana kale kale uchisilu wa MCP nde umenewo amagadzi manja
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Chalwera sakuziwa chimene akupanga ....kuononga misonkho ya anthu chifukwa chosaka munthu ... .kunkuyunso ndiye chisilu cha munthu .....tikuonelani ili ndi ziko ....anthutu akuvutika mmalawi muno ndipo anthu mukuwasakawo akunena zoona.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
A kunkuyu asowa zochita, ndipo Ruwala akuneba chilungamo chokha chokha
@partmaulidiPatrick
@partmaulidiPatrick 2 ай бұрын
nkani ndiyoona kunodi kulianthu athuro
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 2 ай бұрын
Ife Kuno ku keep town tikuti atume athu awo tiwone Ngati abwelele ndi Moyo Ngati mumangova E k 47 tili nazo Kuno tikupan nose
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 2 ай бұрын
Kunkuyu adapha Witika bwanji sakumangidwa machende amako Kunkuyu pamodzi ndi Chakwera wakoyo
@AndrewBwanali
@AndrewBwanali 2 ай бұрын
R10 is much
@user-po6ir6eh4z
@user-po6ir6eh4z 2 ай бұрын
Kudana ndi chilungamo mcp paja ntchito yao ndi nkhaza ndi kupha anthu
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Kumkuyu wamba zomwe ayakhula mr ngati uli mdi mutu ndi nzeru wadzimbera wekha
@KereeditseMotsetse
@KereeditseMotsetse Ай бұрын
Machendache kukuyuyo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Kumkuyu ndi chisiru ndipo alibe nzeru ndi ndzukwa palibe comwe amadziwa
@ManganiStanley
@ManganiStanley 2 ай бұрын
anthu opusa awa
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Iwowoso akhala akusakidwa
@OweniMalokooweni
@OweniMalokooweni 2 ай бұрын
That man is staying America not South Africa
@chimwemwecrispo200
@chimwemwecrispo200 2 ай бұрын
Masi ID amenewo kuno tiwapha khalan pheeee muva
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Mizimu ya anthu ikuzunzika chifukwa cha boma limeneli koma dziwani kuti Mulungu akuwona la 40 limakwana
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d 2 ай бұрын
Abwere agalu ameno tipha konkuno mkukuyu chakwela pamtumbo panu
@RobertDJambo
@RobertDJambo 2 ай бұрын
What nonses CID kukamusaka muthu oti sakukudzwa kumenevali kkkkk
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 2 ай бұрын
Matipate yantha ku Malawi chifukwa Cha MCP Chakwera
@JamesMalango
@JamesMalango 2 ай бұрын
Boma lomvesa chisoni Kwabas mbuli zophunzira
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 2 ай бұрын
Boma lathu
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 ай бұрын
A kunkuyu futi yawo inapha munthu bwanji sakumangidwa ndiye akamange munthu ongoyankhula nawonso dzenje umakumbilamo zako nawe so udzagwelamo wokha asiyeni amagwidwa pompano atayeni
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Adapha witika bwanji iye samangidwa mkukuyuyo? Utsigoleri wawo wa mcp wokupha,wokuba ,wakhaza. Amangidwapo angat akukhalira kukhululukira anthu okuba ma billion pomwe okuba chimanga ndinjala akudzuzika kundende , ineyo utsogoleri wa chakwera sikusiyanisat ndi wa mfumu nebukatineza dzanja lalemba pakhoma kasalako alotesedwa ndipo boni kalindo azapepha kuti atathauzire maloto awo owopsawo ,chifukwa akuzikwezat afikapo pomwera zikho zayehova tikuonetani
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 2 ай бұрын
Nenani chilungamo musakidwa nkuphedwa
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d 2 ай бұрын
Mkukuyu anapha munthu paja Galuamangdwa 2025
@mkhokholasamuzonda5094
@mkhokholasamuzonda5094 2 ай бұрын
KUNKUYU panyini pa make
@spargomw
@spargomw 2 ай бұрын
Chitsiru cha munthu Kunkuyu, Waiwala milandu yake yopha Witika, Kumkuyu amfa imfa yowawa kwambiri coz nkhani ya Witika yaululika kut adamupha nd iyeyo
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 9 МЛН
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Piksy TV
Рет қаралды 158 М.
One moment can change your life ✨🔄
00:32
A4
Рет қаралды 33 МЛН
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН
Ndine Gardener Ku Statehouse - Samuel Lwara
4:22
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 10 М.
Moses Kumkuyu Is Useless - Samuel Lwara
6:44
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 3,8 М.
Donald Trump speaks at the RNC: FULL SPEECH
1:32:24
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 3,4 МЛН
A Kalindo Musalimbikitse Umphawi - Shaffie Hassan
18:36
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,6 М.
Angofuna Kukudyela
10:54
Caswel Mkanda
Рет қаралды 3 М.