No video

Mzibambo wina kuMangochi AKUKODZA USIPA chifukwa chogona ndi akazi amwini, Nkhani za m Malawi

  Рет қаралды 24,348

Malawi Page

Malawi Page

Күн бұрын

SUBSCRIBE here for more videos goo.gl/aYvIXK
Malawi videos in English and Chichewa

Пікірлер: 49
@isaacbandah3617
@isaacbandah3617 3 жыл бұрын
Irene moyo, nkhani zinazi uzibwelesa ndi la vidio kake kuti tizikukhulupilira sono ndikuwona ngati wayamba kupeka nkhani page yakoyi timayikonda komano wayamba maboza uzikhala src pa nkhani zako 👏👏
@duwasemoyo8984
@duwasemoyo8984 3 жыл бұрын
Ok no problem
@preciouspanjinga4525
@preciouspanjinga4525 3 жыл бұрын
Muli ndi boza aunt mumangomatula nkhani zapa fb kubwera naxo pano nkhani ya ayaya unaifotokoza ngati unapita kukaona matenda awo,chepesani boza
@kondwanidette6532
@kondwanidette6532 3 жыл бұрын
Mabodza ifee aiiii mwachuluka kunena zabodza Never trust you again Musiye program imeneo
@duwasemoyo8984
@duwasemoyo8984 3 жыл бұрын
Sibhodza abro
@LukaThawe
@LukaThawe 4 ай бұрын
Zaboza izi Iya
@frezarphiri5223
@frezarphiri5223 2 жыл бұрын
Hahaha 😂😂 apo ndizabwino akazi amafuna kusilika
@IgnancioKachimanga
@IgnancioKachimanga 14 күн бұрын
Eeeee koma apa ndiye 😢😢😢😢😢
@WizeyManyozo
@WizeyManyozo 15 күн бұрын
Aaaa tiziona bwanji kt. Ndosilika mm nkhan ya zavu zimaveka kt. Mzonama aa mangofotokoza n nokha km zinthuzo simaonesa atolankhaniw. Alikut aaa komaso kufotokoza nkhan kumakuvutan inu aaaa
@Dickson-iz6mz
@Dickson-iz6mz 4 ай бұрын
Keep it up
@MphatsoMatchaya
@MphatsoMatchaya 3 күн бұрын
Zaboza izi video ili ku
@IreneEmmanuel-uv8vm
@IreneEmmanuel-uv8vm 4 ай бұрын
@samalanimacdonald9373
@samalanimacdonald9373 3 жыл бұрын
Kkkk usipa zimachitika koma sjngadziwe kuti nkazi ndi otsilika Kaya, koma waine ndinatsilika kalaso watsoka ndi yemwe adzafusile nkaz wanga maliseche ake adzasanduka bwanzinganga
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 10 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 Irene
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf 5 ай бұрын
Iwe nawenso munthu angadziwike kuti ngosilika akazi nayenso samadziwa kuti wasilikidwa aaaaa
@CharlesFCNkhata-ir8jk
@CharlesFCNkhata-ir8jk 5 ай бұрын
Isaac and I jacob
@justinedamson8862
@justinedamson8862 Жыл бұрын
Kkkkkkkkkk km iwe zinazi zaboza ndithu
@YohaneAntonioBarjoane
@YohaneAntonioBarjoane Жыл бұрын
osipa womwewu WA somba??? malawi wanyanya.
@johanalberts8339
@johanalberts8339 3 жыл бұрын
Tafufuzani kae anthu munatenthetsa za yaya olo mudzipanga ka video mwina we can believe olo anakakodza Chambo
@MphatsoMakowa
@MphatsoMakowa 4 ай бұрын
Ndagi gize
@thokobeula8576
@thokobeula8576 3 жыл бұрын
Umanama iwe,unatinamiza zakwa ayaya....choka apa
@duwasemoyo8984
@duwasemoyo8984 3 жыл бұрын
Kkkkk sinaname koma it was what ma media monse amanena thats why natumiza mene anakachezera nawo amayiwo
@chifunilopatrick3846
@chifunilopatrick3846 3 жыл бұрын
Apo e moto 🔥 tsikana ameneyi boza lakula
@danieljulius2522
@danieljulius2522 Жыл бұрын
Oho mavutotu 😂😂
@GreciphiriGaute
@GreciphiriGaute Ай бұрын
EEE zoopsa bwanji
@user-hj3xl2uk9z
@user-hj3xl2uk9z 8 ай бұрын
Sorry
@brendachigodo1946
@brendachigodo1946 3 жыл бұрын
Ireen unaliko kuphoka kkkkkkk koma pola moto kufotokoza ngati unkayendera limodzitu
@user-qp5uy5hh1f
@user-qp5uy5hh1f 8 ай бұрын
Zovuta izo
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 4 ай бұрын
Tiwonetseni anthuwo tiwaone kuti tikhulupilire
@CharlesFCNkhata-ir8jk
@CharlesFCNkhata-ir8jk 5 ай бұрын
Driemo
@moyowrobert3331
@moyowrobert3331 3 жыл бұрын
Mmmmmmmmm koma zinazi ayi asov
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v 17 күн бұрын
Mistake
@ruthtimothy9583
@ruthtimothy9583 2 жыл бұрын
Mmmmmm
@jameszambezi6948
@jameszambezi6948 Жыл бұрын
Iweyo ndi otsilika kapena ayi
@mathewsthomas1699
@mathewsthomas1699 3 жыл бұрын
Koma uziwa bwanji kuti mkazi uyu ndiwosirika
@softzandani3163
@softzandani3163 3 жыл бұрын
Koma mumayamba mwafufuza kaye kapena ?
@duwasemoyo8984
@duwasemoyo8984 3 жыл бұрын
Eya it’s true
@johanalberts8339
@johanalberts8339 3 жыл бұрын
😂😂😂😂
@suwedilawrence9622
@suwedilawrence9622 3 жыл бұрын
Ukunama ayaya inu bwanjiii
@zakeyophiri4308
@zakeyophiri4308 3 жыл бұрын
Iweyo bwanji
@giftchinyamamtombosola2424
@giftchinyamamtombosola2424 3 жыл бұрын
Nde mwat tiziona kaye ngat mkazi ali otsilika uona bwanji? Osangonena kut mchitidwe ogona ndi akazi a eni uthe bwanji? Unprofessional reporting
@user-hp8du2lx3z
@user-hp8du2lx3z 9 ай бұрын
Zaziiii
@jeydenstevenumer6988
@jeydenstevenumer6988 3 жыл бұрын
kkkkkk lrene 😂😂😂😂😂
@sostenlankhulani7289
@sostenlankhulani7289 3 жыл бұрын
Ndinu opusa kwambiri! Mumatiuza nkhani ya ayaya yet you haven't researched on it! Makape, improve your garbage
@johanalberts8339
@johanalberts8339 3 жыл бұрын
😂😂😂
@innocentngogwe
@innocentngogwe Жыл бұрын
Ayi sibwino umenewo siumuthuyi
@WizeyManyozo
@WizeyManyozo 15 күн бұрын
Aaaa tiziona bwanji kt. Ndosilika mm nkhan ya zavu zimaveka kt. Mzonama aa mangofotokoza n nokha km zinthuzo simaonesa atolankhaniw. Alikut aaa komaso kufotokoza nkhan kumakuvutan inu aaaa
Magic trick 🪄😁
00:13
Andrey Grechka
Рет қаралды 57 МЛН
Sky News Breakfast: The latest from the Middle East
3:04:51
Sky News
Рет қаралды 29 М.
Live: Protest in Chicago by Pro-Palestine groups outside DNC call for Gaza ceasefire
3:43:26
KULONDOLOZA ZA IMFA YA AGNESS KATENGEZA...@MibawaStudios
18:50
LIKI-LIKI Ladies
Рет қаралды 45 М.
phuzitsi wina wa school yosula aphuzitsi wapeza nkazi emwenso ndi phuzitsi akupanga zadama.
16:28
MWANA WA M'BUSA APHEDWA KOKABA (part1)
11:38
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 41 М.