Koma akutumaniwo Ali pa chintchito choyipitsa ena. Ndege ikaphulitsidwa imaoneka chonchija? Ukuti yaphulutsidwa koma onse osafa ndiye mumakong'ontha kuti afe enawo kupha umboni ukuuza ana? Ukundiuza kuti ndege imeneija inatera pa malo ngati ameneaja? Mwafatsakotu ku Botswana ko mpaka mumalankhula ngati wokhudzika ukufuna kugwetsa wina. Guys olo mutaipitsa chotani ngati MCP ikudzawina idzawinabe mufune musafune chifukwa ifenso we have the brains to reason. Keep on decampaigning MCP but the results will be against your will and that will bring instability to this beautiful nation.
@user-xx4jb9se3z7 күн бұрын
God is with you Mr mtanyiwa .asiyeni awa mcp ikupita basi
koma munthuyu kwathu asabweleko ndikapha Ngati njoka manyi Ake chakwelayu😮😮😮😮😮
@user-pt8wb4vw6r8 күн бұрын
Antanyiwa mwasala pang ono kulangidwa nmulungu mabozawo musiye mulungu wakwiya ndi maboza anuwo mulungu simtanyiwa ayi mau wogothawo anthelathu mlape
@meganabigail-ye7fw8 күн бұрын
Munya nonse a Mcp kuphatikiza ndi president wanuyo mumaona ngati kupha munthu chophweka Muziona ngati si iwe yembekeza Ana kapena azukulu ako they will be in for it, Mwazi mwazi mwazi n mwazi again every where mukuona ngati mulungu angakondwe nazo.