MCP YAKOZANSO UPANDU OLEPHERETSA MADEMO OMWE MALAWI FIRST AKONZA

  Рет қаралды 8,596

TIDZIWE TV

TIDZIWE TV

9 ай бұрын

TIDZIWE TV

Пікірлер: 32
@IbrahimDailes
@IbrahimDailes 9 ай бұрын
Wina aliyese osauka amene mane a kt chakwela ndi boma lake lili bwino ameneyo amagwa khunyu srs mutu siukugwila (shit)
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Mwaswela bwanji achimwene anga Kodi nkhanga zilipo? kkkkkkkkk I like it nkhanga zaona
@ashikalam8616
@ashikalam8616 9 ай бұрын
Big up Big man ❤😅
@user-nz8mq4ff3e
@user-nz8mq4ff3e 9 ай бұрын
Nkhangaaaaaaaàaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaasaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaàaaaaaaaaaaassssaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaàaaaaaaazaoooooooooooooooooooooooo oooooooooooooooooooooonmwadzuka bwanji a Malawi anzaga kulikonse kumene muli Lelo pa 4 th october this Mr tanyiwa Limpopo AFM Rodio
@BILLYMACHOMBE-fw5nn
@BILLYMACHOMBE-fw5nn 9 ай бұрын
hugs great to Great
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 9 ай бұрын
Nice
@user-wd7lk7nx7m
@user-wd7lk7nx7m 9 ай бұрын
Chikwera galu weniweni
@ArmandosebastiaoLano-yw5iv
@ArmandosebastiaoLano-yw5iv 9 ай бұрын
Fire
@alickalick6509
@alickalick6509 9 ай бұрын
Chakwera amawona ngati ndizophweka kukhala otsogolera dziko apa waziwonera yekha basi akapume sitikumufunanso amutengenso Chilima onse achokepo
@MathewsMANDUTU-lh6oo
@MathewsMANDUTU-lh6oo 3 ай бұрын
Mvuto ndife amalawi kutengeka,,,,, muzadya katutu,,, thumba la fertilizer 4,500,,, passport 14000,,, ndi kutengelani ku Canaan,,, Maka ndi utsogoleri wa chakwera, ameneyi ntchito zake ndi zitatu monga satana, kupha, Kuba, ndi kuononga. (Capetown south Africa)
@stevejizaremu3396
@stevejizaremu3396 9 ай бұрын
😮achakwera gate out
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 9 ай бұрын
Ulemu wanu Sir...
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Antanyuwa mulungu akusogoleleni
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Tadzuka bwino kuno ku Zambia mumakwana antanyuwa
@paulgodfrey3361
@paulgodfrey3361 9 ай бұрын
Akunama nafe
@StanleyTembo-fl7cc
@StanleyTembo-fl7cc 9 ай бұрын
Wabaya pamenepo kkkkkk ndinu dolo
@lamecknyadani1905
@lamecknyadani1905 9 ай бұрын
Yambisani chipani basi... Malawi muno sitikuonamonso ozamuvotela🤣🤣🤣🤣
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Zilipo nkhanga,,
@Shaffi-hh1gt
@Shaffi-hh1gt 9 ай бұрын
❤❤❤
@ImraanJafali-dk7rg
@ImraanJafali-dk7rg 9 ай бұрын
Kwavuta kwambli ku dziko lakwathu mmmm
@EnochRickson
@EnochRickson 9 ай бұрын
Ku MCP kwadzadza ma coward ndi kuba komans kupha...ana a mahule....Malawi 1st ndi 1 basi
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 9 ай бұрын
Malawi crocodile party, pachionngolero,
@Goliath461
@Goliath461 9 ай бұрын
Chakwera ndi opanda anzache chiyenda yekha
@user-ib7vr3zm2f
@user-ib7vr3zm2f 9 ай бұрын
Achita bwino kupanga chiwembucho,ndipo mcp ndi moto,tiyeni tose tikalepheretae azikachitira kwina kuno ku lilongwe zopusa sitifuna
@HashimKazembe-eq4yi
@HashimKazembe-eq4yi 9 ай бұрын
Ndikakufinyila konko galu iwe
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 9 ай бұрын
Boma ili ndi manyaka, nsanza zenizeni
@amadichembe4068
@amadichembe4068 9 ай бұрын
Ndina dabwa Inyo nkhanga sizikumveka nati kapeba zauluka
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 9 ай бұрын
Tiyeni waka uko vindele imwe walomwe
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 9 ай бұрын
Iwe nawe ni galu nadi , palije icho ukupulikapo apa
@user-mv1er5zr7e
@user-mv1er5zr7e 9 ай бұрын
Kodi iwe sukuwonA Mene zithu zilili Ku Malawi basi wuziti vindere
@kantionsankhulani
@kantionsankhulani 9 ай бұрын
M'makwana muzangosowa
@BILLYMACHOMBE-fw5nn
@BILLYMACHOMBE-fw5nn 9 ай бұрын
See
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Was ist im Eis versteckt? 🧊 Coole Winter-Gadgets von Amazon
00:37
SMOL German
Рет қаралды 34 МЛН
The day of the sea 🌊 🤣❤️ #demariki
00:22
Demariki
Рет қаралды 105 МЛН
AMENE ALOWE M'MALO MWA ACHILIMA KU UTM/ NKHANI
15:37
HOT 265
Рет қаралды 2,4 М.
Kodi Baibulo limene timawerenga ku Malawi kuno linachokera dziko lanji?
15:34
Zamanyazi mukafukufuku  wanimfa ya saulosi chilima
5:45
Nthambi Malawi
Рет қаралды 13 М.
Tanthauzo la Mayina a Malo osiyanasiyana ku Nyasaland.  (Now Malawi)
18:09