Nkhani Yomvetsa chisoni Nyamata waphedwa Chifukwa Cholowa m'munda

  Рет қаралды 23,608

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

Nkhani Yomvetsa chisoni Nyamata waphedwa Chifukwa Cholowa m'munda

Пікірлер: 58
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 2 ай бұрын
Hmm Koma dziko ndilozunza ambuye atichitile chifundo ndithu
@user-nz5ts9zp2l
@user-nz5ts9zp2l Ай бұрын
Apa chilungamo chiyende ngati madzi ,apolice amene munapanga zimenezo muli pompano mukunvesera nkhanizi ndikuwuzani chinthu ichi mukachigwilenso chigawengacho chilandile sentesi ,mukugwila ntchito yaboma malamulo aja akuti opha nzake aphedwe Ali kt ? Nzimu wamunthu osalakwa ukulila kunthaka, inu apolice lamulo lotulusa chigawengacho munalitanga kt? Ndalamazo munalandilazo mukabweze atakhala mbale wanu mungatani ,Malawi wanthu wantendere ,koma uwu sintendele musatilankhulise udyo apa kabwezeni ndalamazo chigawenga kachigwileni chilandile sentesi basi apo biiiii oba nkhuku ose kundende atuluke alive milandu,ambuye mulowerepo apa
@ElizabethKhosa-gx3wt
@ElizabethKhosa-gx3wt Ай бұрын
Zovesa chisoni analimuthu oti sanapange songolo lamaphuzilo Ake Koma Malawi 😭😭😭😭😭
@ChiphaHara
@ChiphaHara Ай бұрын
Kutengera malamulo kumanja osayiwala Aliko yehova kumwambaku mkaziwona
@user-ip6pt3rw7f
@user-ip6pt3rw7f Ай бұрын
kozani mwakabisila chigawengacho
@CiprianoBindissone
@CiprianoBindissone Ай бұрын
Dziko lopanda nkhondotu ili ntenderewo ndiuti mpake amakutukwanani jb wanthu opusa
@motelewabanda8724
@motelewabanda8724 2 ай бұрын
Koma kwbir ndaona kut apolice masiku ano akuyanja ndalama not chilungamo kma osataya mtima mulungu alipo kumwambaku amenya nkhondo inu muli cheteee zikomo
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Ай бұрын
Inuyo akubanja mukawauze a police kuti munthu mwamutulutsa mulandu osakambayo ife timupitira kunyumba kwake tikamuphera konko nayenso apite diso kuli pa diso pamenepo mpanene angadxiwe kuti sakukwanitsa ntchito yao,musagonesoyi akubanja muchite machawi, mukamupha akakakusekerani mukawauzekuti analinso wamisala finish ku malawi kilibe police
@TadalaTembo
@TadalaTembo Ай бұрын
Zoonadi
@APOSTLEBJ-tc5fp
@APOSTLEBJ-tc5fp 2 ай бұрын
There is no justice in malawi 😢😢😢
@BaxterChipofya
@BaxterChipofya 2 ай бұрын
God is able chilungamo chioneka pamenepo
@user-kx3kg1rn8n
@user-kx3kg1rn8n Ай бұрын
A police akwathu anazolowera kulandira zimphuphu amawamanga anthu osauka olemera mola Ake kulibe kupolice
@marthaalichangamile1424
@marthaalichangamile1424 Ай бұрын
Akubanja nkhani musayisiye chomcho apolice azolowela kudya ziphuphu akuma tulutsa zigewenga chifukwa cha ndlama funani lawyer basi
@SuwemaHafizaayami-gy2hn
@SuwemaHafizaayami-gy2hn Ай бұрын
Sorry for the loss mama zosakhala bwino koma abale dzikoli iiiiii😢😢😢
@morgansilungwe
@morgansilungwe Ай бұрын
pakuchitika zachinyengo mama.kasumeni kuma bungwe ndi ma lawyer aboma aja akuthandizeni.dziko lathu linawola koopsa maka kwa anthu osauka
@user-ks3uw3pq7d
@user-ks3uw3pq7d 2 ай бұрын
Ndawona kwa thu after long time
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d Ай бұрын
Kayiperekeni nkhani ku mabungwe osachedwa apa ayi
@APOSTLEBJ-tc5fp
@APOSTLEBJ-tc5fp 2 ай бұрын
Malawi police God will punish you and judge you harshly.
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 2 ай бұрын
Akubanja pepan kwambr km limban mtima muitane a police ku headquarters ku area 30 Lilongwe akuthandizen nawonso akalephera pitan ku court direct.Musalole wa police kukupusitsani mu njira iliyonse .
@HenryGulani-fq5js
@HenryGulani-fq5js 2 ай бұрын
Kom Ku Malawi kwachuluka katangale ine ndili Joz ndichitapo Kathu ndikuimbilani chimene chikufunika kungomuona wamodziyo ndi kumutema Tema batsi
@RoyNamwili
@RoyNamwili Ай бұрын
Police ya 2020 mpaka pano ziphuphu zokhazokha. A khoti atulutsa bwanji chigawenga mu ceil ya police before hearing? Mupite Kwa ma lawyer aboma muthandizidwe.
@PeterChilombo-ou2cd
@PeterChilombo-ou2cd 2 ай бұрын
apolice nda galu asanamizire akhoti iwowo apolice ndamene akuononga dziko lino chifukwa cacinyengo
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 ай бұрын
Sorry May his Soul Rest in peace.koma nkhaniyo sinayende bwino ai
@OliverNkhoma
@OliverNkhoma Ай бұрын
Weruzani nokha munthuyo chifukwa a court samagamula mulandu usalowe court
@richardmalowa821
@richardmalowa821 2 ай бұрын
Mabungwe ndiamene akhale apolice panopa apolice ntchito sakuikwanisaso opha nzake aphedwe basi
@user-li4fd3zg9w
@user-li4fd3zg9w 2 ай бұрын
Tangompitirani patali ameneyo nayeso apite azibale ake ave kuwawa ngati momwe mwavela inu amati choipa sabwezela km apa kubweza basi ngati kuli kupsa tikakumana kugahena konko
@LukaAron-el5qh
@LukaAron-el5qh 2 ай бұрын
Inu akubanja musalole zopusazo a police adya ndalama nkhaniyo osayisiya choncho ai bama yachakwerayi itithesa ntundu osalora ai police chilungamo kulibe
@NumbDee
@NumbDee 2 ай бұрын
Malawi dziko lomvensa chisoni . Moyo wamunthu kupita choncho koma chilango palibe zoona?
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 2 ай бұрын
Nkhani imeneyi silongosoka yalowa chinyengo Pakhutulidwa ndalama zankhani nkhani KUYAMBIRA kuntunda uko Chakwera kumatsika mpaka pansi kulibe chilungamo malamulo lero Ali pansi pa ndalama kwathesedwa milandu ikuli ikuli yakusazakadza chuma Cha boma kuikirana kumbuyo anthu akuba chifukwa anaba limodzi ndi bwane ndende ndi ya ife osaukafe ingowasiyani
@SamsonKunthani
@SamsonKunthani 2 ай бұрын
Ineyo mpaka nditamubaya Police officer yo kuti tione zomwa.apolisi andipanga.
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 ай бұрын
Police yathu masiku ano inasintha ikukondera ambanda ndi akupha, nkhani yanuyi siyoyamba,zinachitikanso ku Blantyre chaka chomwechino, driver wa lorry anaphedwa, chifukwa chokoza m'munda mwa chimanga. Mpakana pano okuphayo akutetezedwa ndi aPolice. Ndiye a Malawi tiyeni tilimbe mtima. Chilungamo kulibe.
@user-zv3cy2xj5p
@user-zv3cy2xj5p Ай бұрын
Ingomukonzani nokha ,mukuchedwanadzo zodandaula
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 2 ай бұрын
Mmmh koma munthu akuopsa kupsa kuposa Chinyama chakuntchile
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v Ай бұрын
Komatu mukamapha adzizanuwo mudziziwa kuti boma lanu likulamuliraro lichoka musamale kwambili
@terezamponda6382
@terezamponda6382 Ай бұрын
Chisoni
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Akaweluza ndimwini bas
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 2 ай бұрын
Dziko lathu lalowa chisawawa chifuwa cha kuvuta kwa Ndalama komanso kusayenda bwino kwa Boma.
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Bola akanayika lamulo loti opha nzake nayenso aphedwe, chifukwa zimenezi zikuchulukira. Nanga munthu mpakana akamuphe chifukwa cha chimanga? Koma Malawi pano satana akuyenda ndi mapazi Kodi anthu amamupha nzawo kuyiwala kuti nawonso adzapita komweko, Koma zachisoni ndithu MHSRIP
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 2 ай бұрын
Khanza zimenezi bwanji guy's
@MisheckAselo
@MisheckAselo 2 ай бұрын
Pano ngati munthu wakulakwira police sikufunika kuigwiritsa ntchito kumangopanga zapamtundu
@EvelynWilliams-ec5fx
@EvelynWilliams-ec5fx 2 ай бұрын
😢😢😢😢😢😢
@user-ku2fe8nb3j
@user-ku2fe8nb3j 2 ай бұрын
Uku nde kwathu mangochi m,bomamo,,,Koma pepani
@user-sr6hc3pv8o
@user-sr6hc3pv8o 2 ай бұрын
Zangovuta akanangopeza loya
@user-zv3cy2xj5p
@user-zv3cy2xj5p Ай бұрын
Koma ndikuti kumeneko
@APOSTLEBJ-tc5fp
@APOSTLEBJ-tc5fp 2 ай бұрын
Apolice amange anthuwa chonde
@user-pw1kl3vo5d
@user-pw1kl3vo5d 2 ай бұрын
Craction yafika pochititsa manhazi kumalawiko
@EuritaDeric-fz3ds
@EuritaDeric-fz3ds Ай бұрын
Apolice sakugwira ntchito yawo mmmmm
@ziyamikanmakowa5981
@ziyamikanmakowa5981 2 ай бұрын
Apolice anasiya ntchito yotetezela anthu akonda ziphuphu
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 2 ай бұрын
Zosakhala bwino
@GidionJonas-sr4zr
@GidionJonas-sr4zr 2 ай бұрын
Òooo my god😢😢😢
@RedsonRichard
@RedsonRichard Ай бұрын
😢😢😢😢😢
@user-tt1kv3oh7c
@user-tt1kv3oh7c 2 ай бұрын
😢😢😢😢
@user-ds3co5sm4k
@user-ds3co5sm4k Ай бұрын
Mmmmmmmmh 😢😢
@user-vg1lj5gs4z
@user-vg1lj5gs4z Ай бұрын
Money talks okey
@user-pj3qi7gb3s
@user-pj3qi7gb3s 2 ай бұрын
A police adya ndalama
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 2 ай бұрын
Mzimu wake uwuse mumtendere. Vuto lamakhoti akumalawi amayikila kumbuyo munthu olakwa pamene olakwilidwa ndamene amakhala kundende, AMBUYE TITHANDINZENI zolengedwa zanu tatha nzeru.
@GodfreyzigambachavulaChavula
@GodfreyzigambachavulaChavula Ай бұрын
Tiyeni tiwone khani iyo yili pa yona 1 vs 1 chifukwa yona akatumika na chiuta , kweni yona . akazemba chiuta akamu ona kweni wathu wakamuwona yaya. Akaluta nakukwera ngalawa kufika pakati panyanja chiphepo chikakula. Wakapephera yona ndiyo akapangisha kuti wathu washuzyike. Wathu waka pephera chomeni kuchema chiuta. Yona akawa kuti agona katuteni akaluta Paso akasanga yona gagona. Akamfumba kuti kuchitachi, wanyako wakupemphera , yona akari pepani , vyose ivi ndapangisha ndine, IPO ine ndine mdipanye magi .pala tingalutirila palikhani yinandi .khani iyo njakuzomerezya kuti ndananga ,chiuta apulikenge na kugowoka ameni
@user-xx7mk3fw8v
@user-xx7mk3fw8v 2 ай бұрын
Very bad
Rudo Ibofu, Dickson And His Older Lady | Issues Pane Nyaya
1:00:59
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН
УГАДАЙ ГДЕ ПРАВИЛЬНЫЙ ЦВЕТ?😱
00:14
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 3,8 МЛН
🤔Какой Орган самый длинный ? #shorts
00:42
Akuchita kusankha anthu omanga; Chilungamo kulibe ku police
10:42
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 7 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 106 М.
Türkmenistan | Jenaýatçy Hökümete Hyzmat Eden Günä Geçileri
15:32
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 187 М.
Ehe le! Mipui thinrim in Dr chhuak tur an dang riap mai le || Report Kimchang
20:50
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН