No video

Palibe Zogulitsa Chipani Ku Mitambo - Shaggy One

  Рет қаралды 2,934

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

On Nyasa VoiceBox, Shaggy, a member of UTM, stated that UTM is not up for sale. He warned that if anyone attempts to sell off the party or engage in similar actions, there will be serious consequences. Shaggy emphasized that UTM will remain UTM and will not be infiltrated by opponents from outside due to the greed of internal members.
Ku Nyasa VoiceBox, Shaggy, yemwe ndi membala wa UTM, adati UTM siyikugulitsidwa. Iye adachenjeza kuti ngati wina ayesa kugulitsa chipanicho zotsatira zake ayamabanapo. Shaggy adanenetsa kuti UTM ikhalabe UTM ndipo sidzalowetsedwa ndi otsutsa ochokera kunja chifukwa cha umbombo wa mamembala amkati.
#malawi

Пікірлер: 29
@TressLuka
@TressLuka Ай бұрын
Zoona Bigy osanyengeleraaaaa. Atsogoleri akhare mzika zamu UTM basi ( Mai Chilima kapena Akweni . Boma titengaaa! Osaopa, Osafooka, Osatopaaaaaa ❤❤❤. Bravo Bigyyyy!
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Ай бұрын
Mwapenga inu kozani kuchipani kwanuko osati muzidana ndi dpp mwalo monena amene anagwesa ndege kuchikangawa
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk Ай бұрын
Kwa ine Mary chilima ndilibe naye chifukwa coz president wathu afa mosayembekezela apo ayi mayi kaliat atitenge basi zinazi ayi
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Akaliyati ndi phuma sangawine
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
Kuyankhula ndiye kumeneko, amene alliance, UTM ikhale patsogolo osati tidzingoperekeza.
@theochibwana
@theochibwana Ай бұрын
Muyambe kaye mwawatenga a utm omwe atsala ku mcp.....musanamizile dpp,zake zili clean
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q Ай бұрын
Sure shaggy sukunama sitiimva
@fortunekamdumli-xy5zn
@fortunekamdumli-xy5zn Ай бұрын
Bola kaliyati than Mary chilima
@HarryMsudzula
@HarryMsudzula Ай бұрын
Mukayamba izizi zomabwera ndi mavoice ngati zigawenga kumatulusa mau opseza like this tikutulukani mwayamba zachamba chipani ichi chikufunika munthu wachikoka koma mukachiumira mukhala choncho ndidzimau ngati am the chair with aLimbe depot zamphamvu pano ayitu zauchigawenga ayi
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Akaliyati ngati akufuna kubwelela kudpp angopita okha asagulisi chipani chifukwa chansanje poti ausi ndi avoice
@ziwani3682
@ziwani3682 Ай бұрын
Uyu WA mcp uyu
@user-os4iz4tn9z
@user-os4iz4tn9z Ай бұрын
Ngati uli mnyamata utha kupita ku convention and mentality yoti ya umwiniyi ikuonetsa kaumbuli wez be civilised like Fredo ngati uli mnyamata coz iwenso ungathe after all UTM siingawine payokha ndipo eee umbuli ndi nthenda
@user-nb8wg3fh4u
@user-nb8wg3fh4u Ай бұрын
Akugula a mcp iwe
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Musalimbane ndi dpp inuyo a utm mwagwa nayo bas
@user-ie4ci3zh7j
@user-ie4ci3zh7j Ай бұрын
Ulibe dzelu unachoka kwabwino munapita kwa kupha, ineso ndi nyamata
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
A utm timakupasani ulemu tsopano mukayamba kulimbana ndi dpp mukunya ndi inu ana
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Inu a utm musalimbane ndi dpp mulimbane ndi amene anagwesa ndege aja dpp musalimbane nayo inuyo ndi ana dpp ndi akatundu
@user-ie4ci3zh7j
@user-ie4ci3zh7j Ай бұрын
Nde unthengawo ukuuza ndani wamisala iwe, mesa munagulisa kare ndi maunduna aku mcp usatinyanse ndi uchinyamata wakowo, chipani chilibe anyamata ndi chiti? Pitani ku school kaye mukaphuzire kaye kenako uzalowe ndare
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
😂😂😂😂kusokoza😂
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Ай бұрын
inu musathe mawu .and muxarodxe chara ku Dpp .roxani chara ku mcp komwe wapha chilima
@user-mj2te7vl6p
@user-mj2te7vl6p Ай бұрын
Imila iweyo please
@user-gn3gy5iq5x
@user-gn3gy5iq5x Ай бұрын
Unadzuzidwa pa zifukwa zako koma DPP ilibe nkhaza koma iweso ndipanja ukusiya boma la nkhaza ilipoyi lokupha ... Zimene ukuyakhulazo ungozitembenuza Kuti unene boma la chakwera uone uzuzidwe koposaposa mwinaso kuphedwa kumene
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 Ай бұрын
Koma guys tizikozana kuima panokha simungawine. Chifukwa kumakandulo kunja mosayese kt mukukhala nokha nokha zipani dzina zikubwelaso kuzaipasa moto kut mcp iziva kuwawa. Ndye mukawona gulu mwati ndi athu anu Iiii
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere Ай бұрын
Usadzipisitse mphwanga DPP ndichipani chachikulu ndipo chiribe any pressure from UTM Ngati Pali Ena omwe achoka Ku DPP kubwera Ku UTM akufunako udindo kumene ndethananawoni Moti kumanyoza kapena kutukwana DPP sizikupindulirani, komaso musaiwale ma members Anu Ena muwasiya Ku MCP ndepangani zoti amenewo mukawatenge mukhale pamodzi mukonze chipani. Komaso malangizo anga nawe, Pangani zomwe mungathe Ngati UTM Koma Mary Chirima musamuikemo chimenecho ndichibwana,sankhanani nokhanokha osati Mary chonde mumulakwira kwambiri
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
Koma Mary chilima mumuphetsatu uyu Komanso chipani sichaku banjatu
@JonathanMsiska
@JonathanMsiska Ай бұрын
UTM 2025 ikutenga Boma mosavuta Inu mutsathamangile kujoyina chipani chili chose ayi Inu mukhale Mutu ofunayo ajoyine Kwa Inu akhale m'chila chifukwa anthu povota adzapepetsa maliro a Chilima nde malirowa ndi a UTM osati zipani Zina ayi Mary Chilima ndi Akweni afatse bwino bwino enafe kwathu nkuwuka zinthu basic dekhani Boma mutenga.
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
Malodza 😊
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Ukubwebwetatu iwe
@JamesLongwe-qz9fd
@JamesLongwe-qz9fd Ай бұрын
Choka garu iwe😅😅
Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN (Part 2) - Pastor G Shumba
19:32
Nurse's Mission: Bringing Joy to Young Lives #shorts
00:17
Fabiosa Stories
Рет қаралды 4,1 МЛН
КТО ЛЮБИТ ГРИБЫ?? #shorts
00:24
Паша Осадчий
Рет қаралды 3,7 МЛН
Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN - Pastor Shumba
16:55
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 7 М.
Bambo Wamzeru Sangapite Ku Bawo Mnyumba Mulibe Chakudya - Mr Abdull
9:11
Chakwera V Mutharika: 2025 Kuli Gule - Redson Munlo
23:01
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 9 М.