Part Two: Dr Cassim Chilumpha | Kung'alula Chilima Ndi Lazarus chakwera

  Рет қаралды 33,328

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

EXCLUSIVE: Part Two | Dr Cassim Chilumpha Interview 2024

Пікірлер: 140
@frankjamesmanere9470
@frankjamesmanere9470 2 ай бұрын
From Chipiku to president, ngakhale Dr Chilumpha adabwa
@stanleykaludzu-bm4pm
@stanleykaludzu-bm4pm 2 ай бұрын
Kkkkkkkkkkkk
@martinsailesi1731
@martinsailesi1731 2 ай бұрын
Nothing but truth Long live Dr chilupha
@MafunaseKamoto
@MafunaseKamoto 2 ай бұрын
Bwana Cassim Chilumpha is a genius...Mwatiuza chinsisi chimene dziko lathu likuvutikira pa chuma
@user-mr3vw1ym3r
@user-mr3vw1ym3r 2 ай бұрын
Mkulu uyu akafuna kuyankhula chilungamo sanjenjemeratu, long live Dr Cassim Chilumpha.
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 2 ай бұрын
Well spoken with good experience
@YusufuKaifa-fr4wt
@YusufuKaifa-fr4wt 2 ай бұрын
❤❤❤ God bless you for love this our malawi
@JohnPetro-vv3er
@JohnPetro-vv3er 2 ай бұрын
Malawi need people like Dr chilumpha very brilliant
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 ай бұрын
Waoooooooo mr Chilumpha.Now. U are Speaking God bless you
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Very true Mr chilupha, chilungamo chimawawa inu mmalifunila dzikoli zabwino.. 🔥🔥
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 2 ай бұрын
Kuyakhula kwa bwino dr cassim chirupha❤❤❤
@PatrickNamakhoma-zm6kq
@PatrickNamakhoma-zm6kq 2 ай бұрын
he seem to be a good and experienced leader. alibe mbiri yakuba
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
I love ❤❤ Dr chilupha chakwela ndiosakwanila Pau president zoona
@user-ql3of8rf4z
@user-ql3of8rf4z 2 ай бұрын
Azathu olilanu 😂
@user-oc6xd4tv9l
@user-oc6xd4tv9l 2 ай бұрын
Following 🎉
@Harlod5566
@Harlod5566 2 ай бұрын
Uyu nzeru zirimo ndithu. Ndipo alibe nkhwidzi ndi munthu koma Chilungamo chokhachokha. Sungalamulire bwino opanda experience (UKADAULO) Walongosolanso bwino za chisankho ndi zina zambiri. Wa nzeru akuvomereza.Bingu anamumanga komaonani akuyamikira ng'ono wake Peter Muthalika. 🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔❤️👍
@AustinChikaoneka-ow2rv
@AustinChikaoneka-ow2rv 2 ай бұрын
Come on Kaka Chilumpha you are the Leader.
@PreciousChizonga
@PreciousChizonga 2 ай бұрын
I support your opinion Koma zoti pali Bola mwawiliwa ndiye kwaine ai Peter kulekerera zinthu two much ngati chakwera yemweyunso ndiye sindikusiyanitsa ndianthu okhutitsa mimba zao kuiwara udindo .
@user-gf6eh9ms5i
@user-gf6eh9ms5i 2 ай бұрын
Dam truth DR Chilupha i love this
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 2 ай бұрын
Apayu Legend nde mwayankhula momveka bwino okumva wamva
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 ай бұрын
Thokozani chiwaya you're doing the best man kept up this what we want to here man
@user-xb4fo7tk6b
@user-xb4fo7tk6b 2 ай бұрын
Thank you so much bwana, it means a lot to me
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o 2 ай бұрын
He is speaking the truth, respect
@user-co3ws7sw8j
@user-co3ws7sw8j 2 ай бұрын
That's true Kuvota kawiri ndigwelo lamabvuto onsewa,
@Mickeykasambula265
@Mickeykasambula265 2 ай бұрын
Chilumpha iweyo ndi dolo 🔥
@EricKaikhediKhozalimoChirambo
@EricKaikhediKhozalimoChirambo 2 ай бұрын
I have always been worried about the bill for the entire electoral process.
@JamesChigaru-fg7tc
@JamesChigaru-fg7tc 2 ай бұрын
Long live dr
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Reality Mr Kaka
@LongiMtimabii
@LongiMtimabii 2 ай бұрын
Long live dear father
@sShamus-dj4zq
@sShamus-dj4zq 2 ай бұрын
Cassim he's a true leader
@georgemponda
@georgemponda 2 ай бұрын
This is true.
@user-ie4ci3zh7j
@user-ie4ci3zh7j 2 ай бұрын
Ameni ur talking we made mistakes to vote chakwera
@wisemanbanda8465
@wisemanbanda8465 2 ай бұрын
The man is genius ...he's saying the truth
@chifundochinsampha4113
@chifundochinsampha4113 2 ай бұрын
Chilumpha kanangopepha kuti akuthetsele mulandu wako osati zopusa ukunenazi
@FrankBaison
@FrankBaison 2 ай бұрын
Chulungamo chimawawa😂
@juniormkandawire
@juniormkandawire 2 ай бұрын
Ali ndi mlandu wanji ndipo zopusa ndiziti galu iwe
@PreciousTepatepa
@PreciousTepatepa 2 ай бұрын
Very Genius
@HopeKhembo-qe7qs
@HopeKhembo-qe7qs 2 ай бұрын
💯% even a tac shop they need experience people what more a country
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 2 ай бұрын
I agree
@zumuweasly4773
@zumuweasly4773 2 ай бұрын
The guy is retiring so fast....
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 2 ай бұрын
Nde a chilumpha mene mwakalambilamo mungakhaleso sogoleli ayi ndithu
@roxtonmbawa8012
@roxtonmbawa8012 2 ай бұрын
Majority rules , chakwera was chosen by majority ife titani nanga, cassim chilumpha adamangidwa ndi Dpp he must wait dpp to come back
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 2 ай бұрын
Peter is good chakwela Achoke
@samuelsergio5343
@samuelsergio5343 2 ай бұрын
@ChristopherMasangano
@ChristopherMasangano 2 ай бұрын
Following
@andymasingajunior
@andymasingajunior 2 ай бұрын
A Chilumpha adziwe kuti Democracy is very expensive, 2025 tivotanso katatu, ndipo mavoti achiwiriwo tidzapanga nthawi ya mvula.
@LawgiverSolomon
@LawgiverSolomon Ай бұрын
Ndipo palibe adzafike 50+1
@user-nn5fz5wj6n
@user-nn5fz5wj6n 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@SupiaSamson-wb5ct
@SupiaSamson-wb5ct 2 ай бұрын
Wanena chilungamo cassim
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Kkkkkk koma kumeneko Panali pakamwa chabe 😂😂😂 koma chilupha auzeni
@timothymhone2340
@timothymhone2340 2 ай бұрын
Kkkķk komaso
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e 2 ай бұрын
Ulemu wanu bwana Chilumpha
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
Tiyamike Thokozani Chiwaya chifukwa ukuyesetsa kulondola aliyense, ndipo ukukwana Thoko. A Mr. Chilumpha ali ndi mtima okonza Malawi mosakaika, koma akhwima, koma akunena zoona.
@user-xb4fo7tk6b
@user-xb4fo7tk6b 2 ай бұрын
Thank you so much bwana, it really means a lot to me
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 2 ай бұрын
Chilungamo chabwanji ichii❤❤❤❤❤❤❤
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 2 ай бұрын
Uyu ndi munthu wa bwino Allah akudalitse mene mwayakhulilamu ndi zosowa kuyakhula chulungamo mwa uamikilaso Peter bingu pazomwe anachita pa Malawi
@user-xb4fo7tk6b
@user-xb4fo7tk6b 2 ай бұрын
@@ElizabethMajiga thank you so much Eli
@georgemponda
@georgemponda 2 ай бұрын
Akuti iyeyo sanagwilepo kuchipiku😂😂😂😂😂😂
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 2 ай бұрын
Zoona simukunama achilumpha ambuy akupatsen Moyo wautali
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 2 ай бұрын
Ambuye akudaliseni achilumpha mwanena momveka bwimo kwambiri
@user-jn2oc3cn3q
@user-jn2oc3cn3q 2 ай бұрын
Akuti ine sindimagwila ku chipiku km cassim chilupha
@Boijeezymakan
@Boijeezymakan 2 ай бұрын
Ndipo live
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h 2 ай бұрын
Wayankhulatu chilungamo
@OmarManjawira-ex1yc
@OmarManjawira-ex1yc 2 ай бұрын
Gogo Cassim Chilupha concerd with this government,,,, from Chipiku to President 😂
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 2 ай бұрын
Munthu you akuyankhula za nzeru ndithu ulemu wanu kuyankhula kuposa pulezidenti chakwera
@goodvisionmedia2023
@goodvisionmedia2023 2 ай бұрын
Mr kulakhula momveka kwambiri
@LuciasZepete
@LuciasZepete 2 ай бұрын
Chakwera alibe nzeru ataaaa
@HopeKhembo-qe7qs
@HopeKhembo-qe7qs 2 ай бұрын
A MEC mukamalandila za anthu oimilila like MP and presedent please ask for experience please
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv 2 ай бұрын
Achilupha mukunena chilungamo
@KinosiKameta-ud1ps
@KinosiKameta-ud1ps 2 ай бұрын
Chilugamo nchowawa
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
Mr. Chilumpha mukusongosola chilungamo, Chakwera ndi chilima sadakonzeke komanso ni mbuli pa kuyendetsa Boma. Chakwera amapusha Wilber lomaso crerik ku Chipiku basi. Sadziwa chilichonse za boma.
@Dorah-zl9uf
@Dorah-zl9uf 2 ай бұрын
😂😂😂
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 2 ай бұрын
It's true what chilumpha is saying, malawi we made a mistake
@user-wn2hm2dc8e
@user-wn2hm2dc8e 2 ай бұрын
Yes Mr chilumpha We made a big mistake
@user-ni4nw1ee2f
@user-ni4nw1ee2f 2 ай бұрын
Kuyankhula kwabwino
@patriciap.bandah3385
@patriciap.bandah3385 2 ай бұрын
Anthu wodziwa ndale ulemu wanu, awuzeni anthuwa sakudziwa chomwe akufuna lero lino ati akufuna mnyamata oganiza bho
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 ай бұрын
Chipani chonyansa, choipa, chamanyi==MCP
@user-fl7br3dw4h
@user-fl7br3dw4h 2 ай бұрын
Dzoona kaka chilungamo ndi chilungamo bas
@AndrewkhamisiMalinda-oi9lw
@AndrewkhamisiMalinda-oi9lw 2 ай бұрын
Osangopita kwa apule ndikukaunikila Pomwe akulephelapo bwanji
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 ай бұрын
Uyu ukalamba wamufikadi mmafupa ndithu. Zoti Chakwera was leader of opposition sakudzika? Ku america akukutchulako did Trump hold a public office before the presidency?
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r 2 ай бұрын
Chakwera ndi Tambala Party ndi Anthu opanda Phindu
@user-ju7vc1uv7m
@user-ju7vc1uv7m 2 ай бұрын
Atupele muluzi an akambapo kale
@odarm4334
@odarm4334 2 ай бұрын
Akuti "sindimagwira ku Chipiku iyai" 😂😂😂😂
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 sanamangeko ndi toilet yomwe ku assembles 😂😂
@FrankBaison
@FrankBaison 2 ай бұрын
Zoonadi chakwera sakukwanila kukhala president
@HopeKhembo-qe7qs
@HopeKhembo-qe7qs 2 ай бұрын
Vuto laku Malawi oimba Ati akhale MP.azisudzo MP
@jonathanNkhata-nl2de
@jonathanNkhata-nl2de 2 ай бұрын
Akut simagwira kuchipiku
@user-se8ze3fn3o
@user-se8ze3fn3o 2 ай бұрын
Chipiku boy 😅
@TrinityManeya
@TrinityManeya 2 ай бұрын
Zamzeru kwambili
@pierrekhabwiri3841
@pierrekhabwiri3841 2 ай бұрын
Vuto lathu nd lot anafe sitimamvera sitimamvera akuluakulu kuteroko or apapa tikimva ngat mukut chakwera nd wabwino koma mmmmmhhhh mwa inuyo bwana muli mzeru koma ife omverafe mmmm
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 2 ай бұрын
Nkhalamba iwe unakhala 10 years unakwanisapo chani pa u vice president
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw 2 ай бұрын
Kkkkk so you can compare Malawi with USA mwaganiza bwanji kaka! Mwakalamba ingopumani akazi Anu Ali bwanji
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 2 ай бұрын
Kkkkl koma Zina 😂😂😂😂
@PaulNtonya
@PaulNtonya 7 күн бұрын
Mukunama kuti zikolino ndilosauka ndinunokhanokha anthu osakonda dziko lathu lino inukuwina rero mufunaso muremere kaye inundiabare anu apaparibewabwino
@ChikumbutsoPortpher
@ChikumbutsoPortpher 2 ай бұрын
Unakalamba
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 2 ай бұрын
Madala oona patali kwambiri
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 2 ай бұрын
No fundo iwe that's why anakuphatula Amuluzi then anaona bingo wamutalika
@EuniceSomanje
@EuniceSomanje 2 ай бұрын
😂😂😂
@danielmsowoya9107
@danielmsowoya9107 2 ай бұрын
Mwa inu muli magazi a UDF simunganene chilungamo baba
@charleskafodya7019
@charleskafodya7019 2 ай бұрын
🤐😛😛😛
@victorbanda9039
@victorbanda9039 2 ай бұрын
Chilumpha Kani ndichitsiru chomchi nde bwanji pitala wakoyo sanakupatse mabilion ukufunawo
@LotiBanda-uo5vy
@LotiBanda-uo5vy 2 ай бұрын
Chilumpha misala iyi
@lonjezomainjeni5803
@lonjezomainjeni5803 2 ай бұрын
Chilumpha ndi dolo amalawi timakhala ndi phuma koma next year achoka osadandaula
@audreymoffat1356
@audreymoffat1356 2 ай бұрын
Mau omwe anatichenjeza ndi kulozera pa debate aja ndi Atupere Muluzi ndi awa akupelesera ndi kaka
@danielmsowoya9107
@danielmsowoya9107 2 ай бұрын
Vuto mpira umayamba kuuona ukatuluka mu ground. Mwakhala m'boma zaka zambiri lero mwayamba kuona mavuto a anzanu
@wisktepani-bo3fw
@wisktepani-bo3fw 2 ай бұрын
Zoona ndithu taziona ndi maso bola mutharika
@MilikaKilion-tn1bn
@MilikaKilion-tn1bn 2 ай бұрын
From chipiku to president 😂😂
@user-bn3fg7sm2o
@user-bn3fg7sm2o 2 ай бұрын
Kulankhula mosaphyatila,zoona,zokhazokha
@OrtonKabbichi
@OrtonKabbichi 2 ай бұрын
Chilima analakwira a malawi chifukwa cha jelasi
@blessingsmangulama8442
@blessingsmangulama8442 2 ай бұрын
zala zathu zinatilakwisa. tingozidula basi
@cosmaskwalira-phiri4710
@cosmaskwalira-phiri4710 2 ай бұрын
Dr Chilumpha you also failed by not cooperating with your boss Bingu. You lost our trust from that time. Sounding frustrated now won't help you.
@GilbertKaliwa
@GilbertKaliwa 2 ай бұрын
Kodi iwowa angaloze, chiani chimene anapanga Ali mp ku chia munthawi ya udf I was there nothing Ata kukoza hot springs madzi mawir a
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 2 ай бұрын
Zoonadi ndipo muthalika
@wapenyapatali5849
@wapenyapatali5849 2 ай бұрын
Kkkkkk! From salesman kuchipiku to presidency 🤣🤣🤣
Chegutu : Ruvimbo wekuurairwa $100 onzi opfuka asati avigwa
1:03:06
THEY made a RAINBOW M&M 🤩😳 LeoNata family #shorts
00:49
LeoNata Family
Рет қаралды 43 МЛН
Slow motion boy #shorts by Tsuriki Show
00:14
Tsuriki Show
Рет қаралды 8 МЛН
Scary Teacher 3D Nick Troll Squid Game in Brush Teeth White or Black Challenge #shorts
00:47
A Simbi Phiri Akhuza Imfa ya Dr. Saulos Klaus Chilima
22:44
Zodiak Malawi
Рет қаралды 82 М.
Rudo Ibofu, Dickson And His Older Lady | Issues Pane Nyaya
1:00:59
ZOMWE ZIDALI KU BALAKA 🙌🙌🙌🙌25 July 2024
27:52
HOT 265
Рет қаралды 13 М.
MOSES KUNKUYU EXCLUSIVE INTERVIEW
56:13
Zodiak Malawi
Рет қаралды 27 М.
Cruise 5 with Rebecca Malope
39:09
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 29 М.
Leonard Mambo Mbotela PART 2 - The 1982 Coup
14:37
Jackline Lidubwi
Рет қаралды 169 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
LERO BON KALINDO WANG'ALULA NKULU WA ASILIKALI 26 July 2024
15:05
THEY made a RAINBOW M&M 🤩😳 LeoNata family #shorts
00:49
LeoNata Family
Рет қаралды 43 МЛН